Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
My wathu flora suya nice one ❤ timakukondani mama
Estamos juntos gentes aqui em Moçambique
From Mozambique, landilani moni inu nonse muno
Koma mchemwali wa Kalanka sadziwa nthawi yobwerera pakhomo pa achimwene. Hiyaa. Banja lizilephera kumasuka 😂😂😂😂😂😂😂
Me I was waiting this Mr kalanka nice
Kkkkkk amuna awo a Nagama ndi ambala , kkkkkk kupatsa manyazi 😅😅😅😅😅😅😅
Kkkkkk achitsime pamka kuba zithu mu shopright nawo atitani eeeee kma mumakhala pa khomo panu thawi zonse kwa chimwene chekalanka mumafunako ma drinkis kapena kukawawona kkkkkkkkk Ilove you guys mumatha ❤❤
Flora mmakwana koma achitsime akhalike kkkkkk😂😂😂😂😂😂
Well done Guys.Chisangalalo chosatha.Kuphunzitsa chikhalidwe chathu mwa Dongosolo.Keep it up ❤❤❤❤❤❤❤
Giling'ande wayasa moto 🔥
Basi Mr shop rite zakwana kukalipa. nafuneya alibwanji eee ndilibe mawu. nanunso Alamu tsikunditsiku kwachimwene anu bwanji 😅😅😅😅😅😅
Me too I was waiting this 😂😂😂❤
Chitsime kudzangoyisokoneza yakuba pamene paja ndi nkhani ya Sokonezo haahah amuna kuchenjelaa kkkkkkkkkkk. Koma Farai ndi Joshua ali kuti abaleee
Much love guy's mmandivesa ku Koma ❤❤
NDIYITANENI INE NDIZAKHALE MWANA WANAMOYO 😅😅😅😅
Well done guys ❤
Km muramuyu tu ndi zodiac mmmmm
Beautiful ❤️
Keep it up 💯👏👏👏👏
Machetemachete atero Mr Chizime ❤❤❤❤❤ at timachita Multiply 😅😅😅😅😅
a maliro ulesi...kwambili.ati simungawone shortage ahyi😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
I was waiting for this ❤
Mchemwali wa Kalanka umabebesa hvy 😂😂😂😂Queen kumudzi tsopano 😂😂😂 Maliro ndye uli nd phuma nchito wangoyamba kumene koma wayamba kale kugawa kamba ukhalitsapo koma 😂😂😂😂
Ndipo ndie wasowa kkkk farai
koma amfumu kazi...ayayayay😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Welcome to Mfumukazi Queen 🎉 apa wabwelasi tione kuti ndi Che Padera muthana bwanji😂
😂😂😂😂😂😂 eeehhh koma giling'ande😂😂😂😂😂😂
Queen wafika m'mudzi
😂😂😂😂 ndmakunyadilan kwambiri nose koma malilo iweyo sukufuna tchito 😂😂😂😂
we call spade spade😂😂😂😂😂😂😂
Kma mulomwe uyuuuuu 😂😂😂😂
Welcome queen pa home vg koma ndisazakuone utaima ndi a padera ,ine ndi ma joshwa tizakuponda
Ndipo kkkkk😂😂
🔥🔥🔥🔥
Maliro wayambiratu ntchito asanalembedwe😂😂😂😂
Kkkkkkkkkkk. Koma achitsime
Team Akalaka ndi madam awo
Akalaka ali ku kitchen😅😅😅😅
Eeh Chitsime, mutu wake ndi plastic yeni yeni.
Ndisamwe dilikisi😂
Missing falai guys ❤
Me too
Me 3
Ndipo wasowadi
Akaranga one inuyo khani yachikondi
Mr kalanka very nice
Ife ndi aku blantyre
Koma anyamata awiri wo abwera kumene angochoka palibe akometsa yiwo
Akuti alowa mmalo mwa gututu ndi nzake uja koma sakufikapo alikutali kwabasi
mpaka ShopRite kubamo eeeee mamuna wa luksharp
Very nice mumandifilisa
Kdi falayi alikuti abale wasowa
Hahahaha KAZI gani ndakuona
Kkkkkk kma dirikisi yomweyo
Kodi a mfumukadzi ndi amuna anu muna bwelerana liti ? 😂😂😂
Team iyiyi inabwela kuzankhala
Akalanga mpaka Jacket. Mwaipatsa mototu.
