inu palibepo busa pamenepo kodi chomwe asiyila achina Yasini gama Alexander kwambiri ndi azitsogoleri ena a original osati anyamata ojiya wa mene akuonekela ameneyu angakhale m busa ali maso mwamwamwa ngati mfiti
Ana AJoka Inu!! Even Jesus Insult Azitumiki onyenga okanda Ndalama ndi osoweka chilungamo tadzigugudani mumtima mwanu kuti Lero lino ku Mw a Kufafanana ndindani??
Akanazitchula dzina, mpingo, ndi Dera lomwe akutumikira. Like a bishop Msusa, archdiocese of Blantyre was chipani Cha Montfort Missionaries eyetu thus introduction in full.
inu palibepo busa pamenepo kodi chomwe asiyila achina Yasini gama Alexander kwambiri ndi azitsogoleri ena a original osati anyamata ojiya wa mene akuonekela ameneyu angakhale m busa ali maso mwamwamwa ngati mfiti
Palibedi...makape
Leave the Bishop Msusa alone his the only one who's honest than those after money ,azibuda enawa mmm
Devo is under control here in Malawi anthu azipembezowo Malo moyima pa chilungamo akusakha kudya ndalama ndkubisa choonadi😢
Azibusa enawa anapatsidwa ndlama chilungamo chimawawa
Khoma ndiye ndaninso shameless man
Busa amakhara ometa Mbali chonchi
Azibusa achinyengo,akufuna Michele asatipusise
Azibusa olephela kuzifotokoza bwino 🤣🤣🤣🤣 pamalawi paipa mphavu ka yesala
Bishop koma ameneyi
Azibusa olephera kuzitchura komwe a Kuchokera mmmmm zodabwitsa
😮Awa si abusa koma mimbulu.
Nkhandwe😢
Iwe pawekha ndindani
Long live Thomas Msusa,
Bakili muluzi tv atiuza mayina awo ife phee
Zaziii anyamata adzikwanje ameneo osadzuwika bwino ndechani ao nga MCP
Anthu adapenya...asiyeni akumbe golide boma lopanda Pake ili palibe chanzeru chomwe ringachite chokhudza migodi
Shame on you abusa achinyengonu
Azibusa akukana chilungamo musadandawule azibusa China chizaziwika
msusa +gama+sulemani ❤
Azibusa achinyengoh aja ndiamenewo odana ndichilungamoh, Chakwera waatuma amenewoh
This bishop he's standing on truth
Anthu omwe alephela kuzitchula mainao ndio akutipusitsa go ahead msunsa chakwela ndibmfiti
Ndipo zodabwitsa tu
Otumidwa awa ndi MCP,chikangawa party
Ana AJoka Inu!! Even Jesus Insult Azitumiki onyenga okanda Ndalama ndi osoweka chilungamo tadzigugudani mumtima mwanu kuti Lero lino ku Mw a Kufafanana ndindani??
Bishop ni yemwei sitikuaintha msusa otsutsa ni omwewo anyamata odziya olephera unena kocokera
😂komainu😂
Zisiru zaathu muzidya ndalamazo azibusa onyenga inu ,mukulephela kunena koma mwachokela agalu amcp inu
Zalandila ndalama uko ife atibowe zaugalu
Mubusayo anene zoona ndionama ameneyo simubusa
Simubutsa uyo ndi ojiya uyo
Komatu Koma ohooo mudzitenge bwino kwambiri mulungu akukuonani
Awa si abusa. Ndi tchito chabe. Amadikira salale. Moto uwakathe.ine m'malawi weniweni. Katolika ndiimene inayambisa matipate. Mipingo iyi inalikuti. Chitani manyazi.
Rp uli ku times Kodi.welcome
Azisogoleli otumikila munthu osati Mulungu chifukwa Chake akudana ndichilungamo kma chibanzi mwadyacho chizakusatani one time
Panyopawo ma concerned religious leaders osewo.
Ndipo asamale
Mbava zobisala ku zipembedzo
Maganizo ake ndi ake Palibe zoti amayembekezera kuti anene kuti chani
Azikwanje awa si abusa
Vuto ndiloti bishop ali kundende chifukwa chopha munthu wachi Albion
Mmbusa saoneka chonchi komanso sayankhura chonchi
Ngati sapenga misala anthu away kaya tiyeni tili mmaso, pemphero patsogolo, Mulungu wathu ndi wamoyo ndi chilungamo.
Azibusa amaoneka chomcho
Kunamizila ubusa
Abusa ngati mwameta m'mbali simungandiuze zochita 😂😂😂😂
😂😂😂
Ndiye bwanji mumayikapo Brian Banda mumafuna chiyani kodi???
Agalu amenewa siazibusa otumikira Mulungu koma amatumikira satana.
Msusa sanalakwitse ayi.Idyani ndalamazo agalu inu.
Si achipembezo, azibisa bwanji.
Zisiru za azimbusa mulungu azingathe koopsa ndithu ndalama mwalandirazo mutsegure nazo mimba mwakamwazi
Mwati golide ku nthalire?
