UTM ikupanga gwilizano ndi DPP. Kodi Chakwera ava bwanji??

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 11 июл 2024

Комментарии • 585

  • @user-qq1uj7ct6n
    @user-qq1uj7ct6n 25 дней назад +37

    Zipani zonsenzi zili pansi pa DPP. so lingaliro labwino kubwerera Ku DPP
    watching from Cape Town

  • @LukaAron-el5qh
    @LukaAron-el5qh 25 дней назад +39

    Mai mawu anu ndi amphamvu ambuye awadalitse

  • @LysonMtalika-tb6fk
    @LysonMtalika-tb6fk 25 дней назад +24

    Very true Madam, we need to have strong party for alliance

  • @EmmyYafete
    @EmmyYafete 25 дней назад +10

    Very true mandam ,ndazikonda kwambili bwerelani kwa amai anu basi tingwetse MCP ,

  • @augustMag
    @augustMag 25 дней назад +10

    Mau amphamvu Mai atigwira mtima Bambo wanu APM akulandilani ndi manja awiri sangalore kuti ana Ake asowe kopita iye qlipo

  • @EnetChiomba
    @EnetChiomba 25 дней назад +5

    Eishii koma apapa zikhala bwino bwanji ndipo zitero ndithu❤❤

  • @Namphuno
    @Namphuno 24 дня назад +4

    You have proven to have big brains than other men in UTM, you have our support

  • @paulkalizangoma5904
    @paulkalizangoma5904 25 дней назад +5

    This is what Malawians were waiting to hear from you. You made a right decision. Thumbs up to you all. We are fully supporting you, and we shall be behind you forever.

  • @MarcosDjussa
    @MarcosDjussa 15 дней назад +1

    Komatu amai awa alankhula zomanga Malawi wasopano God bless you mama

  • @EnriquedakazifoxZifox
    @EnriquedakazifoxZifox 22 дня назад +1

    Powerful massage madam and am looking forward for the mgwirizano that is coming viva 🇲🇼 🇲🇼 🇲🇼 viva DPP,,,, watching 👀 from Lusaka

  • @user-lg6ym4hz3w
    @user-lg6ym4hz3w 25 дней назад +1

    Mai inuyo very true watching from LESOTHO ndipo ndi Mulungu amene wakunong'onezani kuti muyankhule mau amenewo

  • @user-fq4kv8dj4t
    @user-fq4kv8dj4t 25 дней назад +6

    Mai mwayankhula za nzeru koopsya ndipo iiiiih sindikutha kukumvesesani kuti nzeru zinenezi bwanji inuyo

  • @LubaniLameckmbewe
    @LubaniLameckmbewe 25 дней назад +11

    I totally agree with you

  • @user-ru2pm6nl3u
    @user-ru2pm6nl3u 25 дней назад +4

    Mayi uyuyu amaganiza mwachungu ngati mwamuna 🎉❤❤❤❤❤❤❤

  • @HappyKanyangala-oq1kk
    @HappyKanyangala-oq1kk 25 дней назад +2

    Ndinu mburi zedi mulipachangu koma choononga komaso kachipani kanu kakuntha nanga ku d p p mulibepo Udani a a a si wa UTM iwe ukufuna kuononga mpunga WA UTM

    • @PetrusTlhokwane
      @PetrusTlhokwane 25 дней назад +1

      Samamva asiye adzaziona ayiwala zimene adamupangira mademo APM azabwezera zonse zija mmmn they have to learn through mistake with tose alayasi km UTM bwanji mwayamba kuti gwesa phwayi

    • @HappyKanyangala-oq1kk
      @HappyKanyangala-oq1kk 25 дней назад

      @@PetrusTlhokwane yes edid

    • @selinaSingini
      @selinaSingini 21 день назад

      Dpp yikanakhara kut yimamukonda chilima sakanachokako nde musaiware kut chilima nayo anapangira kupya mtima kulowa Ku mcp kut achose dpp mu boma mukwiyo umapangisa munthu kut asapange chinthu cholondola dekani popanga zinthu

  • @ChristopherChimbalanga-ez5he
    @ChristopherChimbalanga-ez5he 25 дней назад +7

    Mau ogwila mtima kwambili 💙💙💙🔥🔥🔥

  • @Sammy-vb1ed
    @Sammy-vb1ed 25 дней назад +1

    Chakwera sakupuma bwino. Madam mumaganiza mokuya I agree and let's vote dpp utm afford udf, tigwilane manja.

