Takulandirani ku Mapemphero a m'mawa kuno ku Mvama CCAP Church. Otsogolera mapempherowa ndi abusa Hamilton Yassin Gammah. Mulungu akudalitseni pokhala nafe!
Following from capetown, you have changed my life before I thought I was a christian but wansn't after listening from your preaching now I know whom I am. Continue blessing us with words of God Rev. Yassin Gamah🙏🙏
Following from capetown, you have changed my life before I thought I was a christian but wansn't after listening from your preaching now I know whom I am. Continue blessing us with words of God Rev. Yassin Gamah🙏🙏
Ulariki wabwino okoma abusa. osati enawa kumangolarika zandalama
Powerful mumandidalitsa koposa Abusa ziphunzitso zanu nthawi zonse Ambuye apitilize mphatso ili mwayinu Amen 🙏
Amen pastor, the message is very good and touching.
I like your preaching,you are blessed in this field of teaching.
Wonderful preaching from you man God may almighty God help me I know who I am I by the preaching from your messenger continuing blessing him
Uwu ndiye uthenga wosintha munthu. Wa ma PAPA original osati tima papa tangodzipatsati ayi. May God bless you reverend
Ambuye zikomo chifulukwa cha mau anuokoma am very blessed..
Ambuye mulemekezeke. Uthenga umenewu ndi wanga vwandikhuza zoona
I like your preaching,you are a true man of God, god bless you,am from Zambia lusaka
My life is changed because of your teaching 🙏 God blessed
Abunsa please ndi mafuna kuti ngati kungakhare kotheka ndi mafuna uthenga wambuye udzindifikira chonde Abunsa Ameen
Am from Zambia powerful teaching
🎉🎉🎉❤❤❤ abusa tsegulani what's up group kuti ena aziva nawo unthenga wabwinou
Anatsegula kale
Am so much blessed by the message
Powerful revelation Rev Mvama CCAP
Abusa timadalitsika nanu.Osati enawa mulemera miracle money
Am watching you from Lusaka Zambia
So powerful hallelujah Amen 🙏
Ulaliki wanu abusa umasintha Amen
Abusa awawa mmmm amalalikira
True message 🇿🇲
Anthu ofunika kusafa aja koma awa, nkhawa timachira. 😂😂😂😂😅😅😅😅🤣🤣🤣🤣😁😁😁😁😛😝😋😜This man! Jesus! Jesu!
Monga upangili wachakwera it's very bad😢😢😢
Well spoken Reverend Gama
Good papa yemeneiyo
Man of God mumatisismusa kwambiri
Km ndngatan kt ndziwasata ma live service
Amen man of God👏👏👏
Am blessed poster🙏
Thanks pastor mumatitsitsimutsa
Never be surrounded by wicked people. Amen. Watching from Lusaka Zambia
Amen and Amen Rev mwaphunzitsa a T\A akwathu a T/A Kunthembwe ntchito yawo ndi imeneyo yokachitila umboni komatu ulaliki uwuu awumve 🙏
S
Amen a man from God
Amen Man of God
Am blessed today with you man of God
Mulungu atidalitse tonse
I'm blessed by you servant of God.
I can listen to him the whole day. Amen Rev. Gama!!!
Well done pastor
Amen abusa
Phunziro lapamwanba kwanbiri ambuye akudaliseni Abusa
Blessed pastor 🙏🙏
Am very much blessed
Ameen 🎉
Amen 🙏
Keep on pastor
A men ❤❤❤
Emenem
you always stand on the truth
I connect Rev
Great message
Really blessed here for this morning devotion
Ambuye alemekezeke
Amen ndadalitsoka
Kodi Abusa school yomwe munapitayo enawanso anapita komweko Eeeeh mwainu muliuthenga
Mmaitha abusa
Nda dalitsika nowo ulariki kuchokela ku capetown
Ulaliki otsitsimutsa Mulungu atamandike pitirizani a Busa kulalikira
Super
Amen & Amen..
Inuyo mumatha abusa koma kwinaku. timangomva zomwe zomwezo tulo mkati ambuye akusamaleniabusa
Amen & Amen
Good message
Amen 🙏 Lord
Mvama paster
Zili kuntchito kuno mbalazo moti ndayamba nao kubako nanga ine mtsale😢
Mumakwana paster
Zoonatu izo
❤ thank you so much it's true what you are saying amen 🙏
Zoona abusa
To God be the glory ❤
😊
Zikomo kwambiri abusa
❤
God bless
Amen 🙏🙏
Amen amen 🙏🙏
Following
Mukuyakhula ndi moyo wanga
flowing
Zikomo abusa kuti Pasa chakudya cha uzimu zkom
Amen
Keep. It. Up A BUS ,A
Blessed
Uphunzitsi wabwino
Aurora Nobre Moçambique
Zibwino abusa
Zaphavu
Ndadalitsika ndi kuphuzitsidwa
S
Simukunama ameneaja alingat amene waphuzila mawu amulungu amaposa amene wamaliza maphuzilo akudziko kulimba zoona mogwilizana Ni salimo 1 vs1
89
Patseniko nambara ya abusawa ya Whatsapp p/s
Amen Man of God
Amen 🙏🙏
Amen
Amen and amen
S
89
Amen man of God
Amen