I was about to die after I stay 3days without listening bakili muluzi TV. I love this man. Mulungu alemekezeke. Ng'ona party mwagwanayo mboli zanu nonsense.
Iweyo ase bakili muluzi aaa ndakutayila Kate go ase God ahead u my brother. Ineso ndinali ndiwa history koma data analysis ya history yako respect bro umazukuta
Welcome back Brother from BAKILI MULUZI TV. Otichosa nkhawa ndi Zitonzo tikukumana nazo mu Ulamuliro wa MCP ndinu : Brother from BAKILI MULUZI TV freedom fighter ✊✊ Brother Mtanyiwa from Limpopo FM freedom fighter ✊✊ . Keep moving forward and fight for the better Malawi. Stay blessed 🙏🙏 Stay safe ✊ ✊ History is the best teacher ✍️
Mumatha madara inu ndi madara❤❤❤❤mfumu ukusungeni ndi moyo mpaka ena kumanama kuti akugulani anandinyasa bwanji welcome back musamasowe muzatimpha ndi nkhawa
Eeee apa ndiye mwatikhazika ntima pansi.Anthu amakamba zambiritu ena mpaka kumati Ng'ona party yakugwilani koma Mulungu alemekezeke eee😂😂 Ng'ona zagwa nayo 🕺🕺🕺
Am very happy to hear this station back again here in Zambia 🇿🇲🇿🇲🇿🇲 very clear and loud
Actor safa wamba makape nonsense magwanayo muyankhulenso kut wasowa. Yemwe wasowa uja ndiwanu waife nde ndiuyu wabwera ngat coming ❤
❤❤❤❤❤❤ auxeni kut uyu za moyo wake akuyang'anila ndi mulungu not chakwela
❤
Auze 😂😂
Ndipo auze❤❤❤❤
Bakili muluzi tv is back to those who are happy let's gather here
I never get tired of listening to this best Tv. My day is complete only when I hear " akulu akulu". Ine ku mtima kuti myaaaaaaaaaa
My best tv,mulibwanj sir ife tinali ndi nkhawa kuti mulipo❤❤❤❤❤
Welcome back the hero we're happy to hear from you again,, listening from Capetown
Tinakusowani achikulile Apa zilibwino.
Am happy to hear this olo chibwezi changa chatha dzuro tendere ndaupeza ndi bakili tv ❤❤❤❤
Kkkkkkkkkkkk
@@Alice-z7t4z am serious bola Bakili tv
😂😂
😂😂😂😂😂😂😂
😂😂
Iam very happy that Bakili Muluzi TV is back . May God continue blessing you.
Mukuva bwanji agalu inu achina vikangawa komwe muliko BAKILI MULUZI TV adabwera ku dzakhala mukhaula agalu inu ku MCP big up man we love you
Thanks brother for coming again we were worried where is our brother God bless u 🙏 always standing for the truth without fear
Machine he is here welcome back big man ❤❤❤
Welcome back shasha wanthu
Welcome back big man
I was about to die after I stay 3days without listening bakili muluzi TV. I love this man. Mulungu alemekezeke. Ng'ona party mwagwanayo mboli zanu nonsense.
Timadankhawa welcome back Bakiri muluzi TV ❤❤❤❤❤❤❤
Shame to haters 😂😂😂 Glad to hear your voice boss ......May God continue protecting and Shielding you boss..
