Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Even ma Surname ake, Ngoziyankhuku eti🤣🤣🤣🤣
Osati undimenya kumati timenyedwa hahahahah Ching'asy
😂😂😂 uyu ndiovuta kulera Jokes
Jokes am happy for youThat spirit of asking zamavuto and matenda paukwati zikuyenela zitheka ma church
😝😝 koma mr jokes iwee anakoza kungochoka zako atakomoka
Yonse ndi minda kkkk kukana kuvomeleza kulakwisa😅 abusa
Undimenyaaa? Uziti timenyana😂😂😂🙌ching'aning'ani adha
By then how are you 😂😂😂, Mr Jokes mwaitha nkaz uja Ali ndi mimba yamwini😂
Chomwe ukufunacho Mr jokes uchipeza ndithu.suukufuna Banja iwe😂😂 km kulimbandi Mdalayo
From Capetown with my two eyes watching with big smiling. Mwina wa amoya athonyiwa. Ukwatiwu uthera zibagera
😅😅😅😅 koma iweyo ching'aning'an atimenya eti 🎉😂😂😂😂 goood job guys
Live from krugersdorp town Jozi...iwe umath basi❤
Koma ching'aning'ani ayi ndithu usazamfe ...uzit undimenya timenyedwa for me 😂😂😂😂😂😂
Kkkk abusa nawonso m'munda wa getsemani
Yosee ndi Minda🤣😂🤣🙌🙌
Zili bwino guys, Mumakwana Watching from RSA in Cape Town, Big up 💯👏👌🙏🙏🙏!!!
my favorite comedian chinganixy namangwenu❤❤❤❤
Atiii yonse ndi minda ah😂💔🚶ukwati uwuwu sungalimbe abusa inu
Osadandaula muzivala ife tilipompano 😂😂😂😂😂😂❤❤❤❤❤
Oyamba ndineyo sapota Mr jo tujuane mashabiki wa mr Jock's
Ineyo mavuto anandikwana kwambiri 😂😂
Mayina akewo , ngoziyankhuku ,😂😂
Yonse ndi minda kumene 😂😂
😂😂😂Abusa awawa
Watching from mwineriwa vg mulanje
Coming from fb
Yose ndi minda😂😂😂
Basi yonse ndi minda abusa amenewo 😂😂😂
This is amazing guyz🤣🤣🤣 mkazi muzamuona tsiku laukwqti mkakuuzani mumqnditqmbira
I'm here for Mr jokes and Ching'aning'ani
mumaitha Mr jokes 👍
😂😂 bas jokes warepheretsa ukwat
Pamene ndingatopere 😂😂😂
Ine ndisasangalase gulu😂😂
Iye mavuto sakuwafuna akufuna mtendere okhaokha
Ati basi yose ndiminda😂😂😂😂
Ooh yes timalakwitsa kusangalatsa gulu wina mkumajaila kuti imfa ndiimene idzatilekanitse
Kkkk😅😅 jokes wanditopetsa😊😊😊
Zikut bwanji kodi😂😂
🤣🤣🤣🤣🤣 yose ndi minda ya yolodani kumene
Ching aksy ndi machine
Ching'axy sukukukalamba bwino iwe 🤣
Abusa ayiwala dzina la munda😂😂😂😂😂
Koma iweyo Ching'axy🤣🤣🤣🤣
Koma ineo honestly the whole episode palibe ndatolapo
Sanje ibweletsa kaduka
Mr Jokes unabwela iweyo 😂😂😅😅
Painful truth from Mr Jokes. I like that
kkkkkkkkkkkk km ndaseka abusa akut yose ndi minda😂😂😂😂😂😂😂😂😂
🤣🤣🤣🤣🤣udziti timenyedwa
A best boy wo😂💔🚶 Ah
Mr mukumakomesa km chomachedwesa ma episode
Yonse ndi minda😂😂😂😂
Ching'aning'ani ndi Dolo ase eeeeee
Yonse ndi minda😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
👍👍👍👍👍👍👍👍👍😍😍😍😍😍Very niceThis is evidence that MALAWI 🇲🇼"" -~a swing
😂😂😂😂😂😂 ching'asi iwe wa ideni
Kkkkkk good joks izarekanise infa mwina achedwa kufa nanga kkkkkk
Koma Mr jokes mwalemphela kulowa mubanja kkkkkkkkkkkkk
mwatisiya mwendo mmwamba
Kkkkkkk Koma abusaa🤣🤣🤣.. akuti basi yonse ndi munda
Ching'aning'ani uja ndi Dolo kuposa ena tonse pano
Kwisa ma big
Mr Jokes don't force yourself to speak ka voice koti sikanu. Serious ya film to make it look original it doesn't mean kuti usinthe mawu
By then eti akulankhula lilime likusekela mawu onveka tu 😂😂😂
Kaya getseman kaya Eden, yonse ndi minda kkkk...it's Blenac here
Kkkk ati yonse ndi minda😂😂😂
Munda waGetseman🤣🤣💔💔
Munda wa getsemani hahha
😂😂😂mkaz muzamuwon tsik la ukwati ndikakuuzan mukumanditambila😂😂
Koma jocks ndiwe ovuta😂😂😂😂
Kkkkkkk Ching'axy anadza 😅😅😅
Eeee koma yah🤣🤣🤣🤣🤣🤣
I remember those days ngoziyankhuku
Mbambande Mr Jokes ...chilungamo basi kkkkk
