BON KALINDO 8 JULY 2024 BIG MAN WAFIKASO PA MONDAY

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 5 окт 2024

Комментарии • 74

  • @JosephMichael-x7v
    @JosephMichael-x7v 3 месяца назад +3

    Kungotiphera bon kalindo muzakhala nkhondo mmalawi

  • @JamesEuginio
    @JamesEuginio 3 месяца назад +2

    Bwana kalindo mugwirane mana ndi comrade mtambo chifukwa iwowo alibe tulo komaso ngati Malawi first itafuna kuima pa zisankho Malawi ambiri tikondwa inu bwana kalindo tikuona usogoleri mwa inu chifukwa kumuyankhulira mphawi yemwe alibe mawu sikophweka koma kuyankhulira olemera omwe pamapeto pake munthu amalipidwa choncho inu bwana timakupemphererani mulungu agwirise ntchito inu kuti satana achite manyazi kuno kumangichi makanjira

    • @EllenPhiri-xt8pt
      @EllenPhiri-xt8pt 2 месяца назад

      Bon kalindo and antanyuwa bolaso munakangoimila u president that anthu amenewa angokhala chete akusekelela zomwe chakwelayu akuchitazi😢😢😢

  • @MacleanKwacha
    @MacleanKwacha 3 месяца назад +4

    Our president komaso mukudziwa kuti kulilongwe kuno kukuyenda anthu akuitanisa chiphaso chauzika,kumat akuchita kalembera oti pakamachitika zitukuko zaboma asamavutike kupita kwamfumu azingotenga mukaundula?Tifufuzileni mutiuze zoona.

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 3 месяца назад +11

    UTM, AFORD, DPP and UDF must make an alliance and win government, Chakwera out, useless government.

  • @PreciousChlima
    @PreciousChlima 3 месяца назад

    Bon kalindo machine,, koma Aford, UDF, Aford komaso DPP khalan maso

  • @taneesharkamwendo8710
    @taneesharkamwendo8710 2 месяца назад

    president wanga wanga vote yanga

  • @watsonmhango8794
    @watsonmhango8794 3 месяца назад

    Zoona Mr DC president wa Anthu osauka

  • @EVERSONGalatia
    @EVERSONGalatia 3 месяца назад +1

    UTM PDP AFORD CFT PP and UDF must make alliance

  • @EllenPhiri-xt8pt
    @EllenPhiri-xt8pt 2 месяца назад

    Keep it up mr DC

  • @DavieMuziwo
    @DavieMuziwo 3 месяца назад

    Best DC

  • @HenryKeyala
    @HenryKeyala 3 месяца назад

    Loud and clear

  • @BlessingswazaDyress
    @BlessingswazaDyress 3 месяца назад +2

    Fantastic DC

  • @FaithDonald-ts2pp
    @FaithDonald-ts2pp 3 месяца назад

    The dc❤

  • @JefulyPesulo
    @JefulyPesulo 3 месяца назад +1

    Keep up DC

  • @IssahAluba
    @IssahAluba 2 месяца назад

    ndipo Pena gati useke president mpaka kuligawa dziko ai zikomo kuphandoko mulungu akudalitseni

  • @SigoMw
    @SigoMw 3 месяца назад +1

    Onse mapulezidenti opuma Ali nkhwinthi ngati akumetetsa kwa kaondo ku 36, akupweteketsadi mtima chifukwa palibe akumveka kupatula inu akalindo. Ma radio ndi ma TV pa Malawi kulibe ife tikudalira inu akalindo, amtanyiwa ndi Wa bakili muluzi.

  • @voicedumathindwa
    @voicedumathindwa 3 месяца назад +2

    Mnthuyi ambuye amdalise akumenyadi ufulu

  • @peterchimatiro4093
    @peterchimatiro4093 3 месяца назад

    The DC

  • @Manlymw
    @Manlymw 3 месяца назад +1

    Keep it up the dc

  • @Chiso2019
    @Chiso2019 3 месяца назад

    Ine koma opposition yi.....imamunamizila kut akusokoneza ndi anankhumwa,nankhumwa anakuchokeraniko ife timayesa ziyamba kubebano koma manyaka okhaokha

  • @CostanceLalli
    @CostanceLalli 3 месяца назад

    This government must go out we don't need this mcp

  • @AidajoseMangueni
    @AidajoseMangueni 3 месяца назад

    Kodi mesa a UTM anachita kuchokera ku zipani opositionizo? Akukolola zimene anafesa amenewo.