Mwaitha Big timada nkhawa ❤️
Ndipo kwambili mwava mmmm
Ndipo🙌
Ndipo nkhawa zinali biii 🔥🔥
❤❤❤ase usatiphanu ndi nkhawa afiti ena amkati wamangidwa wel come back my bro opanda iwe sitingadziwe zinthu moto kuyi buuuuuuuu
Kwambiri tamva choncho ndithu kuti chilipo chachitikira big boss wa
Ndine nde tinalidi ndi nkhawa kwambili welcome back love you ❤❤❤❤❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉
Ndipo ine ndidali ndinkhawa kwambiri
Welcome back dude ine olo sima simakomayi apa am very happy to hear your voice
God continue to keep you safe Mnali ndi nkhawa now very happy to hear your voice
My best tv ever let's gather here guyz
Bas apa ndipha nkhuku tsopano coz mtima siunali Malo ndizomwe zimavekazi Mmm I love this guy 🔥🔥🔥
@@AllanWilsonbandakkkkkkk
Mundilole ndimwe energy drink tsopano
Nice to hear your voice Boss Man, all respect to you ❤❤❤❤ history is indeed the best teacher, proud of you always 🔥🔥🔥🔥
My hero eee iweyo ndikatundu❤❤❤ musamasowe bwana
Iam very very happy to hear your voice again bakili muluzi tv.
Thank you very much
The best tv Bakili Muluz,....Long time
Ana achepa bigman welcome back 🔥🔥🔥
Iweyo ase bakili muluzi aaa ndakutayila Kate go ase God ahead u my brother. Ineso ndinali ndiwa history koma data analysis ya history yako respect bro umazukuta
Apondiye waying'amba atumbuka ambiri anasowa ntendele kwambiri nthawi imeneyo keep going mr we love you
Heshiiii kumamveka zambiri kunjakuno I'm happy kuti mulipo timakunyadilani welcome back big boss 😂😂😂
Welcome back Mr Bakili Muluzi TV, you always teach us the history.
I was there. Kamuzu even bought Chakufwa Chihana, and Du Chisiza junior.
I was in fear now am glad to hear your voice again timakukondani we need change this stupid government anthu akupha awa
munatiimilika big up Bakili Muluzi tv
Bakili muluzi tv number 1 dzikomo mwafika mchimwene tinadankhawa mulungu azikusamalilani live kuno South Africa pretoria side
Welcome back Brother from BAKILI MULUZI TV.
Otichosa nkhawa ndi Zitonzo tikukumana nazo mu Ulamuliro wa MCP ndinu :
Brother from BAKILI MULUZI TV freedom fighter ✊✊
Brother Mtanyiwa from Limpopo FM freedom fighter ✊✊ .
Keep moving forward and fight for the better Malawi.
Stay blessed 🙏🙏
Stay safe ✊ ✊
History is the best teacher ✍️
M,makwana bige
Lelo ndiife akapolo ziooneka chaka chikubwelachi pavoti aga
Allahamdulillah for to welcome back big bro bakili muluzi tv my allah guide and protect you all the time allah akbar respect to 🇲🇼🤲
Have been searching for your new videos. Happy to
Umakwana iwe sungasowe ngati chilima long live BM TV
Watching from state house Malawi 🇲🇼 ❤❤
Ine ndinasiya kudya kusapezeka kwanu brother pa line 😭😭😄😄
Apa mntima wadekha history is a best teacher came again🎉🎉🎉🎉
😂 😂 😂 😂 Inenso mtima wakhazikika
Bakili muluzi TV ulibooo !!!!! chifukwa umadana ndi ma pulezidenti opusa komanso a satana god bless you for ever.
Ndimadera nkhawa kwambiri welcome back my bakili muluzi tv
Thanks God to here your voice again the biggest thing 🙏 🙌 ❤️
WELCOME BACK MY BROTHER 🎉MOTO KT BUUUU!!!!
