Koma izi ndiza boza kuno ku South Africa timonela news😊 ku SABC amanena kuti asilikali A South Africa mothandizana Malawi Tanzania Kenya akumenya as peace keeping force moti Asilikali awiri a South Africa A mwalira
Bodza bodza asilikali achitezo cha african union kuli south africa Tanzania Malawi kenya moti asikali awiri a ku South Africa aphedwa week yomoino bodza bodza
akusithanisa ndi mafuta kodi iwowo aku DRC wo mafutao amapanga okha olo amagulaso naonso? mesa amagula and amapitila ku dooko la dalesalam nanga vuto iwowa lilipati kuti azigula okha mafutao
Kamunthu kodzungulira mutu ka chakwera bwanji otsapeleka ana ako mkadziwako nda bare ako ndi wamisala inu uyoyo komaso zikhare chinkhope kunyasako ndi mtima momwe
Afunika kukamba president ngat ayenda aut or akabwela afunika kukamba, comwe comwe amacita nako Keanu kumawi mwacita over mudziko murivisisi but muri umphawi
Palibe chomwe akulakwisa.... Opusa ndi asirikaliwo....they supposed to protect us all not to be cheaply manupulated by stupid dumb leaders... Ngati leader akupanga zopusa...atsilikali ndamen amamuthamangisa not just following nonsese
Am following you from Pretoria 🎉❤❤
Thanks ulemu wanu big God bless you because you make us happy
Poti asilikali a Malawi ndiopusa ndikale alolelanso zopusazo .
But MCP never repeat on 2025
Thank you boss,,,we always appreciate you
Brothers n sisters tiyeni tigwilane manja Kuti ziko lathulino😢😢😢😢
Good work .... amalawi chakwela akutisewelesa kwambili watikwana
Always your talking the truth story God bless you big man ❤
Thanks for the update we have been waiting for this
Confirm that
Following mwachidwiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii, you're genius keep it up
Am following you, please may you Also teach us about Hutu and the Tutsi of Rwanda as Paul kagame is president of Rwanda
Amalawi chakwera wationongela dziko uyu,,,,, ndipo inu amene mukutaya nthawi pomuwombera manja ndinu opusa,,, anzakeawenga zokha zokh
We are proud of you bg man, only you our hope
I support good deal....
Deal ili bwino kwabasi
Thank you big wathu true story 🙏🏼🙏🏼☀️☀️☀️
Aaaa ine adzakambe za masambuka death paja peter muthalika akukhudzidwa
@@GeorgeMphale-n8qBaai waikamba iweyo mesa ukudziwapo kanthu
Anthu amat akumangani ifeee kudandaula
God bless you boss please musamasowe chonchi
Kuyendetsa dziko mumawona ngati limayendetsa ndi dziko limodzi, amathandizana chinchilla ndithu
I love bakili muluzi tv news 📰 they tell the truth we are following you from Zambia
❤❤ chakwela basi dziko wayigulisa palibe za Malawi apa 😢😢
Yaaa Chakwela ndi dolo,
Thank br for letting us know 😂
We are together big man!!
What then shall we do . ?
Thank you blather ❤❤❤❤❤
Respect to u brother
Always respect
Respect brother❤
Salute big man
akulu ndinu apaderadera, god bless you,
Make History ya abraham Lincoln
Keep it up our jenius
Good documentary
"a Malawi akufuna kumwa Tea" 🔥🔥😂
Kkkkkkkk inde inde tufuna tea ife
Best tv in africa
Zikhale ng'oma anakufikapotu😂😂😂😂
Popanda bakili muluzi TV bwezi a malawi 🇲🇼 tili mu mdima
Chakwera mbuzi yeniyeni
Zikharr Mbuzi yeniyeni
Asilikari nawonso angoona zinthu zikuonongeka. Bwanji osangopha Chakwerayo basi tione zina
Big up💪✊
Koma izi ndiza boza kuno ku South Africa timonela news😊 ku SABC amanena kuti asilikali A South Africa mothandizana Malawi Tanzania Kenya akumenya as peace keeping force moti Asilikali awiri a South Africa A mwalira
Kumapha mtundu wa a Malawi pofuna kulowetsa ndalama thumba mwawo ,Koma akulu awawa ndi Mulungu yekha awapange sorted ,Mulungu anachokera nzeru anawachotseranso
Best TV
Chakwela ndi president wamisala Komaso
Ziwanda zakumidima zikumuvuta kwambili ndipo Ngati amalawi tingalole kulamulidwa ndi chakwela 💯% zilala milili ikhala yambili kwabasi
Mbuzi ya presidente iyi
KAGAME tu ndi chilombo, amalawi samalani ndithu.tufunsani ife aku DRC tikuuzeni khani zo badwitsa za KAGAME.
