MFUMUKAZI COMEDY SERIES..20/09/23..Flora Suya's👉+265883106798

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 1 окт 2024

Комментарии • 70

  • @mariahyunavictor7657
    @mariahyunavictor7657 Год назад +1

    Koma banja la apadela kukonda kudyaaaa!!

  • @henrymikeas
    @henrymikeas Год назад

    Holly ghost fire sumanena uli njala😂😂😂😂

  • @BernardoDonacianoHonorio-xo9yc
    @BernardoDonacianoHonorio-xo9yc Год назад +1

    Ndiwo tadya apazi ndalama zake mwazitenga kuti, padera, atakhutano kkkk

  • @latkecepatrick3019
    @latkecepatrick3019 11 месяцев назад

    Farayi, Padera and Giring’ande mwandipha 😂😂😂😂.
    Padera kukoma mkamwa kufuna ngongole.
    Kod Farayi ndi Princess Chitsulo eti?

  • @charlesdzinyemba9493
    @charlesdzinyemba9493 Год назад +1

    Koma aPadela mupole moto mwakhutakhuta ndiye kumafunsa kuti ndalama mwatenga kuti?
    Bwanji simumafunsa nthawi yomwe anakupatsani kuti mukagule ndiwo

  • @samsonphiri5349
    @samsonphiri5349 Год назад +1

    Mmaitha guys keep on going ,

  • @emmanuelnambazo8212
    @emmanuelnambazo8212 Год назад +1

    Manuwelo😂😂😂

  • @RoyimaKanyimbo-rq6so
    @RoyimaKanyimbo-rq6so Год назад +1

    Mbambande

  • @ishakatimbe7341
    @ishakatimbe7341 Год назад +1

    Watching from Johannesburg guys mumakwana

  • @mikeilahmendes1643
    @mikeilahmendes1643 Год назад

    Macheza agiling'ande ndi padela mukumatalikisa akubhowa

  • @dhaoudhiabedinegomaseko2363
    @dhaoudhiabedinegomaseko2363 Год назад +1

    😂😂😂😂😂😂 Mfumukazi ndi Mr Shopright akungoyang'anizana kwavuta

  • @CharityMnthali
    @CharityMnthali Год назад

    Anamoyo kuipasa moto much ❤

  • @SamMasese-ok5on
    @SamMasese-ok5on Год назад +2

    Faraih the best

  • @HappinessMkwinda-fz2wn
    @HappinessMkwinda-fz2wn Год назад +2

    Ati mai Kalanka😂🙌kmnso padera uzingongola kangat🤣

  • @CharlesZimbiri
    @CharlesZimbiri Год назад

    Kkkkkkkkk pqdera mwadya mwankhuta ndye kumafutsa kuomwe kwachokela ndalama ya ndiwo 😂😂😂😂😂😂😂

  • @ChancyMpunga
    @ChancyMpunga Год назад

    Kma bambo padela kufunsa mutankhuta

  • @mayahomar8578
    @mayahomar8578 Год назад +1

    🎉🎉🎉🎉🎉

  • @SumezSumez-lz9iq
    @SumezSumez-lz9iq Год назад

    Koma kunyumba kwa padera amakonda kudya

  • @patrickdzombe461
    @patrickdzombe461 Год назад +1

    Padela wakhuta ndie ukuyamba kufunsa komwe kwachoka ndalama

  • @EstherZintambira-sq3yy
    @EstherZintambira-sq3yy Год назад

    Anamoyo apaseni toti ndalama ndiyao

  • @saifullahalick407
    @saifullahalick407 Год назад +1

    Eeeee! Koma Flo, Nanyoni ndi ShopRite ndiye wawakhaulitsa

  • @Cooliodaxymw
    @Cooliodaxymw Год назад +1

    Amfumukazi ndi x wawo aphana ndimaso

  • @kadayainno
    @kadayainno Год назад +1

    Tomato wa 100 mpaka kunyamulitsa waganyu,koma padera kkkkkkkkkkk

  • @RukayyahFanes-wr1fh
    @RukayyahFanes-wr1fh Год назад +1

    Nthawi yachakwera K500 ndichan?

  • @harrisonnavayah6480
    @harrisonnavayah6480 Год назад +1

    Onse kumowa mfumukazi x Gili

  • @giftblack7690
    @giftblack7690 Год назад +1

    😂😂😂😂😂 apa ndikusowa poti ndigwile umu muli bomba agiling'ande nde afumu kazi aliyese ali yekha yekha osayankhulitsana apadela ati mzimu ukagona ndinjala eish koma mafalayi anakonza nthawi zose amasokoneza zinthu Kkkk mumatha guys next nde kuliso Bomba ❤❤❤

  • @mthawisakaunda
    @mthawisakaunda 4 месяца назад

    Beautiful namoyo

  • @JustenChikanda
    @JustenChikanda Год назад +1

    🤣🤣🤣🤣 koma padera anakonza akuti nzimu sugona ndi njara kkkk

  • @ChisisiSaynett-nm7uq
    @ChisisiSaynett-nm7uq Год назад +1

    Koma kuli serious mfumukazi ndi x wawo 😂😂😂😂

  • @patrickmkhalipa-my4en
    @patrickmkhalipa-my4en Год назад +1

    Farai ni 🔥🔥

  • @harrisonnavayah6480
    @harrisonnavayah6480 Год назад +1

    Onse kumowa mfumukazi x Gili

  • @mollymasangano473
    @mollymasangano473 Год назад

    Hahaha 😆 😂 show 🤣 😂 😆 😄 😅 👏 🤣 Apadera adzikagopephera HOLY GHOST FIRE 🔥 😄 😉 😀 😆 😜 🔥 😄 😉 😀 😆 HOLY GHOST FIRE 🔥 😄 Mulungu awamvera Chinsoni koma a X BOY FRIEND 👦 😄 aaa Mufumukazi kikikiikiki

