Mr. President Chakwera was elected by Malawians to fix the problems left by the previous DPP government. Instead of addressing these issues, he has been busy traveling from one country to another, using our foreign reserves. He claims these trips are for our benefit, yet we see no results. The country is facing serious challenges, and now he wants Malawians to support him despite his failures. It’s a shame that some continue to support wrongdoing, but we will not starve in silence. As the president travels, Malawians are suffering. Prices of basic goods are too high, and life is becoming harder every day. We were promised a better life, but things are only getting worse. People are struggling to find food, pay for school, and access healthcare. It feels like the government is ignoring the problems we face. We need a leader who listens to the people and works to fix these challenges instead of focusing on personal benefits.
Guys koma chikangawa atha akuononga ndalama zanthu kwambiri dzabwera ndi kanthu uyu mr president your time is over seriously 😑 will don't need you again go back to chipiku business
Apatu chakwela akuchita bwino chifukwa ife amalawi ndi anthu wosayamika munamuchosa peter kuti sakupanga bwino ndiye apa mulungu akukuphunzisa china chake kuti amalawi tinapanga mistake
Nchifukwa chani atola nkhani a MBC okha ndiamene amafunsa Chakwera? A Malawi tilibedi mtsogoleri koma President tilinaye. Kuyrndayenda! Mavuto ali phwi!
Kod koma kumalawiko anayamba wabwerako president waziko Lina kucheza kwanji koyenda Muthu mozi iye samafuna kuyenderedwa kod galu opanda zeru uyu kumangoyendayenda hule lalimuna
Ine ndilibe nthawi yomvetsela zomuyamikila chakwera he is a hartless president mfiti satana uyu anthu akuvutika koma he doesn't care anthu akudya chitedze ku machinga or kukawayendela chitsilu cha president oipa mtima kuposa satana koma Mulungu mwini chilichonse akuonatu one day ayankha kulira kwa ana ake asazione kupambani
Maulendowa mukuti NDI aphindu, manga nchifukwa ninji chuma chathu sichikupindulila nzika za Malawi Koma nzika za mu MCP zokhazokha. God will at any cost punish us selectivity because of lies on the expense of the poor
Whatever kaya zomwe akupitiliza zopindulira ife km tatopa nazo coz he always asks help kmno what have we done with those helps kmno chomwe unagwetsela kwacha
Ayi tikonze pamenepa mai chakwera si mayi wa fuko lamalawi siwona ndi mai wa fuko la a nthu aku Lilongwe kukasiya komweko ine ayi,mai wa mtundu wanji osapita kukayamwitsa ana ake ku machinga komwe njala yafika powoosya
Chitukuko chanji galu iwe mfiti , umangolakhula ngati uli ndi nzeru koma uli muthu ofoila, iwe yako ndiyakhupha basi yomwe taona ife , amalawi inetu uyu ndiphaa akundinyasa kwambili
Peter mutharika said
We have a president but we don't have a leader
Ndipo kwambiri
Holiday after Holiday let's be honest this guy it's living his Best dream life, selling the layman hope 😢
Asilikali pofunika uyu akupitaku asakabwelertso, azapedze miyala pa airport ndi jinga za ka banza
Mr. President Chakwera was elected by Malawians to fix the problems left by the previous DPP government. Instead of addressing these issues, he has been busy traveling from one country to another, using our foreign reserves. He claims these trips are for our benefit, yet we see no results. The country is facing serious challenges, and now he wants Malawians to support him despite his failures. It’s a shame that some continue to support wrongdoing, but we will not starve in silence.
As the president travels, Malawians are suffering. Prices of basic goods are too high, and life is becoming harder every day. We were promised a better life, but things are only getting worse. People are struggling to find food, pay for school, and access healthcare. It feels like the government is ignoring the problems we face. We need a leader who listens to the people and works to fix these challenges instead of focusing on personal benefits.
How will i forget SKC? His soul continue rest in peace,
Forever in our hears
People are dying with hunger the man of country just go there and there god is not sleeping never
Ine ndi wa mcp koma palibe chazeru chomwe chikupanga president wathu
iwe nde munthu.
