Ati Gule uyu Salivina Bwino Mmbwalo.

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 13 сен 2024

Комментарии • 51

  • @OssmanAbubaker-k3q
    @OssmanAbubaker-k3q 26 дней назад +9

    Chilungamotu chimenechi osaopatu osafooka osatopa kkkk

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 25 дней назад +6

    achewatu amenewo chilungamo kuyenda ngati manzi

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 19 дней назад +1

    Anthu awa ngati saphedwa ndi mwayi chifukwa ndi kwawo kwa chimwendo banda ....muthu amene amakonza ziwembu zonse ku mcp

  • @AbudulKamodzi
    @AbudulKamodzi 25 дней назад +3

    Mcp ndimbola achuluka ndi anthu ufuna kusilemereza okha osanganizira mavuto awena

  • @user-fy7qk6kk5s
    @user-fy7qk6kk5s 25 дней назад +2

    Ife tikufuna tidzidya msima kuyambila mamawa,masana,madzulo, usiku imeneo nde D.P.P

  • @IssahAluba
    @IssahAluba 13 дней назад +1

    chakwera achewa anuwo akukukanani mukti bwanji next year 😂🙌

  • @user-sw8bb3iz7x
    @user-sw8bb3iz7x 21 день назад +1

    Ochewatu omeo😊

  • @user-fy7qk6kk5s
    @user-fy7qk6kk5s 25 дней назад +1

    Zoona,zoona A.P.M wawina kale olo mr chikangawa olo adzabele sizizanukha kanthu adzipita gwape amenei D.P.P oyee!

  • @ChikumbutsoDavid-t4h
    @ChikumbutsoDavid-t4h 20 дней назад +1

    Angotula pas bassss

  • @Supiyanoamidu-ic7ys
    @Supiyanoamidu-ic7ys 20 дней назад +1

    Ochewa anzanga 🙏🙏

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 12 дней назад +1

    Ogogo....shame lazalo

  • @ChikumbutsoDavid-t4h
    @ChikumbutsoDavid-t4h 20 дней назад +1

    Sakunama amenewa nd akudowa amenewa

  • @LukaEthibwi
    @LukaEthibwi 13 дней назад +1

    Palibe chikukoma analowera kuononga Malawi okondwa ochepa

  • @user-lj7lm6ly7z
    @user-lj7lm6ly7z 25 дней назад +1

    Professor afa peter muthalika😂

  • @PiliraniDanielDaniel
    @PiliraniDanielDaniel 25 дней назад +3

    Ife timuvoteraso Chakwera! Dowa yake iti inu munamepo apa! Anthu atatu oti angogulidwa ndiye kumati Dowa ingavotele nkhalamba yosankha mitunduyo

    • @AbudulKamodzi
      @AbudulKamodzi 25 дней назад +1

      Achewa inu ndi agalu chifukwa mavuto alipanopa sakuwona kuti uyu anavotela mcp tonse tikulila limozi

    • @joegibsonzulu2599
      @joegibsonzulu2599 25 дней назад +1

      Tsankho silingapose zomwe aluchita Chakwera ni nyau zinzake. Tsano anthu ali ni ufulu osankhula uyo alufuna. Dziko sila Chakwera ili ayi.

    • @MaritaBanda-p4z
      @MaritaBanda-p4z 25 дней назад +1

      iwe ndichisiru osaganiza ndi chikangawa wakoy akupas zingat kut uzilakhula zoduka mutu galu ukuvutikaso chitsiru iwe ubwin wake tonse tikugula zodula limoz

    • @chrissyamanda5510
      @chrissyamanda5510 24 дня назад

      Inuso inu nde opanda nzerudi
      Kutengela kuti ndi ochewa onzanu
      Muluvutika or panado muzipatala
      Tsankho lipose asùweni akowo opatsa udindo okhaokha
      khalabe usasunthe uwone 2025
      Poti mudzabela mpake mukukula matako

    • @Eric-gb9ms
      @Eric-gb9ms 24 дня назад

      Iweso uli wekha don't be stupid

  • @louisbonongwe8537
    @louisbonongwe8537 3 дня назад

    Adha awa ndi anzeru akuyankhula zogwira mtima

  • @tasmania527
    @tasmania527 25 дней назад +3

    Si Dowa ya genuine iyi. DPP siingaphule kanthu ku Dowa. Ochita kugulidwa awa kuti abebetse DPP. Phuma chipani cha DPP, kuwina sikulongolola-owina 2025 ali phee. You can tell kuti anthu awa nga phuma through their leader's speech. A Mutharika kuyankhula mbwelera yokhayokha ngati kuti ma voters onse ali mmanja mwawo."Dikira madzi apite ndipo uziti ndadala".

    • @FrancisMazamba
      @FrancisMazamba 25 дней назад +2

      Mot lwe sukuwona mavutowo lne kwanthu ndikasungu Koma sininganene Za chikangawa Kut wapanga chitukuko

    • @tasmania527
      @tasmania527 25 дней назад +1

      @@FrancisMazamba Waboza iwe ukungopanga disguise. Chakwera ndi dolo osati zinazi.

    • @MzadziWanga
      @MzadziWanga 25 дней назад +3

      ​@@tasmania527 udolo wake pakupha chilima ndi ena aja ndi uchigawenga mzomwe akukwanisa plus kugwesa kwacha daily, mkuthwa mkamwa kma pa ground ndi 0/10

    • @ThokoLungu-tq6pw
      @ThokoLungu-tq6pw 25 дней назад

      Ndi brother wanga uyu from dowa Ndithu Sanagulidwensoi unama zed mmmmm

    • @tasmania527
      @tasmania527 25 дней назад

      @MzadziWanga Don't forget kuti munatiphela anthu 20 ku mzuzu, munapha ma Albino, munapha Njaunju, munapha Chasowa. Imfa ya Chilima yinali ngozi chifukwa ndege yinali yakutha ndipo mulibe umboni woti anaphedwa, nde shut up.Nkhanza zanu ndi kuyipa kwanu mumachita kunyada nako ndipo zinali pa mbalambanda.

  • @GeorgePatels-go7wj
    @GeorgePatels-go7wj 25 дней назад +1

    DPP Moto Kuti buuuu

  • @ChomboNgosi
    @ChomboNgosi 24 дня назад

    My vote

  • @user-kt5bq2wg6v
    @user-kt5bq2wg6v 25 дней назад +1

    Bodza ili, mavuto adalipo kuchokera nthawi ya kamuzu,
    Komaso inuwo a Dpp. Nthawi imene mudali boma bwanji wosathetsa mavutowo.

  • @TelezaManyela
    @TelezaManyela 14 дней назад

    zoonadi akunena bamboyu

  • @CustomMphandauyo-oe3jq
    @CustomMphandauyo-oe3jq 25 дней назад +2

    Anzawo akugaula nursery pano... Anthu awulesi awa

    • @MaritaBanda-p4z
      @MaritaBanda-p4z 25 дней назад +1

      koma zomwe akuyakhulaz ukuzimveses bwino lomwe chikangawa iwe

    • @chrissyamanda5510
      @chrissyamanda5510 24 дня назад

      Ulesi ndiwe osati
      Zagwilizana pati
      Mudamuphelanji chilima asatana inu

  • @JohnPetro-vv3er
    @JohnPetro-vv3er 25 дней назад +2

    Amalawi ozindikila kwambiri

  • @RAJABSTYLESTYLE-yi1el
    @RAJABSTYLESTYLE-yi1el 25 дней назад

    kugulidwa kotai koditu zamavuto alipano sikuti munthu ungsmunsmize