Simunamve pati chakwera akanakhala kuti akuyendetsa bwino boma lake anthu bwenzi akumukuwa? That's why I said the problem is governance a Malawi tikukwiya chifukwa chosayendetsa bwino dzikoli kupha plus kuba luck of wisdom these are major problems
Iweo chakwera wakoyo nosenu mapwala anu chakwera ku mwela kuno ndie sitikumufuna ndi ku mpoto tizamuponya miyala mwana wa gwape ameneyo wamva iwe mbuziwe ,akumantchedwa mtalimanja ujatu akazangosemphanisa ma vote azafa ngat mbuzi ya chibudu ndi miyala kapena kumuzinga kumene mzake wathawatu ziko lokhala lake uko ku Mozambique 🇲🇿 kunoso ena alithawa ziko awonaso si ku church ⛪️ kuno ai
Zinthu sizili bwino yes koma we need respect inu otsutsa musatilowe kwambiri ngati malawi ndi wanu nokha, musamagwiritse ntchito dzitsiru kuwononga dziko la malawi, honestly we need respect Malawians this madness must end
RIP chikangawa 😢😢
Ngati akukuwidwa kwawo Ku eraz eeeee mbola kwambili
Utsogoleli sumakhala wokakamira 2025 tizabayana basi
These people are not hating the president but the governance
Haibho what r u talking about.kkkkk who is leader.some decision always coming from who
Simunamve pati chakwera akanakhala kuti akuyendetsa bwino boma lake anthu bwenzi akumukuwa? That's why I said the problem is governance a Malawi tikukwiya chifukwa chosayendetsa bwino dzikoli kupha plus kuba luck of wisdom these are major problems
Who is governing if I may ask?
Bro let's not go far with this
Kusowa ulemu Kwa presented of Malawi
Chikangawa Anya koma Ngati akukhuwidwa bwana wa kukuyu ndindani kamanganya kkkkk
Lilongwe mwandinvesa kukoma kwambir keep it up and continue
Convoy chonchi in time of fuel shortage or even in good times is unbelievable & irresponsible of this president & his government
Kwachema......AMalawi atopa tsopano.....Kulamulira Dziko simasewera ayi.....😢😢
Yomweyo galuuyu akutizuza
Chakwera must go people are tyrd of him
Vinyo vathadi 😂😂😂😂😂😂 yoooh
Tidzaonese mkwiyo nthaw yavoti bwanji abale
mkwiyo tayambapo........ sitikumufuna
Koma chakwera akanakhara wonganiza akanangotura pasi wudindo palibe chomwe chikuyenda mavuto okhaokha
😂😂😂😂😂
Mikwiyoooo Mikwiyoooo yakhwithimalaaaaa!!!!!!!
Mikwiyo Mikwiyo yagandapalaaaaaaa !!!!
Ibwere Mfumu Ina idzatiweruze .
It's just shinkangawaw must have to leave early at state house I'm in the estan cap 🧢🧢🧢 APM is my favorite for everyone
Bwana president anthu a kukasiya okha sangakuwonitsen check your steps
Paja amalilila kuyendesa dziko ndilimenelotu aziona CHIKAKULA PATUKA
Kkkkkkkk kwachema ku Malawi kuno basi chakwela anthu sakumufuna kukala kofuta kudzawina ndipo uyuyu asayelekedze kubela kudzachitika zoopya kwambili ku Malawi kuno uku ndiye kuli Lilongwwe mumati kwanu sopano tiyelekedze ku mwelaku kukakumana nadzo zotani
Tili okozeka kuchotsa mbuzi imeney nyawu
Kumwera komweko alikonso ena a boma ndilomweli 😂😂 . And zonsezo zikuchitika sizinayambe lero . Owina azawinabe basi
Olira sitimamutora mawu mkamwa😀zilirani nthawi yanu😂 Chakwera my vote 🔥
Kkkkkkkkkkkkkkk
Zako zili pabwino, uzazindikira bwino 2025
Zako zili bwino koma kumakhala ndi umuthu pali athu ambiri omwe akuvutika... Ana a njoka
Ayi mwachita bwino mwationetsa chifukwa nsete zimenezi zikuzinamiza kuti boma ndilomweli koma sakudziwa kuti tisintha president 😅😅😂😂😂
😂😂😂😂😁
Kma galu amenayo watiojezatu
Wakupha chilima mbuzi yamunthu
Zinali chimozi mozi mbuyomo ,apanso zili chomwechi ulendotu uwu.kutopa Kwa amalawi ,osamalubwalubwa zomwe simunganthe kukwanitsa.chigalimoto Cha mchenga chakukanikani ,kumpha munampha chilima kuja si solution yot muzalamulirenso kma mwazipalamilira mkwiyo mizimu ya anthu amene aja ikuvutisan simunat izi ndizo zowawa zoyamba
Inuso munamutsika sichoncho 😆
Zili bwino, more fire 🔥 🔥 🔥 🔥 🔥 🔥
Chakwela wazinyelela ndithu😅
kunavutatu
Nthawi yoti akonze a MCP inapita, ndipo sangakwanise panopa.