Bola iwe unaganiza bwino m'bale wanga
Kkkk muzamuvotelebe bas osamutaya kkkk
Zaziiiii anthu akuvutika ndi njala muzipatala mulibe mankhwala anthu akufa kusowa chithandizo Basi maulendo uku ndi uku ziko osasintha muvaso wagwesa kwacha eeee tilipamavuto ineso basi ndipite konko ku 🇬🇧 💃🏻💃🏻
Akuchita kufanana ndine wosaphunzira zochitika zake kumangoyendayenda ngati mbuzi yosamagirira pa chingwe mmmm usakabwerenso kumalawi kuno🙆♂️🙆♂️
Ambuye mupheleni mundege momwemo ameneyo
What kind of President is this....and he still do promiseles
Ndalama zimene akuyendelazo sanga paste anthu tikufa ndi njala,😢
very an unfortunate !!!!!! God give us wisdom Malawi is at Stake
Inuyo kuyendako mukungoyenera kutero, cz mpando wa upule munawufunatu abusa,😢 ndiye paja mbuzi imadya pomwe yamangiliridwa, Nanu dyerantuni zanu, inuyo simunabwere kuzatumikira a Malawi ayi,, koma family yanu isangalalale 😢😢😢😢😢
I born in freedom country where there was leaders not president like this nyapape God will deal with this fool president
Malawi Is A Failed State.....under Chakwera......
JB akubwelatu komweko be careful
Ndithu abwere nsanga
Ngati akuwelenga comment iyi adziwe kuti ife tikumufuna
Guys koma chikangawa atha akuononga ndalama zanthu kwambiri dzabwera ndi kanthu uyu mr president your time is over seriously 😑 will don't need you again go back to chipiku business
Chakwera zopanga zako ndizochimwisa kwambiri, ndipo ukhoza kumuyankhulitsa munthu udyo, Chilima uja anali akatundu koma iweyo chakwera panja penipeni.
Kd Zina sangamatume anthu ena km chimunthu ichi kukonda kuyenda akatero agwetsa kwacha kapolo uyu tikhara bwanji otukuka akungoyenda yenda komaso kuba ndalama za Malawi chakwera walanga Malawi ndpo waika ziko lathu pamavuto
Chadabwisa anthu mu speech ya achakwelayi ndi chani ?
Ndipo sindikuchiona chodabwitsacho koma ndangoipidwa ndi ulendo opanda phindi kwa a Malawife@@JosephKamoto-k5j
Vote yanga I voted for chakwera but I regret because of the pain he has brought to me
Awa atitha ndiithu 😢😢😢😢
Chakwela mmmm ayi ndithu muthuyuakuyenda tisaname ndipo Malawi ali m'mavuto akulu ndipo akadali m'mavuto
Palibe chingamveke chifukwa anthu akufa ndinjala iyeyo palibe chichitika iye nde phindu ndichan iyeyo akunjoya ndi azibale ale pamene anthu akudya chitedze
Msonkhano wa nambala 80 adziwe kut azapitako ena this is is nonsense kulipo ndikuononga misonkho yathu ndegeyo isakabwelele kuno ife tatopa
Apatu chakwela akuchita bwino chifukwa ife amalawi ndi anthu wosayamika munamuchosa peter kuti sakupanga bwino ndiye apa mulungu akukuphunzisa china chake kuti amalawi tinapanga mistake
Ngati boza 😂😂😂😂 Peter amalakwa chani
Nchifukwa chani atola nkhani a MBC okha ndiamene amafunsa Chakwera? A Malawi tilibedi mtsogoleri koma President tilinaye. Kuyrndayenda! Mavuto ali phwi!
Pobwela kumeneku sindidabwa kwacha ikagwaso
Mutukul pakhom umalandila ndiwe t maviako kukuyu mbolo yako pam na chakwera
Mtukula pakhomoyo kwaenafe kwathu sanafike, kusonyeza Kuti Malawi ndi wawo
Mtolankhani moti angofunsa koma akuesera kufotokozera zomwe a president akukachita ....what kind of reporters are there at MBC........
I don't like this guy anymore,God help us please!
