Nkhanga zaona: Zitsankho tizilephelesa paka America ilowelelepo. MCP yalowa chiwewe

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 8 сен 2024

Комментарии • 99

  • @BenissoneErnesto-eh6zs
    @BenissoneErnesto-eh6zs Месяц назад +8

    Live in Mozambique The Best muthanyiwa

  • @SegherireSichali
    @SegherireSichali Месяц назад +5

    Chonde zisankho zilepheleke 2025 ndipo pakhale boma longogwirizra apo biiiiii kudzakhala nkhondo yoopysa.

  • @MonijaKataika
    @MonijaKataika Месяц назад +2

    My brother Ntanyiwa munasowadi sure yooo🙌 lero mwabwera ndithu .Kodi mmazachekera kuno kuti moto uphulike chonchi lero?..😂😂😂 welcome back we missed u yesterday.

  • @AnnieBanda-rb2dk
    @AnnieBanda-rb2dk Месяц назад +3

    Dr chikangawa chakwera, eeeeeee koma eya nkhani zake chikangawa abale watha anthu kumalawi,

  • @user-zl9vj6hc6y
    @user-zl9vj6hc6y Месяц назад +5

    We want report for chilima's death.. before election.

  • @shadreckphiri1799
    @shadreckphiri1799 Месяц назад +6

    If MCP is allowed to participate in elections before Chikangawa report, then Malawians are finished.

    • @robertmkandawire9898
      @robertmkandawire9898 Месяц назад +1

      No, my brother we need the report now. Remember they said, report will be out in August 2024!

    • @ewn-mc6jv
      @ewn-mc6jv Месяц назад

      I see kuti afuna apange delay mpaka chisankho chichitike

    • @user-lu5db5qk2o
      @user-lu5db5qk2o Месяц назад

      Zoona amenewa asaimilenso.

    • @SandraIssa-lo8il
      @SandraIssa-lo8il Месяц назад

      Komatuu ndipo apereke report limeri, asatana amenewa kwabasi. Chilima's soul will fight for the truth to be vindicated. We are praying every day , God will answer these prayers

    • @user-ww4ei5fb7d
      @user-ww4ei5fb7d Месяц назад

      A opposition akanatiyimirira pankhani ya report yi

  • @MonijaKataika
    @MonijaKataika Месяц назад +2

    Let's fight for the man guys who is I prison for forwarding the song to the group yoti sanayimbe iyeyo..mpka 2months ku maula a Dayton muhone

  • @HaliJana
    @HaliJana Месяц назад +2

    INU MUNTHU AKUPHA WANTHU ANGAWINESO BWANJI OLO ATABELA SITIKUMUFUNA ANGOONONGA NDALAMA GALU AMENEYO

  • @user-jn9tz3li3v
    @user-jn9tz3li3v Месяц назад +3

    Thanks Mr Ntanyiwa, zimene wanena za a Busa opepera a Synod of Livingstonia.

  • @user-tw9nl6ks9d
    @user-tw9nl6ks9d Месяц назад +1

    Chikangawa on repeat😊

  • @AnnieBanda-rb2dk
    @AnnieBanda-rb2dk Месяц назад +2

    Yomweyo aulure agalu amenewo anthu oyipa amenewo

  • @VictorChiwaya-sb6tg
    @VictorChiwaya-sb6tg Месяц назад

    Big up munthu wamkulu,,mumatiyimilira potiziwisa zimene zkuchitika kuseli

  • @MustaphaCassim
    @MustaphaCassim Месяц назад +2

    Anthuwa amwalira ndi maganidzo.

  • @franciscomalola92
    @franciscomalola92 Месяц назад +1

    ulemu wanga onse upite kwa chikangawa man , ,chakwera ulemu wanu ndi magazi amene munavala kale

  • @CathreenKadwala
    @CathreenKadwala Месяц назад +3

    Inu ndi 1,palibe angamake kwainu

  • @Yaqub-nk4pu
    @Yaqub-nk4pu Месяц назад +1

    Big Ntanyuwa well spoken

  • @SymonChimwaza
    @SymonChimwaza Месяц назад

    Ulemu wanu, go ahead

  • @user-wp9js5vu6s
    @user-wp9js5vu6s Месяц назад +1

    Chikangawa sitikunanso achoke bs

  • @ChrisjuZiyaya
    @ChrisjuZiyaya Месяц назад +1

    Koma ngati ma plan ake sndamenewo nde let's other way to remove these mbava kma tikadalira zisankho ndithu tizalira.