Zilimani osamangotaya nthawi pano .
TAMUTOPELA NYANI AMENEYU NDE AZITI ABWERESO 2025 AFUNA AMALAWI TIZAKHALE CHANI. MFITI YA PRESIDENT
Umunthu ndiofunika munthu atha kukhala ndizeru kma umunthu ulibe zimakhala choncho
Mulungu anamulanda ulemelero pano chongotsala chikwangwani.
Ma president onse after kamuzu pa maulamuliro wawo zinthu sizinafikepo povuta mmene zafikira panopa, president wamtundu wanji osaganiza
Mmmm kmaaa Lilongwe yakwiyatu ndiyeee winaukuoona zimenezi ndiye uziti ndi kuimira MCP.. Ineoo uisovebwino.. Kwachema... Lilongwe dzuka iweee mulandu sukomera chinasi warakwawarakwa basi. Apazavuta odala
Bola kwinako chingokuwidwa , koma kuno chizagendedwa
KOMA NDIPOOOO KUMACHISUNGILA MATUMA AMIYALA CHITSIRU CHIMENECHI
Ndipo live chikangawa watikwana basi
Iweo chakwera wakoyo nosenu mapwala anu chakwera ku mwela kuno ndie sitikumufuna ndi ku mpoto tizamuponya miyala mwana wa gwape ameneyo wamva iwe mbuziwe ,akumantchedwa mtalimanja ujatu akazangosemphanisa ma vote azafa ngat mbuzi ya chibudu ndi miyala kapena kumuzinga kumene mzake wathawatu ziko lokhala lake uko ku Mozambique 🇲🇿 kunoso ena alithawa ziko awonaso si ku church ⛪️ kuno ai
During campaign they might kill him, mark my word palibeyi akumufuna afa Ndi tambala wakeyo
😂😂😂😂😂😂 RlP chakwera 😂😂
Ndikuti kumeneku
Olo apakati mutavotera chakwera wanuyo angawine? Muripo angati chigawo chapakati? Za ziiiiiiiiii
Mmmmmmmhu ndalira Malawi wavuta anthu tikusowa popumira
This ll be in my book called THE HISTORY OF THE RIDERS
Malawi wanga😢😢😢
Dzuka Malawi Dzuka 🇲🇼 Dzuka Malawi 🇲🇼
Kkkkkkkkk chakwera mayooooooooo ine wamwalila
Ndipo mukamatere unga'amba zithuzi mukutipatsa mangolomera bola mukadangosiya ukundiye kutenderera chakwera mukupangaku kuti tidzamuvotere gulu Ife apakati sitingavotereso president wakumwera ndiye kufuna kudzavutika kumeneku
Bodzatu limenelo udzinamiza
Chingamu chalala basi, tichilavule😂😂😂
Munkhalira edit yomweyo azanu akutipula pa ground MCP boma ndilomweli
Manyi enieni.
Amanu inu zaziiii galu
Ngakhale mumuyipitsire mbiri koma ife tidzamuvotera tili pheeee mulira muwona ndipo musadalire otsutsa
Ndie kuti mukupezeko cholowa koma malawi ngati amene ndikudva kuwawa sindingamuvotele
Kkkkkk kod chimwendo alikuti chisilu chimenechija chisiwonela eka
Nzakale kale izi
Magalimoto ndi akale pano anaika zima Toyota Prado za 2024 ija awo anachosa
Mademo ukukuwakana ajatu ndi amenewo uziwapeza kunseo komweko
😂😂😂😂😂😂 zowona abale inu.
😂😂😂😂😂😂
Boma ndilomweli tingosintha president basi😂😂
Hmmmmm ayi zikomo.zomvetsadi chisoni.
