PROPHECY FOR MALAWI -The road to 2025 will be chaotic &will cost lives|Prophet Emmanuel Zomba Malawi

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 8 ноя 2024

Комментарии • 30

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js 4 месяца назад

    Let God be God

  • @JessicaKumwambe-ss4cn
    @JessicaKumwambe-ss4cn 4 месяца назад

    Inenso uneneri uwu naumvapo ndipo kuzakhetsedwadi mwazi

  • @jimmyphalanya
    @jimmyphalanya Год назад

    Amen

  • @marthansaliwa7732
    @marthansaliwa7732 Год назад +1

    God forbid. Nothing will happen to Malawi. We pray for our country

  • @ZaithwaBanda
    @ZaithwaBanda 4 месяца назад +2

    Emmanuel ndi prophet wa DPP tikumudziwa kale kkkkkk

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js 4 месяца назад

    Oweruza ndi ambuye

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js 4 месяца назад

    The end of Alliance.Iziii zichitika

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o Год назад

    Aneneli onyenga palibe chimene chingakuthandizeni anthu amulungu

  • @michaelkallyz2425
    @michaelkallyz2425 4 месяца назад

    So are they now planning to arrest Peter Mutharika in order to sail through?

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js 4 месяца назад

    Pano uyu apha anthu

  • @robertbobsabuli4726
    @robertbobsabuli4726 Год назад +1

    Is he a prophet or politician ?

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js 4 месяца назад

    Zoona boma ili limadialira kugawa ndalama ndikupha

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js 4 месяца назад

    This is only for prophetic people

  • @hagayichiluwe
    @hagayichiluwe 4 месяца назад +1

    Zaziiiiii

  • @KingGazzaha.k.aWarriorman
    @KingGazzaha.k.aWarriorman 11 месяцев назад

    Kom anthu inu mumamva bwanj kd muri mkachisi cha mulungu kom muri busy ndizadziko uneneri wanji umenenewo kutumidwa chan compain ndi m'church momwe?😅😅😅😅

  • @alickchiumia2616
    @alickchiumia2616 Год назад

    Kkkkk lalikilani za ufumu wakumwamba osati za ndale

    • @LeendaDeborah2005
      @LeendaDeborah2005 4 месяца назад

      Nde kutanthauza kuti andale sadalengedwe ndi mulungu?? Ndinu opepela bwanji

  • @Dan44-x5b
    @Dan44-x5b 5 месяцев назад +1

    Tell your lies tpo other people not tolearned Malawians. Iweyo mmene ukuyankhulira ukuonekeratu kuti ndiwe Mlomwe wa DPP so stop the nonsense

  • @BerthaKasambala-y5k
    @BerthaKasambala-y5k 4 месяца назад

    Baibo rimat muyambe mwathanga ufumu wa murungu ndipo zonse zizaku satani auzeni anthu zaufumu wamurungu osat zimenezo komanso muzisiyanisa maganizo anu ndi kurankhura kwamurungu chifukwa zinazi ndimaganizo anu nkuma nama kt murungu wakuwonesa murungutu samarankhura chisawawa awowo ndimaganizo anu akuru paribepo yesu apa just wasting time for nothing kkkkkkkkk kuzisaka man

  • @tasmania527
    @tasmania527 Год назад

    False prophets

    • @LeendaDeborah2005
      @LeendaDeborah2005 4 месяца назад

      And you as a true prophet you should tell us. Nde munyatu ndi miliri yomwe izakugweleniyo anthu osanva mulungu akamakuyankhulani

  • @ganizanistephano-gi5lr
    @ganizanistephano-gi5lr Год назад

    Izizi izi boma likuyenera kuzichita regulate
    Osati aliyense akakhuta bonya azichita prophesy.
    Total rubbish

    • @LeendaDeborah2005
      @LeendaDeborah2005 4 месяца назад

      Iweyo you are not God. Mumayankhula mofoila musadabwe zazikulu zomwe zizagwere mudziko mwathu muno. It is all because of people like you. Mumanyalanyaza nde tiyeni get ready for what is coming on your way

    • @ganizanistephano-gi5lr
      @ganizanistephano-gi5lr 4 месяца назад

      @@LeendaDeborah2005 munachitidwa brainwash nkuona ukutero.Its was so clear and glaring kuti the road to 2025 will be chaotic simply bcoz MCP yaphwanya chipangano.....
      If you read newspapers, kumvera/kuonera kwagwanji, Hot Current and other current affairs programs on radios and TVs mukanszindikira kuti these so called prophets read btn lines za mmene zinthu zikuyendera ....and come up with these FAKE PROPHECIES.
      Wake Up my dear !!!

    • @MWayne0
      @MWayne0 4 месяца назад

      😂😂😂😂