Ndikhare oyamba kuchita comment,izizi zikuchitika Chifukwa cha mwini wake CHAKWERA. Atatuluka kufuna kulankhura kwa a MALAWI sanapereke chisogozo kwa POLICE malingana ndi mphavu zake. Ankangopempha apolisi kuti apake investigate pankhani ya zikwanje chikhalirecho anthu akuone atatenga zikwanje malo mongomuwuza kulu wapolisi kuti alamule apolisi akamange anthu aja ankangozungulira. Chiwembu cha ku MBOWE, DOWA,Aford party adamenyedwa, komanso sewu wa NCHINJI anayika road brock kumaswa magalimoto zonsezo adapanga a MCP sanamangidwe. Anthu wa akubwezera siolakwa ayi pokhapokha azikwanje aja amangidwe zonsezi zidzatha
This is the beginning of the signs of the later days spoken from the bible. Lawless shall increase before the falling away of many. Apocalyptic events have started.
Ndikhare oyamba kuchita comment,izizi zikuchitika Chifukwa cha mwini wake CHAKWERA. Atatuluka kufuna kulankhura kwa a MALAWI sanapereke chisogozo kwa POLICE malingana ndi mphavu zake. Ankangopempha apolisi kuti apake investigate pankhani ya zikwanje chikhalirecho anthu akuone atatenga zikwanje malo mongomuwuza kulu wapolisi kuti alamule apolisi akamange anthu aja ankangozungulira. Chiwembu cha ku MBOWE, DOWA,Aford party adamenyedwa, komanso sewu wa NCHINJI anayika road brock kumaswa magalimoto zonsezo adapanga a MCP sanamangidwe.
Anthu wa akubwezera siolakwa ayi pokhapokha azikwanje aja amangidwe zonsezi zidzatha
Bravo nchalos well done ✅
Muching,ambe kwambiri mwanvaaaaa😂
😂😂😂😂 Kumawi kokoma
Guys muching'ambe chonse mwachita bwino kwambiri agalu amcp watikwana kwambiri
Well done ncalo akhulupiledi kuti cikangawa mmalawi muno sitikumufuna akungoba, kunyenga kupha palibe ca mzeru akucita.Waziyambisa yekha ku lilongwe kukhapa anthu opanga mademo tie nazoni a mcp nonse panyoo panu ndi cikangawa wanu yemweo
Rise and fall of chikangawa government of MCP
Boma loyendesedwa ndi mbava komanso zigawenga .....chakwera akuyenera kuchoka basi .....mbuzi ya munthu imeneija
Apakire azipita kwao kukasiya galu ameneyo chakwera nayeso amatuma azikwanje
This is the beginning of the signs of the later days spoken from the bible. Lawless shall increase before the falling away of many. Apocalyptic events have started.
kkkkkk koma ndiye yakwiya ndi mizimu sure
Ndanva kukoma kwambili palibe chifukwa chosekelela satana ayi
Iye akuona ngati kuti akamapeleka mphavu kwa nyamata azikwanje aja ena sangatheso kupanga kalikose
Km ngat akumukana athuwa chakwela naga bwanji mulungu kumwambako mmmmmmm mizimu yakwiya zd
Ichoke fiti imeneyi❤
Achoke 😂😂😂😂😂😂
Muvi oyang,anila
Vuto ndi chakwelayo coz anthu akumawasira ulanuliro manja mwake
Adzifuse chakwela paizizi ndikoyamba pambiri yandale kuchitika izizi matsoka ake amenewa kulonjeza km osakwanilitsa ndikoopswa zd
Waziyambitsa ekha izi chakwerayu chifukwa akumakondela anthu achigawo chapakati .
Kma sizabwino,,😂😂😂
Itchoke itchoke A Malawi adatopa
Mavuto alipo kwambiri
Chakwera sakufunikanso ayi ndi kummwera asazabwelenso ....
Mbuzi ya munthu
Akhulupililedi kuti sitikumufuna
😂😂😂😂😂😂 zavuta abusa repaint and go back to the work of God
Sakakwanitsako umbava wakulila
Kkkk
Ku nchalo kulibe makape.A sena sasekerela nyasi
Dziko lomwe mulibe asogoleri oopa Mulungu ma drama sakutha Amalawi tukapanda kusamal Mulungu atikwiira tikukhala dziko lomwe mwadzaza ziwanda zasatana Mulungu atipase sogoleri wachikondi ndi anthu ake izi sdzingachitike ayi
Vuto analephweretsa mademo anaziyamba ok amcp
Ndiye mwapindulanji za ziiiii, USAVAGE
Apindula kuti asamamuone sakufuna kumuona
Nawonso anachita zimenezi 2020 mlngo umene umamulinga malo nawonso udzalingidwa ndi omwewo.
Inu zikwanje zija mumapindura chan anthu anyau inu azipita kwao kukasiya
Chakwera must fall more fire
Akabwera police kungowayang,Ana ndi diso limodzi madzuro pano ndikuwasatira kwawo kuongola bwino bwino
Chakwerayu ndiozuza koso chigawenga
Nchalo sigawa kamba
Azipita azikanyenga azake a mcp
Azipita kubusa
Analakwaji chakwela???
Analakwanji chilima?
Achita bwino
mwachita bwino anyamata..... akagwere uko....