Mwinad ambr tinang'ezedwaditu 😂😂😂 ati ndfufute 🤣🤣🤣🤣 I will never stop watching Usauver Coz of Patrisha, Ganizani, Ngozo, Edo, Tonde, Abusa, Albert n Takondwa mmatha guys 🔥 apapanso mukubwera bho momwe mwawonjezera nthawimu zikubeberabeberabe ❤❤
Only this series have won my heart i really enjoy ngozo and Patricia's part the most koma ma part anthu enawo they are really spicing the episodes amazingly....big up to u guys. N.B. Piksy shd date Sangie chabwino or kwa 1 month only ❤😂
Let me go and vote for usauver as the best serie....ndifufuten
fufu fufu🤣
Anakung'eza🤣🤣🤣
This is getting serious first I was thinking kuti potaisila nthawi but then u people your trying to win our hearts aaaa inu munabwera kuzakhara
Exactly
It is growing 😅
Team Ganizani always ndikuseka basi😂😂❤
Keep up the good work guys
This is so beautiful more especially family ya hyphen 🎉🎉
Mwinad ambr tinang'ezedwaditu 😂😂😂 ati ndfufute 🤣🤣🤣🤣 I will never stop watching Usauver Coz of Patrisha, Ganizani, Ngozo, Edo, Tonde, Abusa, Albert n Takondwa mmatha guys 🔥 apapanso mukubwera bho momwe mwawonjezera nthawimu zikubeberabeberabe ❤❤
I tried watching this series in the past i never liked it koma gave it another go this series i think im hooked.. Loving it so far Gani ndi nyatwa 😂
Zilipobe zong'ezana koma anyamata inu kampolama mpakana 😅😅😅😅 ayi ndithu kwatilani musiye zibwana😂😂
Izikhala yaitali chonchi apapa zilibwino usauver team🎉
Mmene timati latha apa layambanso kubhebha🎉❤, nice one. Komanso Gani was Kampolama necessary 😂😂😂😂😂 Gani iweyo ndi 1
Hyphen Always Amakonda nkazi wake 😊 kulikonse alilimodzi 🎉 zobhebha keep it up Mon Kwa aunt Tina
Ntebe ndi baltasar engongaa 😂
Only this series have won my heart i really enjoy ngozo and Patricia's part the most koma ma part anthu enawo they are really spicing the episodes amazingly....big up to u guys.
N.B. Piksy shd date Sangie chabwino or kwa 1 month only ❤😂
Panopa nde ikumatalika bwino 🔥🥳🥳🥳 and this season et 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Share link we have to vote for this series otherwise i love this so much 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Usauver my best serie ever, next episode changu ma guy ,, Gani afotokoze bwino ubale waiye ndi Mai ake anzake😂😂😂😂😂
Ndipo straight
Kukutentha mmalo moyasa fun mukuyasa bulb😂😂😂...usauver🎉🎉🎉❤❤❤
This is getting more en more fun and interesting ❤😂
Amkolo of the year😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Km ngozo nd pat eshiiii kkkkk . Munasowa guyz musamatero! Very brilliant
Koma ine banja la Piksy limandiwaza
This is more than acting ndithu 😂😂
Kkkkkk km Tonde ndi Ganie HaHaHaHa they will kill me serious..
😂😂
Amakhala ngat ana
😂😂😂😂😂 ndaseka mpaka kutsamidwa
Ganie nd tonde they will kill me seriously 😂😂😂 anyway congratulations and keep it up 🎉
😆😆🤣uyu ndi Jabu...sangie akuti Jabulosi hiiii komaaa
Enafedi mwina tinang'ezedwa 🤣🤣
Ofunika mutifufute guys 😂😂😂😂
😂😂😂 tinang’ezedwa
😂😂😂
Aaaaahahaha😂😂😂
😂😂😂zoona, zikudabwitsa
Koma ganizani kaya unaganiza motani😅😅😅😅😅
Ati apa oau broz afika
Kumufufuta kenako theche akuti kampolama aaah koma anthu awa amacheza zotani mwati 😂😂😂😂
These guys ali mwalaaaa
N I have vote for them as best serie😂
Kampolama , 😂😂 tinakolana tinakolana basi tikakumana tizing'ambana mateche😂😂😂
Ndipo ndasekeramo kkkkk
Koma this Takondwa girl eeeeee akuitha
Ngati ndadya milomo ndi ya nsomba 😂😂
That Kid Character is Just Crazy 🤣
Koma achina @piksy ,mundikhululukila ,part iyoyo ya uncle akulalatayo,wa camera akuoneka ,next tym muzapange check bho bho,am big fan kwambili
Team yaganizan ndi hayehaye basi😂😂😂
Inenso ndaona pa glass paja😅
😂😂😂 gani fufufu ndafufuta 😂😂😂😂 kapolama😮
Mfana amakamba Albert yo ndi ndendende sikono😂
😂😂😂😂😂😂 Ndipo inu
Samaonekatu kkkkkkkkk!!!
"ine ndangoti mukunjoya sinnapemphe kuti mundigaile iyai... aah ee kodi nanga, atibweresere ka galasitu"🤣🤣🤣 Achimwene awo aakazanga
Jededayaaa kufunaaa kuposaaa Mr fowandede🤣🤣🙌
Camerayi muziwabwerekako a MBC .... So nice graphic
Ndipo😂
Episode masasuuuu munasitha ma G .... More feels from here Michigan...
