BRIAN BANDA NDI ULADI MUSA ZAKUMANA KU CONVENTION KULILONGWE ATENGETSANA |

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 9 сен 2024

Комментарии • 15

  • @P2favorZBNthengwe
    @P2favorZBNthengwe Месяц назад +7

    People they go to MCP because of money not loving the party, care for next year enjoy this time guys

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 Месяц назад +2

    Ndi awo akukhapanawo

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 Месяц назад +1

    Bwera iwe ku mcp ko for good it's your choice. Wanena kuti zipani zina zose ukuziziwa bwino ndiye ukuganiza kuti ndindani sakuyiziwa mcp mwina siukukumbikira zakuchikangawa pa 10 june

  • @Yanjanani
    @Yanjanani Месяц назад +1

    Kd MCP ndichipan cholamula? kapena ikulamula ndi Onse alliance??

    • @henryphiri6100
      @henryphiri6100 Месяц назад

      Chakwera wati MCP ndichipani cholamula.anaphadi Chilima anthuwa

  • @PrinceLuckKondowe
    @PrinceLuckKondowe Месяц назад

    Mukhaledi konko ku chikangawa musazatuluke akazaluza zisankho tizakufinya enafe siandale koma zimatikwana tikamaona anthu amene sakukhutisidwa ndizimene alinazo tizingoti anthuwa ndiamene akuononga Malawi 🇲🇼

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w Месяц назад

    A Musa ndi hule wa ndale, bwanji sanasinthe zinthu ali ku zipani zonsezi adazisiyazi.

  • @danielmagwaya1074
    @danielmagwaya1074 Месяц назад

    MCP zimvomelezani kt dzina lakukanika, zomwe mukuchitazo kulingat kimugwira mkazi akuchita chigoloro osamusiya kumangomukakamira timat imeneyi ndi mphongo yoputsa

  • @PrinceLuckKondowe
    @PrinceLuckKondowe Месяц назад

    Anthu amene akuononga Zikoli ndi anthu oyendayenda muzipaniwa coz sakufuna kutukula ziko koma kudya nawo. Amalowa muchipani chikakhala muboma chikatuluka nawoso amatuluka. Sakukonda chipani a galu amenewa.

  • @SolomonBewula
    @SolomonBewula Месяц назад

    Muyao okuba uyo

  • @BarwickSalanje
    @BarwickSalanje Месяц назад

    Mr uladi musa lakura ndi dyera basi

  • @user-gj4li2gc8o
    @user-gj4li2gc8o Месяц назад

    Dpp tippex government

  • @kondwanimunthali7401
    @kondwanimunthali7401 Месяц назад

    Nonsense

  • @BarwickSalanje
    @BarwickSalanje Месяц назад

    Mr uladi musa talk like you are a man you can't compaire udf and mcp