Am a graduate from mca, I did bachelor's in accounting and auditing - 2021. Mtamaliza xul mnapita ku blantyre kuchoka ku mzuzu, kut mwina ku town simkachedwa kupeza ganyu Koma guys there is real life after college eeh 😢😢 ndinayamba yoyitanila ma minbus mu limbe market pa 4ways, ndapanga izi kwa chaka ndi half anthu oti anali amzanga kumandinyoza plus ena kumandisala ena kumanditenga opusa komabe simnagive until pano pakatipa Mulungu anandidalitsa ndinapeza timaganyu ku sffrfm & mec pano mnapeza capital mnayamba business.. anthu amkandiseka aja pano akumandipempha ndalama... mmmm dziko ili kaya. Nice song and I can relate 🙏🙏💯😻
After graduating from MIJ I started looking 4 a job but no avail. And then I back in class to pursue another course ,I graduated agen with a degree in strategic management while searching 4 a greener pasture.tinayamba kuyendetsa lorry pa rank ,to make it worse my gelfrnd called me that ndilibe tsogolo and she left me. I cried while kneeling down to God asking for his favour. Guys mulungu sataya wake for sure. Am working now In government.
After I graduated from Exploits University in 2019 with Bachelor's degree in Human Resource Management i thought straight away I will get a job koma eeee Nakathera kumunda kukhala mlima wa chimanga then kupeza capital kutsegula barbershop koma.... Ndekha kumadabwa kuti zoona izi koma pofika kugona mu barbershop mmomo But never give up Mulungu sataya wake in 2021 I was employed by Blantyre Water Board, mpaka pano ndili konko Trust God and the process..... Nyimbo apha iyi Anga anali mantha
Am a graduate from mca, I did bachelor's in accounting and auditing - 2021. Mtamaliza xul mnapita ku blantyre kuchoka ku mzuzu, kut mwina ku town simkachedwa kupeza ganyu Koma guys there is real life after college eeh 😢😢 ndinayamba yoyitanila ma minbus mu limbe market pa 4ways, ndapanga izi kwa chaka ndi half anthu oti anali amzanga kumandinyoza plus ena kumandisala ena kumanditenga opusa komabe simnagive until pano pakatipa Mulungu anandidalitsa ndinapeza timaganyu ku sffrfm & mec pano mnapeza capital mnayamba business.. anthu amkandiseka aja pano akumandipempha ndalama... mmmm dziko ili kaya. Nice song and I can relate 🙏🙏💯😻
Ineso ndapanga program yimeneyo pa MCA abale inu 😢
Eeish bro this lyf😢😢
Moyo ndichocho
Nthawi zimachitik
A very touching and motivating story
After graduating from MIJ I started looking 4 a job but no avail. And then I back in class to pursue another course ,I graduated agen with a degree in strategic management while searching 4 a greener pasture.tinayamba kuyendetsa lorry pa rank ,to make it worse my gelfrnd called me that ndilibe tsogolo and she left me. I cried while kneeling down to God asking for his favour. Guys mulungu sataya wake for sure. Am working now In government.
🙏🥳
Anakupatsa mwai ase
@winstonpchilonga6712 ndpo sukunama..anandiuza zimenezo mwenz ngat ,ine nxt month mkumapeza job eeeiah God really works and amalola zinthu zina zipite kt wina apeze mwai
eish it's getting hard everyday in this world,glad how you finally made it,it's all God's plan.
@preciousjonas5468 on a slow pace bro ..trust in the Lord bas
After I graduated from Exploits University in 2019 with Bachelor's degree in Human Resource Management i thought straight away I will get a job koma eeee
Nakathera kumunda kukhala mlima wa chimanga then kupeza capital kutsegula barbershop koma.... Ndekha kumadabwa kuti zoona izi koma pofika kugona mu barbershop mmomo
But never give up Mulungu sataya wake in 2021 I was employed by Blantyre Water Board, mpaka pano ndili konko
Trust God and the process.....
Nyimbo apha iyi
Anga anali mantha
Eee fropa ndiwe shasha🔥🔥🔥🇲🇼
nyimbo za uthenga wa bhoo always stand out! nice concept ma guy
Ndinu madolo ma guy 🔥🔥 nyimbo mwapha
The reality in verse 2 man eeeh. Ma dropouts angogula magalimoto . God helps koma, for we walk by faith and not by sight .
