BON KALINDO LERO 12 AUGUST WANG’ALURA MCP AKUTI AKUPANGA MA PLAN OFUNA KULIMBANA NAYE KOMA SAMUTHA

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 9 сен 2024

Комментарии • 245

  • @Rometcma
    @Rometcma 29 дней назад +13

    Ndikadakonda bon kalindo utakhala president kwinako Malawi angasithe coz umphawi mumaudziwa bwana🎉🎉🎉

  • @user-gl8hc8fh4v
    @user-gl8hc8fh4v 29 дней назад +5

    The DC, President wa a Malawi osawuka, Malawi First go deeper

  • @augustMag
    @augustMag 29 дней назад +2

    Azingokenzeka kuzabera chisankho Cha 2025 osati azilimbana ndi anthu komanso osati azilimbana ndi Inu the DC Chilungamo Cha Amalawi Boooon Kalindo 🔥🔥🔥🥳🥳❤❤❤❤

  • @allanjosamu
    @allanjosamu 29 дней назад +4

    munthuyu mutu sugwira ndavetsetsa coz munthuyu akupanga target ma lndividuals😮😮😮

  • @isabelmartin7567
    @isabelmartin7567 26 дней назад +1

    The DC ❤

  • @martinndawala8125
    @martinndawala8125 29 дней назад +4

    Tamangooyikani Audio straight basi. Osatinso kummaiyankhulira kaye, voice yanuyo ikumapweteka mkutu.

  • @RebeccaNvenya
    @RebeccaNvenya 29 дней назад +4

    More 🔥 the Deeeeeceeee mwana oophya kwambiri 💪

  • @DominiqueChitimbe
    @DominiqueChitimbe 29 дней назад +7

    the DC ❤akamuna muna

  • @PeturosiNyirenda
    @PeturosiNyirenda 29 дней назад +3

    Apambaze amenewo 🤣🤣🤣🤣🤣🙆🙆🙆🙌🏽🙌🏽🙌🏽💥💥💥💥💥

  • @AndsonAcd-j6i
    @AndsonAcd-j6i 29 дней назад +1

    GOD BE WITH YOU BON KALINDO

  • @YasenYasen-q9g
    @YasenYasen-q9g 23 дня назад

    Dc❤❤❤❤

  • @user-rf4br1fv2z
    @user-rf4br1fv2z 29 дней назад +6

    Mmmmm wankali samadzing'amba yekha tsiku lidzakwana akalindo

    • @SanudiMcDonald
      @SanudiMcDonald 29 дней назад +3

      Iwetu iwe unya ndi chakwera wakoyo

    • @lucianoGeoffrey
      @lucianoGeoffrey 29 дней назад +1

      Pita ukakumane naye nde uzatiuze zomwe ukazione

    • @Musa1828-l5d
      @Musa1828-l5d 29 дней назад +1

      Pamtumbo pako ndi Chakwera wakoyo munapha chilima inu fiti simuwina agulu onukha kuthako

    • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
      @AbdulsharifulKalipinde-m6u 29 дней назад

      Iweyo koma ndiye uny'a nayo
      Chaka chake sichino

    • @user-vm7iz6oz6r
      @user-vm7iz6oz6r 28 дней назад

      Ukanakhara wazelu ukanakhala chete ,😡mwadzi...

  • @HamissMaidaz-x4h
    @HamissMaidaz-x4h 29 дней назад +1

    The dc mwana owophya kwambiliiiii❤❤❤❤❤❤

  • @ChiccoJelly-wp5wj
    @ChiccoJelly-wp5wj 28 дней назад +1

    We need to have 10 people in Malawi like Born kalindo

    • @GotepoBanda
      @GotepoBanda 26 дней назад

      Mau koma awawa olo alipo five

  • @user-sv5yi9gt4u
    @user-sv5yi9gt4u 29 дней назад

    DC kuno ku Kasungu tiyankhulireni , akufuna kupeleka ngongole koma chodabwitsa akufuna ma lD ,ndiye kuno anthu akupeleka ma ID maka ife ma MUSLIM, chonde bwana DC tiyankhuleni

  • @MAFUNSOMOLESI
    @MAFUNSOMOLESI 29 дней назад

    I like you so much Mr president watu

  • @lovemorembedza9145
    @lovemorembedza9145 29 дней назад +2

    Aaaaaah inu zachapani zigwirizana bwanji ndi za dziko ndindani angalimbane ndi munthu openga

