Zandikhudza komanso mantha kuti dziko laipa choncho , how many innocent people who have been victimized and faced untimely deaths just because of , this world is been sodomised , we thank God for rescuing your precious soul , only God knows why He allowed you to come across inhumane acts but a day is coming all these evil people will pay for their evil behavior, I cry for the innocent souls in the hands of these beasts
I came across this guy when we were doing donations he really cares for the street kids. He is taking care of many young boys and girls. God bless him
Ooh God is God indeed,this is a calling ❤
Ur name is something else ,eish this God ndagoma naye ine
Miracle working God, Yahweh 🙏
First comment ndakhala ndikuidikira part 2 imeneyi
A long waited part
ABale MULUNGU apose pa menepa this is really meaning of your GOD knows mmmmh
God knows indeed 🙌🙌
Thanks God
Zandikhudza komanso mantha kuti dziko laipa choncho , how many innocent people who have been victimized and faced untimely deaths just because of , this world is been sodomised , we thank God for rescuing your precious soul , only God knows why He allowed you to come across inhumane acts but a day is coming all these evil people will pay for their evil behavior, I cry for the innocent souls in the hands of these beasts
I appreciate to you my brother this is my ambition ❤❤❤
To God be the glory
Nyimbo ikhale ya Favoured cctas " moyo wanga akuusunga ndicholinga
❤❤❤ ambuye azikudalitsani a God knows
I too need this God 🎉 I even tear 😢
Moyo Wanga ausunga nd cholinga ❤❤❤❤❤❤
Mulungu apitilize kusunga moyo wanu 🙏🙏
WAY MAKER & MIRACLE WALKER.❤❤❤
Wow!we Thank GOD
Mmmm ndagwidwa mantha.ziko lapansi kukuchitika zinthu zoophya
GODKNOWS chonde udziwe kut Yehova Ali nawe ndi cholinga
Zina ukamva eeeeh
Kumwamba kuli Mulungu guys
Chonena ndilibe ambuye mukule ndithu muzonse amen
Almighty God
Ambuye Ali Nanu cholinga ndithu mulungu ndiwadongosolo🙏🙏
Ambuye Mulemekezeke nthawi zonse
Amen 🙏🙏
God bless you
Groly to Almighty God 🙏🙏🙏🙏
Bola lilipo apa pango'ono bwanji osauza athu amene ali mundegemo zomwe zikuchitika bwanji osathawa ku airport kumakhala athu ambili bwanji pokwera ndegepo osakuwa
From brit's to beid buliji ndi wulondo ot utha Kuyenda 3 months or more
Eyiii koma mkuluyi wakumana ndizinthu Komabe Mulungu amamukonda kwambili
Koma tikapsa yoooo dzikoli kukuchitika nyasi Mulungu atithandize kwaazanthu omwe akuchitilidwa muchitidwe umeneu
God is good
Inali plan Mwanayo ndi bambo akewo cholinga kusokoneza umboni anthu ama deal ngati amenewo samusiya ndi moyo
the Drug Cartels... thats true Bro
Eish this world is full of evil
Mulungu aliko ku mwamba 🙏🙏🙏🙏
Zosezo anali ma plan A Mulungu kuti moyo wanu uphulumuke sizophweka ayi pokuza malile anu
Eeeee Koma kunja kuno anthu akuchitilidwa nkhanza mmmmm
Ambuye apitirize kukusungani ndi moyo wanthazi ndi wautali
GOD CARES
Kodi atsikana awiri amene amagwira nawo ntchito aja anali ochokera dziko lanji
Malawi
Mpulumutsi wathu ndi yehova ekha basi
Zonse nkumwamba!!!!
Ziko lapasi 😢😢😢😢😢😢😢😢
To God be the glory