BANGWE NAYO YAKUNGANA! TAMVANI ZOMWE ALANKHULA A SAMEER SULEMAN NDI PETER MUTHARIKA - DPP LIVE TODAY

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 23 янв 2025

Комментарии • 113

  • @LawrenceMoffat
    @LawrenceMoffat 15 дней назад +4

    Guys there can be more people but mind you those are not going to vote for DPP

    • @HarrisonMakunda
      @HarrisonMakunda 15 дней назад +11

      Chimozimozi mcp,,koma Dpp ndi yowinawina

    • @GodsFavourite1
      @GodsFavourite1 15 дней назад +7

      @@LawrenceMoffat mutu wako wachita dzandzi gologolo iwe

    • @WilliamMajiwa
      @WilliamMajiwa 15 дней назад +3

      Ndye ukuganiza angavotere nazikwanje?

    • @kennedychinguwo1640
      @kennedychinguwo1640 15 дней назад +2

      @LawrenceMoffat uchira sunati ndipo mudzathawa nokha ankhaza inu

    • @samdiverson9733
      @samdiverson9733 15 дней назад +3

      Pulpit wa mcp iweyo do you think kuti pangapezeke munthu kuvota zikwanje APM aimanso awinanso ❤❤❤❤❤

  • @ShadreckNyati
    @ShadreckNyati 14 дней назад +2

    Destiny is from God to be a leader is not easy APM this is blessings from God 🎉🎉

  • @EthelSokosoko
    @EthelSokosoko 15 дней назад +4

    Beautiful to hear APM acknowledging that it's GOD Almighty at work in his rallies.

  • @MemoryNdhlovu-e4w
    @MemoryNdhlovu-e4w 14 дней назад

    From south Africa 🇿🇦 Apm my vote 🗳

  • @RebeccaChikalenda
    @RebeccaChikalenda 16 дней назад +10

    Kma uyu apweteka gulu et 😢😢

  • @GeraldChilundu-e3v
    @GeraldChilundu-e3v 15 дней назад +2

    Boma Boma ilooooo behind Peter Muthalika

  • @MakheyiChabwera
    @MakheyiChabwera 15 дней назад +5

    Ngakhale wamkula komabe muli mzeru....

  • @DeborahMmango
    @DeborahMmango 15 дней назад +2

    Woyeeeeeeee dpp koma mukuti gulu limeneli kaya wina komwe aliko Kayatu ndikuti😂😂😂😂😂

  • @MustaphaCassim-t7g
    @MustaphaCassim-t7g 15 дней назад +1

    ❤❤❤❤❤Kunabebatu

  • @LawrenceBelson
    @LawrenceBelson 15 дней назад +7

    Ndipo ndizoonadi anatumidwadi ndi mulungu APM

  • @LameckGamah
    @LameckGamah 15 дней назад +2

    APM my vote ❤

  • @ChilindaJustin
    @ChilindaJustin 15 дней назад +2

    Ife mziko lamalawi amutilamulila ndi APM pa 16 September apa chikangawa nayo azavotera APM bus 😅😅

  • @MarthaMtonga-qt6tc
    @MarthaMtonga-qt6tc 15 дней назад

    Apm Bomaaaa❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @peterthawi
    @peterthawi 15 дней назад

    we love you APM❤

  • @ajasikalonga3210
    @ajasikalonga3210 16 дней назад +5

    We are watching live frm cape town south africa

  • @AliceLuka-x2z
    @AliceLuka-x2z 15 дней назад +3

    My vote Mr APM

  • @NEDGIFT-p5t
    @NEDGIFT-p5t 15 дней назад

    ❤❤❤❤✔️

  • @GabieBlack
    @GabieBlack 15 дней назад +2

    Yoswa uyo

  • @Enock-gu5ff
    @Enock-gu5ff 15 дней назад +2

    NKHANIYI ndi yoona dpp ndi game izizi nde zoona zake

  • @NdaonaMsowoya
    @NdaonaMsowoya 16 дней назад +3

    Live from kep town south Africa pallr

  • @GeoffreyMguwera
    @GeoffreyMguwera 15 дней назад +4

    Zowonadi ndi ntchito ya chawuta iyi.

  • @YankhoMthepheya
    @YankhoMthepheya 15 дней назад +4

    Tonsefe nga DPP

  • @PatricaTchuwa
    @PatricaTchuwa 15 дней назад +1

    Mkango💥💥

  • @ENOCKWISICK
    @ENOCKWISICK 16 дней назад +4

    Koma mukuona khwimbiii la munthu 😂 where is mcp now

  • @peterthawi
    @peterthawi 15 дней назад

    ndipo mcp yinangobwela kuzagwetsa kwacha...kuwononga zinthu .nthawi ya adadie ngini yinali bho heavy

  • @Jackson-iv2kx
    @Jackson-iv2kx 14 дней назад

    Is he God to save Malawi

  • @UmaliMmussa
    @UmaliMmussa 15 дней назад

    My vote APM

  • @RichardAlick-o8k
    @RichardAlick-o8k 15 дней назад

    Apm my vote

  • @BrightPhiri-c6h
    @BrightPhiri-c6h 15 дней назад +1

    From Joburg. Adad ma Vote.