  • @user-ri8em6my2e
    @user-ri8em6my2e 25 дней назад +4

    Mau mau,udani wampaka muyaya mundale mulibe Tiyeni kwaADad bola Ng'onazi tizitulutse 🔥🔥

  • @fahadwalipeya8656
    @fahadwalipeya8656 25 дней назад +3

    Muli power speach inuyo mama🙏🙏💯💪

  • @PeterNamphwanya
    @PeterNamphwanya 25 дней назад +4

    You is best futures ❤❤ 100% that's one plan A not B ❤❤❤❤❤❤❤🎉

  • @NumbDee
    @NumbDee 25 дней назад +2

    Patricia kaliat ndi makina paokha welcome back mom ur loved

  • @mrcoolthegreatthinker3363
    @mrcoolthegreatthinker3363 25 дней назад +2

    Powerful mama mwaganiza kuposa mwamuna ndakukondani🎉

  • @OwenWalter-nz7uo
    @OwenWalter-nz7uo 25 дней назад +1

    Omwe akusunga udaniwo tawafunsani kuti kodi wina watichosera chiyembekezo chathuyu ndi awa omwe tinasiyana nawo mwamtenderewa kwabwino kulowera nkuti? Coz pakakhala kugawanikana kwazipani MCP sichokadi u are right

  • @MussaHassani-zg1hm
    @MussaHassani-zg1hm 24 дня назад +1

    Thanks Mai anthu mwayankhula bwino kwambiri thanks so much for ur spish

    • @PeterChilombo-ou2cd
      @PeterChilombo-ou2cd 23 дня назад

      zoona koma tipange zimodzi chakwera achoke udani pambuyo pangani zomwezoo moto kuti bhuu!j

  • @lovenesskampira
    @lovenesskampira 25 дней назад +4

    Powerful message mama

  • @user-lp8wj3vq4x
    @user-lp8wj3vq4x 25 дней назад

    Well done mama nkhani.imeneo ndiyabwino tiyeni ku dpp. Amene akufuna ku mcp sianthu.amenewa

  • @KennedyJabesi-x6h
    @KennedyJabesi-x6h 11 дней назад

    Good advice ,join together to remove the devil.plz.

  • @user-wl4nd7ic1s
    @user-wl4nd7ic1s 25 дней назад +1

    Wake uppp UTM family, that's right decision madamm, let's forget about the past!!!

  • @JimmyHarawa
    @JimmyHarawa 25 дней назад +14

    Good decision sitikufuna njara ku Malawi

  • @user-yz4mx7py3b
    @user-yz4mx7py3b 25 дней назад

    Powerful tiyeni amalawi tidzuke tigwiranane manja Mcp paulendo anthu akupha inenso I wish kuti Mcp imwalire viva UTM viva DPP Rest well our hello

  • @BentryMwagomba
    @BentryMwagomba 25 дней назад

    Thanks madam for the advice

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w 25 дней назад +1

    100% mai, UTM, DPP ndi AFORD gwirizanani mugwetse MCP ndi chakwera atitopetsa, mai wa nzeru kobasi.

  • @user-wx1jt5fd2j
    @user-wx1jt5fd2j 23 дня назад

    Mwaganiza mokhwima maganizo abale athu a utm kupanga mgwilizano ndi DPP komanso tili ndichikhulupiliro kuti zipani mwanenazo mosogozedwa ndi Ambuye komanso anthu kulilira dziko lamalawi pamene lafikapa liphulidwe pa moto osatira azipanizo sionse angakondwere koma ambuye achite kufuna kwake pempho a DPP zichepeseninso pa anzanuwo kondanani samaliranani khululukirananipangani umodzi ochokera pansi pa mtima may God bless you

  • @marthansaliwa7732
    @marthansaliwa7732 25 дней назад +3

    Mphechepeche mwa njobvu sapitamo kawiri. UTM iyime paokha ili ndi tsogolo kungatalike. Sitikufuna kubwereza zomwe zachitika ku MCP.

    • @RoyKambalame
      @RoyKambalame 25 дней назад

      Ndipo zoona osabwereraso mmbuyo Maso patsogolo

    • @CharityMhone-uk9ym
      @CharityMhone-uk9ym 25 дней назад +1

      Koma kuima pa nonkha simungatenge boma never popanda kuphatikizana ndi chipan champhamvu 😮

    • @user-tk6wf2eg4z
      @user-tk6wf2eg4z 25 дней назад +1

      Imani nokha tione dpp nde ndiyamoto ndikale

  • @user-te4ii6sz2v
    @user-te4ii6sz2v 21 день назад

    This is practical and very positive politics.
    Let's follow this path. I never new that in UTM there are some pipo who think like this. There is so much unnecessary noise which pipo think is politics but nope.
    God bless you.

