Zifukwa zomwe Brian Banda anachoseredwa ntchito

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 7 сен 2024

Комментарии • 42

  • @salimmkumakumakitombi-yc7pw
    @salimmkumakumakitombi-yc7pw 8 месяцев назад +10

    Nkhani yanuyi ndikukupatsani 15% .Kanakondwa kuti mukayambire kawili kufufudza .... zikanakhara kuti Brian amapanga ziphuphu Brian bwedzi atamangwidwa kalekale kutengera ndimmene Brian amachitira polidzudzura boma .. zotiso kunyumba kwake kumakhara apolice zabodza.zoti kunyumba ya mayi mpaka a police 6 zabodza .iyeyo anali IG ndani .

  • @wadilikasingini500
    @wadilikasingini500 8 месяцев назад +10

    The way I know and follow Brian he is a man of integrity and he can't do that, Ife a Malawi tinazolowela kuipisa dzina la mzathu akamachita bwino

  • @paulmakaula4937
    @paulmakaula4937 8 месяцев назад +2

    Brian ndi president wa Malawi wa mtsogolomu! Brian chipempherere ichichi

  • @ruzuwanmoyenda23
    @ruzuwanmoyenda23 8 месяцев назад +4

    MFUNDO zomuchotselazi sizikundigwira mtima zikumandimvekela mwabodza

  • @macdonaldkufankomwe
    @macdonaldkufankomwe 8 месяцев назад +3

    People wake up please! These issues or stories will not take you anywhere in life. Focus on your daily business for your success.

  • @johnynamano3862
    @johnynamano3862 8 месяцев назад +6

    Achimwene ine ndimachokera ku Chileka kufupi ndi agogo ake koma kunalibe a police amalondela kunyumba kwake

  • @hakeemQadango
    @hakeemQadango 8 месяцев назад +2

    wakupasa ndalama zingati chakwelayo Kuti ukambe zimenezi iwayo ndi chakwele 🐕🐕🐖🐖

  • @VeronicaSekobi-is6dk
    @VeronicaSekobi-is6dk 8 месяцев назад +4

    You never disappoint your people with information keep up the good work 🎉🥰

  • @ConfusedAtv-bs4gc
    @ConfusedAtv-bs4gc 8 месяцев назад

    Koma kumeneko ndalama andale ananyambitamo umu mboma azizitenga kuti zoti aziwapasa anthuwa ayambanso maulendo opita kunja kuti akayambe kupemphaso tikumakamba mobweleza kuti aliyense amene akudziwa kuti wadya misonkho yamalawi tsiku likubwela zonsezo muzazosanza ngati muli ndinzelu pano zingobweza nokha ndalamazo

  • @user-jn9tz3li3v
    @user-jn9tz3li3v 8 месяцев назад

    Ayenera kulipila Chakwela ndi amene anali SPC, mmene zinalili za APM ndi Mhura

  • @BannetChaduka-ei7qq
    @BannetChaduka-ei7qq 8 месяцев назад +2

    Mukuti anachotsedwa nchito mosatsata malamulo,kusonyeza kuti Munthuyu amayeneradi kuchotsedwa koma motsata malamulo?

  • @UssenCobra
    @UssenCobra 8 месяцев назад

    Mumakwana 👌

  • @moseskavalo3304
    @moseskavalo3304 8 месяцев назад

    Mbanva zokhazokha iziz.. We know these people

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r 8 месяцев назад +2

    Ndiye chifukwa chake pano brian akulimbana kwambili ndi achakwela akukhala ngati sintola nkhani

  • @GiftMULOMOLE-sd7wc
    @GiftMULOMOLE-sd7wc 8 месяцев назад +2

    Sam uchite improve pochita compile komaso uzichita Kaye practice kuwerenga ma story ako before releasing your Video. Komaso uzifufuza bwinobwino before releasing your Video.

  • @user-hb9sm9hn9g
    @user-hb9sm9hn9g 8 месяцев назад

    Chilungamo chiyende ngati madzi

  • @ChikuCharlie-bf4nj
    @ChikuCharlie-bf4nj 8 месяцев назад

    K103 000 000 new blazer in town 😊

  • @petermtema5241
    @petermtema5241 8 месяцев назад

    Umatha samu mavitha keep it up

  • @user-wy8lk7ns7i
    @user-wy8lk7ns7i 8 месяцев назад

    Mulungu alowelerepo

  • @paulmakaula4937
    @paulmakaula4937 8 месяцев назад

    Zonama zimenezi kuba nduku kukupitililaku

  • @user-xh1ve5ym3l
    @user-xh1ve5ym3l 8 месяцев назад

    Brian Banda ndi munthu wamkulu alandire ulemu wake.

  • @christopherstosherchimbuwi676
    @christopherstosherchimbuwi676 8 месяцев назад

    Of course zamveka ndiye ndichifukwa chani aboma amakanika kukaonekela??? +

  • @user-vh9uk1jy7w
    @user-vh9uk1jy7w 8 месяцев назад

    Osokonenza kwambiri

  • @randolphkazembe229
    @randolphkazembe229 8 месяцев назад

    Ndikuyamiken blo potipatsa satanetsatane wa nkhani yokhudza Brian koma ndipemphe kut muziyesako kugwilitsa ntchito chichewa chabwino ,mwati akhothi anangokhadzula kut,pamenepa mupaunikile.

  • @BishopMagalasi-wp9ii
    @BishopMagalasi-wp9ii 8 месяцев назад

    Mpaka ma body guard kwa Mai ake ? It is tit for tat.

  • @user-kv4cs1ot3x
    @user-kv4cs1ot3x 8 месяцев назад

    Amupase zake basi

  • @CharlsChiyembekezo-xu4wk
    @CharlsChiyembekezo-xu4wk 8 месяцев назад

    timakunyadila pitilizani

  • @NumbDee
    @NumbDee 8 месяцев назад

    Ampase zake basi

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r 8 месяцев назад +1

    Kuzitukumla abriani

  • @giftblack7690
    @giftblack7690 8 месяцев назад

    Chakwelatu mukunena zowoona chakwela ndi mbuzi yamunthudi ndipk ndimbavadi komaso garu satana

    • @DanielNamate-nk9so
      @DanielNamate-nk9so 8 месяцев назад

      Mbuzi ndi iweyo, makolo ako, abale ako komanso amzako onse

  • @user-md5uv2cg6i
    @user-md5uv2cg6i 8 месяцев назад

    Analiso wachamba bwanji koma akamalankhula ngati wanzelu

  • @user-hb9sm9hn9g
    @user-hb9sm9hn9g 8 месяцев назад

    Brian ulemu wako

  • @user-bz7iv1rq2f
    @user-bz7iv1rq2f 8 месяцев назад

    Kkkkkk

  • @lawrenceblacktealyson8015
    @lawrenceblacktealyson8015 8 месяцев назад

    Mbava iyi

  • @lawrenceblacktealyson8015
    @lawrenceblacktealyson8015 8 месяцев назад

    Mbuzi ya mumthu iyi