  • @alomuddin8801
    @alomuddin8801 29 дней назад

    Boni kalindo DC ukumuyiliradi Mmalawi osauka, pitilinzani kuwaunikira azipani zomwe zikufuna kupanga mgwilinzano 2025, kmso kumuunikira munthu wa kumudzi chifukwa munthu wa kumudzi amangovota moti zingomuchoka mosaonetsetsayi mosaonetsetsa

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b 29 дней назад +1

    Love you Bon kalindo we silute you forever❤

  • @DavieMathyola
    @DavieMathyola 26 дней назад

    Osaopa osafooka comrade tanyiwa ,karindo again via bakili muluzi tv

  • @mbonilekisebe2286
    @mbonilekisebe2286 29 дней назад +1

    The DC mwana owoopsa kwambiri... Umakawana aise. Afiti a MCP sakupuma nawe bwino

  • @TerezaJaenda
    @TerezaJaenda 29 дней назад +2

    Sazanthekadi mmmmm katundu waboma kkkk🎉🎉😊

  • @JohnMota-o2u
    @JohnMota-o2u 29 дней назад

    Ba Bon K nanga mbaa mwakanika bwanji kumuchosapo chakwex yu galu oluma samakuwatu

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 29 дней назад +1

    The DC bon kalindo akunama iyeyo mr chikangawa aziwa chaka chino

  • @MonicaChanza
    @MonicaChanza 27 дней назад

    DC amatiyimirira ....ulemu wako....

  • @AllieJonassi
    @AllieJonassi 29 дней назад +1

    The D.C umakwana and proud of you

  • @GiftMakowa-k9f
    @GiftMakowa-k9f 29 дней назад

    Ulemu wanu Mr DC timakunyadilani kwambili❤❤❤

  • @HêsâGàttãh-f5c
    @HêsâGàttãh-f5c 29 дней назад

    DC et🎉

  • @Simionluhanga
    @Simionluhanga 28 дней назад

    Auze DC wathu

  • @GiftMakowa-k9f
    @GiftMakowa-k9f 29 дней назад

    Koma dc atakhala kuti kumalawi alipo athu 20 ayi futi kumalawi zitalila kale chifukwa ndimuthu wolimba mtima kwambili

  • @leviecashmere7555
    @leviecashmere7555 28 дней назад

    Chisankho I chichi mulungu azakhle pa tsogolo

  • @user-gl4wc9pq4e
    @user-gl4wc9pq4e 29 дней назад +2

    Chilipo chikukusata Bon Kalindo

    • @Musa1828-l5d
      @Musa1828-l5d 29 дней назад +2

      Simungamuthe Kalindo munama kwambri, munapha Chilima anthu oipa inu simuwina 2025 kumtumbo kwamako galu iwe

  • @user-hs2dw7ly2c
    @user-hs2dw7ly2c 29 дней назад

    The DC

  • @user-vc6cy6et4h
    @user-vc6cy6et4h 29 дней назад

    No to Nyawu party

  • @OssmanAbubaker-t2i
    @OssmanAbubaker-t2i 29 дней назад +1

    Ulemu wanu the DC timakunyadilanitu pachilungamo osaopa osafooka osatopa

  • @awaliaustin381
    @awaliaustin381 28 дней назад

    The Dc

  • @EvasonThupilifana
    @EvasonThupilifana 29 дней назад

    Kom A mcp musamale chifukwa tonsefetu ndife okwiya kwambri chakwela mbuzi yamunthu

  • @Rix297
    @Rix297 28 дней назад

    He is making total sense.
    Aluza ku convention atiphweteka awa.

  • @ehinsupport3217
    @ehinsupport3217 28 дней назад

    Bon kalindo ndi mbuzi kwambiri. Every day kumankamba dzautsiru basi.

  • @MartinChapita
    @MartinChapita 28 дней назад

    Akhalitse Dc

  • @LameckGamah
    @LameckGamah 28 дней назад

    Awa kwao kwatha let's see, time is coming amalawi atopa.