  • @TelezaGoodson
    @TelezaGoodson Месяц назад

    😂😂😂😂😂😂 ati kumupitikitsa muthalika relo mwazindikiratu

  • @MustaphaCassim
    @MustaphaCassim Месяц назад +1

    Gendeni chikangawa

  • @user-dh1oi8mb4v
    @user-dh1oi8mb4v Месяц назад +1

    Mcp must go tatopa nazo ndipo zobela zisankho muyiwale agalu inu

  • @anthonynkhoma4265
    @anthonynkhoma4265 Месяц назад

    Pitani pa ground mukapange campaign. Apo biiiii mcp idzawina mosavuta. Campaign sapangira imfabya munthu

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 Месяц назад +5

    Osadandaula Malawi si Rwanda kapena Zimbabwe tidzaichotsanso ngati 1993 Tjis Malawi Criminal Party. Sitikusewera ulendo uno.Sitingaluze Chilima ndi chisankho zinthu ziwiri.tinaluza kale potiphera Chilima

    • @AnnieBanda-rb2dk
      @AnnieBanda-rb2dk Месяц назад

      Zoona kuluza zinthu ziwili chifukwa cha galu chikangawa chakwera uyo munthu opusa galu munthu oyipa ameneyo

    • @henryphiri6100
      @henryphiri6100 Месяц назад

      @@AnnieBanda-rb2dk munthu anapha sidik mia kunamizira covid.wathamangitsa amsowoya ku chipani pano watimalizira Chilima. Chilima ekha anapha olakwika.ife sitimaopa Zimbabwe si Malawi

    • @AnnieBanda-rb2dk
      @AnnieBanda-rb2dk Месяц назад

      @@henryphiri6100 galu ameneyo awononga zinthu kwambiri kumalawi koma chilima yokha anaswa mitima yathu galu ameneyo chigawenga, eeeee ayi munthu oyipa kwabasi ife nde sitiopatu ngat akuopseza aziopseza nkoko iye galu chakwera ndi Malawi ife amalawi ndeno chomatiopsezera ndichani galu ameneyo osachikerera chigawenga chimenecho, chikazuse kaye chilima muchikangawa

  • @THOCCOChimbali
    @THOCCOChimbali Месяц назад +1

    Mbambande comrade

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d Месяц назад +1

    Mukatelo muzikila apilce kumbuyo kumati apolice akuvutika chosecho apolice o ndimweso akuthandizila mavuto ku Malawi ine zimandimandinyasa mukamamenyela ufulu apolice aaa

  • @ChimmsRichardOrden
    @ChimmsRichardOrden Месяц назад +1

    Azibusa opusa a Livingstonia mwalandiliratu mphoto yanu

  • @evansjohn7766
    @evansjohn7766 Месяц назад +1

    Muzingokalila kulimbana ndi DPP,monga muzirimbana ndi awawa.aaaa.....amalawi vomelezani kuti zakuvutani basi

  • @user-ww4ei5fb7d
    @user-ww4ei5fb7d Месяц назад

    Koma boma iri nkhanza ndi kupha sadzaleka 😢

  • @CostanceLalli
    @CostanceLalli Месяц назад +1

    Zingowoneka pa 2025 pano

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole Месяц назад

    💯 %mtanyiwa ❤❤

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon Месяц назад +1

    OSANGOPANGA MADEMOWO BWANJI IYE AKAMAFIKA KU BLANTYRE AKUMANEKO NDI MADEMO ZIOUONETSAKUTI MADEMO SANGACHITIKEYI TILIMBE MTIMA BASI

    • @user-ww4ei5fb7d
      @user-ww4ei5fb7d Месяц назад

      Ndipo iye akupitiranji akudziwa kuti kuli mademo? Akusaka akalindo awanamizire kuti apanga challenge president. Za ziiii zinafunika kupanga pa 9 tione kuti adzanamizira chani

  • @user-oh9bh1cl3b
    @user-oh9bh1cl3b Месяц назад +1

    Koma opposition are you dead or what mungoyanganila movie zoona?? Can't you get example from EFF in RSA

    • @SellinaSanena
      @SellinaSanena Месяц назад

      Akufuna awone kaye ma plan awo opposition ituluka ndi bomba

  • @user-mf5ce9wj4m
    @user-mf5ce9wj4m Месяц назад +1

    Kodi mademo siukwiya ndipameme anakapa cholinga asabweleko Chakwela.