AState of emergency under chichewa board leader
Amathandiza iweyo Ife Siti kuwona phindu eeeee tili pamavuto😢😢😢
Machendeako boy uribechison ndidziko rako nde mayiyo arikukamwa nyindu umuze nyero wake ayendebwino😢😢😢😢😢😢
ine ndiwa MCP...KOMA at least akanamutuma MAnganya to represent him.chanzeru palibe apa😂😂😂😂
Munthuyu zimafunika aitanidwe afusidwe basi. Anthufe tikuvutika iyeyu akkuononga ndalama zathu.
Kod koma kumalawiko anayamba wabwerako president waziko Lina kucheza kwanji koyenda Muthu mozi iye samafuna kuyenderedwa kod galu opanda zeru uyu kumangoyendayenda hule lalimuna
Ine ndilibe nthawi yomvetsela zomuyamikila chakwera he is a hartless president mfiti satana uyu anthu akuvutika koma he doesn't care anthu akudya chitedze ku machinga or kukawayendela chitsilu cha president oipa mtima kuposa satana koma Mulungu mwini chilichonse akuonatu one day ayankha kulira kwa ana ake asazione kupambani
Rubbish president forever
Ntchitozo ndi zabwino,kulakwako mkupha ,anthu,
Ndikumene,kumanyasa Amalawi
Maulendowa mukuti NDI aphindu, manga nchifukwa ninji chuma chathu sichikupindulila nzika za Malawi Koma nzika za mu MCP zokhazokha. God will at any cost punish us selectivity because of lies on the expense of the poor
ndalama zomwe akuonongazo , sangawagulire chakudya amalawi omwe akuvutika ndi zoona,
Mulungu akuchitile chifundo
Umayakhula fundo zakho ndthu km kt ukwanise.chabe ndthu watikwan ndthu.ndye muwon Peter muthalika sanalonjeze chithu osachitka mayaz ndchifukwat sanayambe sapasidwa zin lodabwisa
Koma Monica naye mwati ndi munthu wanzeru ???Chingovomera zilizonse
Ndege imachagidwa per hour
How much kukafika ku USA
Ma allowance
Bwanjii osangopanga zoom meeting
Zafuwa basiiii
Pamenepo akamabwela azitiuza kutimizlngoyatu yagwa chiliga choti abwezele ndalama zomwe walnogazo😂😂😂😂😂
Bola mimba za family yake zikukhuta iye vuto alibe, munthu opanda chisoni ndi myoyo ya anthu ena😢
President ofoira
2030 iwetu uzakhara ulipanjatu suzapitiliza kulamlira mtukura pakhomo unapasa ndani
The most stupid headline I've ever seen 😅😢
Can you manage. Sorry brother we are dying because of you
Eish komatu kuyenda
Chakwera patumbo pako iwe munthu ochitisa manyazi kwambiri nyasi yamunthu iti
Chakwara kuyenda Ngati Traspotar Koma chikangawa noses
Inunsotu muzibweretsa ma topic a phindu pa page lanuli tizitha bundle nzopusazi?
Mr Moyenda eish tizamva ndiumphawi bas
Palibe chanzeru chomwe akuchita chakwera😢
Akat a Malawi akhala akuvuti panopa tasiya kuvutikako chuma akungononga ameneyi
Kodi mai chikangawa chidzungu amatha? Why i am asking? Sindinamvepo atalankhula or comment even m'nsonkhano wa chichewa.