  • @samueljuma4452
    @samueljuma4452 29 дней назад +4

    Kalindo my guy,thana nawi agalu amenewa athe onse ena atengerepo phunziro achule achabechabe

    • @abe9104
      @abe9104 26 дней назад

      this is true i know this man

  • @DorisNkwanda
    @DorisNkwanda 26 дней назад

    The Dc...... Mwana wA line katola

  • @user-le9su3mt7r
    @user-le9su3mt7r 28 дней назад

    Chikangawa party

  • @GreevinWaMugowa-j9c
    @GreevinWaMugowa-j9c 28 дней назад

    Ndiwe Bon Mwana Owoopsya kwambiri muziko lonse la Malawi

  • @AnthonyChirwa-t4g
    @AnthonyChirwa-t4g 29 дней назад

    The DC mumatiimilila asiyeni agaruwo chao palibe

  • @JOHNMPEMBA-p3i
    @JOHNMPEMBA-p3i 24 дня назад

    Tamvanao 😮😮😮😮😮

  • @SailinggggJapaneseggg
    @SailinggggJapaneseggg 26 дней назад

    ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @abe9104
    @abe9104 26 дней назад

    my brother man for others woman u are number one

  • @ChilekaMoyenda
    @ChilekaMoyenda 29 дней назад

    Boni khalindo

  • @user-mi5pe3wd6d
    @user-mi5pe3wd6d 28 дней назад

    DC alozeni bas

  • @ehinsupport3217
    @ehinsupport3217 28 дней назад

    Osamamutsatira wamisalayu

  • @JohnMota-o2u
    @JohnMota-o2u 29 дней назад

    Ba Bon K nanga mbaa mwakanika bwanji kumuchosapo chakwex yu

  • @WITTNESSMBOBADINHONJOLOM-bv4un
    @WITTNESSMBOBADINHONJOLOM-bv4un 29 дней назад

    Tiyeni nawo bon kalindo aña achepa ngt àli madolo tikakumane chikagawa

  • @GiftJulius-gx2kb
    @GiftJulius-gx2kb 29 дней назад +1

    Mwana wa line katole😊😊😊😊😊

  • @SARGENTZIMBAMAGABA
    @SARGENTZIMBAMAGABA 28 дней назад

    UTM koma musitisilizaaa koma mulumgu alowerelepooo

  • @SternMoyo
    @SternMoyo 26 дней назад

    Mmmm koma DC

  • @user-ni4nw1ee2f
    @user-ni4nw1ee2f 28 дней назад

    Koma Born kalindo ndakakutundu 😂😂😂😂

  • @agnesschauya7687
    @agnesschauya7687 29 дней назад

    Aaaa zaziii, ofuna kuzipha salengeza, panga zomwe umatha tiwone

  • @user-ir3kb9ee9f
    @user-ir3kb9ee9f 29 дней назад +7

    💪💪 Viva DC

  • @SARGENTZIMBAMAGABA
    @SARGENTZIMBAMAGABA 28 дней назад

    Malawi kung'amba kkkkkk koma DC kkk

  • @JessieKholopa
    @JessieKholopa 29 дней назад +1

    Uyu eee ndi akatundu omanga ndi mawaya👐👐👐

  • @DanielNandajester
    @DanielNandajester 29 дней назад +1

    Awa koma apange resin chifukwa chachani mmmmm tapanga zako Bon

    • @Musa1828-l5d
      @Musa1828-l5d 29 дней назад

      Pamtumbo pako galu ndi chakwera wakoyo munapha Chilima simuwina anthu onukha kuthako inu

  • @LessonBester
    @LessonBester 29 дней назад

    The DCCCCCCCCCCCCCCCCCCCCCC Mwana oopsa kwambiriiii!!!!

  • @FrankJosiah-w8f
    @FrankJosiah-w8f 29 дней назад +1

    The DC mumakwanila

  • @ChikumbutsoAntony
    @ChikumbutsoAntony 29 дней назад

    Ur hello

  • @HOMEAWAY-h7t
    @HOMEAWAY-h7t 29 дней назад

    The DC❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @user-gj4li2gc8o
    @user-gj4li2gc8o 29 дней назад +1

    Munthu waufiti samazitama a bon iwe ndiwe saiz yanga osat ungalimbane ndi ziko

  • @MayesoBikefa
    @MayesoBikefa 29 дней назад

    Viva dc mwan wachabe

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 29 дней назад +3

    aboni kqlindo akuoneka kuti zokamba zawathela

    • @user-rz9rm4cb8x
      @user-rz9rm4cb8x 29 дней назад

      Kod apopo sanakambe or akunveka ngati akuimba nyimbo

    • @DanielNandajester
      @DanielNandajester 29 дней назад

      @@user-rz9rm4cb8x akuluwa a kupanga target mcp bac chifukwa adakanikanika kupita Ku embassy mpaka kum@ngonyoza awa nde Kaya ingonenani kuti mufuna dpp osati kumazembera