  • @MikeArthur-jd2ij
    @MikeArthur-jd2ij 3 месяца назад

    Thus our DC 🔥

  • @MexcoJepter-p5f
    @MexcoJepter-p5f 3 месяца назад

    Koma azipani zotsutsa tapanganipo kanthu inuuuuuu Bon Kalindo ndiye akuyesetsa kukutsinani khutu ndipo CHAKWERA ndinduna zake akufuna kupitiliza kuba mubomali😢😢

  • @trustchiwalo9225
    @trustchiwalo9225 3 месяца назад

    Eiish!!

  • @AliciaMaphanga
    @AliciaMaphanga 3 месяца назад

    Powerful the DC❤❤❤

  • @StellahGwagwala
    @StellahGwagwala 3 месяца назад

    Matiimilila DC Landilani ulemu wanu

  • @AndrewKonondo
    @AndrewKonondo 3 месяца назад

    Bwana DC, ipatseni moto tili nanu, akapangaso chibwana zodzabera chisakhocho tidzangomenyanapo mmalawi muno, ndi mbuzi za anthu

  • @RobertKanaphwatiwa
    @RobertKanaphwatiwa 3 месяца назад

    Ulemu wanu mr Kalindo tulutsani ndondo nthawi yakwana bwana

  • @ashrafffaque
    @ashrafffaque 3 месяца назад +1

    Machine athu The DC

  • @ZettaImuranYunusu
    @ZettaImuranYunusu 3 месяца назад

    Mr dc dziwani Izi... Zipani Izi DPP UDF AFORD ADD onsewo a kupanga zinthu zoti ayimile mu 2025 Ndipo inuyo musakayikenso ai

  • @HamanjaManyela
    @HamanjaManyela 3 месяца назад

    Awawa achoke a MCP

  • @NkhomaMaupo
    @NkhomaMaupo 3 месяца назад

    Ubwino wake achewawo ali m'boma

  • @GodfreyKamphiripiri
    @GodfreyKamphiripiri 3 месяца назад

    Machine ❤❤❤DC

  • @LameckBanda-ph2nh
    @LameckBanda-ph2nh 3 месяца назад

    The DC ❤❤❤❤

  • @DalitsoMatope
    @DalitsoMatope 3 месяца назад

    Munthu uyi mulungu azimutetedza until mcp out of power,,,,Dpp ,,Afford,,udf,,,,why are you not listen to kalindo

  • @ChifundoNinje
    @ChifundoNinje 3 месяца назад +1

    Abale a dpp mukutani

  • @ThomasMlowoka
    @ThomasMlowoka 3 месяца назад

    DC 💪💪

  • @ZawadiAllani
    @ZawadiAllani 2 месяца назад

    🙏🙏🙏🙏🙏

  • @siphiwenyirongo2568
    @siphiwenyirongo2568 3 месяца назад

    Mmm

  • @InnocentEdasi
    @InnocentEdasi 3 месяца назад

    The DC 🔥💗🔥

  • @DaveDambo
    @DaveDambo 3 месяца назад

    The DC🔥🔥🔥

  • @MacleanKwacha
    @MacleanKwacha 3 месяца назад

    Ineyo ndkunena pano ,dzulo laliwisi moti akazanga achita kukana kuti mwina akufuna kubwera zisankho

