A JOYCE BANDA ATULUKA TONSE ALLIANCE 11 August 2024

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 9 сен 2024

Комментарии • 241

  • @gumambalule7675
    @gumambalule7675 29 дней назад +4

    Your Excellenccy Madam Joyce Banda, this is a pure show of political maturity. Ankhalakale pandale ngati inu mukuyenera 4:32 kuphunzitsa atsogoleri amawa good politics like this. What you have done here ndi zodabwitsa komanso zapamwamba. Honestly sindimayembekezera kumva inu mukulankhula chonchi. May God bless you with more wisdom as displayed here

  • @JarvisJames-e9o
    @JarvisJames-e9o Месяц назад +18

    Maganizo abwino Mai we support you from Lusaka zambia

  • @lacksonsiyadi943
    @lacksonsiyadi943 Месяц назад +10

    Akuti koma utm ndi mcp sizingatheke kugwirizananso anaiwala maiwa ??????

  • @SteveniBanda
    @SteveniBanda 27 дней назад +2

    Akufunachani ameneyu nthawi yoseyi analikuti amatani asatipusiseso anthu ayiwalakale

  • @GaryMakhumula-mu3du
    @GaryMakhumula-mu3du Месяц назад +15

    bolako mmayiyu pan'gono Than chakwera, APM my vote 😎

  • @WilliamNhlane-fd9hi
    @WilliamNhlane-fd9hi 29 дней назад +2

    Joice Banda please mukhale pamndanda woima pa president because ulamuliro wanu unali bolani than utsogoleri ulipowu

  • @MphatsoGoodson
    @MphatsoGoodson Месяц назад +7

    Yes Mai khani ndiimeneyo mwachita bwino mwachako😊

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Месяц назад +12

    Ndakayika ngati Mcp ingadzawine chisankho chifukwa mizimu inaphedwa kuchikangawa ija idzakhala ili ku chisankho komweko 2025

    • @user-ww4ei5fb7d
      @user-ww4ei5fb7d Месяц назад

      Kkkkkkkk

    • @user-eh1mg3ww6d
      @user-eh1mg3ww6d 29 дней назад

      @@user-do2cs8nf4b ndipo ndipephelo lal
      Nga daily kuti mulungu atichotsele zikhanilazi zimenezi

    • @SolokingChimzy-yt7dj
      @SolokingChimzy-yt7dj 28 дней назад +1

      😂😂😂😂😂.nanga ngat anthu aja ali kugahena inu muli ndi mphavu yochosa mizimi Yao frm the hello kubwela kuzisankho?

    • @user-ww9rj2wx8d
      @user-ww9rj2wx8d 28 дней назад

      Ndipotu eeeeeeee chakwela mulungu amuone

  • @user-qp8kh2hj9o
    @user-qp8kh2hj9o Месяц назад +9

    😂😂😂😂Akuti anasokoneza UTM singagwirizane ndi MCP Indee mama🙌🙌🙌

  • @limbanikamanga7514
    @limbanikamanga7514 Месяц назад +1

    "Munthu kuti uzitchule mtsogoleri nde kuti anthu azikhuta" - Joyce Banda, circa 2024.
    Anthu ali "eh mfundo koma zimenezi"
    As a country, we deserve what we are going through.

  • @FefieTenisha-du7ge
    @FefieTenisha-du7ge 29 дней назад +1

    I don't understand the level of confidence and faith that harbors in the minds of politicians
    They know they can't win but they dish out money like crazy
    What do they benifit? The godly praises or what?

  • @user-uv5rf4zt5q
    @user-uv5rf4zt5q 29 дней назад +1

    former president if u were still president Malawians could hv changed for better life for all.

  • @victormbewe7462
    @victormbewe7462 Месяц назад +6

    I think ku MCP kwachuluka kudzikonda komanso dyera

    • @SaidiMbawa-st6bj
      @SaidiMbawa-st6bj Месяц назад

      Sizinayambe lero kutuluka gwilizano pamakhala vuto

  • @ConfusedAstronaut-qv6wq
    @ConfusedAstronaut-qv6wq Месяц назад +1

    Thank you Mama Banda,mwazindikira mtunda munakwera uja unaligned opanda madzi,mangotayako thawing,tiyamike poti mwanyamulako miphika yanu ndi madengu omwe.

