JB mpaka waonetsa ma Certificate ake ndipo wamuonetsa Baghaya kuti PHD yake ndiyopanda ntchito 😳😳

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 18 сен 2024

Комментарии • 75

  • @pauljosephmakaula6835
    @pauljosephmakaula6835 9 часов назад +5

    Free career talk, very educative and informative! Bravo JB 👏 👏

  • @ayamijackson1443
    @ayamijackson1443 9 часов назад +6

    Jb ndiwed mamuna mn i learn something from you excacty ❤❤❤❤

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 9 часов назад +4

    JB basi mutayeni Baghaya mwamung'alula mokwana

  • @user-oc8nj3or6y
    @user-oc8nj3or6y 9 часов назад +4

    😂😂😂😂Baghaya wafoama komwe aliko😂😂in English nyekwelification😅😅

  • @mphatsokaliasi
    @mphatsokaliasi 10 часов назад +2

    Zatani kt mpaka aziyakhula modekha Chochi ndiye wakamba za zeru hvy apa sitikuziwa kt amaliza motan koma komwe wakamba apa zandigwira mtima bola zisathele maphuzo apa big up

  • @mohamedriazshreef8697
    @mohamedriazshreef8697 9 часов назад +3

    Number one jb ❤more fire 🔥

  • @greychizaka4088
    @greychizaka4088 10 часов назад +2

    JB yo ndi heavy weight kwambiri😂 mulekeni afale

  • @JacquelineKanjedza
    @JacquelineKanjedza 9 часов назад +1

    It really shows kuti a lot of pple do love anthu olimbikitsa kudya zaulere

  • @chikaonekarh
    @chikaonekarh 8 часов назад +1

    Kkkkkk koma JB wandiwaza at amangojambulitsa kachipinda kamodzi pabalaza Pali shashingiii wina

  • @ibrahimatibu8784
    @ibrahimatibu8784 10 часов назад +2

    Galu ameneyo akudya galu ku China

  • @yowasschitsosa5348
    @yowasschitsosa5348 8 часов назад +1

    Paja xul imangochotsa umbuli osat uchitsilu, kukhala ndi phd kma munthu ndi m'mphawi kkkkkk

  • @satielsatinox5267
    @satielsatinox5267 6 часов назад

    Mavyete my childhood friend...i know him ndiwanzeru plus his twin brother Mclester....mafana oti ndima cousin a Walter Nyamilandu angakhale makape? zosatheka....bravo Alberto umakhwana❤‍🔥❤‍🔥❤‍🔥

  • @johnkatapeh7182
    @johnkatapeh7182 9 часов назад +2

    Nice 👍👍👍👍❤

  • @vidahlinyama7150
    @vidahlinyama7150 8 часов назад +1

    Well said akulu

  • @mzondinkosi1151
    @mzondinkosi1151 2 часа назад

    Because he was not selected. If he had a degree,he would be saying something else- backing it up.

  • @AndrewjemesJemes
    @AndrewjemesJemes 9 часов назад +2

    Ma fact okha okha

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 5 часов назад

    Apapa JB ndaziwa Kut si kape ur morethan strong I learn something else.

  • @BENARDMPHANGA
    @BENARDMPHANGA 9 часов назад +2

    Iweo nd dolo katatu

  • @GeorgeMkalemwa
    @GeorgeMkalemwa 8 часов назад

    U were one of my up pple to look to you have sense ❤

  • @mohamedriazshreef8697
    @mohamedriazshreef8697 9 часов назад +4

    24:59❤❤🎉

  • @mohamedriazshreef8697
    @mohamedriazshreef8697 9 часов назад +3

  • @hawardmkandawire673
    @hawardmkandawire673 Час назад

    Wamuyamba dala morton apo😂😂😂 mawa abwela ndi fire pano😅😅😅
    Akuonetsa zoopsya

  • @dorcaslouisamwango2428
    @dorcaslouisamwango2428 2 часа назад

    JB wayankhula za nzeru kwambiri very true what you have said

  • @stanleymollen7273
    @stanleymollen7273 6 часов назад

    Generally, fanz ya BAJ sindiona ngati ndi amzeru..