  • @PetrusTlhokwane
    @PetrusTlhokwane 25 дней назад +1

    Koma a mayi inu mutizuza kwambiri ndipo you have to learn through mistake muyambilaso tose alayasi tatopa ndi kuliratu ife Chaka chino Chigoliyati chinalephela khondo kwa David nde inu bwanji a UTM km DPP yanuyo 2020 munayipangila mademo nde mwayiwala km mukazi wa Loti adayang'ana m'mbuyo ndikusanduka chulu

  • @amoschataika7440
    @amoschataika7440 25 дней назад +1

    Very Bravest speech Sister I salute you

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 25 дней назад +1

    Mcp ikuchoka mudzina La Yehova usogoleli umene Mulungu sakondwera umene Mulungu sakondwera nawo amaugwetsa or patavuta bwanji

  • @sarahnachu914
    @sarahnachu914 20 дней назад

    Very amazing let's unit ❤ watching from Cape Town

  • @henryibrahimsailes4638
    @henryibrahimsailes4638 25 дней назад +1

    Ndipo akapanda kutuluka tiwatulutse ndiifeyo UTM,DPP, AFORD combine with UDF mcp will be defeated mai iminoyo ndi amzeru kwambiri

  • @ivychithyoka1551
    @ivychithyoka1551 25 дней назад +8

    Zoonadi ma tigwirizane NDI DPP,ATM,AFORD+UDF ......moto buuuuu

    • @JackMvura-ik2td
      @JackMvura-ik2td 24 дня назад

      Ikugwetsani MCP sizamwana😂😂😂😂😂😂😂 chakwera motoooo komaso chakwera kuwina DPP yonse tidzaponyanso Yamanja alomwe kwao sitikuyesa

    • @wisdomchilanga723
      @wisdomchilanga723 22 дня назад

      Dpp, UTM,Alford, and UDF chonde phalani ziko pamoto tikudalira inu

    • @JackMvura-ik2td
      @JackMvura-ik2td 22 дня назад

      @@ivychithyoka1551 chakwera akupha Goliath ndi mwala umodzi 2025 gwirani yesu Adani muwaponde bwino achakwera ndikuthandizani kuponda achepa

  • @user-vm7iz6oz6r
    @user-vm7iz6oz6r 24 дня назад +1

    Kwambili izodi ndizoona 1 to 1 inu nokha ndi mcp kt mungamuchose mm ayi simungathe pitan ku dpp and UDF komaso afodi basi anawa azinyera ndiiithuuu

  • @masterchitabwino898
    @masterchitabwino898 25 дней назад +4

    UTM ndi DPP palibe udani if anything UTM yabadwa kuchokera ku DPP. Peter is cool ndiyemwe anamukonda SKC kuti ayambe ndale.

    • @isaihmagani5697
      @isaihmagani5697 25 дней назад

      Chabwino ndakumvani nde tinene kuti UTM itsogole ngatidi Pali kumvanadi

  • @dankopland-dp3vx
    @dankopland-dp3vx 25 дней назад +1

    UTM ngati ikufuna kuti omwe apha Chilima adzalipire akuyenera kupanga mgwirizano ndi chipani cha DPP kuti achotse MCP ndikufukula imfa ya Chakwera poyera koma ngati satero nkovuta DPP kudzagwira ntchitoyi pamene UTM imawanyoza pa kampeni

  • @WilliamNhlane-fd9hi
    @WilliamNhlane-fd9hi 25 дней назад +2

    Well spoken madam boss 🙏🙏🙏

  • @brainsmkumbwa6267
    @brainsmkumbwa6267 25 дней назад +1

    Tilowele ku DPP komweko basi,aDadi munthu womvetsa akatilandila,adadi sadziwa kupha munthu chifukwa chophangila maudindo ndi ndalama

  • @swintonchirwa1897
    @swintonchirwa1897 25 дней назад +1

    That's true Comrade there is no permanent political enemy in politics

  • @user-td6qe4gr6w
    @user-td6qe4gr6w 23 дня назад

    Atsogoleri a DPP, UTM, UDF & AFORD pangani smart, strong, transparent alliance kuti tisinthe dzikoli. Amayi mwalankhula mawu a mphamvu.