  • @user-rc3ze2oi7u
    @user-rc3ze2oi7u 29 дней назад +1

    MAI BANDA NDAYAMIKA CHIFUKWA CHA SPEECH YANU YA BWINO YOSANYOZA MUNTHU THAT'S GOOD GOD BLESS YOU

  • @Kamwachale
    @Kamwachale Месяц назад +1

    This is politics at its best. PP is still with MCP, it's just a strategy of dividing votes in the south

  • @chiefmitengo
    @chiefmitengo 29 дней назад +1

    It's obvious Tonse singapitilire , ma cadets akuona ngati PP and MCP zayambana,. Ng'oooooooo😅. Musova. Chakwera and Joyce Bomaaaaaaa❤❤❤

  • @chifundocharles2348
    @chifundocharles2348 Месяц назад +6

    Let's move 😂😂😂 DPP 🎉

  • @WanangwaMfune
    @WanangwaMfune Месяц назад +5

    Mayi awa anachita kuabela mavote

  • @kagisocollen
    @kagisocollen 28 дней назад

    Thanks so much

  • @chiefmitengo
    @chiefmitengo 29 дней назад +1

    Amene akupanga support DPP ndi asatana ndipo mukalangidwa kumwamba agalu inu afiiti, tchito kutukwana Azimai Basi, munabadwa kuti Kodi? Pitala wanu wamanyiyu kwawo ndikuti? Mama Joyce Banda wakumasulani.

    • @JusticeNyirenda
      @JusticeNyirenda 26 дней назад

      Zako izoooo 🥱🥱🥱 DPP 🥳 kwinaku 💙💙💙

  • @user-wq9ex2sf3b
    @user-wq9ex2sf3b Месяц назад +5

    Chakwela chikangawa from Zambia 🇿🇲

  • @user-vm7iz6oz6r
    @user-vm7iz6oz6r 28 дней назад +1

    Komat muthuy sanatuluke mu mcp

  • @user-oc9vl9xz8e
    @user-oc9vl9xz8e Месяц назад +1

    Paja a Malawife ndi zitsilu akakupasani nsalu basi muzakavotele chifukwa cha nsalu muzizavutikanso muone maiwa anaba ndalama azadya moyo wawo onse komanso zizukulu zake inu mukugona ndi njala 😂😂😂😂

  • @PriscillaKhumbanyiwa-i1d
    @PriscillaKhumbanyiwa-i1d 28 дней назад +1

    Vuto amalawi mumaiwala simachedwa kukopeka

    • @Lee-lee-w1r
      @Lee-lee-w1r 21 день назад

      Ndipo nde Simukunama. Ndi anthu opepela kwambili

  • @SimeonAbraham-u2j
    @SimeonAbraham-u2j Месяц назад +1

    Mayi mumachedwa kutuluka Ku mandaku mwayitha our vision is in you

  • @kagisocollen
    @kagisocollen 28 дней назад

    Thanks

  • @fosternyirenda-wo4eb
    @fosternyirenda-wo4eb Месяц назад +1

    Angapezeke ndi namba ya mai Banda ,ndigaireni plz

  • @alickmkatsonga172
    @alickmkatsonga172 29 дней назад

    This is disadvantageous to DPP, kuno ku southern region we need one unified political block, apoo biii MCP will have a smooth walk over come 2025,
    DPP, UDF UTM PDP zonse from region imodzi

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj Месяц назад +2

    Achita bwino kwambiri chipani chilichose chiyime pachokhapachoka ndiye bwino chigawo chapakati pali chipani chimodzi pomwe kumwera kuli zipani zambili kupoto kuli ziwiri

  • @emmanueljelemani4203
    @emmanueljelemani4203 Месяц назад +4

    Munasokonezadi your excellency UTM singapangedi alliance ndi MCP... 😂

  • @DinaRobert-q6w
    @DinaRobert-q6w 25 дней назад

    Am in Tanzania listerning to my former president,I wish I could visit you .but I don't HV transport .what your talking are very fuandastically