  • @MuneerYusuf-py1lz
    @MuneerYusuf-py1lz 3 месяца назад +1

    Komadi afasa kwambiri azuzeni

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 3 месяца назад

    Ife UTM tsitiwelengela kuti chipani chotsusa ayi ichi ndi chipani cholamula boma ndi MCP itsewo alephelela lidzodzi kuyendetsa dziko NSONO A MCP KAYA APATSA NDALAMA KAYA TSAPATSA NDALAMA IDZO ZAWO AKUDZIWANI koma munthu wadzelu nsangasalale ndi munthu amene wapha bambo ako ndikumakuwudza kuti ndikutsamalilani bwino ana inu pomwe bombo wawoyo mumalephela kumutsamalila loko anawo bambo wawo ali moyo msimawathandidza UTM mistake yanu ndiyimene umalidze chipani chanu ndanena kuti kumalidza off course ifa ya CHILIMA yachepetsa mphamvu zanu mwina nsimukudziwa NDE MCP AMALAWI YAKWANO NDE OTSUNSA BOMA CHIHANA MUTHALIKA MAYI PATELO ATUPELE KALWUWA NDI ENA OTSE MUTSAKHELE CHETEEEEE KHALANI PAMODZI NDIKUPANGA CHIGANIDZO KUTI UKAMBELE MBELE AKUPANGANI A MCP NDI ARP muchita bwanji chifukwa kungopatsa pata kawili MCP kukhalatso boma amalawi OCHULUKA TiKUFA KOMATSO ULAMULILO UWU WACHIPANI CHIMODZI UDZAKHADZIKIKANO NDE MAMVUTO AKULU KU MALAWI

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp 3 месяца назад

    Dc ❤❤wi love you

  • @PemphaChina
    @PemphaChina 3 месяца назад

    From njedza village

  • @mathewsnachuma8086
    @mathewsnachuma8086 3 месяца назад

    Boooooooooooorn kalindoooooooooooooo

  • @FanizoKawindula
    @FanizoKawindula 3 месяца назад

    Pita iweyo ku khothi ko Mesa umati ndiwe president

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w 3 месяца назад

    Koma abambo inuyo mukuyesesa kunja kukacha mulungu apitilize kukusungani ndi moyo koma ndimati ndi pephe inuyo simungambise chipani chani ndi achina m,tanyiwa bakili TV tikuvitelanitu chifukwa mumaoneka ndinu amaso m,phenya

  • @CHIFUNDOCHINA-lp9lg
    @CHIFUNDOCHINA-lp9lg 3 месяца назад

    KING

  • @SmilingFishingRod-zc4wx
    @SmilingFishingRod-zc4wx 3 месяца назад

    Nkhani yonveka bwino
    Nanga a Mwananveka muli kwanikiii? Monga inu.

  • @AlasonPaulo-ht7zb
    @AlasonPaulo-ht7zb 3 месяца назад

    Azibambooooo

  • @FranksonKatundulu
    @FranksonKatundulu 3 месяца назад

    Akufuna udindo uyu aaaaaa
    Popeza adamumana udindo. ndiye akuona kut aDPP azamupatsa?

    • @JamesEuginio
      @JamesEuginio 3 месяца назад

      @@FranksonKatundulu ndiye ukuganiza kuti what way followard if akalindo akufuna udindo iwe iwe tanena chabwino mchiti?

  • @SamsonWyson
    @SamsonWyson 3 месяца назад

    Dccccc

  • @ChomboNgosi
    @ChomboNgosi 3 месяца назад

    ❤❤❤❤

  • @RachealHarawa-xc9gs
    @RachealHarawa-xc9gs 3 месяца назад

    Mulindimfundo zabwino

  • @osaukaonjoya
    @osaukaonjoya 3 месяца назад

    Tokotani akolo

  • @DenisJamu
    @DenisJamu 3 месяца назад

    Fadah

  • @ISSAHKAINGA-zz1op
    @ISSAHKAINGA-zz1op 3 месяца назад

    ACHALUME KUTI CHUBWIIII

  • @DavieMuziwo
    @DavieMuziwo 3 месяца назад

    Best DC

  • @EmieMtendere
    @EmieMtendere 3 месяца назад

    The DC

  • @Maxcarcare-g1d
    @Maxcarcare-g1d 3 месяца назад

    The DC 🔥🔥🔥🔥🔥

  • @FrancisGama-qb7ze
    @FrancisGama-qb7ze 3 месяца назад

    The DC

  • @SemuKaunda
    @SemuKaunda 3 месяца назад

    The DC