Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Koma mdyangu imanagwiritsa ntchito anointing original fukwa nde timayikonda from middle east 💃💃♥️💃♥️ inabwela kudzakhala
Nice comedy bg up frola❤
Kkkkkkkk gain aborn
Banja likunjoya umu ndila Sasoka
Zowona eee
Madzi okolopelawo ukadamuthira nao mulelembayo akuyamba dala iyaaaa
Ching'ax mpaka kulila😂😂😂
Kkkkk Queen ndi chemwali ake muli boh featuring Mulelemba m'busa onyenga kkkkkk
Tikudikiraso Ina frola mumativesa kukoma kuno ku cape town 😂😂😂😂
Keep the fire burning guys mmakwanira 🔥🔥🔥Shout-out to Flora Suya mmakwana mama ❤❤❤Welcome back Mr Mdyangu 😂
More fire ukali wanu..tasowa chizungu chamai mdyangu
Ndipo Ali kut kaya
Alipo she has been ill but she is better now
Chiphwanya bwela ukwatile ine suzakhumudwa 🤣🤣🤣🤣
Kkkkk
Osanditenga ine bwanj🤣🤣🤣🤣
Koma jerous down manyumba akufunika apetedweeeTimakonda ma movie Anu ngakale tili kutali we lo❤ you more
Baja Latha losayamba 🤣🤣🤣🤣 chiphwanya ndi 12345678910,11❤
Faka iweee
Koma tifane ndi amunako ndi perfect match 😊😊
Komanso mai shokoshoko😂😂
Watching form South Africa cape town mativesa kukoma
Bambo aju apopa kwambili 😂
Queen uzakhala gain aborn kkkk koma ndaseka
Osamadelera ayi😅
😂😅😅😅
Koma chiphwanya ma banja ndiye ndi osayamba ndi bweran ine undikwatile 😅😅😅
Junior azioneka junior-yodi 😂😂😂😂😂
🔥
Koma chiphwanya hahahah
😂😂
Nice gyz mumatiimirila❤
Sanatenge angonyamula😂
Tafika❤❤❤
Make chiswe...ai
Ndilipano kudikira kuti Mercy adzapanga chani akadzapeza Qeen ali m'nyumba mwake
Koma bola ndidzapeze nkaz ngat wasasoka
Mumakwana tikuphuzira nawo zambiri makalidwe god bless all people's of you
ayi mukutinvesa kukoma watching from cape town cant wait for next week mukutipasa zochita pa kapa❤❤❤
Ati bambo a Manuel chimwene mukuzuzikira kumeneko chan. Tiyen tilerere manual... Lol
Kumuchondelera
I always proud of you guys keep it up 🎉🎉🎉🎉❤❤
Kwachema
Koma Muli mitu Umu amvekere lero ndiwamachanza kkkkkk
Achipwanya 😂😂😂😂 ayi zikomo
Khangati ukupanga Aamina 😅😅😅😅
Koma plz 😂😂😂😂😂😂😂 zafika pa Love😂
Sasoka ndi Tiffany🔥💯
Tili pano coz of you guys
Zili bwino kwambiri pitilizani
Koma queen 👑 athera mmanja mwaamuna
Mposo
😂😂😂
Kkkkkkkk ine ndigona ndi phwete guys,mlelemba ayi zikomo 😂 kuti junior azikhala junior di ,wakumana di zakeyu bro🎉😂😂
Sasoka masiku ano wafatsatu, wasiya kuseketsa, ali bzy ndi nkhani za banja
Ayi mumativesa kukoma guys mli apa ❤
Next week kuchema
Durban south Beach point tikumva kukoma 😂😂😂😂 mulelemba kulalikila
😂😂 koma mulelemba uzamenyedwa ndi ubusa wakowo
Tandigaileni contact ya mkazi Shokoshoko please
Sasoka n his wife on 🔥🔥🔥🔥
Kkkkk km2 queen. Nawe mtengwa wamdyangu wapaesa pakwanu pachtengwapooo eeet
Ching'aning'ani ndiwe opupuluma uzafa imfa yachoima Galu iwe. Hule
Kma mdyangu tamusowa😂
Sasoka unapeleka Mon wanga
Mwatibesa kukoma kuno ku Zambia
Watching from South Africa , Eastern Cape ,keep it up guys
Kodi conedy ya m'dyangu mumaxedwa kuponya xifukwa chiani!??!?
