If you are here for Farai please say Ayeee!!!! Hahahaha Farai ndi more! Kudos to the whole team of course. This is beautiful and entertaining! Keep up the good work!
😂😂😂😂😂😂😂koma farai ndi gututu mukutengetsanatu, akuti shoprite ija ine ndemwe accountant Ine ndemwe wogulitsa ine ndemwe secretary kkkkkk koma ndaseka kkkkk😂
Congulatulations gilin'gande kuyitanisa mbale wako kuzayanganilanpankhomo . Amfumukazi its certain kut sapeza kanthu from m shoplite kkkk😂 banja silitha kwinako kkk
More fire keep it up guys , mfumukazi ndi kawawa kuposa mdyangu comedy 😂😂😂, I like and enjoy watching this comedy ❤🥳🥳🥳🤗🤗🤗
Munamatu inuyo😂 mdyangu naye ndi fire fire 🔥🔥❤️🥳🥳🥳🥳🥳
More fire 🔥🔥 watching from Eastern Cape South Africa tsitsikamma
Guys, you are the best! You have made me stop watching Nigerian comedy films.
Keep it up!
Ulemu wao❤😊
Giling'ande and Mfumu kazi, anakumana, equal to equal 😅😅😅
this soapy is an ideal watching it in diaspora, it gives a clear picture of our real life in the village. keep it up fellas.
Farai kkkkkk ndi moreeeee fire
Koma mfumukazi ndi giling'ande mwakometsa😂😂😂
Farai emweyo 🤣🤣🔥
farai anadza kudzakhala...more love
If you are here for Farai please say Ayeee!!!! Hahahaha Farai ndi more! Kudos to the whole team of course. This is beautiful and entertaining! Keep up the good work!
Farai❤🎉
000😊
@alinafesawasawa3905 p
Kheledza ochejeka😂😂😂 chizungu for me
Keep up the good work much love you guys ❤❤❤ koma ya small apples 😂😂😂😂😂
This padera man eee ai best
😂😂😂😂😂😂😂koma farai ndi gututu mukutengetsanatu, akuti shoprite ija ine ndemwe accountant Ine ndemwe wogulitsa ine ndemwe secretary kkkkkk koma ndaseka kkkkk😂
Apwetekana😂😂😂
Guy's you're the best. Keep it up ♥️♥️
So interesting , Farai more 🔥 fire.
Koma gututu yekha sadzatheka 😅😅😅😅😅😅 akuti alodza falai chifukwa cha nagama koma abale zinazi.nagama ndie akuziona kwambiri adakaziona
😂😂😂Giling,ande ati yabwera yokungana bataliyon
😂😂😂😂 koma gututu akut wayankhura chani Falayi chizungu kaya 😂😂😂
You are all best actors❤ mukutimvetsa kukoma😂😂
Ur the best gyz munabwera mumatisangalasa small apple
Umaziwona ngati wa clever? Gututu🔥🔥😂
Gututu kaya 2 pin akabweza bwanji 😂
Naye gututu eeeeee😂😂😂😂
Banja la mfumukazi ndi gilin'gande Lili Pam ntendere😂😂😂
Koma ndaseka agiling,ande nda mfumukazi 😂😂😂
Can someone pleas help me pharai ndi Princes chisuro?akufanana
Koma Farai ndi more usamasowe 😅😅😅😅😅
Koma farai aaaaaaa mutu wake sugwila ndithu😂😂😂😂😂
😂😂😂 Koma falai ndi🔥🔥🔥🔥🔥🤣🤣🤣
Chiphwanya akuti amfumukazi alibe nzeru sanagamuleko nkhani molongosoka kkkkkk
Mutimvetsa kukoma gys nonse😂 limbikirani kutseka paka mutu kupweteka😂😂😂😂more 🔥 gys 😂😂
😂😂😂😂😂 small apples masau guys mumatha Gift black from capetown musazafe muzangosowa
Zaulendo uno😂😂😂
giling'ande Kuinyumwitsa Mfumukazi kkkk❤
Mumativesa kukoma ma guys❤
Amfumukazi ayamba kuopa kuno kkkkkkk😊
Mumatha guys keep it up
Big up guys😂😂 proud of you
Koma penapake banja ndi lokoma bwanji 🥳🥳🥳🥳🤣
Khan ndi next week frola wapeza Mamuna
Good job
Kkkkkkk nanyoni kuopa kumeneko 😅😅😅😅
😂😂😂😂😂😂
Chiphwanya apha munthu, kupha munthu saona kathu hahahaha more fire ❤❤
Ndife ndikachaso ambuye alandilandila😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂 kom muli chizungu umuh 😂😂😂
Chabodzatu😂
Guyz more fire,nose mulibwino mwakumanadi mumaitha
Amatha
Koma banja la Fumukazi layamba kubeba Gututu mpaka chikwanje pakhosi?