  • @NEDGIFT-p5t
    @NEDGIFT-p5t 15 дней назад

    Nyanjanyanja PA home

  • @JusticeNyirenda-y9e
    @JusticeNyirenda-y9e 16 дней назад

    ❤❤💙💙💙

  • @LucyJoacquim
    @LucyJoacquim 15 дней назад

    Izooooooo!!!!

  • @ProsperTulambe-lh8ju
    @ProsperTulambe-lh8ju 14 дней назад

    "Ngati nkani imeneyo kuno kulibe dziwani kuti ndiyabodza "that's a fallacy

  • @GraceMasiye
    @GraceMasiye 16 дней назад +2

    Bomaa ilo,bangwe woyeee A pm my vota

  • @BonganJupter
    @BonganJupter 8 дней назад +1

    Dpp yomweyo

  • @SherifaG.Mlelemba
    @SherifaG.Mlelemba 15 дней назад +3

    15,yo nde yatalika bwanji?🙆

  • @WelceMakace
    @WelceMakace 15 дней назад +3

    Ati kungokhosomola akumawanga 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣😍 koma guys 👦

  • @UmaliMmussa
    @UmaliMmussa 15 дней назад

    Viva APM

  • @ruthchikhoswe6028
    @ruthchikhoswe6028 16 дней назад +1

    🎉

  • @AdamAhamad-g7u
    @AdamAhamad-g7u 15 дней назад

    Chipwala chako Lazarus September paundo

  • @MemoryChikakuda
    @MemoryChikakuda 15 дней назад +1

    Ambuye mutsogole anthu anu tikuvutika

  • @PetrosSamuel-rs9wk
    @PetrosSamuel-rs9wk 15 дней назад +1

    Kkkkkk ndale zakumalawi chilichose chakwela ndi chakwela izi ndizowona zawonjeza 😭😭 thumba lachimanga 70 pn muthu suli pa tchito ukayitenga kuti njala yochita kukomza 😭😭 chakwela pasana paako muthu ùmapasidwa ulemu ndimene ukupangila zithu zako

    • @ChipiGrant
      @ChipiGrant 15 дней назад

      Misonkho inu eeeeee kumalawi kwaonjeza maiko amzathu inde zinthu zimakwera km sikumalawi akuvutika ndi akumudzi odalila ulimi fertilizer wa subside kuli mziiiii yooooo!!!

  • @FredahFrank-k9g
    @FredahFrank-k9g 15 дней назад

    Boma ilooooiioii

  • @PatriciaAlomwe-oz8wc
    @PatriciaAlomwe-oz8wc 15 дней назад

    Mose uyo APM

  • @HamiltonSinosi
    @HamiltonSinosi 15 дней назад +1

    Ana anu tikunyomzedwa moyenda kamba ka upamuliro wankhadza ulipowu bwana.

  • @TamikaKaponya
    @TamikaKaponya 15 дней назад +3

    APM tikuti pepani tinachita kusaweruzika pa ulamuliro wanu😂😂

    • @ChipiGrant
      @ChipiGrant 15 дней назад

      Ndipo nde mzenizeni tilape ndithu tinachita kusayeruzikadi amalawi ❤

  • @user-ii9ch7oz8n
    @user-ii9ch7oz8n 13 дней назад

    Nkhalala bwanji madala mwakalambadi mpaka mau

  • @TameeraInglis
    @TameeraInglis 15 дней назад

    Chakwere ayambe kuchotsa zithumwa. Ndi. Ndondocha zake. Ku statehouse nthawi. Yake yatha .

  • @peterthawi
    @peterthawi 15 дней назад

    Mcp yija nayo yikavotela Dpp...Zafika pa

  • @ChipiGrant
    @ChipiGrant 15 дней назад

    Koma suleiman eeeeee ndikatundu muli mfundo abale anga mukuona bwanji after apm ndi suleiman basi dpp isazachoke inabwera kudzakhala

  • @MakheyiChabwera
    @MakheyiChabwera 15 дней назад

    Kkkkkk. Chikangawa angafike apa

  • @AkimeSaisonGamela
    @AkimeSaisonGamela 15 дней назад +1

    Zonse zakwela ndi Chakwela Mau a APM

  • @Princevenasiyo-b4b
    @Princevenasiyo-b4b 14 дней назад

    Nokha tawonani m'mene akupangira mikonoyo akukanika kugwira ndi mic yomwe, kkkkkkkk koma zinazi, koma mukumva akulankhulazo? Kkkk awuzeni azingolemba tiziwerenga akulankhulazo sizikumveka olo pang'ono.