  • @jacksonmaster2288
    @jacksonmaster2288 9 часов назад +1

    Uyuyu ndi katundu,,, dolo kwambili

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 10 часов назад +1

    Uyu okudya achuleyu amabowa in fact jb ndi shasha

  • @hawardmkandawire673
    @hawardmkandawire673 Час назад

    Machine okhaokha akumanapo jb versus morton baghaya😂😂

  • @BrandinaMphuka
    @BrandinaMphuka 4 часа назад

    Kkkkkk maveteeeee more fire JB umandiwadza iweyo

  • @user-rg4du4vu9r
    @user-rg4du4vu9r 6 часов назад +1

    J,b ndinfana woganiza bhooo ntaye uyo azibunyura uko

  • @GiftMpando
    @GiftMpando 3 часа назад

    JB ndiakamunadi
    Sazikonda ngati enawa kumangotiwalira at Ali Ku chana
    Kumangotumizira zinthu zina zokuti tikumazíonanso mu bt kumalawi komwekuno
    JB umakwana😅😅😅😅😅😅😅

  • @mzeewandembonyirongo2972
    @mzeewandembonyirongo2972 2 часа назад

    Mathematics is a very important thing in life. People can have money with xool. Very true...but you cannt have a country without pipo with esucation noooo...you thought it wrong...

  • @chifundocharles2348
    @chifundocharles2348 53 секунды назад

    This is educative 🎉🎉🎉

  • @aminikondwani9361
    @aminikondwani9361 9 часов назад +1

    JB ndikatundu

  • @raphaelfrank1616
    @raphaelfrank1616 Час назад

    Apa nde kumenya kugwesa 😂😂😂

  • @vidahlinyama7150
    @vidahlinyama7150 8 часов назад +1

    Zoona zeni Zeni izi

  • @AlfredManjawira
    @AlfredManjawira 8 часов назад

    Iyi yokha nde wanisangalatsa wakamba ma wise

  • @giftkamwiyo9175
    @giftkamwiyo9175 9 часов назад +1

    Zakawawa dzuchita kubeba

  • @NovemberMmangathayo
    @NovemberMmangathayo 51 секунду назад

    😂😂😂koma jb umakwa

  • @hawardmkandawire673
    @hawardmkandawire673 Час назад

    Ulibo and wise big Big

  • @bensonMuyaba
    @bensonMuyaba 2 часа назад

    Morton Baghaya ndimfana wabho

  • @FelixBoss-yn9pe
    @FelixBoss-yn9pe 8 часов назад

    Pajatu ife timanena kuti JB yu osazamphweketsa

  • @Ramosfresh
    @Ramosfresh 5 часов назад

    Osaphwasula mutu wake kuti uzioneka bhooo bwanji

  • @SymonNamalomba-sh3fu
    @SymonNamalomba-sh3fu 2 часа назад

    Basi amalawi nonkha nonkha kumalimbana ndi uchisiru

  • @MustafaAjalu
    @MustafaAjalu 8 часов назад

    Kunyozana siku ngati thandize fosefe ndi a malawi
    Tiyeni tizilakhulana moremekeza na

  • @JusticeKalemba
    @JusticeKalemba 3 часа назад

    Koma certificate yaku poly siikuone ifeo ku xul sitinapite koma ma log timawaziwa

  • @mikebernabechimundi3472
    @mikebernabechimundi3472 8 часов назад

    From Kamuzu to Chakwera tonse tima feeler achina JB even Barack Obama amadziwa Kuti Ghetto ndi nyatwa, who Is Baghaya???😅😅😅

  • @fahadmilanzi
    @fahadmilanzi 8 часов назад

    Jb uli bhoo koma ndikupemphe asamatukwane

  • @stardlassim9537
    @stardlassim9537 8 часов назад

    I go for jb

  • @AbelBnkhoma
    @AbelBnkhoma 9 часов назад +1

    mavyete

  • @MadalitsoKachelenga
    @MadalitsoKachelenga 8 часов назад

    Ulibo jb , auze afana apa malawi apenye . Osati munthu uzikamba zobunyula. Ndaku Fila hev man.

