I think Chakwera he must resign guys because he lie to us us a Nation He give us a long information about the death of Chilima He didn't speak the truth on the whole sanga that been happening
Nanunso chotsani Ndale za Udani,be more civilized. Chakwera has nothing to do pa Ngozi ya Ndege yomwe yachitika ku Malawi. Remember at first zimamveka kuti Chakwera force Chilima kuti apite ku Maliro ku Mzuzu kenako MDF ndikudzalongosola zonse momwe zinakhalira nthawi yomweyo Adani a Chilungamo ndikudzasintha Tone. Tiyeni tiike kuopa Mulungu pa TSOGOLO.Tsikulina we will be answerable pa zomwe tikulankhula ndikuchita pa Dziko pano. Mulungu akuona
Koditu zinthu zonama ngakhale atazikonda Anthu 1 Billion zimakhalabe zonama basi ndiye mutha kumupopa nzanuyo but the thing is you are encouraging him to continue exposing his stupidity, Ignorance and foolishness.
Jane Assah ananena kuti a MCP anapita kunyumba kwake kukamuophyeza kut akapanda kuwina pa yenda mwazi.People never believed her but today see what they havee done to our Chilima
Munthu wanzeru zake akamvere iwe munthu wakuti sulikuno, umbuli uwu, black box imatengedwa ndi eni omwe anapanga ndege, nobody else muziwanamiza ma cadet anzanuwo achisiru inu
Koma inuyo muli ku joni ndiyeno mukutiwuza kuti tipite ku mademo mmmm iwe awuze abale ako ayambise mademo popeza ntchuma amadya ndi anthu andale ife tifele zayeni
Big boss you have freedom to tell as what you know osabisa pano wina aliyense chakwela sakukondwela naye chakwela is fack man munthu oipa kwambili ndiponso mulungu amulange kapolo ameneyo wapha chilima noh kubisa pano we will fight with him kut tikhale ndi freedom yabwino atill end of life
Time. Everything has the right time. Speak truth, and if you can defend it, stand ready to defend it with evidence. These videos will surely speak in your defence if at all they contain truth.
Chilima has become another God in Malawi and Malawians can not manage him, nkhani ya chilima azangoipondeleza ndikuwapatsa chi banzi alipansogolowo😢😢😢😢
Following closely until full information is shared & our action as malawians is required. Black box tiyiwone and hopefully, the data shouldn't have been tampered with by then .... Mawa following live kunonso
Zikhale akapitilize kugulitsa kaunjika...kunkuyu akapitilize zake za ulonda....Chimwendo akapitilize ulimi w fodya...enawo akudziwa komwe anachokera!....
I think Chakwera he must resign guys because he lie to us us a Nation
He give us a long information about the death of Chilima
He didn't speak the truth on the whole sanga that been happening
Nanunso chotsani Ndale za Udani,be more civilized.
Chakwera has nothing to do pa Ngozi ya Ndege yomwe yachitika ku Malawi.
Remember at first zimamveka kuti Chakwera force Chilima kuti apite ku Maliro ku Mzuzu kenako MDF ndikudzalongosola zonse momwe zinakhalira nthawi yomweyo Adani a Chilungamo ndikudzasintha Tone.
Tiyeni tiike kuopa Mulungu pa TSOGOLO.Tsikulina we will be answerable pa zomwe tikulankhula ndikuchita pa Dziko pano.
Mulungu akuona
Iiih abale
Chotsani ndale zomangoda anthu with no any valid reason. Chotsani ndani za tribalism
You gat my back chimwene,,,,we need more Pipo like you,,,, osaopa,,osatopa,, osafooka 💪💪💪💪💪💪
Koditu zinthu zonama ngakhale atazikonda Anthu 1 Billion zimakhalabe zonama basi ndiye mutha kumupopa nzanuyo but the thing is you are encouraging him to continue exposing his stupidity, Ignorance and foolishness.
Chilima is at peace! Heaven has welcome son of Malawi, he fought a good fight he has finished the race, RIP.
