ATSOGOLERI AMIPINGO INA LERO AWUKIRA ZOMWE ANAYANKHULA BISHOP WA CATHOLIC ZOKHUNZA INFA YA CHILIMA

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 26 дек 2024

Комментарии • 433

  • @Malawian-q5f
    @Malawian-q5f 22 часа назад +13

    Mipingo yaboza, this all means Bishop Nsusa is a powerful man of God, awa adjacent ndalama. Machende awo

    • @FidelisKumwenda
      @FidelisKumwenda 20 часов назад

      Ayi. Let us not shield our Bishop. The statement shouldn't come from a respected person like Archbishop Msusa. I don't understand what went into his mind.

  • @HappyLuhanga-f8g
    @HappyLuhanga-f8g 19 часов назад +2

    Bwana bishop my God bless you all time

  • @johnchidothi5215
    @johnchidothi5215 22 часа назад +7

    Inuyo, amene anakulemberani zoyankhula, amene anakutumaniyo nonse mulibe nzeru

    • @KirsleyjonnyChisale
      @KirsleyjonnyChisale 7 часов назад

      Ndaononga Data yanga pachabe..Nonse so called faith leaders pathako panu Ana a MCP inu..Ana opusa koma akuakulu

  • @edsonndalama2334
    @edsonndalama2334 17 часов назад +2

    Ife sitikukudziwani kuti ndi inu atsogoleri, ife tikudziwa Arc Bishop Msusa, ameneyo ndiye mtsogoleri weniweni amene dziko likumudziwa

  • @NdemboBrothersAdam
    @NdemboBrothersAdam 21 час назад +3

    Mwangotola masheikh opanda Haq komanso adyera

  • @MathiasFuso-g8l
    @MathiasFuso-g8l 22 часа назад +4

    Ndithu ndithu mulungu akulangeni, pompo pompo kuyambila pa thupi lanu mpaka mmanyumba mwanu, mubwereso tsoka ngati lomwe linagwa kubanja la chilima. In the name of mighty God.

  • @TiwalumbeNathan
    @TiwalumbeNathan 23 часа назад +6

    If you are true men of God ask Holly Spirit to tell you the trueth😅😅😅😅

  • @ANTHONYMKOCHA
    @ANTHONYMKOCHA 18 часов назад +1

    Anyamata ojiya awa. Bishop Luke Msusa moto

  • @dennismkombe7193
    @dennismkombe7193 23 часа назад +4

    Koma Malawi, it's really dramatic

  • @mohamedriazshreef8697
    @mohamedriazshreef8697 6 часов назад

    We love ❤️❤️❤️❤️ you ❤️❤️❤️❤️ nsusa

  • @RobertWisky
    @RobertWisky 23 часа назад +4

    Tangotulutsani Blackbox ndiyomwe a Malawi itadzawamasule muzonsezi.

  • @LouisChabwera-y2w
    @LouisChabwera-y2w 18 часов назад +1

    Koma ndalama inampereka ambuye yesu,,, koma zoonadi izixi kuv ala makolala nkumalankhula za boza