Ndipo silizakonzeka😂😂😂
kkkkk mfumu mkazi amaopaso
😂😂😂😂😂 gututu wayamba zosamaliza . Eti wati Cha , does that mean sunave
Kkkkkkkkkk banja lija kuno
Amfumukazi apepera ndi agiling'ande
Ameneyo diye gringande
Ngiling'ande ndi Mfumukazi same watsapp group❤❤❤❤ Farayi kkkkkkkkkkķkkķkk
Small apples
Basop😊
Kkkkkk km falai ai zkm
Kkkkk koma Farai wadza
Akatundu😂😂😂
Km gututu nde wakumana nazo kkkkkk
❤❤❤❤❤❤
good work gys
Kkkkkk koma falai eee
Koma mfumukanzi ndi Giling,ande mumakwana ndipo mumandipeza
Kwayaka moto😂😂😊
Nyumba ya Gututu ili kuti kodi?kapena amagona my street?
Ine ma comment akundivuta athu osewa ❤❤❤❤❤❤❤❤
Koma mfumukazi kkkkk banja ili limakoma
Proud of you guys
Following ❤
Mwaiwona 1 sauzande?😂😂😂
So happy with you guys,
Zili fireeeeee!🔥💨
Mumativetsa kukoma guys 😊
Congulatulations gilin'gande kuyitanisa mbale wako kuzayanganilanpankhomo . Amfumukazi its certain kut sapeza kanthu from m shoplite kkkk😂 banja silitha kwinako kkk
Banja lalimbano la mfumukaz😂😂😂😂😂😂
Mfumukazi muli nchikonditu😂
"Small apples"😂
Mfumukazi ndi giling'ande anakumata okhaokha 😂😂😂😂😂😂😂😂
Mfumukazi made my day
Simo apozi 😂
😂😂😂😂Komatu mfumukazi
Farai amandi waza........
Hu na mado😂😂😂😂😂😂😂
Farai kkkkk
Anaghama mwaiona 1000 yanga? kkkkkkkkk km Chiphwanya❤
Kkkk
small aplles kkkkkkk
😂😂😂😂😂
Hu izi mado? Kkkkkkk farai
What does have that to do with you 😅😅😅😅
Kkkk 😂😂😂 afalayi 😅
Kodi gututu zizunguzo anakaphunzilila kuti😂😂😂😂😂😂
😂😂
Farai I love ❤️ you ❤️
Farai came to stay....😂😂😂😂
Small apples 😂😂
Police siingandimange ndamanga ma police ambilimbili
❤❤
Ine koma nagama
Koma farai😂😂😂
Koma guys inuyo mukutiimirira pa malawi pano
😂😂😂🤣🤣🤣
Chiphwanya😂😂😂
Farsi ndi Farai
Falai😂
Chimphanya 😂😂
Giling'ande wandiwaza lelo
😂😂😂😂😂nanyoni mantha
Mumaitha guys