Amen
Osamawatenga a Malawi ngati opusa. Bwera uzapange mademo akowo ma propaganda omwe mukubweletsawa aphetsa anthu ku ntcheu. Ndeno inuyo musamangolubwa kumeneko
Jane Assah ananena kuti a MCP anapita kunyumba kwake kukamuophyeza kut akapanda kuwina pa yenda mwazi.People never believed her but today see what they havee done to our Chilima
Lestening and following up from zombaa
Mulungu akupase zelu zambiri broh ❤❤
Ndipo zoona
I agree with you on the fact that we don't analyze and digest what people tell us. lt looks like when it comes to political sense we sleep
Munthu wanzeru zake akamvere iwe munthu wakuti sulikuno, umbuli uwu, black box imatengedwa ndi eni omwe anapanga ndege, nobody else muziwanamiza ma cadet anzanuwo achisiru inu
Keep doing ur best.....we rally behind u
Enamu mungopanga support koma mulikunja bwerani
Iwe chitsiru ngati ufuna kupanga ndalama chifukwa choti utamike ndiwe galu
Listening from bembeke dedza surely this is un understable
Waiting patiently
i love the way you are putting your words bro ❤❤Big 👆
Koma inuyo muli ku joni ndiyeno mukutiwuza kuti tipite ku mademo mmmm iwe awuze abale ako ayambise mademo popeza ntchuma amadya ndi anthu andale ife tifele zayeni
That's true bwana auze mudzi wa kwao upite ku ku mademo ife asatiputse ayi
Exactly
We are waiting for you big boss
Please we are all waiting on 🫂
Big up to you brother let's change our nation
Wow we are waiting
Thank you brother
Live from Mozambique. Keep it up.!
Continue working 💪 hard 💪 🙌 🙏
Malawi wachema uyu
We are proud of your intellectual capacity Biggy.
We're waiting to hear from you.
He is trying to use you and you are supporting him?
Bweran my Malawi osamangolubwa uko inu
Following from England 😢😢😢 , Our Vice president SKC Rest in Peace 😢😢😢😢
Uyuyu wandikwana….
Ma speech ake oyambisa nkhondo basi 😢
Unathawa Bungu ku malawi usatipusise apa
That good New s
Let's go 🔥😁
We support you big boss mulungu akhale nanu
Nice work
They're now in panic mood. They underestimated Malawians on their plans because of greed and stupidity.
It’s too late now they underestimated
Big boss you have freedom to tell as what you know osabisa pano wina aliyense chakwela sakukondwela naye chakwela is fack man munthu oipa kwambili ndiponso mulungu amulange kapolo ameneyo wapha chilima noh kubisa pano we will fight with him kut tikhale ndi freedom yabwino atill end of life
Tsono iweyo uzatsogolere mademowo osati kumangokamba uli kwamereca pamene anthu kuno akuphewa.
Thank you for supporting the truth.
Live from Gaza
Even he must resign i suport u
Watching from pietermaritzburg south Africa
I am surprised Malawi as small in size as it is can it take more than 24 hours without tracing the plane??? Watching from here in Bulawayo
may Allah reward you big
Ipase 🔥🔥🔥🔥🔥
Yes we need people like you to change Malawi
Live from Moldova 🇲🇩
Time. Everything has the right time. Speak truth, and if you can defend it, stand ready to defend it with evidence. These videos will surely speak in your defence if at all they contain truth.
We are support you following from canada
We are support you following from Ntcheu Central BAWI near Nsipe
More fire from Dubai
Salute ..salute😂😂😂😂😂...kalata ya ku Donier ndaikonda 😂😂😂😂😂
Company ya Donier inatsekedwa kale coz sinkapanga ma profit, it was Germany company.
We r behind u bro, keep it up bro
Izo nde mzeru big boss
Keep it up my gee 💪
Chilima has become another God in Malawi and Malawians can not manage him, nkhani ya chilima azangoipondeleza ndikuwapatsa chi banzi alipansogolowo😢😢😢😢
Mvuto inuyo mlikunja nde ma demo tipanga bwanji?