  • @user-gg9hw4oj2v
    @user-gg9hw4oj2v Месяц назад

    Thank you bro

  • @AustinRashid-s4h
    @AustinRashid-s4h Месяц назад

    Nkhanga ❤❤❤

  • @TottiesJackie
    @TottiesJackie Месяц назад +1

    Akaphedwe nkoko satan munthu oipa ku college of medicine

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js Месяц назад

    May God humble the abusas

  • @YamikanAbubakary-my4ie
    @YamikanAbubakary-my4ie Месяц назад

    Kuwuuwa kwa a garu sikurepheletsa njomvo kumwa madzi 😂😂😂😂😂😂😂
    Chakwera 2025 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥90%vote ✔️🤣🤣🤣🤣🤣

  • @user-mh7cc8up4i
    @user-mh7cc8up4i Месяц назад

    Azibusa achinyengo amapta kokathokoza kuti anachitabwino kumpha chilima azibusa onyenga adyela koma mulungu akuwona zosezo

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js Месяц назад

    Tippex,nde anene anthu opha vice president,wakuba,

  • @GraceZumazuma
    @GraceZumazuma Месяц назад

    Musamati a President a Ntanyiwa mudziti chakwera pa u president sakukwanila dyelekezi Lucifer ameneyo

  • @petermasenti2084
    @petermasenti2084 Месяц назад

    Opposition sikuthandiza a malawi Koma zobera mavotizo ndiye ayi Kuli bwino malawi tizangomungawanapo

  • @MulowokaBlessings
    @MulowokaBlessings Месяц назад

    Akhupilire za DPP izo zaziii a Kalindo

  • @DalitsoMatope
    @DalitsoMatope Месяц назад +1

    Amalawi tigule malengeni

  • @fannyzimba149
    @fannyzimba149 Месяц назад

    Koma Zikhale mavalidwewa bwanji???

  • @user-ky4ce9gb6j
    @user-ky4ce9gb6j Месяц назад

    Limpopo number 1

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e Месяц назад

    Apule asandukatu Mulungu kodi.

  • @zelliachamboto5744
    @zelliachamboto5744 Месяц назад

    Fokolo for sure,,FOKOLO AZibusa adyera hakweeee,,,

  • @YamikanAbubakary-my4ie
    @YamikanAbubakary-my4ie Месяц назад +1

    Chakwera 2025 🔥🔥🔥🔥🔥🔥90%vote ✔️

  • @user-rc3ze2oi7u
    @user-rc3ze2oi7u Месяц назад +1

    AKUNAMA AMENEWO TIZAGWEBANA BASI

  • @DavieMosesJulius
    @DavieMosesJulius Месяц назад +1

    Tonse sitilora tilipo tithamagitsa ameneyi

  • @ThomasMwandila-tn7cf
    @ThomasMwandila-tn7cf Месяц назад

    Ripopo ndinyasi kungofunakuroka amarawi mitu bwanji kumarimbikutsa mtendere

  • @ThulaniPrince
    @ThulaniPrince Месяц назад

    Zekariya 11
    15 Pamenepo Yehova anayankhula nane kuti, “Tenganso zida za mʼbusa wopusa.
    16 Pakuti ndidzawutsa mʼbusa mʼdzikomo amene sadzasamalira zotayika, kapena kufunafuna zazingʼono, kapena zovulala, kapena kudyetsa nkhosa zabwino, koma iye adzadya nyama ya nkhosa zonenepa, nʼkumakukuta ndi ziboda zomwe.
    17 “Tsoka kwa mʼbusa wopandapake, amene amasiya nkhosa! Lupanga limukanthe pa mkono wake ndi pa diso lake lakumanja! Mkono wake ufote kotheratu, diso lake lamanja lisaonenso.”
    Apule

  • @user-ti2vs9jl1w
    @user-ti2vs9jl1w 18 дней назад

    Koma chikangawa Mulungu si munthutu?

  • @MosesDzonzi-em5px
    @MosesDzonzi-em5px Месяц назад +1

    Kodi ndinu a ku Namibia eti?