Amalawi ameneyu akumanana ukutu ndikuyamba chabe
Kkkkkkk koma ndaseka kumwela so nkomvetsa chisoni otsadziwa kuti mvula yagwa muli yambakata musewu shame mudakadyabe zitedze next year zidutsa pamenepo kungodalila zawulele mukhawula
Ndikumwera Kumeneko kkkk kukamphata ase wanva
Umbuli ndi ndale sizigwilatu kamphata ili ku mmwela??
ineso ndwanyawu but this government is full of shit
Kkkkkkk watha vinyo💔💔💔
Zaboza izo kuribe ku malawi
😅😂😂😂😂
Lilongwe tigawana iyi 😂😂😂😂
Tatopa naye uyu
Tivota ndife kuno Inu phee mudya chitedze mpaka mukagwada Kwa pitala wanuyo
Zamuvuta chakwera amaona ngati ndizophweka kulamula dziko
Chikangawa avomereze ziko lamukanika😂😂😂
Adani luu kukamalizitsa makombo kkkkk
Wati kwana chakwera mwana ochokera kuchibwenzi dzamalongotsoka
Gendani guys
Mwana obadwa kuchibwezi watiudza ntanyiwa sham chakwera
Malo ake akuti chitsilu iwetu ukufuna kunamiza athu
Akanakhala mtsogoleri wa nzeru atapanga quit chikangawa anampha Vp wake chifukwa cha position
Eeeeee
Kkkkkkk muli bo qmalawi ife sitidya ndqle zopusa
Thanks so much
Kulilongwe nako anthu ayamba kumukuwa, arsenal pa kwawo, onse omene amati boma ndilomweli pano ayamba kunyasidwa naye, this is too much.
Mbolatu
Peter paja ankagendedwaso koma ankakupatsani ndalama mukamazipenter palibe pa bwino a Malawi
Kulibe kuti chigaao cha pakati anthu Ali happy ndi a chakwera
Mmmmmmm
Zisintha zinasintha bwanji nthawi ya jb atangowina apm xinasintha after chaka ndalama inankhazikika Nkhani ndi utsogoleli ameneyu apite watizunza
Ndipo magalimoto akewo oyenda apha mwana kwathu nsewu opita kwamalembo surtaday
Mbolozao a mcp aonaso
Chowona Nzako chapita.mawa chili kwa iwe.
Zinthu sizili bwino yes koma we need respect inu otsutsa musatilowe kwambiri ngati malawi ndi wanu nokha, musamagwiritse ntchito dzitsiru kuwononga dziko la malawi, honestly we need respect Malawians this madness must end
Kodi otsutsa atani ???? AWA ndiaMalawi musadane ndizipani
Can you respect someone who do not care about your welfare?
They should really wait for votes not what these people do
Nthawi yake yatha chikangawa Chakwera.
Madera enanso winayo anenatu asaonengati apambana nkwawo komweko aonanso
Achakwela adziwe izi.anthu,safuna kuti achakwela aziwagawila ndalama akubazo ayi.chomwe, akufuna amalawi, katundu atsike mitengo,akumizi adzitha kulowa muma shop kukagula kathu koma zomwe akuchita achakwela,alibe ntchito ndi munthu aliyese.chschikulu,analowetsedwa,pa u president basi ndiye izi,ndi nthawi yoti aziwe ngati president amalowe ndi vote achakwela chawo palibe,olo anabelu azaname zowakokela a chakwela sadzalamulilaso malawi.mpaka,kale chifukwa chopanda zelu
Munthu ukakhala kt ukuchita bwino ambiri amakukonda
Kkkkkkkkkkkk anthu atoperatu🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉😅
Kunena chilungamo chakwera akutizunza akanangozisiya
Zoona zake ndithu
Sizidayambe lero izi even nthawi ya Peter zinkachitika nkhani ili pamavotedwe
Mangolomera achani akupha chanu pale bvomeleza zakukanikani
Achoke kumene
Comment @edenBrigadia iwe anthu alima bwa fertilizer Ali okwera😂 think wise pachilungamo bs
Achoke ameneyu watikwana
Wait for votes not these ignorance
Awa sangawine olo atabela,, nde mukati wait for vote inunso mukunama
U think or Uli iwe athu adzidana nawe akauvotele
Kumtumbo kwachakwera President opanda chisoni kunyini kwamake
Iwenso pa nyelo pako pankholo pamako galu mbolo Yako ndiwe chitsilu
Bola ilo
Inu athu tatopa nawo achikangawa
Apm ankapatsidwa ulemu iyeyu ndiye wata kuti apatsidwe ulemu? Komanso muyeso omwe umamuyesela nzako nawenso omwewoooooooooooooooo aziwona kuno adzagendedwa
Nkhondo iliko 2025
Mulungu amulanga chikangawa😂😂😂😂😂😂 ndipo sanati