  • @anniewhite3497
    @anniewhite3497 Год назад

    Mfumukadzi gonjani mugonjere mr Shopprite😂Apadera inu zoona kumafutsa komwe kwachoka ndlma mutadya kale?😂😂😂😂😂😂

  • @LenzoImedi
    @LenzoImedi Год назад +1

    Mumakwana apadela

  • @mavutojackson9264
    @mavutojackson9264 Год назад +1

    🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @benjulius6070
    @benjulius6070 Год назад

    Watching from Michigan guys keep it up guys ❤❤

  • @JohnChibalo-wf8gr
    @JohnChibalo-wf8gr Год назад

    apadera mwadya idya idya mwakhutha ossmufunsa nkadzi komwe watenga ndalama mukufunsa mutakhuta tidziti mukulondola ? Kapena ndili ndi kuchikamwa .? ❤❤❤❤❤❤❤

  • @modiseusi4412
    @modiseusi4412 Год назад

    Ndthandizeni guys kod anangongola lastvweek uja ndi ndani???

  • @storytambala6088
    @storytambala6088 Год назад

    Koma Farai, kukhala ngati ine ndingakukupe ndikhofi sizinawoneke.

  • @danieleneya808
    @danieleneya808 Год назад +1

    🎉🎉🎉🎉mwabwera kuzakhala guys

  • @mussachitambi
    @mussachitambi Год назад

    Apadela kkkkkk guys akufusa atadya akausa kuti ndatenga kwa mamuna wina

  • @abrahamnkosi4160
    @abrahamnkosi4160 Год назад

    😂😂😂😂 msamuyang'ane ameneyo akulozani.
    Watching from south Afica storms river eastern cape

  • @JohnChibalo-wf8gr
    @JohnChibalo-wf8gr Год назад

    Padera yakwiya ndi mizinu ngongole ikukanika zotuluka tuluka zabweleranso ❤❤❤

  • @JohnChibalo-wf8gr
    @JohnChibalo-wf8gr Год назад

    amfumu ndi amunanu mwakunapo musiyanapo bwa .?

  • @MunillLasheed
    @MunillLasheed Год назад

    Padela wayamba kutumidya ndiwo😂😂😂

  • @KimuEmmanuel-lv9wt
    @KimuEmmanuel-lv9wt Месяц назад

    Ine ndingofuna number ya farayi❤

  • @yohannkhoma9958
    @yohannkhoma9958 Год назад

    Atii bamboo ameneyo musamuyang'ane akulodzani

  • @JohnChibalo-wf8gr
    @JohnChibalo-wf8gr Год назад

    Galanka asakusokonedzere banja nsikana wina anakulidzapo nafuneya yemweyo ❤❤❤❤😂

  • @dicksonmlera2777
    @dicksonmlera2777 Год назад

    Inuyo guys mmakwana mwayenera kulandira ulemu

  • @aishaayatu8653
    @aishaayatu8653 Год назад

    Koma namoyo wayitha kwasiya awiri wiri

  • @hassanumali2761
    @hassanumali2761 Год назад

    😂😂😂 holy ghost 👻 fire 🔥

  • @chikondiyossefe
    @chikondiyossefe Год назад

    Agilin'gande abwelelane ndi afumukazi ❤❤

  • @FaruqueNeves-cx3kt
    @FaruqueNeves-cx3kt Год назад

    😂😂😂😂😂😂😂😂😂bg gili apanga zotani di fumu

  • @JohnChibalo-wf8gr
    @JohnChibalo-wf8gr Год назад

    Namoyo wayitha wapase mpata anthuwo

  • @boydkawana5739
    @boydkawana5739 Год назад

    Miss shoprite falai

  • @grayjames904
    @grayjames904 Год назад

    Padela ku Dikila. Akhute kae

  • @Pungwe123
    @Pungwe123  Год назад

    Mai padera sadzatheka😂😂😂😂

  • @abrahamjunglejnr5974
    @abrahamjunglejnr5974 Год назад

    Banja la padela mavuto 🔥🔥🙌🙌🙌😅😅😅😅

  • @PatienceChimenya-t6d
    @PatienceChimenya-t6d Год назад

    Farai chepetsani pakamwa❤

  • @LolenUziel
    @LolenUziel Год назад

    Next week kuli zithu

  • @madalitsosandram1576
    @madalitsosandram1576 Год назад

    Nice comedy

  • @daviekamanga1417
    @daviekamanga1417 Год назад

    ❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉

  • @gideonluhana9914
    @gideonluhana9914 Год назад

    Falayi ndi 1

  • @QADA-D-MW
    @QADA-D-MW Год назад

    ❤❤❤

  • @Mahirublackchimzy
    @Mahirublackchimzy Год назад

    Watching live from Cape Town RSA,, Mfumukazi acting imandiwaza kwambili nkabwela kumeneko will make sure kuti Nzajoine nawo basi and be part of this Group 🔥🇲🇼