I love this move
Akalanka😂
Amaliro apeza zochita 🤣🤣
Mumativesa kukoma guys ❤
Me too I was waiting I love Mr padela
Kkkk koma mlomwe uyu akubebesa
Good work madam
Achoka my ghetto ya mdyangu abwera kumudzi a khwini
Ndiamodzi ose muoneso kalanka walowa kwa ndyangu even fumukazi anadzabwelaso kwa ndyangu miyezi yapitayo ndiamodzi ndithu
padela imeneyo ndeitiyo muli kt koma nawo achisime sazatheka dzuwa ili mungamapute gilinyande kkkkk
Where is falai
Farai farai please
Mr agilingande mumakwana
Masamu ayambikapo
KKK kunyanyala ngati chisoni hahahaha
Muonjezereko nthawi izikhala 30 to 36 minutes
❤❤❤❤❤😂
Wakuba wangwidwa mmmm Kom gusy ndy mwagomusiya siya wakubayo
Mr padela🎉
Padela eee ndamusowa
Anthu inuyo mumatimvetsa kukoma
kkkkkkkkkk Amaliro tsopano mu Shoprite
Munabwera kuzakhala inuyo ......(Malawi 265)
Kkkk
Chisime ati wagula, eni ake palibe,
Where is Padera 'The Delazi'?
❤❤❤❤❤❤❤😂😂
Anagama ndi àchitsime ulemu wanu
Kkkk koma Marilo kkkk
Koma mlomwe zanga uyu
Apadela ali kwaaa??
Mumativetsa kukoma
Namoyo❤
camera mbola
Amaliro pepani zochita
😍
Mulungu si Patrick 😂
Akuti ndimagula kkkk
Alamuu😂😂😂😂😂
Opanda padela sikukoma ai
My wathu flora suya nice one ❤ timakukondani mama
Estamos juntos gentes aqui em Moçambique
From Mozambique, landilani moni inu nonse muno
Koma mchemwali wa Kalanka sadziwa nthawi yobwerera pakhomo pa achimwene. Hiyaa. Banja lizilephera kumasuka 😂😂😂😂😂😂😂
Me I was waiting this Mr kalanka nice
Kkkkkk amuna awo a Nagama ndi ambala , kkkkkk kupatsa manyazi 😅😅😅😅😅😅😅
Kkkkkk achitsime pamka kuba zithu mu shopright nawo atitani eeeee kma mumakhala pa khomo panu thawi zonse kwa chimwene chekalanka mumafunako ma drinkis kapena kukawawona kkkkkkkkk Ilove you guys mumatha ❤❤
Flora mmakwana koma achitsime akhalike kkkkkk😂😂😂😂😂😂
Well done Guys.
Chisangalalo chosatha.
Kuphunzitsa chikhalidwe chathu mwa Dongosolo.
Keep it up ❤❤❤❤❤❤❤
Giling'ande wayasa moto 🔥
Basi Mr shop rite zakwana kukalipa. nafuneya alibwanji eee ndilibe mawu. nanunso Alamu tsikunditsiku kwachimwene anu bwanji 😅😅😅😅😅😅
Me too I was waiting this 😂😂😂❤
Chitsime kudzangoyisokoneza yakuba pamene paja ndi nkhani ya Sokonezo haahah amuna kuchenjelaa kkkkkkkkkkk. Koma Farai ndi Joshua ali kuti abaleee
Much love guy's mmandivesa ku Koma ❤❤
NDIYITANENI INE NDIZAKHALE MWANA WANAMOYO 😅😅😅😅
Well done guys ❤
Km muramuyu tu ndi zodiac mmmmm
Beautiful ❤️
Keep it up 💯👏👏👏👏
Machetemachete atero Mr Chizime ❤❤❤❤❤ at timachita Multiply 😅😅😅😅😅
a maliro ulesi...kwambili.ati simungawone shortage ahyi😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
I was waiting for this ❤
Mchemwali wa Kalanka umabebesa hvy 😂😂😂😂
Queen kumudzi tsopano 😂😂😂 Maliro ndye uli nd phuma nchito wangoyamba kumene koma wayamba kale kugawa kamba ukhalitsapo koma 😂😂😂😂