    • @EstherDebwe
      @EstherDebwe 25 дней назад

      ​@@user-rz9rm4cb8x😂😂😂anthu kufika potopa😂

  • @user-xs3pk1vp8i
    @user-xs3pk1vp8i 29 дней назад +1

    Daily kunyodza MCP chakuntha ichi

  • @manuelsamuel293
    @manuelsamuel293 29 дней назад

    We support you Kalindo

  • @KingTroy-t5e
    @KingTroy-t5e 29 дней назад +1

    Koma kutchuka unakufunisisa 😂😂unayiwelenga boh uli kuti nditchuke ndizingotukwana MCP 😂😂ndiwe dolo

  • @FosterChinzimuBanda
    @FosterChinzimuBanda 28 дней назад

    The DC mwana ophya kwambili❤

  • @ruthkundwe7448
    @ruthkundwe7448 29 дней назад

    No rest for the wicked,DC kachilungamo kalilmo

  • @user-ky4ce9gb6j
    @user-ky4ce9gb6j 28 дней назад

    Ndipo anthu amenewa akuiputa nkhondo kwambiri

  • @GaryMakhumula-mu3du
    @GaryMakhumula-mu3du 29 дней назад +1

    Ati nkatikati mwanyamamo muli nchenga hehehe!!!😂

  • @CharlesWyson-ue5fz
    @CharlesWyson-ue5fz 29 дней назад

    the dc mwana oophya kwambili

  • @KebdngzWarren
    @KebdngzWarren 27 дней назад

    Dc

  • @KondwaniJohn-mm3gk
    @KondwaniJohn-mm3gk 29 дней назад +1

    Waufiti samazitamandila....awa ndi mantha chabe

  • @chirwaellace1093
    @chirwaellace1093 29 дней назад

    The DC mnyamata oopya kwambiri, mufatu mkalimbana naye

  • @SteviePatrick-g2p
    @SteviePatrick-g2p 29 дней назад

    Number one the DC

  • @ChikkaLemani-qw6fn
    @ChikkaLemani-qw6fn 29 дней назад

    🔥🔥🔥🔥

  • @JenetPhiri-v5f
    @JenetPhiri-v5f 25 дней назад

    Fatsan phili

  • @johnmponda9070
    @johnmponda9070 29 дней назад

    Koma ine nkhani ya njuchiyo mwinatu nduna zinazi sizikudziwa akusewelatu amenewa😊😊😊

  • @MacPayesa
    @MacPayesa 27 дней назад

    Kkkkkkkkkk Koma Bon kalindoo

  • @EkaliKapito-y8q
    @EkaliKapito-y8q 26 дней назад

    Mwana wa mulanje weniweni

  • @PhalesNotta
    @PhalesNotta 28 дней назад

    Ndipo ayidya momvutadi ameneyoooooo😊

  • @CharityBanda-lm5cj
    @CharityBanda-lm5cj 29 дней назад

    Chimene amafuna kalindo sachidziwa oipa ndamene amabweletsa chisokonezo mdziko

  • @user-ps2us9vn8g
    @user-ps2us9vn8g 28 дней назад

    The voice of DC

  • @MaduraAlbertoJose
    @MaduraAlbertoJose 29 дней назад

    Hiiiii chakwela ali male

  • @Alfanimalanga
    @Alfanimalanga 28 дней назад

    9:19

  • @LastingsLalikamtawali
    @LastingsLalikamtawali 21 день назад

    ❤❤

  • @IshmaelMateyu-gl7rt
    @IshmaelMateyu-gl7rt 28 дней назад

    Viva DC😂

  • @DanChirwa
    @DanChirwa 29 дней назад

    Ngati amangova mulanje mulanje ayiziwira pa the DC

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 29 дней назад

    A Kalindo langizani chipani chanu chikupita ku komvesyoni pa 18 August nanga munthu umalangiza zinthu zitachitika kale

  • @PraiseDuweh
    @PraiseDuweh 29 дней назад

    Km ichi amwene

  • @MazwaiiMkhize
    @MazwaiiMkhize 29 дней назад

    Mmm!! Zoonadi, ngathi munthu walephela, obviously it shows that, kwa yiye mphamvu Mulungu wazilanda.

  • @user-dy4gc2hr5e
    @user-dy4gc2hr5e 29 дней назад +1

    Uyu ndi big man the DC chakwera chakwera ndimwana

  • @user-oe3dz7dy4j
    @user-oe3dz7dy4j 28 дней назад

    Ichidi ndichamisaradiiii!!!!!! Wangokura mutu koma zelu aribe