Great song lads👑🔥
Geez mwapha sound iyiyi @ Flopa and Amidu ,all the best 🎉🎉
Ndipo eeeee this year tumaliza koma eeeee Mantha eeee lord have mercy with me👏👏👏
Mantha ndiye tilinawo ochuluka 😢😢😢😢😢, lovely song ❤❤❤❤❤
Mwapha guys ✌️🍻 UNIMA ndi CHANCO
Nice message keep it up
Massive truck you guys got blessings just that the platform in Malqwi isnt easy To reqch to the top🎉
Makwana Flopa🔥
Those who failing in love with the hook let's gather here
Ada awawa hook aika🔥🔥
Uku nde kuimba uku,ndinaphunzira koma pano ndili outside of my country,am working here my education is useless to me
Eeeee anthu wa akupha kwambili 💥💥💥💥💥
Combination iyiyi sinapalepo🔥🥳
Mwapha azibambo👏🏽🔥
Mulungu samasiya yemwe anakhetsa thukuta lake kulimbikira. Tsikulina chimazapezeka chochita. It's just a matter of time. Nice tune Geez
The concept....the lines...my guy flopa u delivered..Amidu as usual...am amazed boys🔥🔥🙌🙌
Track gat all the struggles that graduands anticipate ku world but people just don't know✌🏽 nice one guys
Hit kwambir
Ife tamaliza pompo pa ntchinji koma pano ndikawona miracle ndi chinga, Simmene kulili Ku industry bro Flopa D
Ndasala ndi semester imodzi yokha , matha andizaza 💔
Tidikirebe komaso tipempherebe... Big up unima all will be well🎉
Things that every college student like me fear....
The future
coz we ain't sure if this degree is our way out, at least we hope so. So help us God🤲🏾🙏🏾
Nyimbo mwapha guyz,izizi nzomwe tikudutsa after Xul
Mantha fire mwapha ma guy
iweo ase Dego ija sitinabetse, uli bhoo ase
Life is not fair
Nice tune ma Dollo🔥🔥🔥
Peter amidu yi eeee NDIWACHABE kwambir chorus ngat akuyimba bass guitar mu blackmissionaries
😂 😂 😂 😂 😂 Ndipo zoonadi moyo ngobvuta lero tili Jonzi kumakhala ndimajigisi mushop pheee 🙌🙌🙌🙌
Inu ndi madolo guys tikufuna nyimbo ngat izi ❤❤❤
Unima well presented.. Song talks about reality of life😢😢😢
This is great guys 🔥🔥
Ifenso ena anatinyoza If. pano akudya pakhomo panga Za mmawa siziziwika samalan Lilime keep on pushing
Nice music 🔥
@@DONNEXKhama-bk1gy keep winning
Local artist with reality yapa ground💯💔🔥
Fire my Gee
Big up ndakutenga basi ndizivela iwe basi
Track mwapha boys 🔥🔥
Nice song young stars 🔥🔥
Nyimbo yi ndi yokhudza 🥺 Enafe ikutikumbutsa tsogoro lathu lotayika🥺
Ambuye ayankhe nyengo zathu 🤲😪🙏
Nice gingii👌👌
Nyimbo yanzeru ❤❤
Nice❤️🔥
Represent ma guy 🔥🔥
Great hit❤❤❤❤❤
Ayi Malinga ukufuna azilume Jahmeil yu
Ma guys inu muli ndi luso. Keep pushing dudes
Nice some guys.mantha achulukadi🔥🔥
Mwapha nyimboyo madolo
The songs hit in all angles 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Eee mantha 😢 mulungu akhare nafe.
Positive song bro.... I like it
❤❤ mumakwana inu
Ndinu madolo🔥🔥🔥
This song 🔥🔥🔥🔥
everything we live to almighty God 🙏
Mwapha guys, so nice
Reality 🤗 True definition of Life after college 😢
Ambirife atichulukira ndi mantha😢
Wow!🤝
i can relate and I love the song ,it is based in real life situation
❤❤❤ Nice tune ma gee ikunveka pa 99.9% ku Durban Ladysmith kuno
Ndipo inu😢😢😢
Kupha sound🔥🔥
Chanco🔥🔥
Akt this course is very marketable eee zazii🙌🙄
Nyimbo yaona u finali wanga, 😭😭😭
🔥🔥✅
Great song..... Kelvin Sings
Nice 🔥🔥
Talented 🎉🎉🎉🎉🎉
I want to come back 😢🙌🏻
Hyphen style nice guys what a tune🔥
Mwapha iyi
muli uthenga, mumatha ma gee . RESPECT
After kumvera 2018 degoss outgoing I knew Flopa ndi dolo
😢😢😢ineso ndili ndimatha ndikamaliza school link tilibe shaaa...maguys mwaipha
Mantha basi bro keep it up
Hit🔥
Reality Check.... Nice Tune
Nice😊😊😊
Nice track
Bad boy Dolla tipanga ife mafano ayi odalitsa ndi Yaweh
OSAOPA BRO FLOPA D❤ MULUNGU ALIKO🙏
Manthawo nde ndi nyanja
Great song ma biggy
Iyi ndi hit ma guys
here at Luanar mantha😢😢
Ndili ndi mantha😢
Nice one my geez
Ndpo ndikuopa 😭💔 After all I don't have any connection mu industry
Poguguda mtima kumakumbukira umakhala kumanzere
Flopa D X Amidu = Hot hit song 🔥
My artist
Real life situation 😢 Matha. On repeat
Mantha 🔥
Ine chitengereni diploma ya Nutrition koma ya Distinction mpaka lero no work
🔥