  • @user-hw5xx9kb2s
    @user-hw5xx9kb2s Месяц назад

    Jezebel nkhope ngati munthu wakufa mxieem

  • @user-vu4cz1mt4f
    @user-vu4cz1mt4f Месяц назад

    Vuto timasowa kusongoleledwa Koma wina atangot tien ndekut kuzachema size

  • @EmilyKanyika
    @EmilyKanyika Месяц назад +1

    Eya zoona Ntanyuwa

    • @GreevinWaMugowa-j9c
      @GreevinWaMugowa-j9c Месяц назад

      Kulibwino chisankho chilephereke,,ndipo Ntanyuwa wafikapo

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus Месяц назад

    A hyena cant bear a lion(kamuzu banda >>>>DR. chikangawa forest)
    Commenting from inside thickest chikangwa ....Am not able to see you bcoz of chifunga....anyone here raise a hand please

  • @PatrickMaluwaphiri
    @PatrickMaluwaphiri Месяц назад

    Very sad

  • @ChrisjuZiyaya
    @ChrisjuZiyaya Месяц назад

    Dzaka dzomwe takulekererani a MCP zakwana don't bother kuti muloweso m'boma kwatsalako muyambitsa nkhondo kumalawi because atenga mbali onse akhudza zisankho ife amalawi eni ake sitikuwankhulupirira.

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 Месяц назад

    Koma guy's abiyeni adali wooneka bwino

  • @petermasenti2084
    @petermasenti2084 Месяц назад

    Azibusa opepera

  • @user-fr3ge2hf6s
    @user-fr3ge2hf6s Месяц назад

    Koma akunama mulungu awalanga ndipo inu atanyiwa ayalusenu agaluwa

  • @shadreckphiri1799
    @shadreckphiri1799 Месяц назад

    What kind of a pastor is Dr Chakwera sure?

  • @Angelsymon-c4r
    @Angelsymon-c4r Месяц назад

    Kkkkkkkk muyisova ulendowu

  • @daviechannel8603
    @daviechannel8603 Месяц назад +1

    Mmmmmm

  • @user-jn9tz3li3v
    @user-jn9tz3li3v Месяц назад

    Koma Chikangawa azafa imfa yowawa kwambiri kuposa ya Chilima.

    • @AnnieBanda-rb2dk
      @AnnieBanda-rb2dk Месяц назад

      Azafe ifa yoti olo mutembo wake usazaoneke galu ameneyo chigawenga chakupha

  • @KenHaji-z3q
    @KenHaji-z3q Месяц назад

    Wachikangawa vuto ndi amabungwe ndi azibusa ali mbali yake

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc Месяц назад +1

    Malawi inapepeletsedwa,kale kale.kulibe, Anthu olimba mitima,ngati ku Kenya, tiyeni amalawi tibvomeleze,kuti'mphabvu,zathu,tinazipeleka'mmanja,mwa andale.citizen,ya malawi ilibe mphabvu.olo, president atakhala kuti akufuna akhale,pa u president for life zitheka.olo,atakhazikitsa,lamulo loti,tidzimuseta,akalowa mu chimbuzi zingatheke.chifukwa,tili opepela mu African continent.

  • @MaikNkhoma
    @MaikNkhoma Месяц назад

    Wachita bwino panyapako mulomwe

  • @shadreckphiri1799
    @shadreckphiri1799 Месяц назад

    DPP is supposed to be run a young man. Peter Muntharika is too old to do politics.

    • @MarthaBango
      @MarthaBango Месяц назад +1

      Waona zomwe zachitika ku utm saulo's atamwalira?zomweso zingachitike ku dpp iye uja kut achoke panopa,,,dekhani utsogoleri siwamasewela ndi mphatso yochokera kwa mulungu ,even inuyo atakutengani kut mukaime ngat nyamata ku dpp ko simungakhale ndi chikoka ngat cha iye uja,dekhani kae mphuma limeneli lomwe mumatenga nazo zinthu kuziika pa mpando

  • @MussaAndreQuenessi
    @MussaAndreQuenessi Месяц назад

    😅😅ulemu

  • @Omarmamaki-ts9xg
    @Omarmamaki-ts9xg Месяц назад

    😢

  • @MwenyeCheNsoma-gb2yz
    @MwenyeCheNsoma-gb2yz Месяц назад

    Mhu!

  • @AbdullahaziziAmoswalala
    @AbdullahaziziAmoswalala Месяц назад

    😅😅😅😅