President chakwela ndi wamwanotu alibe nazo kanthu kuti anthu ati chiyani iye akuchita zimene iyeyo akufuna basi.kuno ku south Africa a Ramaphosa samayenda ngati chakwela ayi.chikangawa ayi
Madala King 👑 cobra 🐍 ku chokela muzinda wa Maputo inetu ndi mapemphelo 🙏 angatu ndi MCP ituluketu 2025 mwinaso ifeso amene tilikunjafe mtendele tidzawupeza Born kalindo ulemu waketu Allah adzimupatsa moyo wa utalitu
Mmene munkalemelera inu muja mesa munkamanga page house ma church a 50million kumanga ma lodge mu zenzamu kugula ma plot ndiye iwonso zivute?? Ngati simunalemele nthawi ya dpp basi zanu izo
Ine ndikuona ngati Boma ili lazama kwambiri ndi ntchito zakumidima. Chifukwa ndiye lakhazika chete ndi kumata pakamwa anthu pamodzi ndi azipani zosusa. This is not normal at all........ Sangatenge gulu la anthu onsewo kupita nawo kunja pamene Malawi wayaka moto ndi mavuto.
More fire 🔥 Booooon kalindoooo 🔥
Kopuma mkumda basi.
Keep on pushing ameneyo anthu akamamudandaula sapeza mtendere azingoyenda choncho ngat wapenga😊
Boooooooooooon karindo the DC
President chakwela ndi wamwanotu alibe nazo kanthu kuti anthu ati chiyani iye akuchita zimene iyeyo akufuna basi.kuno ku south Africa a Ramaphosa samayenda ngati chakwela ayi.chikangawa ayi
Exactly!!!
Lilipodi siku Lina aMalawi kuzatichela
Awa a bon kalindo muntima munazaza nsanje kwabasi kulimbana ndi munthu oti samayankha ali ena akanachita manyazi
Ndpo chikangawa wanyanya ine ndiona kt amapangila dala kumayendayenda ayiwala zonse mmene anthu amavutikila kt alande boma kumapatsa iye mmmm😮😮😮😮 satanic weniwen
Live DC
Ine chakwera amandinyansa kuyambira kale
Anthu panopa akudya chitedze pomwe ndalama zikusakazidwa. Mulungu akuoneni ndithu.
Madala King 👑 cobra 🐍 ku chokela muzinda wa Maputo inetu ndi mapemphelo 🙏 angatu ndi MCP ituluketu 2025 mwinaso ifeso amene tilikunjafe mtendele tidzawupeza Born kalindo ulemu waketu Allah adzimupatsa moyo wa utalitu
Mcp szachoka mmboma
And chipani chilichonse chikuzapita chokha chokha pa ballot
Kodi mawu a kumayambilirowo ndiye kuti nokha simmadziwa kuti samanveka?
Kasiya boy sazamva
The DC ❤️❤️❤️
Hahahahaha 😂😂😂😅 the DC anyani
Fisi ndi Fisi ngakhale mutamugoneka pa Bedi, adzilowa pansi pa Bedilo ndikumaphwasula Bedilo.
Zoonad zedi brother
Iiiii uyu president wamitsala pafika Malawi pano kutenga anthu chigulu kumawononga ndalama za amalawi ANTHU AKUDYA CHITEDZE ENA GAGA aaaaa KOMA MCP MULUBE CHITSONI NDI ANTHU INU AGALU KWABASI
Awa sanabwere kuzathandiza anthu, anabwera kuzalemera.
Mmene munkalemelera inu muja mesa munkamanga page house ma church a 50million kumanga ma lodge mu zenzamu kugula ma plot ndiye iwonso zivute?? Ngati simunalemele nthawi ya dpp basi zanu izo
Munthu wosamva ngat uyu sindinamuone...Chakwera wationesa evitevite
Afera moyenda momwemo chimwalilireni chilima anakhalako pansi ameneyo Ngati alibe mtendere
Aziyenda sanati
Ine ndikuona ngati Boma ili lazama kwambiri ndi ntchito zakumidima. Chifukwa ndiye lakhazika chete ndi kumata pakamwa anthu pamodzi ndi azipani zosusa. This is not normal at all........ Sangatenge gulu la anthu onsewo kupita nawo kunja pamene Malawi wayaka moto ndi mavuto.