  • @CleverChikowi
    @CleverChikowi Месяц назад +1

    I now conquer with UTM's decision of withdrawing itself from the alliance, it was timely

  • @user-mg6jh7ht9i
    @user-mg6jh7ht9i 28 дней назад +1

    Mayi madeya

  • @bamusmajawa1619
    @bamusmajawa1619 Месяц назад +4

    Bwanjiso Nanga a Tonse alliance 😂

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc Месяц назад +4

    Mai,achita bwino,mcp yatumbwatu,ngati anakalowa okha ku meneku 😂😂😂😂😂moto buuuuu

  • @mathewskapinga5227
    @mathewskapinga5227 27 дней назад

    Nkhalamba iyi songatsogolere dzoko

  • @Blessings-b7h
    @Blessings-b7h Месяц назад +1

    Palibe cha mzeru chimene mungapange amai ofoira inu chitsilu cha munthu dziko linayamba kusokonekera chifukwa cha inuyo.

  • @ignasiolucianobanda8493
    @ignasiolucianobanda8493 28 дней назад

    Basi program ikhale kulandira nsalu aaaaaaa zaziiiiiiiiiiiiiiiiiiiii

  • @user-ji4ed6dl3i
    @user-ji4ed6dl3i 28 дней назад

    Great news

  • @user-xd2uz1bh3l
    @user-xd2uz1bh3l Месяц назад +2

    Apusiseni amalawi opusa wa

  • @chifundoKaluvi-ey5uw
    @chifundoKaluvi-ey5uw Месяц назад

    Mukungovutika boma nila father adadi Peter wamuthalika

  • @GospelMakonyola
    @GospelMakonyola 29 дней назад

    My vote

  • @Mrgfpatrick
    @Mrgfpatrick Месяц назад +1

    Ma civil servants onse avotera JB,chimunthu chimakweza ma salaries ichi😂😂😂

  • @FefieTenisha-du7ge
    @FefieTenisha-du7ge 29 дней назад

    The tonse alliance was an alliance on paper not a pragmatic one...
    It's very unwise and foolish to think that you were part of the alliance
    What contributions did ur party make as part of the alliance for the benefit of Malawians...
    Too late madam former President

  • @SophieBanda-el8ri
    @SophieBanda-el8ri 28 дней назад

    Koma Mesa akuti mgwirizano inali wakuti convention ikachitika ndekuti alliance yatha, nde akamayi atuluka atuluka chiani oti mgwirizanowo palibe watha.

  • @ThokoGomeza
    @ThokoGomeza 28 дней назад

    Mai ndi mai amakhala ndi chifundo mwina tione mai yu

  • @ThokoBanda-c6g
    @ThokoBanda-c6g 24 дня назад +1

    Aibo Jesus 😢

  • @gracesawa-zl6uo
    @gracesawa-zl6uo 28 дней назад

    Congratulations amai 🎉🎉

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h Месяц назад +6

    Mmmm inuyo munalikuti a JB nkhani ya njala aaaaa komanso mukumvekeralabe ka chikangawa

  • @RobertCosmas-bo1uo
    @RobertCosmas-bo1uo 28 дней назад +1

    Otsatira DPP kutukwana amatha

    • @user-fh3dn8kt2j
      @user-fh3dn8kt2j 28 дней назад +1

      Eeeee ndipo alibe anzawo mmmm zochititsa mserutu zopanda Umulungu

  • @ExcitedMackerel-pr4bp
    @ExcitedMackerel-pr4bp 29 дней назад

    Kumanga khola mbuzi zitabedwapo zonse zomwe mukuchita apazi😅😅😅

  • @user-kp8zh9qg2m
    @user-kp8zh9qg2m 29 дней назад

    Akusauka kamba ka iweyo ndi amene munapanga zopoira

  • @PempheroAlufandika
    @PempheroAlufandika 29 дней назад

    Asatinamize awa ndiokomedwa Ku domasi komweko koma town sagabwere

  • @GeorgeKambwiri-xr9ri
    @GeorgeKambwiri-xr9ri 29 дней назад

    Mayiwa sungafanize ndi mbuzi ikulamula panoyi

  • @user-wq9ex2sf3b
    @user-wq9ex2sf3b Месяц назад

    Ami mulungu akudaliseni mwatuka kutose a MCP ndi asatana achikangawa from Zambia 🇿🇲 lsk.