  • @ulemukhumalo7835
    @ulemukhumalo7835 25 дней назад +1

    Osamakakamiza aliyense ali ndi ufulu ndi chisakho chake pokavota. Panopo kuigwetsa MCP nkovuta aaaa nde gwirizanowo ndi dpp?? Mayi mukunama inu kuyakhula konseko ndi mpando musatinamizepo apa.

  • @isaihmagani5697
    @isaihmagani5697 25 дней назад +1

    Zoonadi omwe a kulankhura ndi a DPP kuti UTM ipange mgwirizano ndi DPP, ndipo akuterowoso kuwa vomereza kuwauza kuti otsogola akhale wa UTM

  • @crytoniegrantliffa2431
    @crytoniegrantliffa2431 25 дней назад +1

    Chakwera ndiye mmmmmmm mavutotu awa........utm inakuthandizani koma wokudya bwino kukhala inu nokha zooona?

  • @TiyanjaneMkwate-we8gu
    @TiyanjaneMkwate-we8gu 24 дня назад +1

    Mayi muli ndinzeru zakuya, and l will prefer mau anu anveke ku UTM.

  • @masterchitabwino898
    @masterchitabwino898 25 дней назад +8

    Tiyeni tigwilizane ndi DPP, UDF plus Aford kungotero tagwesa

    • @bysongeorge3243
      @bysongeorge3243 25 дней назад

      @@masterchitabwino898 ndipo chomwe chizachitike ndi zija amati 'Landslide victory', m'gwilizano omwe ungachepetsenso za kugawana mitundu. Nkhani yomwe akamba Mai wo. Atsogoleri omwe akukhuzidwa asakulirane mitima, agwilizane, azichepetse atiphule a Malawi mu nyengo yowawa ngati imeneyi..eesh!!!

    • @user-xm3zl5cg6x
      @user-xm3zl5cg6x 25 дней назад +1

      Kwambili UTM mulungu akudalisen Ife tikufuna Malawi wa rendere osati Opana UTM thenks

    • @SteveChapola
      @SteveChapola 25 дней назад +2

      Thenks utm popangangwilizano ndi dpp atiphera saulosi achoke fayaa

    • @SteveChapola
      @SteveChapola 25 дней назад +1

      Mai kaliyati libikisani anthu ife sitifuna mcp

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 24 дня назад +1

    Osanena Kuti ine zinandi pweteka iyai,munene Kuti m'mene adamu phera, Chilima Aliyense M'malawi zamuwawa, ndiponso nkhani imeneyi MCP tizawona Ku sogoloku Chakwera tizawona basi

  • @KondwaniBanda-j9x
    @KondwaniBanda-j9x 25 дней назад +1

    Komanso chilimatu akanapanda kuchoka ku DPP bwenzii Ali president wathu moto kupita ku DPP palibe vuto

  • @WilliamMasauko-su1wx
    @WilliamMasauko-su1wx 25 дней назад +2

    Chipani cha MCP mchakupha komaso mayi inuyo mukunena zoona ndipo ang'onawo achoke.MCP adzayivotera ana a zikhaleng'oma 👋👋👋

  • @AbrahamTembo-z5k
    @AbrahamTembo-z5k 25 дней назад +1

    Inenso ndine wa pa kanthawi ndithu MCP ndayiwona ndipo ndimaidziwa. Kungoti zangovuta kt zipani zinazi ndizazing'ono nchifukwa chake people will be FORCED to make an aliance with DPP. Koma tikawunika BWINOBWINO, DPP ndi MCP palibe kusiyana. Njauju mkulu wa ACB dafa ngati simunthu mpaka pano milandu idangozizira. UTM tsaopano payokha itha/ ndi AFORD, zitha kuchita bwino ndithu chifukwa imfa ya SKC idachita CAMPAIGN YAMPHAMVU. Makamaka ku chigawo cha ku mpoto. Kubwelera ku DPP itakhala LAST OPTION, yes mwachonchi mowawidwa mtima. Mayi ndakumvani BWINO ndithu, ndipo sindikukutsutsani kwambiri, koma DPP, ikhale last option.

  • @ruthsambaleni-hw5gu
    @ruthsambaleni-hw5gu 25 дней назад +1

    UTM yavutika mokwanira. Izi zomati Bola awa tiwachotse sizithandiza. Za alliance pamapeto. Mangani Kaye chipani UTM siyaying'ono. Ku DPP chilima anavutika. Tikufuna Chitukuko ife. Cholinga sikugwetsa MCP. Tikufuna utsogoleri wothandiza.