  • @GeraldChilundu-e3v
    @GeraldChilundu-e3v 15 дней назад

    Ukunama aisy pita uko wa MCP Mavoti a APM awa

  • @vitumbikophiri-t7j
    @vitumbikophiri-t7j 15 дней назад

    sadzawina mp osavinidwayi okhalira masas ku paria

  • @KakaEdoshentoShaibu
    @KakaEdoshentoShaibu 15 дней назад

    Akt zakwera Ndi chakwera 😂😂😂😂😂😂🤸🤸🤸🤸🤸🤸🤸🤸

  • @ShazidaAlfred
    @ShazidaAlfred 14 дней назад

    Uyuuuu or wakula koma aramulilaso chifukwa nthawi yake wina aliyese amapeza chokudya

  • @SelinaGamaliyere-q8v
    @SelinaGamaliyere-q8v 15 дней назад +1

    Dpp woyee mpulumutsi wa dziko la malawi

  • @user-ii9ch7oz8n
    @user-ii9ch7oz8n 13 дней назад

    kkkkkkk mpaka sitikuva adadi

  • @EllahChikwatu
    @EllahChikwatu 16 дней назад +1

    Boma ilo ngat khale koko

  • @ThokoMsonkho-hy4uc
    @ThokoMsonkho-hy4uc 15 дней назад

    Kubangula ngati mkango mchipululu,kulilima ngati mbalame zakunyanja ,kuwula ngati mvura yokugwa kutali PETER ndikatundu kuchita kuposa Chakwera. Akamayankhura Chakwera ngati akulira kulopa mkamwa. Chakwera achoke! achoke! achoke! Bangwe ikayankhura zimachitka kwawo kwa zibagera kkkķk.

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h 15 дней назад

    Dpp ikuwina ndipo yawina kale believe me

  • @MorrisDzonzi
    @MorrisDzonzi 15 дней назад +1

    DPP woyee

  • @giftchale672
    @giftchale672 15 дней назад

    Mulungu alemekezeke

  • @Thombilly-e3h
    @Thombilly-e3h 14 дней назад

    Koma zomwe zichitike chaka chino eeee mbambande

  • @NokiaNokia-e2t
    @NokiaNokia-e2t 15 дней назад

    Chikangawayo nde anavinidwa

  • @ChifundoPatrickmajor
    @ChifundoPatrickmajor 15 дней назад

    Nafe tili kunja ife tikuti adad woye

  • @JeniferKananji
    @JeniferKananji 15 дней назад

    DPP bomaaaaaaasaa

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 15 дней назад +1

    Trump boma watenga or chakwera vote yake ikupita kwa apm bas

  • @Princevenasiyo-b4b
    @Princevenasiyo-b4b 14 дней назад

    A DPP ndikukupemphani chonde musamukakamize gogoyu zomayendayenda akusiyani pompano uyo, munthuyotu watha ndipo wangosala madzi amozi. gogoyo.

  • @EmmanuelNgambi-y6h
    @EmmanuelNgambi-y6h 14 дней назад

    Mbambande DPP

  • @AbuZunairaHanafie
    @AbuZunairaHanafie 15 дней назад +1

    APM NDI KATUNDU

  • @EDSONNAKULENGA
    @EDSONNAKULENGA 15 дней назад

    Apita mulungu akupaseni moyo wautali masalimo 91:15

  • @GeoffreyMguwera
    @GeoffreyMguwera 15 дней назад

    Nyanja ya anthu

  • @Ajudaf
    @Ajudaf 15 дней назад

    Kunalibeko dan lu wadyela uku asamadzinamize

  • @JescaNgwale
    @JescaNgwale 13 дней назад

    Boma ilo

  • @FraizerKamoto
    @FraizerKamoto 15 дней назад

    Mulela khugwa wathu uyu

  • @JosephSamuel-f6f
    @JosephSamuel-f6f 14 дней назад

    😂😂😂

  • @ThomBen-v4j
    @ThomBen-v4j 15 дней назад

    apa chakwera wakomoka basi

  • @ThokoMsonkho-hy4uc
    @ThokoMsonkho-hy4uc 15 дней назад

    Ndipo ineyo ndimanena kuti BANGWE imaposa Ndilande pa ndale munthu amene walandilidwa pa Bangwe desert ground ameneyo amawina samanyengelera olo akati agawe zibagera inu a MCP musamale

  • @MakheyiChabwera
    @MakheyiChabwera 15 дней назад

    Kkkkkk.

  • @ElizaSoko
    @ElizaSoko 15 дней назад

    🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣👐🤣🤣🔥🔥🔥🔥🔥🤸🤸🤸🤸🤸🤸🤸🤸🤸🤸