  • @JameMirward-vm4dm
    @JameMirward-vm4dm 7 часов назад

    Tsono iweo ukunipo pbalipo ?? Tachotsa chinkhope chakocho

  • @Ahlubyt
    @Ahlubyt Час назад

    😂Baghaya ndi zoba

  • @GraciousFrank
    @GraciousFrank 3 часа назад

    Wayankhula mwa mzerutu lero JB

  • @CrownsowaniCrownautotronics
    @CrownsowaniCrownautotronics 27 минут назад

    Koma jb osamamuputa dala kkkkkk akuphwasulani

  • @mzeewandembonyirongo2972
    @mzeewandembonyirongo2972 2 часа назад

    First to say that some courses or majors are not important my bro JB u missed it all. Economics, Mining, Jorno, Arts, Music etc MBA , political science etc are all important in a country,s development. Mind you those that dont specialize are mostly technician and not professionals. You have mentioned some people here and they did Drama as major at college. But if one dont know may think is not an important aspect in development. You have also talked about doing only components for example in ICT....and dispaised those with Degrees in Computer Science as almost useless. Thats not the case remember the ones that tought you were the same pipo with Com degrees. However you have confirmed that you were not at Poly as a generic student. And you have also wrongly said kuti atumbuka this that. That was wrong. And to be a lecturer is also not wrong. Teachers lecturers make an educated society. Even if they can be poor appreciate thier work. I rest my case

  • @YOMALO.
    @YOMALO. 9 часов назад +1

    Akulila ameneyu...si 37 points imeneyo! 😅

  • @JamesmaxMhonie
    @JamesmaxMhonie 8 часов назад

    Koma abale eish

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule Час назад

    JB

  • @AlickjoiceMatchipisa
    @AlickjoiceMatchipisa 2 часа назад

    Jb mtaye kapeyo niwamisalatu akuchedwesa ase iweyo ndidolo wekha sungadabwe kaya akuti bagamiz zinalake muthu ubongo wake ogwira angamati zoti kulimulungu sakuziwa komaso zoti iyeyo analengedwa saziwa😂😂😂 misalatu imeneyo kape wachabechabe 25 years akuoneka kukalamba kuposa bambo anga azaka 68 😂😂😂 gwapeyo akuchedwesa wamisala anxake ali kuzomba nzeru akuzitamazo ankoze zikolake ndi anthu ake nde ndimutama kuti ndidolo mesa akuti mulungu kulibe nde akhale mulungu iyeyo ndinzeru zake zopoilazo

  • @MuhammadBAKILI-kl2mj
    @MuhammadBAKILI-kl2mj 3 часа назад

    JB wqsadzamuhweketsa

  • @PiusChawinga
    @PiusChawinga 6 часов назад

    Mhu

  • @FranciscoLaissone-t9l
    @FranciscoLaissone-t9l Час назад

    JB ndidolo bansi samakamba za gay.

  • @amonfrancisautotune2073
    @amonfrancisautotune2073 Час назад

    😂😂😂😂

  • @EnockChikaonda-zw5xz
    @EnockChikaonda-zw5xz 7 часов назад

    😅😅😅😅

  • @user-vx5kv8dz3d
    @user-vx5kv8dz3d 3 часа назад

    Man isiyeni zoba ijayo

  • @mphatsochitimbe2205
    @mphatsochitimbe2205 7 часов назад

    Koma akuluwa kunena chilungamo mzeru zawo ndizopelewera

  • @PiusChawinga
    @PiusChawinga 6 часов назад

    Masamu adakuvutani mwabisapo pa math kkkk

  • @mablemwagomba6730
    @mablemwagomba6730 5 часов назад

    Nsanje JB

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 9 часов назад

    Jb ndiwe chitsiru

  • @gaddiemkandawire6436
    @gaddiemkandawire6436 8 часов назад

    Awa chamba awa zawudoli palibe makaladi kuba ngati mukuyakhula za umekhi kuba ma karadi

  • @gaddiemkandawire6436
    @gaddiemkandawire6436 8 часов назад

    Adolo inu tiamkusatani kuwongati muzititumizila zanzeru koma yai mwayanba kupanga zanu zanu komakonda kumasatila anthu sangakuthandizeni chifukwa chani?
    Palibepo phunzilo.mungatengepo ameneyo mukumuti JB kaya ndi amene mukumamuti baghaya oalibebepo vhingaphilepo anthu pa anyhu awawa

  • @BENARDMPHANGA
    @BENARDMPHANGA 9 часов назад +1

    Iweo nd dolo katatu

  • @mohamedriazshreef8697
    @mohamedriazshreef8697 9 часов назад