BON KALINDO LERO PA 23 September 2024

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 22 сен 2024

Комментарии • 38

  • @cassimyusuf6683
    @cassimyusuf6683 13 часов назад +2

    South Africa ndi ziko lolemera koma president wawo samapita kumeneko

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 15 часов назад +3

    Ngati mungapeze mwayi wakupha wa polisi wa traffic. Chitani choncho.

  • @thesocietynews3181
    @thesocietynews3181 3 часа назад

    Keep it up the Malawi First under the dynamic leadership of the D.C. Bon Kalindo

  • @DjshukulanGift
    @DjshukulanGift 15 часов назад +5

    Mmm ndipo ndava chison kupeza athu akumakomoka ndi jala ,wina ndikumagula,Dan lu pandalam ya 500 miliyon ine ndekha soz,ndikumat boma ndilomweli tangoziwa kt satanic yachukuk

  • @OssmanAbubaker-c6o
    @OssmanAbubaker-c6o 14 часов назад +1

    Ulemu wanu the DC ifeyotu timakunyadilani potiyimilira ife A Malawi 🇲🇼 ovutika

  • @FunnyKalimwayi
    @FunnyKalimwayi 14 часов назад +3

    inu achakwela ndachisilu

  • @Drmuhammadchiwona
    @Drmuhammadchiwona 12 часов назад +1

    Tikumvela mwachidwi bwana kalindo

  • @MaggieKazombo
    @MaggieKazombo 13 часов назад +1

    2025 Kwao Gule kukasiya tatopa 😊

  • @BrightZionga
    @BrightZionga 12 часов назад +2

    Chakwera ndi mbava 👿👿

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 12 часов назад +1

    Asiyeni masiku amathera ku chiseko pompano abwerera kuwu busa komweko

  • @JustfiedProperties
    @JustfiedProperties 7 часов назад

    Inu simukuona anthu mmene akuvutikiramu ,ndie mukuti nsanje yanji this is reality ,koma poti choona chimawawa

  • @EnockMatick-p1j
    @EnockMatick-p1j 15 часов назад +2

    Eeeeee kom chakwela azatisiya mavuto

  • @AtupeleChitenje
    @AtupeleChitenje 14 часов назад +2

    Athu ena mitu yawo sim
    agwira tchito panyake chakwera

  • @richardbandah1824
    @richardbandah1824 15 часов назад +4

    Boma ndi chabe Ili ndipo anthu akuvutika kwambiri mmm chakwera ngwa satanic basi,ndie wina adziti bama ndilomweri mmm zachisoni

  • @EusébioLucianoGaiondo
    @EusébioLucianoGaiondo 11 часов назад +1

    🔥🔥🔥

  • @DysonTummiesSajiwa
    @DysonTummiesSajiwa 14 часов назад +2

    Zikomo a Bon kalindo mwathandiza ku Machinga moti apa sitivaso kut ku Machinga kuliso njala apa akudya zimenezo mpaka adzakolole chifukwa simungamabokele zinthu zakut akudya masiku awiri

    • @CharlesJustin-z9s
      @CharlesJustin-z9s 13 часов назад +2

      Bola wathandiza kusina ndikusapeleka kalikonse

    • @kingsleymsampha2260
      @kingsleymsampha2260 12 часов назад

      Kaperekeni inuyo zoti adye Chaka chonsezo

    • @HalimaShafie-q9k
      @HalimaShafie-q9k 12 часов назад

      Iweso ndi galukwabas muthu angathandeze chocho ndiwe galu kwabas

    • @BrightZionga
      @BrightZionga 12 часов назад

      Awanso ndachitsilu bone kalindo ndi president? Mmesa amapemphesa kwa anthu akufuna kwabwino?

    • @joegibsonzulu2599
      @joegibsonzulu2599 11 часов назад

      Tachioneni chi tchende. Iweyo ndi ka Chakwera kakoko mwachitapo chiyani?

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 14 часов назад +1

    Ndpo chakwera tatopa naye kumupeza munthu wina oganiza wanzeru zàke nkumati boma ndilomweri mmmmm km boma la satanic

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 12 часов назад +2

    Ndipo Chakwera waononga dziko , palibe chikuyenda. Magufuli anali akamuna osati nyasi izi.

  • @Jessica-tc7rf
    @Jessica-tc7rf 14 часов назад +1

    Chakwela afe choima

  • @VuyisekaTukwayo-wt5pn
    @VuyisekaTukwayo-wt5pn 13 часов назад

    Garu kobasi ulankhurire anthu UDF kanamiza ankhunguwo

  • @chipanganofackison5185
    @chipanganofackison5185 Час назад

    Ingolekani akalindo
    Osadabwa pano mukupezatu only 40 comments Koma poyamba paja mumapeza more than 700 comments 😂😂😂😂😂

  • @CharlesMateya
    @CharlesMateya 14 часов назад

    Chirimba mtoso 3 weeks no water

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 12 часов назад

    Mulungu atichitire chifundo

  • @SABITIKAISI
    @SABITIKAISI 4 часа назад

    ❤❤❤

  • @IshmaelSamson-g1g
    @IshmaelSamson-g1g 13 часов назад

    🎉

  • @alexandermeke6994
    @alexandermeke6994 7 часов назад +1

    Nsanje ikuphani akalindo 😂😂😂😂no mfundo tsopano zonse zatha moti pali mfundo apa 😅😅😅😅akuyenda komaso zikuyenda zipatso zake zikuwoneka osatsa kachasu wanu uja opandanso mfundo negatiinu APM

    • @JanuaryGwere
      @JanuaryGwere 7 часов назад

      Sinsanje akulu uchisilu bwanji

    • @alexandermeke6994
      @alexandermeke6994 7 часов назад

      @@JanuaryGwere ndi nsanje inu ndi inu nomwe chilichonse ndale dziko lingatukuke ana a njoka inu,a nkhadwe opanda nzeru ngati APM

    • @JanuaryGwere
      @JanuaryGwere 2 часа назад

      @@alexandermeke6994 aaaaaa wabzelu ndinda yemwe mukuwona kuti angapange zinthu mokomela anthu adziko kupatula chakwera fish wamunthu ngati ameneyo

    • @alexandermeke6994
      @alexandermeke6994 2 часа назад

      @@JanuaryGwere chakwera basi ndi machine God choose him koma mavuto sadzatha mpaka yesu abwera