KJV Matthew 24 7 For nation shall rise against nation, and kingdom against kingdom: and there shall be famines, and pestilences, and earthquakes, in divers places. End times signs
Tadutsapo moyo umenewu ndili wang'ono from 1994 tagonelapo mango ophika ife 😢komano those days kunalibe social media that's why zimaoneka ngati mavuto kulibe
Zinthu sizili bwino ku Machinga ko. However,the president of Malawi (Chakwera ) is busy moving around game reserves washing leoperds fighting. Instead of visiting people of Maching who are dying,what is that ! This is stupid leadership
Anthu akumweranu bwanji simumalimbikila ntchito azisogoleli anu ndi amene anakusochelesani inu muli ndi ma president 4 onse akumwera sangakuthandizeni ndipo munazolowera zaulere chifukwa muli kuvutika
Yaaa Allah help our country Malawi
Njala yavuta koma chakwela ndipamene wagundika kuyendela agalu
😭😭😭🙏🙏🙏
KJV Matthew 24
7 For nation shall rise against nation, and kingdom against kingdom: and there shall be famines, and pestilences, and earthquakes, in divers places.
End times signs
Tadutsapo moyo umenewu ndili wang'ono from 1994 tagonelapo mango ophika ife 😢komano those days kunalibe social media that's why zimaoneka ngati mavuto kulibe
This is so sad,ndiye aziti chakwera deliver akuyendereni atate Yahweh nose amene mukunena zimenezi, president wa nsakho ngati uyu sindinamuonepo
Zandiriritsa akuakur tikamadya simayadeya tidzingot zikom ambuye
Chakwera machende ake😭😭
KUMATI UKOZA DZIKO MACHENDE AKO CHAKWERA WAVA MUNO MWALOWA NJALA CHIFUKWA CHAIWE CHITSILU MKUTU MWAKO CHAKWERA
Kodi prophet Davide mbewe Ali kutiko .Kodi ndimayesa ndimbali yomwe akukhala iyeyu
Poor governance lead to misfortune by the way
Zinthu sizili bwino ku Machinga ko.
However,the president of Malawi (Chakwera ) is busy moving around game reserves washing leoperds fighting. Instead of visiting people of Maching who are dying,what is that !
This is stupid leadership
😥😥😥
Zosathala bwino tiyamike alindikuthekela ndandizan ndithu mulung akulipilan zovesa chison tilibe pulezi det
Zosayenda😭😭😭😭😭allah please 🙏🙏🤲
Atiteteze😢
Zokhudza 😭
Kalingonda ameneyo chitedze Ndi choopsatu
Naneso akuwoneka Ngati kalingonda
😪😪😪😪😪
Peter muthalika ndi atupere muluz Ali kut abale awo akufa ndi njala Ali komweko Ali duu sangawathandize abale awo Ali ndi ndalama zambiri zimene anaba
Ufiti koma kumafuna ati anthu akavotele
Ubwino wake akulamuka dziko sindiwo
Ubwino wake si Peter ndi atupele omwe akudya ndalama zaboma
Boma ili lipakire 2025
Tzwona. chakachino
Zikuwoneka kuti ena nkukhala kwawo uko. Mabungwe takapanga proper assessment kuti tiwone chenicheni choyambitsa
Mwina ndiwulesi
Mwina ndichizolowedzi
Mwina ndinjila yongozolowera kupempha
Mwina ndianthu aja samamvera ulangizi wa malimidwe
Tapangani kafukufuku poyanganira zimenezi kuwopela kudzala malimgaliro obwezera chitukuko mmbuyo
Machendeako
Tadyapo ife
Mboliyako galuiwe wamva
Anthu akumweranu bwanji simumalimbikila ntchito azisogoleli anu ndi amene anakusochelesani inu muli ndi ma president 4 onse akumwera sangakuthandizeni ndipo munazolowera zaulere chifukwa muli kuvutika
Iwe tiziti kwanu kuli chokudya chokwanila kapena kulilongwe aliyense ali ndichokudya iwe ndioipa ulibe chisoni wayamkhula mopusa ngati chisilu olo mwana sangayamkhule wayamkhulazo .mvula amagwesa nda. Mako kunyelo kwa nyawu
Mboliyakenso galu ameney
Mawu mwayankhulawo mulungu akuoneni mwapaderadera,,,ndipo mudzawakumbukirenso ! Mulungu sapondereza akulipireni mochuluka
Mulungu akukhulukile kwambiri 😊
Mmmmm athu amakokomeza Ndi kalingonda ifeso timadya timalima zimenezo Iwo akuzitenga zachirendo chifukwa sanadyeko ndikoyamba
Musaletse pliz ndi chitedzedi,,,ine nnali konko kuli mavutotu chitedzecho chikusowanso talawako ndithu
Galu
Muzitha kusiyanitsa pakati pa chitedze ndi kalongonda
Uyu sikalongonda kapena video Yomwe akusaka chitedze azimayi ija simunaone eti? Musamangoletsa zilizonse muziganizira muli Inu