KODI MWAIMVA NKHANI YOMWE BISHOP NSUSA WAING'ALURA ZA IMFA YA SAULOS CHILIMA IJA? AYAMBAPO KUULURA

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 25 дек 2024

Комментарии • 26

  • @AdisonDaniel-t8i
    @AdisonDaniel-t8i 8 часов назад

    Amen salukhutila ndilipot atulutse lake lot alinkhulupilire nda aliyense aliniganizo ake

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 11 часов назад

    It's a very nice advice to pray for rains to come but God is forsaking us because of our hypocrisy Matt 23 v1--Woooe

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w 12 часов назад +1

    Koditu diposachedwa popano mulungu akuikani poyela palibe akukodwa ndi ndi zomwe mukuchita inuyo a mcp olila samuseka pakamwa chule wadabwa m, madzi muli mwake

  • @godfreyvaiya7902
    @godfreyvaiya7902 14 часов назад +2

    Nkhani ithe bwanji munthu munapha ngati nkhumba ,,asatana

  • @chifundobuledi
    @chifundobuledi 13 часов назад +1

    Mulungu wakwiya ndi dziko la Malawi chifuka choti anthu akuphedwa osalakwa.

  • @ClementMagaso
    @ClementMagaso 8 часов назад +1

    Kodi iwo akunena kuti chowona mulibe mukalata la report la imfa la a Chilima. Sanafike poyera mu nthawiyo kuti nawonso aperekepo umboni

  • @Elizabethmanda-es7se
    @Elizabethmanda-es7se 11 часов назад

    ulangizi opusa umenewo mukufuna tidziwopa kunena chilingamo komaso maganizo athu...... a bishop anena zakukhosi kwawo musawa tchingile.... report yanuyo mukagwere nayo uko.... ndinu zisilu nonse ❤

  • @JosephEphraim-j9x
    @JosephEphraim-j9x 11 часов назад +1

    Koma ndiwe wabodza,zoona tikuvutika chifukwa cha kumwalira kwa Chilima?
    Iwe Msusa,panga wako kafuku-fuku.
    Udzilankhula ngati uli ndi achibale,iweyo nkhondo itabuka mdziko muno,ukhoza kuthawa,koma abale akowo ukhoza kuwatenga pothawapo?
    Ambuye akuone

  • @PaulManyamba
    @PaulManyamba 12 часов назад +1

    Ndiye avomeleze zomwe akuona kuti ndi zaboza zosatheka zimenezo

  • @clairemyegha4315
    @clairemyegha4315 13 часов назад +1

    Watikwiyila Mulungu ndizochita zaziko la Malawi. Tiyeni tilape pamaso pa MULUNGU

  • @carlogwiritsani8404
    @carlogwiritsani8404 13 часов назад +1

    As much as we all want to know the truth l wish people who have the full information to come forward and stop complaining because it's not going to change anything

  • @LameckNgwangwa-g3p
    @LameckNgwangwa-g3p 12 часов назад

    Wa bodzaso uyuu nkhani idzatha akadzapeka black box ndipo ma Bishop more fireee

  • @chifundobuledi
    @chifundobuledi 13 часов назад

    Munapha Chilima ndipo iweyo sungaletse a Malawi kuyankhula za imfa ya SKC!!! Chilungamo chidziwika soon or later.

  • @F30-Jet
    @F30-Jet 4 часа назад

    BISHOP akunena zoona

  • @zayedmitawa8345
    @zayedmitawa8345 12 часов назад

    Moti ena akungofuna nkhani ya Chikangawa ingotha basi just like that!!!!
    Msusa wanena zoona.Wina wake ntchito bwezi itaima kapena kutha kumene.
    Nkhaniyi siingathe ngati mmene MCP ndi ma fans ake onse akuganizira.

  • @ShemMwale-i8m
    @ShemMwale-i8m 12 часов назад

    Opusa iwe utikakamize kuti tisiye kulankhula za imfa ya chilima cholinga muzingophabe anthu agalu inu eti??

  • @jackalview7491
    @jackalview7491 14 часов назад

    Kunkuyu iwe tapeleka black box

  • @ChristinaMdeza
    @ChristinaMdeza 11 часов назад

    or ine a bishop mpaka pano sindivesa kuti a chilima di anafa chocho nkhani palibe ibwele apa black box chakwera anapha a chilima kombe chowonadi sichipheka ayi mulungu akuziwa zonse chakwera wapha anthu osalakwa moses yo paja naye ndiwakupha ,

  • @EvanMchere-qf8fs
    @EvanMchere-qf8fs 13 часов назад

    Akukoka nkhani ndi chani iwe chaima anthu 9 omwe anamwalira anaphedwa ndi Mcp wo sanali ofunikila?? Omwalira wo moyowo samaufuna ??Bomaru likanafotokoza chilungamo chomwe chinachitika palibe anakakoka nkhani apa chikusowekera apa ndi Chilungamo basi

  • @johnnyirenda5848
    @johnnyirenda5848 9 часов назад

    Zilipo zotonthozeka koma Za 06 June,2024 Ayi , Tazolowera kuti Cholinga Chasata chikatheka Basi ndi ka Mzimu koti haaa! Zadutsa Basi mmm Apa Ayi Pepani pafufuzike Zenizeni zioneke ziliko Zoiwala Apapa apa Ayi Tere.

  • @Blessings-td4cr
    @Blessings-td4cr 14 часов назад

    Choonadi chake chiticho? Nkhani mukatulutsa voice recorder AKA black box finish!!!! Why are you hiding this machine mbuzi zawathu!!!!!! Mulungutu alipo muzayalukabe zingatani pangatani.

  • @mchipengule
    @mchipengule 14 часов назад

    Anthu a Mulungu muzikhala chitsanzo chabwino kwa anthu, osadzetsa mpungwe pungwe kwa anthu. Sizikupindulirani a Bishop Izi... Be serious.

    • @henryphiri6100
      @henryphiri6100 14 часов назад

      Iyi sinkhani yoti ithe kapena kutsekana pakamwa ayiii.

  • @MayamikoJeke-d5m
    @MayamikoJeke-d5m 13 часов назад

    Nkhani singathe mukubweretsa zabodza chilungamo chizadziwika mufune or musafune

  • @LucksonChipofya
    @LucksonChipofya 14 часов назад

    Amusutsa akufuna nkhani iyi yithe akunamatu nkhaniyi ivuta tisayiwale kwa iwo iyiwale koma ife ayi chilima adawayika m'boma achakwera ndikuyiwala kofunikira kwa nzawo ndikumupha