Hagi ngt sikufuna ma born again akuhagana 😝😂Sitepe Baba gani 😅
Koma iweo umapezeka palipose
😂😂😂 munaikamo mr 400..... U rock guys 🔥
Akamati mayanga ukutani nawo iye alibe mtima wachiziwitso 🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Koma muli Anthu azipongwe umu for sure 😂😂😂
Athadzi awiri mnyumba imodzi ,mlamu amasuka Bwanji 😂😂😂..
Stepy father gannizan😂😂😂😂😂
Kkkkkkkkkk Eishhh 😂😂😂 akuti taziyang'ane mmene ukuonekelamo ungazifune wekha😂😂
Banja la hyphen labwelela m'malo mwake wow so beautiful
😂😂😂😂 Gani ndi tonde ndi azibambo opusaa😂😂😂
😂😂😂😂not yet done kom gani gani gani 😅😅😅😅this guy too much soup aaaaah 😂😂😂
I don't like watching films /dramas /series. But usauver won my heart 💯You guys, you are great
Usauver crew on fire 🔥 keep the fire burning madolo
Kampolama 😂 komwe wachokera sinduvesesa💔🙌😅 ndaseka kuiwala zoti ndili mu toilet😂
Hahaha 😂😂😂😂...at ngat ndadya milomo ndiyansomba
Yophweka kudya ndiyomweyo 😅
Uyu usamumvele kupepesako chonde akumvetsa pain uyuu😂😂😂😂😂
Fufu fufu, ndafufuta🤣🤣🤣
Koma Tonde ndi Gani ndi nkhani zina sure 🤣🤣🤣🤣
Ati m'mene uliri iweyo ungadzifune wekha 😂😂😂
Tonde man 🤣🤣
Am late but it seem like u bring us chips & mpunga wanyama
Kkkkkkkkk Kung,ezedwa kenako kuchosedwa,kkkk kuzagwila kampolama Koma Ganizani ofunika plot maguy
This is the best episode
Patricia zoona mfuso limenero,akhala thawi yayitali bwanji.Gani zaka 10 zakwana koma P wandisangalatsa 😂😂😂😂😂
Km Patricia iwey umandiwaza heavy😂😂🙌
Ndipo ineyo ndimasowa pomuika
Komanso usauver yii imatichosa nkhawa 😂🎉
😂😂😂 undifufute ndy anavuta 😂 ndinamung'eza ngat ndadya milomo ndi ya nsomba 😂😂😂
Gani end sweet daughter 🤣🤣🤣🤣
I will be waiting for you guys 🔥🔥🔥🔥🔥❤
Akuti Ngati ndadyamilomo ndiya m'somba basi😂😂😂 Koma tonde
Kome Edo eish😂 😂 hyphen mubwelerane ndi belita adona aja amatha but where is she ? Wasowatu
😂😂😂😂😂😂Gani and tonde mundifufute , fufufufu 😂😂I kampolama ndipo
Edoh 😂
❤😂😂😂Best apology is an action mesa
Koma ndaseka akut akuliseweletsa Dazi🤣🙌🤣🤣🤣
Ati ndiwe mulera nkhunkhwatu kwanuko eti😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Kampolama ndipooo 😂😂😂😂
Ganizan and tonde😂😂😂😂
Koma Gani chikazati swt step daughter🤣🤣🤣
Team gani😂😂😂😂😂 eeeeh at nakung'eza
km ganizani amwene azandipha 😂😂😂❤
A Edo ndi Albert ndi more fire ndithu🔥🔥
Mundifufute😂😂
Ndinakung'eza kalekale zija? 😂😂😂😂
Ati kampolama ndipo😂😂😂 Gani amakwana
I like today's episode so much 🥰
Hyphen Share cape ya Satori please yikumandiwaza
A Gani Ndi a Tonde, myfavourites
Koma Gani...akuti ine sindikufuna kukudyerani sindikuchoka pano....wandiwaza😂😂😂😂
Ndati ndikufuna chakumwa chakumwa 😂😂😂😂
Best actresses and actors here❤
Gani ndi tonde 😂 you will kill me 😂😂😂😂lol😂
Best of the best.....
Thanks for the long duration
A headmaster abwela ndi moto hahaha
Ababa gani 😂😂😂😂😂
Haha ATI unanding'eza. Kutikumbutsa childhood
Kwanuko ndiwe mlerankhungwa😂😂😂😂
Gani the Step dad 😂😂
Kodi Tonde ndi Gani wa munawatenga kutiko😂😂😂😂😂
Ganizani is now growing 😂😂
Dolo ka infinite Ganizan😅
Kma patricia kufusa wakuchimuna kuti akhara nthawi yaitali bwanji kma ukusunga gani wakuchikaz 😂😂😂😂😂
Patricia akuti anthu amangobwera kudzadya pamaso pa alendo😂😂😂
😂😂 ndipo patricia
Mulerakhungwa weniweni kulera mamuna wamkulu Ngati ameneyu 😅😅😅 Gani wakula kwatilani
koma Edo ngwabodza eeeeh😂😂😂