Family ikukulatu kwabweraso junior
Mai shokoshoko njala ya 3days mpaka eeee ai ndiye dzakuvutanitu ndiye mutani apa?
Sasoka ndi mkz wake akukonesa zinthu
Mai shokoshoko eeeeee olo bambayo sangalibe sithani musamagolusa zilizonse ngati wamisala
Face explanation yake kkkkkkkkkk what a boss Ching'axy
Hahahahah😅😅😅😅 akuti m'bale wamdikumbutsa uja anakwera mu mtengo
Koma gututu nkadziyo akukukhalatu ndipo ndi chipha dzuwa
Kwabwera junior
Mulelemba sure azatibulidwa
😅😅😅😅nyengo imasintha a Qeen
Koma mayi shokoshoko eish munaiwelenga kukaimba Fon yah queen koma mphuma
Big up gyz
Akut ku White House kkkkkkkkk ochiphwanya mmmm😂❤
😂😂😂komatu mlelelemba uzamenyedwa ndi ubusa wakowo
Koma queen ndi sister wako iwe 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Flora suya ndiwe dolo and receive your flowers❤❤❤
Junior sasoka watulukira Kkkkkkkkkkkkkkkkkk
Che mulelemba mumatha kod ubusau munakauphunzilira kut?
Mayi chokochoko mwangokongora koma yoo kharidwe
Mulelemba bodza 😂😂 anointing wanji ? kungoyenga ndalama bwee😂😂😂😂😂
Koma Sasoka ukuonjeza mmmmmm kkkkkkkk love you all
Junior kuzangotera kwachema🔥🔥
Funso langa kod Mr Mdyangu ali kut it has been a while sakuoneka
You guys your seriously keep ur comparative
😂😂😂 ziliko pamudzi pa mdyangu ayi mumakwana guys
Nditsokatu ameneuja koma ndaseka😂😂😂😂😂😂
Lululuuuuu an'dyangu gemu yapheduka ana amasiku ano opanda ulemu
Juuu wafika
Zikwama mwatengaaa?😭 Ambuye akuyang'aneni kkkkk km yeeah
😂😂😂😂 Mphwanga juu kadule mang'ina uku
Eshhh opanda kuonera iyi ndimadwala
Junior azioneka mwau junior 😂😂
More fire sasoka & tifan mumaitha
😂😂😂 Mai Shokoshoko inu ndakita okwiya❤❤❤
Queen iwe ndie susowa pokhala😂😂😂
Koma sasoka ndi tifan mumapanga zenizeni
Mai shoko shoko kulusatu 😂😂😂😂
Mai Shokoshoko mudya mwano wanuwo basi😂
Mulelemba azathela manja mwa athu 😂😂😂
Koma mdyangu imanagwiritsa ntchito anointing original fukwa nde timayikonda from middle east 💃💃♥️💃♥️ inabwela kudzakhala
Nice comedy bg up frola❤
Kkkkkkkk gain aborn
Banja likunjoya umu ndila Sasoka
Zowona eee
Madzi okolopelawo ukadamuthira nao mulelembayo akuyamba dala iyaaaa
Ching'ax mpaka kulila😂😂😂
Kkkkk Queen ndi chemwali ake muli boh featuring Mulelemba m'busa onyenga kkkkkk
Tikudikiraso Ina frola mumativesa kukoma kuno ku cape town 😂😂😂😂
Keep the fire burning guys mmakwanira 🔥🔥🔥
Shout-out to Flora Suya mmakwana mama ❤❤❤
Welcome back Mr Mdyangu 😂
More fire ukali wanu..tasowa chizungu chamai mdyangu
Ndipo Ali kut kaya
Alipo she has been ill but she is better now
Chiphwanya bwela ukwatile ine suzakhumudwa 🤣🤣🤣🤣
Kkkkk
Osanditenga ine bwanj🤣🤣🤣🤣
Koma jerous down manyumba akufunika apetedweee
Timakonda ma movie Anu ngakale tili kutali we lo❤ you more
Baja Latha losayamba 🤣🤣🤣🤣 chiphwanya ndi 12345678910,11❤
Faka iweee
Koma tifane ndi amunako ndi perfect match 😊😊