Guys kodi ife amalawi tinatani😂kodi kufansa kwayife kunatani asilikali akumalawi ndi mbunzi ndipo patumbo pawo akuti asilikali apolice ndimanyi eni eni
Nfiti yayikulu mwafiti onse ndameneyu khopezo Ngati akhwezule
Economy Ili patio pamenepa mwezi uliwose kuyenda koma zovuta
Ulendo umenewu ndi wa number 268 chiloweleni m,boma zaka 5 zisanathe eeish that's wy he want to sell island yanthu😢😢😢😢
A very unfortunate nation
Paja amkagwira kuchipiku anazolowela kutulusa mushop.ndiye angalephele kudyela ziko
Whatever kaya zomwe akupitiliza zopindulira ife km tatopa nazo coz he always asks help kmno what have we done with those helps kmno chomwe unagwetsela kwacha
Ine kungoti chakwera ndi mbuli kwa mbuli zonse bibulo makate
Tisiya Bwanji Kumuda .....ameneyo Unga yopita iyeyo yomaliza ndi imeneyoyo
Etieti akulemba Mutu waziiii chisamudera nchiyani pamenepo
Aaaaa iwe zitithandiza chn wayamba kuyenda 4 years yonsei chilipo chasitha 😅😅😅
Eishee kom chitsilud ndichimene anthu amachilemekeza eishee phindu lake bs ndikutaya misonkho yanthu awa Allah adziku endela mwapadela dela iwe
Ukadakhala iweyo ukadatani kuzolowera kutukwana bas palibepo kumalawi kuno mtsogoleri bas sadzapezeka olo okomera OSE olo utakhala iweyo udzakhumugwitsaso athu
Boma lamasomphenya samatuma wina😂 ngakhale wina amufunire imfa akhalabe ndimoyo kaya otukwana sasintha akhalabe chakwera, kodi m'buyomo atsogoleri samapita kunja? Simunamuvotere zisakuwaweni,
Mwinamudziwe kuti phunzo mumatukwana lija ndi promotion yake 2030 wooooo
Ayende timutisiye sangave sinapalibe anga pange action chaka Chatha kale uyu adzachoke chifukwa chamavoti koma apa sizingatheke inu anthu akufa ndi njala Pano AIP sikudziwika kuti ithekha kapena ai sakusamala zawathu timusiye chaka Chatha kale tithana nae
Ayi tikonze pamenepa mai chakwera si mayi wa fuko lamalawi siwona ndi mai wa fuko la a nthu aku Lilongwe kukasiya komweko ine ayi,mai wa mtundu wanji osapita kukayamwitsa ana ake ku machinga komwe njala yafika powoosya
Kodi maiwa a Monica sangakhaleko panyumba ulendo ulionse ali komko eee ai ziliko
Ndie chodabwitsa chomwe chayankhilulidwacho ndichani???
Kod kulibe Muthu Wina Kuti Atha kumutuma kod
Koma Bambo ameneyi nzeru alibe ndpo nd manyaka enieni🚮🚮🚮
Boma ndi lomweli chikangawa pile, kwacha ikugwa ndipo mafuta akwela oye ali kuunga phew judy's misonkho yathu
Chakwera ndi munthu wovetsa chisoni
Zaziiii iyaaaaa
Chingogwa kumwamba nachoso mesa chinatigwesela wathu chikanagwa kumeneko Ambuye talolani uyo ndioyipa kuyenda yenda mmmm
Koma Munthu uyu mmmm chokamba chagwera mkati watikwana kwambiri
moti amipingo mabungwe anthu tonsefe kulephera kumufusa munthuyu?.
Oyendetsa umugwetsele ku chikagawa
🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
mpakA misonkhano 79 😮
Boma ndilomweli 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂🎉🎉🎉😂😂😂😂😂😂😂
Simuchotsa black box
Munthu akuchuta kufanana ndi falawo
Onena analipo, koma kusamva kwathu
Koma amaiwa anayamba apangako zachitukuko kapena kutsegula timabungwe ngati mai wafuko? Kapena nawo 😂ndi atinkenawo oti alibe focus ina iliyonse ? Chifukwa sindinamveko chomwe amapanga amaiwa koposera kumango londola kulikonse ngati chikwama chapule
Moses ndw galu uzion zoyakhula ulimbe manyaz kd
Bola ndengeyo ingosowa mmalele mommo
Apa ndie mukuona kuti zinthu zilibwino or pali kutukuka apa....or mukungosamala zamimba yanu basi
Galu wa president
Chitukuko chanji galu iwe mfiti , umangolakhula ngati uli ndi nzeru koma uli muthu ofoila, iwe yako ndiyakhupha basi yomwe taona ife , amalawi inetu uyu ndiphaa akundinyasa kwambili
😢koma uyu yekha nde 0 pa 10
Bola usaduse ku chikangawa otherwise
Mbuzi yamuthu kukonda kunyenda mbava hiiii