  • @WilfredKazembe-i6q
    @WilfredKazembe-i6q 20 часов назад +2

    Theres no peace in malawi without black box

  • @rajabkjumbe954
    @rajabkjumbe954 21 час назад +3

    Press briefing yopanda Pake iyi

  • @HappyLuhanga-f8g
    @HappyLuhanga-f8g 19 часов назад +1

    Oro mufune oro musafune magazi a Mr chilima azaima poyera ndi pachoona

  • @ClementMindah
    @ClementMindah 23 часа назад +4

    Bishop nsusa sakunama report silikumveka awa akufuna chithumba masapusi

  • @HassanSaid-q8q
    @HassanSaid-q8q 17 часов назад

    Mwadya ndalama inu...iweyo utuluke chipembezo

  • @PeterNtengamanga
    @PeterNtengamanga 21 час назад +3

    Bishop msusa machine osaopa osafooka

  • @SkeffaKaifa123
    @SkeffaKaifa123 17 часов назад +1

    Bishop nsusa ❤❤❤❤

  • @MasterJasten-l2f
    @MasterJasten-l2f 20 часов назад +1

    Anyamata ojiya 5 pin azibusa ojiya 5 metre Malawi sazatheka

  • @HappyLuhanga-f8g
    @HappyLuhanga-f8g 19 часов назад +1

    Paja Malawi timasapotera zopusa zomangonvera gulu kusiya kunena chilungamo

  • @EsnartGirivin
    @EsnartGirivin 23 часа назад +6

    Anthu mukuputa nkwiyo wa Mulungu.mukukwilila chilungamo,ai zikomo

    • @PaulChafikirah
      @PaulChafikirah 22 часа назад

      Azibusa adzinyengo awa monga mulungu sanakuonetseleni mulibechoonadi mwainu mulikumbuyo Kwa MCP mukudziwapo kwanthu inu

    • @EsnartGirivin
      @EsnartGirivin 21 час назад

      @PaulChafikirah ndipo inu mhhhh ai zikomo

    • @RemitterFlik1130
      @RemitterFlik1130 20 часов назад

      Aka ameneyu akutsogolera mwamboyu ndanyamata ojiya awa asakupusiseni tikanaona ayasin gama Alexander kwambiri ndi azitsoholeri Eni Eni osati mahule azitumiki ngati awa

  • @WilsonKaunga
    @WilsonKaunga 20 часов назад +2

    What is wrong is wrong ,no matter how many people, calling themselves with good names can be there!!!!!

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 22 часа назад +3

    Aaaa sogoleli tangouzani atuluse black box basi

  • @HappyLuhanga-f8g
    @HappyLuhanga-f8g 19 часов назад

    It is really nice what Mr Msusa said Malawians sitimanvesabe what happened to Mr chilima

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 19 часов назад +1

    Zaziii habakuku is the best walezera eti, munganene kuli Black box, cholinga mudyenawo dzamisokho😂idyani koma mulungu akuona zomvetsa chisoni,

  • @JulioChiwalo-t4f
    @JulioChiwalo-t4f 22 часа назад +3

    Ana a njoka awa etiakukwilira chilungamo kamba Ka ndalama zamagazi zaMcp

  • @bonaventureChinkhandwe
    @bonaventureChinkhandwe 19 часов назад +1

    Ameneyo ndi bishop wa mpingo wa pamalo ponse mukupanga apazi zaziii inu mbuzi zokhazokha mfiti za chakwela agalu

  • @FernandoSande-d9o
    @FernandoSande-d9o 22 часа назад +2

    Ojiya adya za Chikangawa awa

  • @PhilipJulius-fm6mx
    @PhilipJulius-fm6mx 18 часов назад

    Fear money on Earth money is too powerful than God the creator n the love of it is the root of all evil

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 23 часа назад +4

    Pali Azibusa adyela akumidima ogonana ndi nkhosa zawo musamale mutha modzi modzi afiti amu Chikangawa inu

  • @AndrewLubero
    @AndrewLubero 23 часа назад +3

    Palibe muukambapo chanzeru Apapa,,,,,,mungopalamula nkwiyo wa Mulungu Apa,,
    Mudziwe kut mwadzi wa Munthu siosewela nawo 💔💔😭😭😭

    • @NapashaFavoured
      @NapashaFavoured 20 часов назад

      Azibusa akulu koma ometa m mbali m mbali ngati oyitanila,, zioneni mbava

  • @BenardKalilani
    @BenardKalilani 22 часа назад +2

    Mwadya ndalama afiti inu muku bisa chilungamo muikidwa pa mbalambanda

  • @RodrickPhiri-j8e
    @RodrickPhiri-j8e 18 часов назад +1

    Awa ndi atumiki abodza alimmanja mwasatana awa dyera too much
    Khope zawo maganizidwe awo chimodzimodzi azitsogoleri a mcp
    Take note bishop msusa asiyeni okha musaphatikize ndi nyasi zanuzo

  • @BrineKajawa
    @BrineKajawa 19 часов назад +1

    Kodi azibusa awawa anayamba afunsa kwa nkhosa zawo kuti akukalankhula zinthu za mtundu umenewu kwa a Malawi? Ndi chifukwa chiyani sadadzudzule zomwe adalankhula Reverend wa Nkhoma masiku apitawo zosapota MCP mu church? History is the best teacher. Let's remember the attacks that the bishops faced in the early 90s.

