ZODABWITSA ZOMWE NDUNA IYI IKUPANGA - HON ENG VITUMBIKO MUMBA. TAONANI ZOMWE YACHITA LERO KU TOPMAX

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 23 янв 2025

Комментарии • 12

  • @GiftChitsulo-g9n
    @GiftChitsulo-g9n 10 часов назад

    Awa ndi akape ayiniakewo akuti Kam,peni ngati sizandale ndichifukwa chani ukujambula ukufuna akuone ndani

  • @mkandawirem610
    @mkandawirem610 4 часа назад

    Mungogwira ntchito osati Za chakwerazo ayi

  • @FortuneDavie-n6z
    @FortuneDavie-n6z 11 часов назад

    Koma njala sizinthu wungowowoza zina zilizose

  • @Hdsagdf-t1n
    @Hdsagdf-t1n 10 часов назад

    Zauchitsilu osangonena kuti mwayamba kampeni mmakampani bwanji

  • @JanetJamesMachila
    @JanetJamesMachila 11 часов назад

    Ndazikonda

  • @RaheemMoosaraheem
    @RaheemMoosaraheem 7 часов назад

    Uyu ndkape et walowesa ndale

  • @judithStuwart
    @judithStuwart 11 часов назад

    Imwe namwe tate mwalutila kukovwira wanthu uku mwakuchita campaign aaaaaa 😂😂😂

  • @harrytuliyani8957
    @harrytuliyani8957 10 часов назад

    Ukuononga nkhani yabwino ija mmalo mogwira ntchito ya boma uli busy kuyankhula za chakwera gwira ntchito yako ukuchita bwino kuwagwedeza ma company

  • @JanetJamesMachila
    @JanetJamesMachila 11 часов назад

    Mukayenderenso mu ndende bwana anthu akuvutika

  • @JackMvura
    @JackMvura 5 часов назад

    Anthu awa akuonjezera moto usi anayatsa kale kuti bomaa ndilomweli uku ena akugawa chimanga mudziko ziliko tiona pomwe adutsire pitala

  • @HerlbertKaalis
    @HerlbertKaalis 6 часов назад

    Ndale ma Company eeeeeeeeeeee chisilu kwambiri kuziyamba bwino kusilizila uchisilu bwanji osayamba ndi uchisilu ndikusilizila Za bwino Nyasi ya Nduna koma adanyela bus anzanu

  • @samchibenene4458
    @samchibenene4458 12 часов назад +2

    Ndilomwero boma