Masiku otsiriza ndichocho
Mwauze azibusawo kuti mituyawo
Akanazitchula dzina, mpingo, ndi Dera lomwe akutumikira.
Like a bishop Msusa, archdiocese of Blantyre was chipani Cha Montfort Missionaries eyetu thus introduction in full.
Azibusa ojiya alobe chima chilichonse ojiya amenewa samapempherela. Mulungu wakumwamba awa
Abusa ogudwa ndi Chakwera ndi MCP.
Ngati ndinu azibusa en en mukanika kutchula mipingo yanu bwaaa mapazi anu
Enanu tmamwa nanu njada mumakwalalamu nde ubusa mwayamba lit?
Komatu background song it's so disturbing bwanji osaika kumayambiliro kapena kumapeto, zochotsa chidwi bwanji
Palibe gulu lazipembedzo pamene paja amenewo ndachikangawa
Kodi othawa ku Mozambique sakudziwa kuti malawi nayenso zizachitika chomwechi 2025 September?😂😂😂
Mbusa akuoneka okalambayo amenyengana ndi galu wake ndamuziwa ndiwakukasia
Brian banda chonde chonde umuyitane kunkuyu uzamufunse about black box ija anati yasungidwa bwino ili kuti basi
Mcp ili pa chi ntchito, eish anthu osafuna kugoja
Ife nde tizathawira kuti ndi smart matic yanuyo Mozambique ndi chisanzo inu a mcp mumuziwe yesu
Lipoti lanji longonamizila anthu ose ophedwao angotulutsa black box anthu amve zomwe mudamuchita chilima ndi anthu ena Aja chakwela mulungu amulange
Anthu amisala amene aja
Azibusa akuba msundwe yonseija
Ayasin. Kulibe. Pamenepo. Koma. Azibambo. Inu. Muli. Ndiumuthu. Azibuss. Inu
Sazibusa amenewo enawoo ndimahule
Alipo Mulungu a mene amaweluza molungama komanso mosakondera
Kukawona kamlomo kakeko
Mwatengatu anthu opephetsa osati azibusa awa. Tsopano amafuna bishop anene zabodza asanene momwe ananvela report 😂 ubwino wake chilungamo chimawawa😂
Azibusawa maina awo ndi achilendo,Kaya awatenga kuti Kaya?
Kabaya kachilungamo munya muona muona kuti mupanga bwanji . Ubwino wake mboniyo ndi Mulungu ndipo anajambiladi muzakhumudwa zonse zili poyera
Lipoti latulukali ndilongo phimbila mabala osati kupooetsa ayi.
Limeli ñdi gulu lopanda nzelu.akufuna anthu azingosekelela zilizonsebasi.
Amene alephera kudzifotokoza bwinooooo😂😂😂
Kkkkk
Ndi chitsilu ichi akuyankhula mwa mantha chifukwa akudziwa kuti akunena bodza
Ndipotu palibe ntendere kufikira choonadi chitatimasura, ojiyawa akuzolowera, achoka ku parliament kojiya kuti boma ndilomweri, ikafika thawi yazikwanje amavara ma face mask uku atanyamura zikwanje, apa ndiawano kususana ndi munthu wa Mulungu nyau zenizeni akuyesesa kuseka mipata yonse Kuti atiseke pakamwa
Wadya zingati, mukutamba dala kuti ena adzikuikirani kumbuyo kodi?
Uyo wamfupiyo osunga tsitsiyo ndi wa 25 àmalima kwangwagwa ubusa wayamba liti?
😂😂😂
Onsewo ndi Mbava zokhazo zokhazo simazibusa amenewo alandira ndalama uko kubwera nkuzamauuza a malawi za manyi asamaletu ojiwo ndithu!!!!
Anthu amene ajaa chomwe amazibisira mchani....
Azibusa inuyo adyela achehewo avule chisoticho
Osazitengela azimaiwo ndi ma hule enawo mmaka azi bambo ndi owo endayenda plas chamba
Abusa akuba
Awa si abusa atumidwa ndi chikangawa adwa ndalama awa
Palibe chamzeru anthu olakwa munthu wayankhula chilunga
Nkhope zonsezi si za Yahova izi zuchita kuoneka zadyera
Palibepo m'busa apa coz Ena mwa iwo ndi ma lectures
Ma battery awo palibe za ubusa anyamata ojiya amenewo
Tulutsani kaye black box
Adya chibanzi anthuwa
Azipembezo za kumidima aibwa awa
Azibusa opusa inu
Mwawuze kut azibusa ambuzi adasinkhanawa ndi makape ..mbuzi zenizeni..adyera kunthiko....anangotolana ukoo...kupusa
Kod kumalawi kuli tendele
Toyemo ulp asatana awa toyeno uko mwadya ndalama inu
Msusa
Mwadya ndalama inu
Pali abusadi apa? Kuchezatu uku ndi Vatican
Azibusa olalikila maminbus awa
Times is toooo biased to be a credible news room
Chilungamo chimawawa
Palibe busa apa