  • @esthermalixani2244
    @esthermalixani2244 25 дней назад +1

    Ndipo amai inu mumadziwa kuyakhula ndipo mukunena zoona ofunika kuchosa MCP osainyengerera

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 25 дней назад +1

    Mayi mwalankhula bwino chilima was a child of apm there is no problem to go back to DPP

  • @user-gd6zb2bv8f
    @user-gd6zb2bv8f 22 дня назад

    Siyani ma udani , mangani chimodzi ngati a Malawi,
    MCP ichoke ndipo isazapezekenso ku Malawi.
    Watching from JOHANNESBURG

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 25 дней назад +1

    Mai MULUNGU azikudalisani chifukwa chamawu anu amphamvu ndachilimbikiso, tiyeni tigwirane manja kuti tichotse ng'onazi m"dziko muno

  • @user-nd9cm3yl7e
    @user-nd9cm3yl7e 25 дней назад +1

    Zilibwino musabweleso mbuyo go forward mayi iweyo ndiwed wazelu kwambiri

  • @anthonysawa2039
    @anthonysawa2039 25 дней назад +2

    I think Bon Kalindo ayamkhuleponso pamkhaniyi kuti a Malawi tilimbe mtima

    • @SolomonNjolomole
      @SolomonNjolomole 25 дней назад +1

      @@anthonysawa2039 adanena kale kuti chokani ku chikangawa party pitani komwe munachokera kwa atate anu ku thyolo.

  • @wilisonbornface4282
    @wilisonbornface4282 25 дней назад +2

    Live from south Africa cape town

  • @PiliraniMukhupi
    @PiliraniMukhupi 25 дней назад +2

    Ndili mbali yanu🌹boma ilo

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q 25 дней назад +3

    Eya mama joinani basi pangani zomwezobasi tibwerere ku dpp basi

  • @TonykalicheloKalichelo
    @TonykalicheloKalichelo 25 дней назад +2

    You r the great mama

  • @MuhammedKandege
    @MuhammedKandege 25 дней назад +1

    Amayi anga mwanyangula bwino bwanji mut mwanga ndikusangalala ndi mawu anga zikomo mulungu akudalitsen pakana zongolo

  • @user-db3mh9wr9v
    @user-db3mh9wr9v 25 дней назад +3

    That's good Idea madam

  • @user-te3ps3kf2t
    @user-te3ps3kf2t 25 дней назад +1

    Yes l gree with you Mai,koma ngati simungamve magnanimous a Maiyi ndiye kuti mulibe magnanimous ofuna kutumikila a Malawi koma kukhutisa mamba zanu osati kuombola aMalawi ku Bagamoyo,please paganism chtheka kugwilana manja kuombola Malawi ku mng"anjo ya moto,machine ngati achitila kuno ku south Africa kupanga boma la Malawi colution Government, osakonda anthu awo mwasiye choncho

  • @Jessica-pg6ep
    @Jessica-pg6ep 25 дней назад +1

    Mwalakhula zoona Amayi ofunika gwilidzano ndi DPP mavuto awonjeza mmm.

  • @ConfusedCupcakes-ke8ql
    @ConfusedCupcakes-ke8ql 19 дней назад

    That is point UTM ikuyenera kupanga mgwirizano DPP

  • @user-rs7vx6hc1k
    @user-rs7vx6hc1k 25 дней назад +1

    Vuto lake limakhala limeneli, timakhala desperate kufuna kuchotsa chipani cholamula ndiye mapeto ake timangopanga ma plan osayang'ana kumbuyo kapena kuti kutsogoloku ziziyenda bwanji.

  • @FazilCastin
    @FazilCastin 25 дней назад +1

    Zowona amayi takumvani ndipo mfundo yogwira ntima❤

  • @fredgabrielnyangulu
    @fredgabrielnyangulu 25 дней назад +1

    Koma2 voice yo ikundimvekera ngati mai mai awa anali a Opposition omwe adali miyezi yathayi

  • @user-fi7ko7bl6f
    @user-fi7ko7bl6f 24 дня назад

    That's good idea Ma, l salute you 💪💪 power to the people.