Komanso mai shokoshoko😂😂
Watching form South Africa cape town mativesa kukoma
Bambo aju apopa kwambili 😂
Queen uzakhala gain aborn kkkk koma ndaseka
Osamadelera ayi😅
😂😅😅😅
Koma chiphwanya ma banja ndiye ndi osayamba ndi bweran ine undikwatile 😅😅😅
Junior azioneka junior-yodi 😂😂😂😂😂
🔥
Koma chiphwanya hahahah
😂😂
😂😂
Nice gyz mumatiimirila❤
Sanatenge angonyamula😂
Tafika❤❤❤
Make chiswe...ai
Ndilipano kudikira kuti Mercy adzapanga chani akadzapeza Qeen ali m'nyumba mwake
Koma bola ndidzapeze nkaz ngat wasasoka
Mumakwana tikuphuzira nawo zambiri makalidwe god bless all people's of you
ayi mukutinvesa kukoma watching from cape town cant wait for next week mukutipasa zochita pa kapa❤❤❤
Ati bambo a Manuel chimwene mukuzuzikira kumeneko chan. Tiyen tilerere manual... Lol
Kumuchondelera
I always proud of you guys keep it up 🎉🎉🎉🎉❤❤
Kwachema
Koma Muli mitu Umu amvekere lero ndiwamachanza kkkkkk
Achipwanya 😂😂😂😂 ayi zikomo
Khangati ukupanga Aamina 😅😅😅😅
Koma plz 😂😂😂😂😂😂😂 zafika pa Love😂
Sasoka ndi Tiffany🔥💯
Tili pano coz of you guys
Zili bwino kwambiri pitilizani
Koma queen 👑 athera mmanja mwaamuna
Mposo
😂😂😂
Kkkkkkkk ine ndigona ndi phwete guys,mlelemba ayi zikomo 😂 kuti junior azikhala junior di ,wakumana di zakeyu bro🎉😂😂
Sasoka masiku ano wafatsatu, wasiya kuseketsa, ali bzy ndi nkhani za banja
Ayi mumativesa kukoma guys mli apa ❤
Next week kuchema
Durban south Beach point tikumva kukoma 😂😂😂😂 mulelemba kulalikila
😂😂 koma mulelemba uzamenyedwa ndi ubusa wakowo
Tandigaileni contact ya mkazi Shokoshoko please
Sasoka n his wife on 🔥🔥🔥🔥
Kkkkk km2 queen. Nawe mtengwa wamdyangu wapaesa pakwanu pachtengwapooo eeet
Ching'aning'ani ndiwe opupuluma uzafa imfa yachoima Galu iwe. Hule
Kma mdyangu tamusowa😂
Sasoka unapeleka Mon wanga
Mwatibesa kukoma kuno ku Zambia
Watching from South Africa , Eastern Cape ,keep it up guys
Kodi conedy ya m'dyangu mumaxedwa kuponya xifukwa chiani!??!?
Family ikukulatu kwabweraso junior
Mai shokoshoko njala ya 3days mpaka eeee ai ndiye dzakuvutanitu ndiye mutani apa?
Sasoka ndi mkz wake akukonesa zinthu
Mai shokoshoko eeeeee olo bambayo sangalibe sithani musamagolusa zilizonse ngati wamisala
Face explanation yake kkkkkkkkkk what a boss Ching'axy
Hahahahah😅😅😅😅 akuti m'bale wamdikumbutsa uja anakwera mu mtengo
Koma gututu nkadziyo akukukhalatu ndipo ndi chipha dzuwa
Kwabwera junior
Mulelemba sure azatibulidwa
😅😅😅😅nyengo imasintha a Qeen
Koma mayi shokoshoko eish munaiwelenga kukaimba Fon yah queen koma mphuma
Big up gyz
Akut ku White House kkkkkkkkk ochiphwanya mmmm😂❤
😂😂😂komatu mlelelemba uzamenyedwa ndi ubusa wakowo
Koma queen ndi sister wako iwe 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Flora suya ndiwe dolo and receive your flowers❤❤❤
Junior sasoka watulukira
Kkkkkkkkkkkkkkkkkk