  • @pauljosephmakaula6835
    @pauljosephmakaula6835 Месяц назад

    Mupweteketsa mwana wanu ku Quatar....hopefully munakawadandaulila bwana president ku Mzuzu...nanga si ndale izi mukapangila ufulu wa ana ndi azibale...

  • @PeterMalunga-t6m
    @PeterMalunga-t6m 29 дней назад

    Kuthekeni kwake kuti munapanga mseu wake aaaaa amayi apo ndiye mwanamatu kkkkkkkkk ine ndiwakoko aa

  • @MercyHassan-p4e
    @MercyHassan-p4e 29 дней назад

    Mayi wafuko mayi Joyce Banda munatimangira nyumba zamarata pakwanthu ku Balaka ndimakunyadirani mama i ❤ you so much

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 29 дней назад

    Maturity Joice,UTM singagwirizane ndi MCP zoona inapha chilima.olo inu ndimadziwa zimakukhudzani koma simungalankhule

  • @chifundoKaluvi-ey5uw
    @chifundoKaluvi-ey5uw Месяц назад

    Kodi Peter ulikut nakusowa I adadi osati njuchi

  • @LackzenSumbudzu
    @LackzenSumbudzu 29 дней назад

    Mau amphavu amayi

  • @IgnancioKachimanga
    @IgnancioKachimanga 29 дней назад

    Kubwezatu mau amai akuti anasokoneza UTM siingagwilizaneso ndi MCP 😂😂😂😂

  • @KikaImran
    @KikaImran Месяц назад

    Ndipo JB salary increament amaidziwa

  • @LastonAlli
    @LastonAlli 29 дней назад

    More 🔥

  • @MadisonMagesi-t8f
    @MadisonMagesi-t8f 29 дней назад

    Kofunika athuwa kuwarodza basi mbuzi zawathu

  • @FrankHaruni
    @FrankHaruni 29 дней назад

    Alowe akamalidzise khani ya lakemalawi

  • @asahelmachila3026
    @asahelmachila3026 28 дней назад +1

    Inde Joyce uli hule zoona. Richard Banda had a wife before you, and you
    had your own husband. You alleged mistreatment from your husband in order to be hule laRichard Banda. You grabbed Richard Banda from someone else and distroyed marriages, both yours and Richard's. So iwe uli hule zedi.

    • @user-fh3dn8kt2j
      @user-fh3dn8kt2j 28 дней назад

      Mmmm koma nkhani zake zomwe za ndale zi?????? Uhuu kupempha tsokatu uku za ziii sizikugwilizana achimwene mwaonjeza

  • @user-gj4li2gc8o
    @user-gj4li2gc8o Месяц назад

    This is a gud move to divide southern region votes ,dpp cannot win with these division ,nankhumwa ,atupere,Joyce Banda all from southern region

  • @user-ln3zx6wo4w
    @user-ln3zx6wo4w 29 дней назад

    Mcp tipweteka tonseija yatembenuka yiliku dpp

  • @amoschisisi2070
    @amoschisisi2070 Месяц назад +1

    Ndege ilikuti

  • @SimeonAbraham-u2j
    @SimeonAbraham-u2j Месяц назад

    J b ndi mbambande amuna ena sangamake

  • @nokosemakolija-xe9do
    @nokosemakolija-xe9do Месяц назад +1

    Ndale za malawi ndi apaseni nsalu ndi t-shirt basi😭

  • @AbdullahaziziAmoswalala
    @AbdullahaziziAmoswalala 29 дней назад

    😂😂😂 ma jokes achuluka ku malawi

  • @KondwaniMunthali-vf1ws
    @KondwaniMunthali-vf1ws Месяц назад

    A iti Ntila,, Khaaaaa!! ❤

  • @AlexManuelMisomali-sv1vn
    @AlexManuelMisomali-sv1vn Месяц назад +1

    No more tonse alliance 😂😂😂😂 so Chakwere, what are you going to do ? And if you think MCP can win 2025 that means you must steal votes something Malawians can't agree and if you think that you can fool Malawians never this can not be happen