  • @GeoffreyEllias-m9l
    @GeoffreyEllias-m9l 22 часа назад +2

    M'busa ometa mbali kkkk mukunama2 abwande inu.

  • @maureengwiranani9096
    @maureengwiranani9096 23 часа назад +5

    Kodi slung ikuyenda bwanji apakkkkk. Azibambonso amanyada hatiii.kkkk

  • @Luwisnjiraduka
    @Luwisnjiraduka 23 часа назад +4

    malo mopemphelela mvula mukulimbana ndi zinthu zochita kuonekeratu kuti ndizinthu zopanda chilungamo

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 20 часов назад +2

    Palibe munganene chomveka apa chilunga ndichomwe alakhula bishop chija amalawi tonse tugwilizana ndi bishop okamba zoona,chikakhaka chisokenezo ndichomwe anabweletsa chakwera ndigulu lake pophaa chilima

  • @LennieNyirenda-w6p
    @LennieNyirenda-w6p 20 часов назад +2

    Tili limodzi ndi abishop msusa nane report sindinakhutire

  • @StanleyChamasowa
    @StanleyChamasowa 18 часов назад

    Azibusa ambuziawa opanda chilungamo agalu namachende chilungamo achibisa ndi ndalama

  • @CostanceLalli
    @CostanceLalli 23 часа назад +3

    Ngati mwadya ndalama inuyo mulungu akuwoneni inuyo

  • @MariaButao
    @MariaButao 19 часов назад +1

    Ku Malawi dzaka zino kwa dzadza ndi azibusa achinyengo.kale ma sheikh anali oopa Mulungu pano adalowa dyera lapa ndalama.musatitaitse nthawi Mulungu akuyenderani mwapadera nonse

  • @JumahIssah-d2n
    @JumahIssah-d2n 22 часа назад +2

    Nonse amene mugwiritsa ntchito dzina lamulungu popanga zoipazi ndithud kumwamba kulibe Malo anu assembles of god ndamene angateteze wakupha nzawoyo

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus 23 часа назад +3

    Nonse abusa angombe inu ndi zitsiru...makape okutha ntchito

  • @VincentKalata
    @VincentKalata 18 часов назад

    Chomwe simukutchulira mipingo yanu ndi chani ngt ndinu achilungamo,panyapanu bwanji

  • @JamesPhiri-h7p
    @JamesPhiri-h7p 23 часа назад +3

    Azisogoleri aboza inu monga nokha simuziwa kt anthu Aja anachita kuphedwa

  • @AdinKassimIman
    @AdinKassimIman 19 часов назад

    Kma chimakhala chani Anthu,chilungamo kumachiona kma kumafuna kuyankha zachamba

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 23 часа назад +3

    Asatana adyera awa, sazibusa ndithu. Mtendere wabwera chifukwa choti munapha Chilima. Agalu inu anthu oipa. Inu ndi andale osati amipingo. Palibe chanzeru chomwe ananena a komitiyo. Yakupwetekani a MCP

  • @kingSoko-wf4pe
    @kingSoko-wf4pe 20 часов назад +1

    Macadet amipingo anali pa press briefing lero amipingo ojiya

  • @MarySinjirani
    @MarySinjirani 20 часов назад +1

    Shame on you force profets

  • @DalitsoPhiri-sq5nl
    @DalitsoPhiri-sq5nl 22 часа назад +3

    Tell Mr kunkuyu and his petroit to bring out black box he tells malawian that a black box is there and it's safe, amalawi akufuna boxiyo

  • @edsonndalama2334
    @edsonndalama2334 17 часов назад

    Gulu la anthu okhulupilira za chikangawa party

  • @BrightZionga
    @BrightZionga 21 час назад +1

    Mimbulu mzovala za nkhosa shame on you only bishop msosa the true

  • @AndrewCosmasmpama
    @AndrewCosmasmpama 23 часа назад +3

    Awatu akudodoma doma akuziwa kuti akubisa chilungamo

  • @Jo-ok4yr
    @Jo-ok4yr 20 часов назад +1

    Zomvetsa chisoni kuthamangira za eni.bwanji sanakuikeni mu enquary ija Inu asilamu,lero ndiye akufunani,kupepela.

