To be honest chakwera walephera wether akukana or akuvomela useless president ever satana wamkulu osakonda anthu amkaufuna u president ndicholinga choti adzapeze polemelerapo not kutukula Malawi otsatila akeso ndi opusa anthu adyela Koma Mulungu alipo salora kuti ana athu adzapeze dziko lathu Lili pamavuto adzaoneni
Sitimafuna kuyikapo mulomo koma nkhaniyo ikhoza kukhala yoona ndithu that's why Bingu samamufuna komatso Peter ananena kuti ziko lilamulidwa ndi Satana koma sanamasule anangoyakhula mwa short cut. Peter Mutharika he's a prophet because anali ataona kale zosezi tikukumananazo panopa
Big up comrade 🔥🔥🔥🔥 may God continue to bless, guide and protect you Brother Man, proud of you always ❤❤❤❤
Comrade Mtanyiwa is here
Never give up Brother, you are a true Freedom Fighter
✊✊✊✊.
MCP you are fooling yourself , and you will never succeed.
❤
I like you my brother go ahead.well done
I support Limpopo FM with Comrade Mtanyiwa God bless you sir
Kkkkkkkk Koma akulu akulu nyatwa music 🎶🎶🎶🎶🎶
Mcp mwawojeza mulungu ndiye adziwa zose
I'm Malawian citizen but we are here in south Africa because our country leader
Muyakhuleni ameneyu ndi galu alibe khalidwe
Ndipo live ❤
FM number one ❤
To be honest chakwera walephera wether akukana or akuvomela useless president ever satana wamkulu osakonda anthu amkaufuna u president ndicholinga choti adzapeze polemelerapo not kutukula Malawi otsatila akeso ndi opusa anthu adyela Koma Mulungu alipo salora kuti ana athu adzapeze dziko lathu Lili pamavuto adzaoneni
Tanyiwa umatiimilila 💪💪💪💪
Comrade ntanyiwa uremu wanu Allah akutetezeni thawi yonse mpaka mubwerere ku Namibia mpaka timuchose crocodile 🐊 mpaka achoke
Welcome home Comrade mtanyiwa
Ambuye azikudalitsa brooh
Mumakwana amunthanyiw🎉
MULUNGU adzikudalitsani nthawi zonse
Ndiponso adzikutetezelani kwambiri
Mmankhwana inuyoooo ❤MR COMRADE pambuyo panu ifee
Welcome back bwana 🙏
I salute you mr Mtanyiwa
Audze azimai otumidwawo kkkkk ndi nkhope zawo zokwinyikazo hahahaaaa
Chakwera kumene uliko ungotula pansi udindo warephera kuyendesa dziko ndi team yako yonse
NKHANGA ZAONA ON LIMPOPO FM RADIO STATION ND COMRADE NTANYIWA Dan ru oganiza mopusa
❤❤❤❤❤❤❤
Kikiki koma Ntanyiwa umakwana mpaka kuonera mpira wa Silver ndi KB.
Ndye mumasuppoter Team yank kuno ku Malawi?
Komanso Bushiri ndi Nkhang'a wa anthu oyipa pa dziko lapansi
Big up bro mumatiimilila bg
Welcome boss, were waiting
Allah bless you Mr ntanyiwa ndipo tikumakupephererani akut Allah akunthangatireni ameen
Mahule inu musiyeni ntanyiwa pa limpopo FM mapeto ake munyeledwa
Pulezident walawi ngat simukuziwa ndi bushiri
Sitimafuna kuyikapo mulomo koma nkhaniyo ikhoza kukhala yoona ndithu that's why Bingu samamufuna komatso Peter ananena kuti ziko lilamulidwa ndi Satana koma sanamasule anangoyakhula mwa short cut. Peter Mutharika he's a prophet because anali ataona kale zosezi tikukumananazo panopa
Kodi comrade nanga ife aku Capetown tidziponya kuti zosonkha
.mumakwanira.bwana.mumatiyimiira
Viva Malawi 🇲🇼
Dan lu chisilu chothelatu chosowa zochita alibe kanthu bulutu opezela ndalama mu ndale.
Ntanyiwa mumakwana
Musamacheze nawo anthu amwenewo ine ndimadera nkhawa kn mozambique
Auze comrade amvetse
😂😂😂❤...Bravooo
Mr comrade mumakwanila km uyu ngat amasat ndalama eish wachimina
koma tyendeleni comrade kukawale chaku kamunzu institute
😂😂😅😂