Penapak naniso m'matipusitsa
Your respect broo
Wasuta maso kufiira ngati fisi
Okupha inu muyaluka
@@vytwistthelion98 katuleni umboni baba osafa ndi mtima
Big up bro🎉
Truth on the ground big
❤
True malawians are bitter
Following sir
We're waiting brother
Koma maliro awawa eee zonena zachuluka kwambiri yoooooh kusowanso choti utolepo tsopano
Most of the enemies you have today are people you once helped in life.
Zoona zake!!!
Ma demo achan mmalo mopanga zthu mwa Bata
Tiyen tisiye mzimu wa skc uziuztsa mu mtendere
Osat uonelele zipolowe
I have questions
1) is this guy here in Malawi?
2) you say remove chakwera ,what is the alternative for chakwera?
Pamtumbo iwe ukufuna uphetse anyamata Mwana Wa njoka pita
Keep the fire burning big Malawi needs people Like you to be developed no fear and never give up
I agree with
I only voted in 1994 but am coming back to vote again to push out MCP.
Khondo yiyambe agalu awa akuwononga ziko lanthu 😊
Nkaka, kudzimva kwabasi, dziko mpaka kulitenga kukhala mmanja mwawo, mpakana kuyamba kuwopsyeza ngati nthawi ya kamuzu chimenecho chilungamo. Koma awona polekela. Ngati Zakanika asayambe kupha anthu Andale ndi atolankhani mwatiwonjeza a MCP.
Fact
Shaaaaaa
Umakwanitsa Khad
Amene mumaimba come record your songs at my music studio in Lilongwe...
Tili mbuyo mwanu bwanji 💪💪
We are following you always brother come on.
Khad,, ndugwirizana nawe kwanthunthu, ndi utsilu kwabasi kulamulidwa ndi mbuli, Ng'oma, kunkuyu, chimwendo banda Okula mitima okhaokha
We're on you brah zamasimba ife Eni Dziko ai
Following closely until full information is shared & our action as malawians is required.
Black box tiyiwone and hopefully, the data shouldn't have been tampered with by then ....
Mawa following live kunonso
We love you brother don't worry
Zikhale akapitilize kugulitsa kaunjika...kunkuyu akapitilize zake za ulonda....Chimwendo akapitilize ulimi w fodya...enawo akudziwa komwe anachokera!....
👍
🎉🎉🎉
Achakwera amangoba ndalama mboma
Achimwene munthu samadzinenera yekha room yomwe mwalowayo ndi yodziwika a military akupezani.
I support that idea of going to dornier company to ask information I think going to help, don't stop bro ulemu wanu
The company was closed down in 2002
Go deeper aseh,tilipambuyo pako
Zoona big mumakwana
Iiiiiii Mau mboni enawa aaaaaa ine kwanga kulira
🤝
Anthu ofunila dziko la Malawi zoipa nde anthu ake inuyo. Mukadadikila report ituluke. Malawi 🇲🇼 wake si walelo simungatinamize or kutipusitsa.
Ndipo ndakwilatu apapa
Koma ndiye takwiyadi😢
That is chilungamo brow.
Friends turned nemesis
Koma ine ndikuona ngati Kell Kay ndi Janta asazachezenso. Chifukwa Tay Grin kukwatira kudzamuvuta chibwerereni coronavirus disease uja sakuonekanso
😂😂😂😂😂😂😂
@@theodoralimeza5945 eti amwene 😂😂😂
Asukuluzeni big athu amenewa atitopesa
Tyen nazon boss man til nanu limodz
Kodi akuona ngat kuphako nde nzeru amusaketu ozamuvotera ine nde aiiiii
We're loosing you soon bro😢...so painful am feeling pain for you my brother
😂😂😂😂
Mbuzi iwe..bwerani muzapange mademo iweyo ndazibale ako