  • @edsonndalama2334
    @edsonndalama2334 17 часов назад

    Msusa wayankhulira ku mpingo wake, inunso madobadoba inu mukayankhire ku mpingo wanu wa MCP wo

  • @YassenYasin-v6o
    @YassenYasin-v6o 23 часа назад +4

    Zazi 😂😂😂 kusowa ngani

  • @KhungwahKalikokha-n9l
    @KhungwahKalikokha-n9l 23 часа назад +3

    Mwatumidwa inu ingodyani ndalama mwapatsidwazo

  • @SkeffaKaifa123
    @SkeffaKaifa123 17 часов назад +1

    Nsusa❤❤❤❤❤❤

  • @HassanSaid-q8q
    @HassanSaid-q8q 16 часов назад

    Bishop mukhale ndimoyo wopambana

  • @junaidiwen5052
    @junaidiwen5052 4 часа назад

    Mayankho osemphano ndi mafunso palibe kumakhonzeka pomayamba zinazi 😊

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 18 часов назад

    Asalamu alakimu sheih,,koma siudindo wakufa kwa chilima ayi, inu sheikh mutu wanu mamva inuyo musatiuze zopepela ayi ,report liti sheih sheih musatilakwitse azitsogoleli awutsilu inuyo ine sheih mussa ,palibe mawu omveka ,dziko lino palibe mtendele ngati chakwera anapha chilima never never muiwale

  • @OdalaBanda-i9c
    @OdalaBanda-i9c 19 часов назад +1

    Ma sheik mukwaonawo amadya nkhumba

  • @FlorenceMwamlima
    @FlorenceMwamlima 21 час назад +1

    Shame on you people tili kumbuyo kwanu Bishop simplicity Nokha

  • @MikeSangano-u8m
    @MikeSangano-u8m 23 часа назад +4

    Mukubisa mpingo mwachokera why,
    Takudziwani kale ndinu a Assembles of God,mwapatsidwa makobidi.munya muona,mizimu ya chilima ndi 8 aja ikuzunzani koopsa

  • @GraceChenda-q2g
    @GraceChenda-q2g 19 часов назад

    Mwadya ndrama za magazi::zizungu zauchitsilu

  • @alickkachepa3801
    @alickkachepa3801 18 часов назад +1

    Mwabitsa mipingo ndiku fotokoza za gawo lawo laku maliro 😂😂😂😂

  • @HappyLuhanga-f8g
    @HappyLuhanga-f8g 19 часов назад

    If sitisiya kukudzudzurani anthu adyera inu mulungu akuyankhureni

  • @GraceChenda-q2g
    @GraceChenda-q2g 19 часов назад

    Atsogoleri opusa kwambiri::kukonda kunyambita ndalama::atiwuze mipingo yawo:: kulumikiza malawi ena atafa?

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 18 часов назад

    Ndinu ojiya tikuonelatu ofe pa mphepopa

  • @GiftChiumbudzo
    @GiftChiumbudzo 19 часов назад

    Koma mulungu akuyenera kuchitapo kanthu kwa inu ayi ndthu kufuna ndalama kumeneko

  • @edsonndalama2334
    @edsonndalama2334 17 часов назад

    Inu ndi madobadoba a MCP awo akufuna apasidwe yodyera ndipo alibe mipingo awo. Enawo ngoyendayenda mu mchesi mu asakunamizeni kuti ndi ma faith leaders ayi

  • @HajieMtenje
    @HajieMtenje 23 часа назад +3

    😂😂😂😂 mukufuna ndalama zokagula ka ufa

  • @MudaMsukwa
    @MudaMsukwa 19 часов назад

    Oyambayo akuyankhula zichani mboli yake bwanj akuyankhula palibe

  • @LanjesiMaluwa
    @LanjesiMaluwa 17 часов назад

    Kungotiwonongera bundle yathu timayesa pakambidwa zamzerutu apa

  • @SteveKanongwa
    @SteveKanongwa 17 часов назад

    Winao akuti nyengatoni banja lake linatha chifukwa cha uhule

  • @jackalview7491
    @jackalview7491 20 часов назад

    Bishop Susa anena zoona,inu mwatumidwa ndi chikangawa

  • @MagieJames
    @MagieJames 19 часов назад

    Kusowa zoyankhula mabozawo sakudziwa ndani , Malawi pano anachenjera mwalandira chibanzi kukamwako palibe comwe tingave mukhalira yomweyo yamaboza mulungu akulangani azimai opanda nzeru mukutaniko kumeneko inu kubala makudziwa kapena imfa maidziwa mbuzi za mamina kwambiri