Uyu ndi Vyetee safunika kumaenda usiku❤❤❤ we loves you bru
Abro mutipha ndi ma BP timadabwatu kuti zataniso Viva BM tv ❤
This is aman never ever disappointed us truth always comes with pain achikangawa nonse muli mmadz
Welcome back my best teacher Mr bakili muluzi TV shame to people who was talking shit for u
I'm so happy to washing this my favourite channel❤ tinamva zot akuchosan ku fec book pg I was very angry for that
Ulemu wanu big brother god bless you 🙏
Wow u r back big man I have missed you n my best TV in Africa
Am here to like everyone's + [positive]coment
Welcome back big brother anthu amalubwalubwa kunjaku amati mwagwidwa
Best of the best my favorite Chanel
Bg musamasowe chonchi ife tinali khumaaa kt Kodi mcp yakugwilani but so far we are happy to here u again
Welcome back btv my family was disappointed to hear that your page is missing on Facebook and you tube
Welcome back Best Tv on malawi your number 1 bwana
Welcome back my loved brother, Listening from Cote D'Ivoire
Best quote of the year, 'gwape amakalamba pakati pa mikango.' Uyu samukwanitsa ndipo tili naye mpaka MCP itadzachoka, ndithudi!
Proud of u big we are very happy timadera nkhawa ndi ng'ona party
Welcome back kuchitekete we are proud of you
Mumatha madara inu ndi madara❤❤❤❤mfumu ukusungeni ndi moyo mpaka ena kumanama kuti akugulani anandinyasa bwanji welcome back musamasowe muzatimpha ndi nkhawa
May God continue keeping you safe 😊😊 this is priceless information we need to hear 🙏🙏
Welcome back my best tv ever🎉🎉
From south Africa loud 🔊 and clear 😂😂😂
Bwana welcome back,, afitiwa Amati mwasowa God is good
Am watching from mtchinji boarder welcome back
Welcome back we miss you anatipangadi deposit
Welcome back our freedom fighter 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Dada waifeyo amalawi tsopano machine bakili TV umakwana koma eee afiti ena amatinamizatu Zambiri zainu, god protect you big bro umakwana
Am very happy to hear that Bakili muluzi tv is back❤❤❤❤❤❤❤
Kkkkkkkk km iweyo aaaa ndidolo wallah God bless you brother mmmm Mulino
Welcome back boss man we are happy for you
Wow history is the best teacher❤
Welcome back bro your number one keep it up
I MISS YOU MY BIG BROTHER The best TV in southern Africa BAKILI MULUZI TV NDI KATUNDU UKHALISE UMATHA KUCHEZA
Welcome back bakili TV
we have been waiting for this one continue to give us the best
😅😅BM TV 📺... Ichi amwene ndichi Game changer 😅
Eeee apa ndiye mwatikhazika ntima pansi.Anthu amakamba zambiritu ena mpaka kumati Ng'ona party yakugwilani koma Mulungu alemekezeke eee😂😂 Ng'ona zagwa nayo 🕺🕺🕺
Tinakisowa welcome back, umatha iwe
Welcome back my favorite tv
Fada iponde fada history is the best teacher super hilarious man
Welcome back big man timadandawura titafa kuti simuribho pepani ❤❤❤💞💯💯💯
Welcome back ❤ kuno ku south Africa timalimba mtima tikamamvera Bakili TV ndi nkhanga zaona mtanyiwa , Mulungu azikudalisani nthawi zonse🙏
Well come back bakili muluzi ndimadandaulatu heavy
Ufumu wanu wayesedwa ndpo walephera🔥🔥🔥
I'm so proud of this channel P welcome back❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
I am very glad to hear that you have come back to online we lo❤ your brother keep it up
Welcome back awuzeni akunamizana anthuwa 🔥🔥🔥🔥🔥
Musilikali wathu kumalawi bakili muluzi TV 💪 God protect you all the time
You're the greatest Historian on the Planet, brother. Glad to hear from you again.
We pray for you God bless you all the time
Sima simakomaso bro mmene sindimakuvanimu panopa ndikagula mega deus agredeser bakili muluz tv from Mozambique
Welcome back pangolin....I missed you alot.....iwe ndi dhilu....
Nkhawa zinali biiii😅😅
Bakili muluzi tv,my brother you are the best for Malawi n world over, keep it up,from your Zim brother in Sa
Please Bakili muluzi fan's let's gather here
We love you Dr Bakili muluzi TV
You're the best of all the world
The only channel I love🎉
Welcome back bravo 👏👏👏👏❤❤