Ati koma mavuto nkachite kuwalumbira paguwa🙌🥲😂😂
Makwana mr
Mpaka Ngoziyankhuku
Mwankhwala anga a nkhawa mr ching'a
😂😂😂😂😂😂😂akuti ine mavuto ndinatopa nao sindingalumbire zavoza😂😂😂
Ching'aning'ani ndi dolo😂😂
My favorite jokes love you
Jokes sazatheka ndithu 🤣🤣🤣
Akut yonse ndi minda 😂😂😂😂
Wachake ilibwino😊😊
Komatu jokis 😂😂😂eeeeh
😂😂😂😂 problem vs problem
Jokes you don't want problems 😂😂😂😂
Chilungamo Cha nyooooo
Maina okhawo nangoziwilatu mavuto alipo 🤣🤣🤣🤣
happy Mr jokes and ching,,,,,,,,💯
Ati utiyo 😂😅 Ching'aning'ani wakana cibale lero 😅😂😂
😂😂😂😂😂😂usalumbiledi bodza jokes mwina imfa sizabweladi😂😂😂😂😂
Undichosela mood ya ukwati kkkkk
🤣🤣🤣🤣🤣yonse ndiminda komaso ching'axy mpaka kukoza amfumu
Yonse ndi minda
Sure, Malawi 🇲🇼 moto
Muziti timenyedwa kkkkk😂😂😂
Even me I don't want trouble 😅😅😅
Munda wa Getsemane, wa Eden yonse ndi minda
Yonse ndi Minda
Chinyaxy adha🤣🤣🤣🤣
Even ma Surname ake, Ngoziyankhuku eti🤣🤣🤣🤣
Osati undimenya kumati timenyedwa hahahahah Ching'asy
😂😂😂 uyu ndiovuta kulera Jokes
Jokes am happy for you
That spirit of asking zamavuto and matenda paukwati zikuyenela zitheka ma church
😝😝 koma mr jokes iwee anakoza kungochoka zako atakomoka
Yonse ndi minda kkkk kukana kuvomeleza kulakwisa😅 abusa
Undimenyaaa?
Uziti timenyana😂😂😂🙌ching'aning'ani adha
By then how are you 😂😂😂, Mr Jokes mwaitha nkaz uja Ali ndi mimba yamwini😂
Chomwe ukufunacho Mr jokes uchipeza ndithu.suukufuna Banja iwe😂😂 km kulimbandi Mdalayo
From Capetown with my two eyes watching with big smiling. Mwina wa amoya athonyiwa. Ukwatiwu uthera zibagera
😅😅😅😅 koma iweyo ching'aning'an atimenya eti 🎉😂😂😂😂 goood job guys
Live from krugersdorp town Jozi...iwe umath basi❤
Koma ching'aning'ani ayi ndithu usazamfe ...uzit undimenya timenyedwa for me 😂😂😂😂😂😂
Kkkk abusa nawonso m'munda wa getsemani
Yosee ndi Minda🤣😂🤣🙌🙌
Zili bwino guys, Mumakwana Watching from RSA in Cape Town, Big up 💯👏👌🙏🙏🙏!!!
my favorite comedian chinganixy namangwenu❤❤❤❤
Atiii yonse ndi minda ah😂💔🚶ukwati uwuwu sungalimbe abusa inu
Osadandaula muzivala ife tilipompano 😂😂😂😂😂😂❤❤❤❤❤
Oyamba ndineyo sapota Mr jo tujuane mashabiki wa mr Jock's
Ineyo mavuto anandikwana kwambiri 😂😂
Mayina akewo , ngoziyankhuku ,😂😂
Yonse ndi minda kumene 😂😂
😂😂😂Abusa awawa
Watching from mwineriwa vg mulanje
Coming from fb
Yose ndi minda😂😂😂
Basi yonse ndi minda abusa amenewo 😂😂😂
This is amazing guyz🤣🤣🤣 mkazi muzamuona tsiku laukwqti mkakuuzani mumqnditqmbira
I'm here for Mr jokes and Ching'aning'ani
mumaitha Mr jokes 👍
😂😂 bas jokes warepheretsa ukwat
Pamene ndingatopere 😂😂😂
Ine ndisasangalase gulu😂😂
Iye mavuto sakuwafuna akufuna mtendere okhaokha
Ati basi yose ndiminda😂😂😂😂
Ooh yes timalakwitsa kusangalatsa gulu wina mkumajaila kuti imfa ndiimene idzatilekanitse
Kkkk😅😅 jokes wanditopetsa😊😊😊
Zikut bwanji kodi😂😂
🤣🤣🤣🤣🤣 yose ndi minda ya yolodani kumene
Ching aksy ndi machine
Ching'axy sukukukalamba bwino iwe 🤣
Abusa ayiwala dzina la munda😂😂😂😂😂
Koma iweyo Ching'axy🤣🤣🤣🤣
Koma ineo honestly the whole episode palibe ndatolapo
Sanje ibweletsa kaduka
Mr Jokes unabwela iweyo 😂😂😅😅
Painful truth from Mr Jokes. I like that
kkkkkkkkkkkk km ndaseka abusa akut yose ndi minda😂😂😂😂😂😂😂😂😂
🤣🤣🤣🤣🤣udziti timenyedwa
A best boy wo😂💔🚶
Ah
Mr mukumakomesa km chomachedwesa ma episode
Yonse ndi minda😂😂😂😂
Ching'aning'ani ndi Dolo ase eeeeee
Yonse ndi minda😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
👍👍👍👍👍👍👍👍👍😍😍😍😍😍Very nice
This is evidence that MALAWI 🇲🇼""
-~a swing