  • @Beatricelikangala
    @Beatricelikangala 22 часа назад +2

    Ambuye akukantheni

  • @AlexMphalasa
    @AlexMphalasa 23 часа назад +3

    Total nonsense may the anger of God be upon you all, what a shame

  • @AmosGeorgejunior
    @AmosGeorgejunior 20 часов назад

    Ndangoluza bundle yanga kumvera izi😢😢😢

  • @FlynessWinga
    @FlynessWinga 21 час назад +1

    Where is black box please?????

  • @mishecksipolo7153
    @mishecksipolo7153 19 часов назад

    Tranquility? Zizungu zofuna kupusitsa anthu mboli yako galu iwe😊

  • @GivenKitha
    @GivenKitha 18 часов назад

    Atumiki onyenga awa adyera awa God said in last days mudzawona athu adyera odzikonda,okonda ndalama owoneka ngati opephera koma mphavu yake alibe look kametedwa kokhako

  • @bernadettachirwa4728
    @bernadettachirwa4728 19 часов назад

    So, according to concerned faith leaders, imfa ya chilima ndi ndale?

  • @IgnatiousKaombe
    @IgnatiousKaombe 20 часов назад +1

    No salt

  • @HappyLuhanga-f8g
    @HappyLuhanga-f8g 19 часов назад

    Let's play together as a Malawians Kuti chilungamo chiwoneke

  • @ManuelMataya
    @ManuelMataya 15 часов назад

    I love Malawi 🇲🇼 🇲🇼

  • @SmilingCompass-vw5ns
    @SmilingCompass-vw5ns 20 часов назад

    Angotolana tolana kumamizila utumiki ndi anthu ojia koma mukunama kwambili mbamva inu

  • @rajabkjumbe954
    @rajabkjumbe954 21 час назад

    Mukayamkha nonse MA sheikh Nanu muli nawo muuizi

  • @starlonJames-qr4xl
    @starlonJames-qr4xl 20 часов назад

    ukawa ona ngat anthu opephela ayi ndinthu siyachipani cha umulungu ai awa ndi anthu omwe agwidwa ndi chipani cha mcp kt adzipanga ma adimvent kapena kt adzi bakila

  • @MosesDicostar
    @MosesDicostar 20 часов назад

    Ndkudikira bakili muluzi tv akululeni mbiri zanū

  • @wysonmaya
    @wysonmaya 19 часов назад

    wosewa chowonadi akuchidziwa koma ndalama ndi chilungamo zinadana awa asogoleli awa mulungu awapase chilango kamba kokonda ndalama

  • @PhilemonLloydGalawanda-tz2zb
    @PhilemonLloydGalawanda-tz2zb 20 часов назад

    Mwadya ndalama Inu azibusa otembereredwa kwambiri

  • @MisheckChangata-k7c
    @MisheckChangata-k7c 19 часов назад +1

    Mulibe mzimu inu

  • @MusaManati-ho4zf
    @MusaManati-ho4zf 19 часов назад

    Mmalo mosonkhana kupempha mvula apa......

  • @G00dwillPhiri
    @G00dwillPhiri 19 часов назад

    Chilungamo or mutachiphimba ndi ndalama, pangatalike ndalama yo idzaulula ndipo chilungamo cho chidzakhala pambsla, Banda,,, Guys, there's GOD above overseer of all that is on earth... "What is not known, does not exist. Check this out!

  • @ernestphiri5507
    @ernestphiri5507 22 часа назад

    Corrupted pastors only truth will set you free bigup our bishop

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 19 часов назад

    Kkkkkkkkkkk😂kuti pwiiiiiiii apa kungopwisa basi, ndisungire data