I believe coz nane ndakula ngati kanyama ka mutchile I was starting working tchito za pakhomo ndili ndi zaka 9 standard 4 tikatsekera school fees malipilo ake,,,,, Ndipo ndimangwira kwa Mahule kumabweretsa azibambo akuluakulu, mu room mwana ndli momo😢😢😢😢😢😢😢 Inu mwaleledwa bwino Zithokozani Mulungu.
Am listening from Zambia next plz
Wow am enjoying the story❤ God knows😊
Watching from Mozambique
Sounds good l
Ndili side yakonko bru. Very interesting
Unapezeka bwanji Uline phone kumabwereka pomwe ndiwe wekha black unali ndi phone mchaka Cha 2000+??? We r waiting for part 2
Q😊
Very touching story
Very interesting
The flashing mpungwe-pungwe words muzichotse/ musamaike sizikuonekabwino
Indeed GOD knows everything
Eeeee nnaimverapo iiiii🙌
part 2 waiting
Kukula mopanda chitetezp Cha makolo mwana amakula mwaukhuluku,amwenewa akundisoundikura mwaukhulukukhuluku eee zaumvava zinalowelera,and ma speaches awo ndumboni watunthu kuti ndikabwerebwerw
Bravo mr God knows maseko
Next please 🙏
😂😂😂😂 Akuluwa anali amisala mutu wawo sumagwira bhobho 😅😅
Goog research keep it up ❤
Koma akuluwa esh😂😂😂
Kuchoka pa kusetsa to production manager 😂
😊lo
Zimkatheka back in those days kwa munthu oti amatha English.
I salute you God Knows.
🎉
Very touching life story and I trust this guy lives a changed life
Part two please
God's time is the best
Next
Next plz
Check aponya
Ibwele ❤
Next phase tiipeza bwanji? I have really enjoyed,, phone anawasiira madam kapena, or he sold mkati mwawulendo
Check ilipo😊
@@mirriamnyongolo-vf6cn Ili pati?
This story is not adding up😂😂😂😂 za ku Chiringa Mfuti kuwombera pa Chiringa MCDE mmmmm I don’t know
MCDE yomweyo😅😅😅
wansembe anaimbira kwawo akufuna kucokako....by that time abale Ake anali ndi phone??? Mmmm
@@mahmoudjohn2382 not adding up. The story is much of a fiction than the truth too many gaps.🤣🤣🤣🤣
Paja kudali ma ground phones brother nanu mwatani kodi
Nex plz plz
Iwe opusa kwambiri umafuna ulemu wake azipatsidwa otani? Pita ukayambirenso akuotche uone
Kangaude kubwera patali patali bwanji
Ayi ayi ayi nkhani ya mkuluyi it's too dramatic 😅
Nxt plzzz 😮
Mmmm zovuta kwamvili
Same same only God knows
Phone yoyamba ya black man inayenda bwanj panthawi imene amavaya kujoweni? nayesotu uyu ndwabodzaso shatapu zake
Ku Brits masiku ano anthu amakwela straight from Joburg to Brits R100
Bro zandikhuza zaphwanuyo ause mutendere
@@ShadreckMwija ndipo mmmm kuvetsa chisoni
Mukudzitenga ngati zabodzanu khalani
Interview yabodza yochita kukoza
Koma yaaaaaa
Kodi umachokera boma lanji?
Km ngati mkulu uyu sakunama eeeeee waziona
Zikumveka ngat bodza I don’t believe at all😂😂😂
I believe coz nane ndakula ngati kanyama ka mutchile
I was starting working tchito za pakhomo ndili ndi zaka 9 standard 4 tikatsekera school fees malipilo ake,,,,, Ndipo ndimangwira kwa Mahule kumabweretsa azibambo akuluakulu, mu room mwana ndli momo😢😢😢😢😢😢😢 Inu mwaleledwa bwino Zithokozani Mulungu.
Nnaimverapo koma siimandikwana
Nkhani yokoma kumvera uku
😂hygiene
😂😂😂😂ndili konko ku brits bro
akuluwa koma zambili akunama
God knows eeeh ur full of stories
No
Ndipo nthawi imeneyo joz isali ngati panotu Pano park station ya Brits yo idathapo kkkkk life timadutsa mwambiri ndithu
😅😅😅
Tikudikira basi
Please tell the reporter to ask abt years of the actions he has been doing.
ooOooooo9
Nkhani yabodza mkati mwake
God Nknows Tchalesi 😅😅😅😅😅
Mnyamata wamphavu dzake kukayithawa mkhalamba man to man kuphiri yet akuti adamenyapo akuba mpaka kuwina ndewu. Iam confusing pamenepa 😂😂😂
Amathawa ndimene imaonekera khalambayo😂😂😂
Part two plz
Next
Zikumveka ngat bodza I don’t believe at all😂😂😂
Muchedwa imwani panado muchira tifuseni omwe tikumuziwa munthu tikuuzeni
Zikumveka ngat bodza I don’t believe at all😂😂😂
Next