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg Месяц назад +2

    mcp yàtha bàsi

  • @SellinahMkandawire
    @SellinahMkandawire 29 дней назад

    Koma mkhani ndiimeyo kaya

  • @gracesawa-zl6uo
    @gracesawa-zl6uo 28 дней назад

    Amai ndili kumbuyo kwanu🎉🎉

  • @LysanJames
    @LysanJames Месяц назад

    Allah be with you mama JB

  • @kangungufoundation2020
    @kangungufoundation2020 29 дней назад

    Mayi waboza uyu osamukhulupilira zinamukanika uyu

  • @patrickkadzeya3020
    @patrickkadzeya3020 Месяц назад

    Akuzotembelera okha amene akukutukwani.Mulungu akudalitseni
    Mayi.

  • @johnlodzani958
    @johnlodzani958 28 дней назад

    Mwakhutakhuta 4years mwaganizano zobwela kkkk

  • @EdsonKamwendo
    @EdsonKamwendo Месяц назад

    Mayi oputsa inu muluzi anakhala akunena kuti mcp musazaivoterenso koma mai inu ndi Chilima mwafera kusata

    • @spargomw
      @spargomw 29 дней назад +1

      Kusamva, onse nd Chilima. Lero Chilima kulibe

    • @RuthBandula
      @RuthBandula 29 дней назад +1

      Mawu akulu akoma akaonekela.taziona Muluzi amanenadi,koma kusamva kwathu😢😢😢

  • @user-nj4pn8gx7y
    @user-nj4pn8gx7y Месяц назад

    Mwachita bwino kuchoka ku CHIKANGAWA kuja❤

  • @BenardChitera
    @BenardChitera Месяц назад

    I support you more 😊

  • @ChikondiChakwiya
    @ChikondiChakwiya 29 дней назад

    Chaka chake ndi chino muphwetekana

  • @user-nj4pn8gx7y
    @user-nj4pn8gx7y Месяц назад

    Tili pambuyo panu Mai ❤❤❤❤❤❤❤

  • @JoshuaNyirongo
    @JoshuaNyirongo Месяц назад +1

    Hoping against hope

  • @MADALITSOKALUSA
    @MADALITSOKALUSA 27 дней назад

    💪💪

  • @jestonkalipu
    @jestonkalipu 29 дней назад

    Akubwela bho

  • @kearabetswemashego3084
    @kearabetswemashego3084 Месяц назад

    Tukamulane bas mayi

  • @alfrededwinmadziataika5869
    @alfrededwinmadziataika5869 Месяц назад

    What about *Michael Usi*...when we say he's a MCP member are we wrong?.

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 Месяц назад

    Mesa munathawa Inu mwabwera 2019 cholinga anthu azakuvotereni akuba Inu mai

  • @chesterphiri7523
    @chesterphiri7523 Месяц назад

    And this has now put Manganya in a very difficult situation 😂😂😂😂

    • @JonesChingaya-yf4gg
      @JonesChingaya-yf4gg Месяц назад +1

      Manganya dyera ndimene yamukulira, koma m'mene zinakhalira muja munthu wa nzeru komanso weniweni wa Utm sakanalora u VP.

    • @chesterphiri7523
      @chesterphiri7523 Месяц назад

      @@JonesChingaya-yf4gg my thoughts exactly, I think that he knew something that we don’t know before Chilima’s death.
      And he doesn’t have political capital so MCP can not keep him come next year.
      The best he can do is to eat and get the benefits of a Veep unless if something unforseeable happens to the incumbent president otherwise no political future

  • @user-uf7xt6gp7v
    @user-uf7xt6gp7v 29 дней назад

    Ndi movie imeneyi.ali limodzi ndi mcp

  • @SimeonAbraham-u2j
    @SimeonAbraham-u2j Месяц назад

    Chakwera ndi mayiwa chakwera akuchepa

  • @ChifundoKaunda-m7k
    @ChifundoKaunda-m7k 29 дней назад

    Tsogolo lathu

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf Месяц назад +1

    mayi inu ndi achitsiru satananso chigawenga iwe

  • @kelvinmphande3754
    @kelvinmphande3754 Месяц назад

    My beloved president