Koma chakwera komwe ali ndi tv iyi sangagone.kuyankhula kokha kukuposa hot curent ya times
Atiganizireko zokha za ku imigration boma litengepo ngawo plz plz tikumva ululu kwambiri kokha ku ma passport
ife dzobeladzo tinadziwakale kut akufuna kuba ma vote mungila yama passport amati sistm ama nama
Koma linali ndi bodza ku DRC kulibe mafuta amachita kugula ku south Africa ndi Tanzania ndi Mozambique,nzosatheka mafuta ku DRC
Best tv
Ine ndimafuna history ya kurwanda kod idayamba bwanji khondo pakati pa matusi ndi mahutu chonde tifuvuzileni broz
Analongosola kale
Malawian people amene angazavotele MCP in 2025 ndiwotembeledwa basi Muthu ameneyo mpaka moyo wake onse
Adatisithanitsa km ku Israel tikulandila 4 million mpabwino bwanji
Ulemu wanu bwana ❤
Kumapeleka Machende I Mean Machine Oonengeka Cholinga Anthu Adzigwa Mphwai Dara Asakalembetse Cholinga Asazavote Ma Plan Opoila Kwambr Zitsiru Za MCP
Bodza bodza asilikali achitezo cha african union kuli south africa Tanzania Malawi kenya moti asikali awiri a ku South Africa aphedwa week yomoino bodza bodza
akusithanisa ndi mafuta kodi iwowo aku DRC wo mafutao amapanga okha olo amagulaso naonso? mesa amagula and amapitila ku dooko la dalesalam nanga vuto iwowa lilipati kuti azigula okha mafutao
Ayaruka garu ameneyi mbuzi kapuku
Anthu ambiri amene tinalembetsa za ma id September 2023 mpaka pano ma id athu sadatuluke
Kamunthu kodzungulira mutu ka chakwera bwanji otsapeleka ana ako mkadziwako nda bare ako ndi wamisala inu uyoyo komaso zikhare chinkhope kunyasako ndi mtima momwe
Uremuwako❤❤
Kukatenga anthu ku D R C kudzaphera mu malawi,ndekuti ku malawi nde koimitira magadzi aanthu nde wafikapo mbusa ,
Our own legendary
Afunika kukamba president ngat ayenda aut or akabwela afunika kukamba, comwe comwe amacita nako Keanu kumawi mwacita over mudziko murivisisi but muri umphawi
One of the best 🔥🔥🔥
Tonsefe tinaripo pomwe APM ndi DPP amalamura dziko la malawi ndipo tikudziwa momwe iwowa ankayendetsers dziko, ndiye tikudabwa kuti TV imeneyi imangowona zorakwa za boma lapanori, kapena tiziti ndinu murendo ku malawi kuno?
Chakwera anakuranda chani uwoneka kuti umalimbana ndi MCP ufuna kuzayambitsa khondo komatu. Uzatera iweyo uzagwina sikare
Iwe vayako wa mcp
Komaso ngozi iyi ndiopsa kwambili bwanji akanaika pamozi china chavetsa chison china chomaliza galimoto tomwe ikunyamula malilo a chilima vp president zoona ikhale iyi kuboma kulibe galimoto zapamwamba chakwela akuonjeza inu
This country mmmmmm 🙌💔 silidzatukuka . Lili mmanja mwa afalao
Ulemu wanu brother
Kod boss mukati mahutu ndi chani boss tiuzeni ife sitikuziwa
Ndi mtundu wa anthu umene umapezeka ku Rwanda. Like ku Malawi we have achewa, a mtumbuka.
Chitsiru chimenechi vuto ndi anthu omwe anamuvoterawo ndipo sikoyenera kuti Congress ibwelere m'boma
Ku mulanje machine amodzi koma kulibe ma form😅😅😅😅
Bambo wa dpp wabodza.Otsati chakwera say your president
Ndimasangalala ndimomwe mumalankhulira mwawukali, galu chakwera ameneyu ndimunthu osanva
Ndayamba kusapota chipani choyipachi cha MCP. Ndimvereni chisoni chifukwa umenwu ndi ufiti.
Chakwela ndi buzi yamuthu Yona uyu atipha
Kod inu agalu amene mukuzusa mukuzitenga ngat ndinu ndani tizit malawi mmene alili mu zimukuona ayi ndunu agalu et
Chakwela you mast go Galu
Osowa cholankhila iwe,ndie mwaluzatu kale ikhale nkhani imeneo zopusa 3:01
uyu si president ayi kodi kuno ku malawi kulibe asilikali tipange order captain ibrahim traore azatenge boma lathu
Koma mposoo Kuno asilikali tinakwilila ndithu
I am on your point
❤❤❤❤❤❤❤❤❤you brother
Koma chakwera ndi mbuzi mpaka chipatala chamunthu kukasegulira iye mmalo mwa minister 😂😂😂😂 galu wamunthu
ndipo alibe manyazi
Mumakwa
I am Fom Moz 🇲🇿
Anthu amat akumangani bg
Chakwera and his entire cabinet looks to have been cursed , coz chilichose chikungoyenda upside down
Opposition yatulo
Vomerani kuti mulibe anthu oti akuvotereni. Mwakhala mukuononga dziko lino amalawi adatopa Nanu.
Ife amalawi sitikufuna chakwera tisavotera Peter mutalika
❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Maboza toooo
This guy mmm atipha
Respect Bossa yama Bossa
❤ Live
ndikamaona khope ya zikhale ngoma amaoneka nga pusi khope yake muyanganisiseni zikhaleyo muvomeleza ndikunenazi
Chakwela ndi mbava ndipo mbava yosadziwaso kuti kunjaku kuli Mulungu
Timakupemphelerani bwana osadandawula, mumatidziwitsa zambiri
Mwaitha bwana
Kkkķkkkkkkk umphawiwu mpaka tipatseni mafuta ife tikupatsani asilikali
Saulos chilimayo pofunika asamalenaye mukatengela zibwana magazi tisambisanapo dzikomuno
Tinasankha njoka
Madolo tisamatsutse taonani lero sugar wafika pa 3500 kwacha 😢
Palibe chomwe akulakwisa....
Opusa ndi asirikaliwo....they supposed to protect us all not to be cheaply manupulated by stupid dumb leaders...
Ngati leader akupanga zopusa...atsilikali ndamen amamuthamangisa not just following nonsese
🙏🙏🙏🙏