Bro muli ndi luso and mukamaimba nyimbo zangati izizi mukhara ndi space yaikulu mu music industry chifukwa oimba amene tili nawo akumangoyamikira azimayi oipawa next project muzajambuleko ku studio kwathu muyeseso zina
Gaga you can do it again. Iweyo kusewero unadza kudzakhala. Waikometsa nyimboyi. Well done to you Condes nawenso umatha kuika massage pamodzi ndiwe katakwe. 😂🎉
Good song 100% taphunzirapo yemwe ukuti ndi wachikondi ndamene angachose moyo wako, si chigewenga chokha
Oimba koma ameneyu osati kumangoimba zochemelera akazi nyimbo koma imeneyi yopeleka uthenga
nyimbo iyiyi aaaa imanifikapo mbava inaba mwachulungamo osatiso monthawanthawa asaa
Finally....I've found the song
Uku nde timati kuimba...... Kip it up🥳🥳🥳🥳🥳🥳
What a song? Super, good, fantastic
There is heavy message in this song.keep it rocking bro😍
🎉🎉🎉❤nyimbo ilimwala
keep up good work ❤❤❤❤
Umakwana bale kuyimba kwabwino uku ine king Chibadula ndakunyadila ulemu wako❤❤
Nyimbo iyiyi imandisagalasa kwambili❤❤❤❤🎉🎉
❤❤❤❤ nice song
Nyimbo iyi imandiwadza kobas nice song
Eu não posso me cansar ao assistir essa música mesmo cem vezes, obrigado meu cara
You have no idea how crazy I’ve been looking for this song.
Nyimbo iyi olo nditawonera ka10 simandikwana nice
Uli ngati ine
you are a musician from above, I love u my man I have subscribed to ur channel pls give me more ok
Hmmmmm music that speaks,well articulated
Nyimbo ya uthenga iyi... keep it up g condes
Dyangu
Nice song
Umatha aise big up
Ndaikonda heavy,kuyimba modekha
nice one and I love the song
Nice song ndipo ndayikonda
Mumatha inuyo man
Agaga mumakwana 😂😂😂😂
All songs are great
I put my comment here because whenever you put your comment I should be reminded and come and watch it again
Bro muli ndi luso and mukamaimba nyimbo zangati izizi mukhara ndi space yaikulu mu music industry chifukwa oimba amene tili nawo akumangoyamikira azimayi oipawa next project muzajambuleko ku studio kwathu muyeseso zina
Avery senstive song which every can listern and get alesson
Keep going brother
mulungu apitilize kutukula luso lanu patsogolo
Ndidolo hvy kuyimba mozndkira hvy
Nyimbo yogwila mtima
Much respect to him, anaipha Fadah ❤❤❤🇲🇼🤝.
Gaga you can do it again. Iweyo kusewero unadza kudzakhala. Waikometsa nyimboyi.
Well done to you Condes nawenso umatha kuika massage pamodzi ndiwe katakwe. 😂🎉
funny how birds of the same feather find ways to help each other even without collaboration but separation to prove nothing matters
Great talent 🙏🙏🙏🙏
Nyimbo number one yamathandaudzo
Good song.
💯💪💪💪 music 🎵
In love with the song...❤❤ good job
Bro inu ndinu oyimba mwamva
Nice
No comment , keep it up
I can give you♾️….or let you take it for yourself without any restrictions ❤
Nice brother
Super story
Gaga mbava ya chisoni😅😅😅
Kuimb like Blessings chimangeni😭😭♥️♥️♥️♥️
Nice message
Project is very good keep it up
Thanks a lot
Nice,muli luso labwino
Nice song honestly
Nyimboyi muli luso, you will reach the maximum views so soon
This is music movie nice
Komande nyimbo iyi unaimba ndipo unaganiza
whatever you choose to create should never hurt another living thing…..
Who was hurt here?
Really songs ♥️♥️♥️♥️♥️♥️
Nice msg
Nyimbo iyi ndiyophunzitsa kwambiri
Powerful song
Uthenga upite mumalo ake 🤣
Kwa omwe amayembekedzera kuona galu atafa gather here😅😅😅
Nice one
Powerful keep it on 🎉
Good story
Eish nyimbo iyi
Mbambande 🔥🔥
Good song continue
Nyimbo yabwino kwambiri komaso yophuzitsa ngat ma Nigerian movies
nzeru tu inu
This fire bra ❤❤❤❤❤❤❤
Man you have the talent
Only that it wasn't promoted enough otherwise the song deserves milion views
Creativity plus talent
wakubayo amafunika kumugulira galimoto
😂😂😂😂😂😂 pamenepot
Hard music
Zoona
Mthano iyi ndaikonda fire fire mtchana
Iyiyi eeh
I like this song
Thanks
Keep it up
Katundu wabwino uyu.
Fire fir😮
Mwalamwala
creativity at its peak
Ndazikonda fadah
Great talent 🎉🎉🎉🎉
Great song bro
Fantastic
Nice song 🔥🔥🔥🔥🔥
Boa música adorei
Old but nice song
Fire fire fire fire
Nice massage
Real art
Dolo🎉
Yes right it happens
Good song
Nyimbo yabwino kwambili