These African drums are really therapeutic they have something connected to healing whenever I listen to them my bones nerve points stops aching as well as the mood swings. I need to come and get better and healed.
Am watching from UK I love you guys, but mfumukazi and namoyo are sorting Mr shop right the pangolini in white boots booting nchaso ( Malawian organic distilled gin.)😂😂😂😂😂😂❤❤❤❤❤❤
Eeeeeeeeeee lululuuuuu moto kuti apa ndiye ikupita kokuya mpaka kwa song'anga ? Akulu akulu mukuyitereka sopano kuseri kuvula zovala ndi mankhwala a wanji amenewo ?
These African drums are really therapeutic they have something connected to healing whenever I listen to them my bones nerve points stops aching as well as the mood swings. I need to come and get better and healed.
where are you from if I may ask, coz you always seems to impressive
Hhj
Mfumukazi boza watching from moçambique tete
Watching from moçambique tete
Ndimaona ngat ndikhala oyamba kuonera😂❤
A Chitsime amakukondanitu a Nagama simunawadyetse zungulira khonde koma 😅😅😅
Watching from Johannesburg south ,Mfumu kadzi ndi dilu❤
Chitsime was best actor in this episode... I can’t wait for next week. Want to see whether Malawi sangoma is more powerful than Nigeria.
Ati ikokele nthawi yakoyo kkkkkkkkk padela my guy❤😂
Namoyo mpaka kwa babalawo 😂 eeeee next week kuchema
Mmatha gyz simupala ❤❤❤
Ia zikomo kwambili frora suya mulungu akufungatile lomba wayamba kuphika nsima yakupya
Comedy iyiyi yimandikomera even ndikubwereza yomakomabe kuwonelera. Ku honeymoon kuchepa ❤❤❤
Watching form South Africa cape town fumumkazi mativesa kukoma
Am watching from UK I love you guys, but mfumukazi and namoyo are sorting Mr shop right the pangolini in white boots booting nchaso ( Malawian organic distilled gin.)😂😂😂😂😂😂❤❤❤❤❤❤
Mmakwana
Kkkkkkkkkkkkkkkk 😂😂😂😂😂😂😂😂😂❤❤❤
Nyimbo mumaimbazo enafe sidzimatisangalasa ai
nzachikhalidwe....akazayamba kujambulira town azizaikamonso nyimbo zachi town🤣
Mwayakhatu
@@NoelKhwimba-bh3ts Tinaona kuti titerotu kaya takhonza kaya?
Watching from south Africa Bloemfontein
Am watching from Zambia much love you guys ❤❤❤
watching from capetown keep it up guys mukutinvesa kukoma
Sanaonepodi nzunguu 😂😂😂😂
Watching from Moçambique
Kamtini mpaka kupangira mankhwala 😂😂😂😂😂😂
Chitsme malangizo ngat munthumunthu😂😂😂
Witching from kempton park more fire mfumukazi
Nice 1 watching from kape town
Kkkkkkkk km muphana achina giring'ande
Good job team 👏 👍 👌 . I love ❤️ you all❤
Watching from Capetown
Mr Shoprite, man of the moment
Job well done 👍 you are all excellent 😂😂😂😂😂
Ndiye taikokeretu nthawiyo 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Popanda padera Mfumukazi ilk chabe 😂😂😂😂😂
Kkkkkk mercy paka wapita kwa Ng, anga
Ndava chakwera wanga
Nice
A Mercy basi avulidwa ndi sing'anga 😂😂😂 Naye Solomoni akuyang'ana sapato kumiyendo ya Farai 😂😂😂 Padera waipatsa moto ndi nkazi wake kubwalo lamfumu 😂😂
Koma guys shop imeneyi kuti mumulipile Morosoni, Komanso Agili atengemonso , farai momwemo koma muli win?😂😂
More fire
Anthu muli pachangu nkuwonela
Ndipo
Koma Namoyo is the best character in Mfumukazi..amatha acting
Yes ku mfumukazi amandipangira act bwino
Km Farai guyz anakoz eeee More 🔥
watching from michigan mumakwana
U kondekitala ku thekelanithekelani😂😂😂😂😂
Nice one, watching from Cape Town
More fire guyz
Milandu tinayisowa kwambiri 😂😂😂
Km chitsime😂😂😂
Koma iyi ndiye Mmmm flora suya simunaphetu ndinthu ndipo chenjeso Ku mdyangu musapuseso ndi isi please ndinthu madamu we love you ❤❤ Koma mumve
Kwavuta uku mmmmm wena apenga misala nditu
I can't wait another part
Koma mfumu kazi amakwanisa
Koma next episode kuchema
Koma molosoni naetu alimo😂😂😂😂
Padera uzamukumbuka namoyo usachite chibwana kkkkk
Alipo Nagama?
Kkkkk mpaka kwasinganga achita nawetu asinganga kkkk namoyo
I'm proud you guys🎉
padera the great kkkkkk et osayikokela bwanj kkkkkk
One love
Falai kkkkk
Namoyo tsopano alendo sukuwaona???😂😂😂😂
Kkkkkk km farai ndi ankolo akewa eeeee😂😂😂
So nice
Ellen ati bwanj mmaoneka chomcho 🤣😂🤣🤣
Padera ndi mkazi wake, Chitsime nae ndi mkazi wake zokoma
Namoyo🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🙌 mhu
Kma Padera ndimbambaande kma Joshua alikut kkkkk
Kkkkkkk anamoyo mupenganazo zamakhwarazo
Is it possible to have the songs in this drama. Anyone to assist?
Aaaaaaa nthawi ikuchepa ine ndiri mbali yanamoyo akadxi apadera anapita kosaka ndalama kusiya banja namoyo kutola tinene kuti walakwa ?
Km Falai aaaa
Eeeeeeeeeee lululuuuuu moto kuti apa ndiye ikupita kokuya mpaka kwa song'anga ? Akulu akulu mukuyitereka sopano kuseri kuvula zovala ndi mankhwala a wanji amenewo ?
Namoyo❤❤❤🎉🎉
Yalelo mbola aah tingoonela anthu omweomweo aah
Molosoni mpaka kuthawira ku toilet kuli kuopa the pangaron😅😅😅
🎉🎉🎉
Km apadera kulalata kkkkkkkkkk😊
Kkkk km mercy, amuna ake ati amene amakutayisila nthaw kupatula bambo a joshua??
Padela sadzatheka ❤❤❤ guys
Koma kkkkk che Jackson chitdime 😂😂😂
A chisime ulemu wanu 😂😂😂😂
I really want to know kuti Jackson Chitsime wachepa nyama chifukwa chani?
Kukula basi, komaso sikuti paunyamata wake anali onenepa
Koma muma chedwa
Farai you r pretty 🥰
🎉🎉🎉🎉🎉 mfumumkazi 😅😅😅
First to watch 😊😊😊
Wamva iwe kkkkkk
Mumativesa kunong'a
Koma nalero ai zikomo 😂😂😂😂😂😂😂😂
Munasowatu anagama😂
😅😅 km2 jakisoni chitsime
Dankeni waying'alula ya achitsime kunoooo
😂😂😂😂😂koma farai kkkkkkkkkk
Nice one
I'm proud of you guys 😂😂❤
Mlandu umeneu nd watch out
Namoyo kufotokoza mwanvemvemve
Apadela avutatu 😄😄😄
Mumakwana❤
Kusakwatira et😂😂😂😂😂😂😂