Koma Mulungu simunthu atimenyera nkhondo
Ndalama sakumagula anthu uphawi sizinthu. 💔💔
Anthuwa akufuna mademo basi choncho sangamve
Ku Hungary wapita kotaninso abale chi munthu chosamva ngati ixhi sindinachionepotu ine
Mmmmmm koma ndizokhudza kwambiri zimenezizi amalawi tiyeni tichitepo kathu
Mulungu aweruza and watsala pang'ono
The Deeee Ceeeee
Boni kalindo the DC mwana woyipa kwambiri
Tsiku lina kuzacha ndithu osaopa
The dc ndimawakuru
Tsiku Lina kudzacha 😢
Chakwera ,nduna zake plus azilangizi ake onse ndi zinyama zopanda umunthu. Mfiti zeni zeni zotamba masana dzuwa lili ng'aaa. Zoona ndithu mmene dzikoli lilili pakali pano iye angapite ndi ma scavengers onsewa kukasangalala ku America? Mtsogoleri opanda chisoni.Mtsogoleri opanda manyazi.Mtsogoleri opanda mzimu wa umunthu olo pang'ono.
Mukhalira yomweyo ku uwa uwa ngati agalu
Inuyo bwampini wanu uja anali ndi manyazi otani iweso nchitsilu kwabasi
Mmmmmmm koma zaonjeza... Abusa alitenga dzikoli
Bon karindooooo
Mwati president wosava?😂💔😂😂
ndipo zowona
Kodi zimenezi umayesa comedy or umalota kapena ndalatulo
Kodi aku UNGA wo sangamuuze kuti akupangazo nzolakwika? Amene akupitawo akukatani? Eish mupha ndi mtima
Zoona kalindo chikangawa ndiwosamva,khutukumve,mbuzi za anthu MCP chipani cha anthu Osama,okuba
Zovuta kwambiri saname chikangawa waonjeza komaAmbuye atithandize, kodi za bakirizi TV ndizoona abare koma nde ngati ziri Zenizeni mbola
Nkhani ndinthawi yovota kt izizi tisazazioneso ndipo ife a malawi ndifedi ovesa chisoni kaya ndi church kwambilikaya sinduziwai cz tilibe kugwilizana pofuna kupeza chilungamo bomali lakanika ili
Zoonad kwambiri zedi boss
Sindikudziwa kt malamulo Amati chani a president zikafika apapa kt amenera kt apitilize kuramura eshiii 😢😢
🤣🤣🤣🤣
AMalawi Tinachita mistake kusakha Boma ili 😭😭😭😭
Ndipo chakwera ndi munthu oyipa mtima iiiii osaganiza za anthu ake ndipo mizimu ya anthu aja yamupengesa
Umakwana mulomweh
Ntchito yomwe ndimagwira ine ndimagwira ntchito kuchipiku
Kusagwira kwamutu ndikuona ngati choncho ndikhana angayendayenda kk
Last days
Mizimu yakwiya kuli nzithu
Mavuto mwayakhulila muja zoona achakwera zoona akufuna atiphe asalemo ekha ndi bushili
Azidya manyi
Ndipo uyu wafikapo pa uchitsilu munthu osamva kulira kwamavoti ake
Anawina zisankho ndipo awinaso 2025.
Ubwino wake osauka ndiamane amabvota oasti olowo muzipani wamafumu, abusa
Kkkkkkkkk sozayenda
Kodi maiko mmene akupitamo, samakhala ndinambala ya anthu opita ndi president?
Amangopita yekha asanamuitane boss
Anabadwa osamva awa
Anthufe ngat tufuna kusitha zinthu nkwiyo wathu tikaonetse povota bas tose tikuona mene zukhalila nde wina kumati boma ndi lomweli ndiwe mbuli yothelat
Mkango waku mulanje
Abon muwauzeso a MSP kuti akatuluka m,bomamo ,akalowa wina asazakhale pasogolo kuzanyoza azawo womwe azalamulirewo chifukwa chakwerayo wawononga zinthu zambiri kuti winayo azakhoze pazapita nthawi yayitali
😅😅😅mm
Chakwela chisilu chamunthu
Kkkkk
Iwe ndiwe opusa kwambili ulibedi mzeru ukugwila ganya opanda phindu ku mtundu wa amalawi president aziyenda osati nkhalmba yanu ija ayi aja akhale pansi uyu akayenda zipatso zake zikuwoneka osati nyasi zanuzo mukulankhulanzo mutu wophulikawo kape iwe
Mzimu mulibe inu, chikangawa 2
@@OdettaLowrence bola inuyo mukusapota satanayo
Inuso ngaboza president uti anayendapo ngat wanuyo aaaa
@@TelemicusNkhoma analibe zochita ikani wanuyo tiwone ayende basi agalu anu
Muyakhula mutatadya inuo koma munakadzwa mene athu akuvutikira sukanayakhula ndthu
😂😂😂😂 pamenepo sakunama Mr Kalindo onse nchimodzi modzi modzi,mwina tisiye kusankha andale tisiye kusankha azipani za ndale