  • @ChikumbutsoJohn-rs4tt
    @ChikumbutsoJohn-rs4tt 25 дней назад +1

    UTM , DPP, AFORD and AFFORD make one thing with concrete agreement we were tired please with MCP regimes

  • @Schoolfees10
    @Schoolfees10 25 дней назад +1

    If we want tizivutikabe let's VOTE for MCP

  • @ShadreckAustin
    @ShadreckAustin 25 дней назад +1

    Kuyakhula kwabwino mama ambuye azikundalisani kwambili

  • @user-ee6be5kl5o
    @user-ee6be5kl5o 25 дней назад +1

    Mau amenewo amphamvu pangani mgwilizano ndi Dpp ganizo la bwino limeneli Mai muli.ndi nzeru

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 22 дня назад

    That's live mama, ndipo simukulakwisa ai.... Bwererani komwe mudachoka ndithu

  • @FocusMathews
    @FocusMathews 22 дня назад +1

    Good watching from Joburg

  • @sebastianphiri4582
    @sebastianphiri4582 24 дня назад

    Mmmmmm mwachita phuma Mayi.Asiyeni a UTM amange chipani poyamba zachipako and alliances ndi step 2.UTM siiyenera kuziperekera kotero monga maganizo lanu.Zija Chilima amati osaziderera,osaopa,osafooka tsono inu mwayamba kutaya His legacy nkuyamba kuopa ,nkufooka nkumapempha kufungatiridwa nkaphwa mmmm samatero Mayi.

  • @JosephLungu-tw1nq
    @JosephLungu-tw1nq 25 дней назад +1

    Ubale umenewu ine ndikugwirizana nawo .apo ine nkakuvoterani mmamawa

  • @MussaAsidi
    @MussaAsidi 24 дня назад

    Ine nndinatuluka ku DPP coz of UTM apaso ndibwelela chifukwa cha UTM 🔥🔥🔥🔥 SKC

  • @user-mw8dq4is6k
    @user-mw8dq4is6k 25 дней назад

    Thats good idea Mai mwaganiza bho Chakwera must go .. Alliance ya Dpp, UDF, UTM ndi Afford ilii mwala Pangan zotheka bas.

  • @user-po6ir6eh4z
    @user-po6ir6eh4z 25 дней назад +2

    Mwaganiza bwino Utm ndipo ambuye azikudalisan nonse

  • @michaelkallyz2425
    @michaelkallyz2425 24 дня назад +1

    Ife tili DUU (DPP, UDF, UTM) kumastand

  • @user-jb5yb9wq3y
    @user-jb5yb9wq3y 25 дней назад +2

    We have to join together gentlemen and ladies indeed

  • @berthamigodi6529
    @berthamigodi6529 25 дней назад +1

    Komazoonad utm or dpp payokha singachose mcp pakufunikadi mgwilizano

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 24 дня назад

    This woman can make a good campaign director for DPP. Mutengeni mutengeni munthuyu ngati sali konko kale

  • @LoveHere-ki8ck
    @LoveHere-ki8ck 25 дней назад +1

    I salute you mama , good decision more 🔥🔥🔥🔥🔥

  • @user-nd9cm3yl7e
    @user-nd9cm3yl7e 25 дней назад +1

    Kumeneko nde kukhala mayi musafooke apm ndiopakale mulungu akathandizani bwino Bg wo athandale km ndalezawo salimbanaso ndithu ayi

  • @yowasschitsosa5348
    @yowasschitsosa5348 25 дней назад

    Munthu okhala pa mtendele akanachoka, mai mukunama DPP or mutapanga alliance ndi UTM simungawine, DPP siinabweletsepo mtendele mai ndnu achitsilu

  • @FaheemChipojola
    @FaheemChipojola 25 дней назад +1

    Mawu abwino mama mulandile ulemu wanu ❤

  • @JafarAnusa
    @JafarAnusa 24 дня назад

    Masha Allah mau amphamvu ndipo kuti dpp igwe chifukwa cha zipani 5 kugwetsa boma is not easy

  • @bysongeorge3243
    @bysongeorge3243 25 дней назад +6

    Chomwe wamanga Mulungu wina sangachiphwasule. M'gwilizano wa Shadow wina uliwonse omwe cholinga chake ndikugwetsa MCP, ndiri nanu pambuyo....

  • @MaryChavula-jz3di
    @MaryChavula-jz3di 25 дней назад +1

    Mukunva koma amalawi? Osakakamila ku mcp ife a dpp timakukondani a utm 🎉🎉❤

  • @RexChimwala
    @RexChimwala 25 дней назад +2

    Ndizowona mai ndipofunika kwambiri kupanga mgwilizano ndi chipani cha DPP basi