MA NURSE NDIMA DOTOLO MALAWI YONSE ATHA KUNYANYALA NCHITO POSACHEDWAPA kamba kavuto lama allowances.

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 17 май 2024

Комментарии • 35

  • @patassonelucaszovuta3431
    @patassonelucaszovuta3431 Месяц назад +4

    Mdalama akupatsa apolice kuti akasake wa bakili muluzi tv malo molipila anthu awa

  • @user-ov2kf9tu2z
    @user-ov2kf9tu2z Месяц назад +4

    Ntchito yathu ndiyotopesa,especially Night shifts,chonde hear our cry ,ndalamazo zituluke

    • @jumbradoone4164
      @jumbradoone4164 Месяц назад

      Tidakupatsanikale mu COVID, ndite amene yamuchepepa ndalama asiye,
      Kunjaku alipo ambili akufuna ntchitoyo.

    • @chifundokapulula8962
      @chifundokapulula8962 Месяц назад

      Very true...

  • @user-ev6bi7jr7g
    @user-ev6bi7jr7g Месяц назад

    Komanso inu ma doctor mukuyenera nso kumawauza zoti kuchipatalako nso kulibe mankhala

  • @webstermbewe8395
    @webstermbewe8395 Месяц назад

    Thanks 🙏👍

  • @Blessings-td4cr
    @Blessings-td4cr Месяц назад +1

    Akudya banzi amenewa akhala pansi,,ma mafiya alipo they are planning kuti awaphwetse.

  • @MadaloMalonda
    @MadaloMalonda Месяц назад +1

    MoH....try to listen to our health workers &help them accordingly, it's not good to have deaf ears

  • @chimwemwechiundira6002
    @chimwemwechiundira6002 Месяц назад

    Overworked , undervalued. No wonder Malawi has the poorest healthcare in the world 😢

  • @user-te3ps3kf2t
    @user-te3ps3kf2t Месяц назад +1

    Brian ntchito yosamalila miyoyo ya anthu si ntchito yophweka,ayenela kuyakhidwa mwachangu,ndipo ngati sakuyakha ayenera kutenga action,ndipo anthu otelewa ndiosafunika ma office antchito zaboma

  • @leonardngala6148
    @leonardngala6148 Месяц назад

    Moto buuuuuu.......ndangokhala pakona kudikira sit in

  • @lotrixrabsonoffen7368
    @lotrixrabsonoffen7368 Месяц назад

    Akulu akulu awa they are intelligent in their own field of study but i think there is a reason why they are not PRO's...or negotiators, literary akulephera kuyankha mafuso pano. simple question, do you have an answer for your proposal? if not why telling their followers kuti Boma has agreed to their demands. they just want to look good to their followers

  • @bayanimponda8746
    @bayanimponda8746 Месяц назад

    Ndipo amene akuti anthuwa adya bans akulakwa kutero. Government is playing tactics of delay.

  • @lloydchimtowe7880
    @lloydchimtowe7880 Месяц назад

    Brian musalimbike za salary ya May. Mupangitsa kuti salaryo isalowe. Honestly the agreement letter in this case equals the settlement agreement.

  • @dastanthindwa6372
    @dastanthindwa6372 Месяц назад

    Brian ,you must improve on conducting interviews ...😊

  • @OliveLiwonde
    @OliveLiwonde Месяц назад

    Wawa

  • @user-ev6bi7jr7g
    @user-ev6bi7jr7g Месяц назад

    Ndalama ndizimene akumwaza m'misonkhano zija koma zoona matama onse aja madokotala sakulipidwa😮😮

  • @chifundokapulula8962
    @chifundokapulula8962 Месяц назад

    These guys are not serious as the increases come from Treasury n have a direct bearing on budget numbers. S

  • @ChikumbusoKhumba
    @ChikumbusoKhumba Месяц назад

    Komaso buran iweyo umayiziwa tchitu yachipatala zakazi ndiiz ndizosiyana

  • @user-pj7hn2ky5j
    @user-pj7hn2ky5j Месяц назад

    Mmmhhh guys athuwa amagwira ntchito yolemesa kwambili .kodi m'boma mukufuna athu amwalire kaye then muzibwera zithu zitavuta kare???shame on you malawi government

  • @maliyamumagiya5325
    @maliyamumagiya5325 Месяц назад

    brain upolo moto musalangulise anthu pambali mwafa

  • @fraserluwemba6364
    @fraserluwemba6364 Месяц назад

    Ndiye wamwano ndi ndani pamenepa

  • @NumbDee
    @NumbDee Месяц назад

    Awapatse zawo anthu awa amagwila tchito yotamandika

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Месяц назад

    Kkkkkkk Brian musatsamwitse anthu😂

  • @RebeccaWalusa-lb5yi
    @RebeccaWalusa-lb5yi Месяц назад +2

    Kodi mukuwapanga chochi madokotala chifukwa mukadwala mumapita zipatala zakunja zipangani koma choyambilira mukanaganiza kuli anthu alibe kalikose pompano muwafuna mulungu akudaliseni zigawani ndalamazo

  • @fraserluwemba6364
    @fraserluwemba6364 Месяц назад

    Kwayaka moto kuti buuu

  • @DanMhone-iw6xg
    @DanMhone-iw6xg Месяц назад

    Brain usawatopese makosanawo please si anthu andaletu awa chepesani moto please

  • @richardmagombo6647
    @richardmagombo6647 Месяц назад

    Dziko la malawi timgosithanisa ndi chigubu cha kachaso 😹😹😹

  • @Nathkala997
    @Nathkala997 Месяц назад

    Nkhani ya mkazi as a classic example in this isuue isn't relevant coz u are not related in any way ..... Auzeni a boma not to give a deaf ear to these unions muphesa nazo anthu osaukafe pomwe inu muzinyamuka wa maiko akunja

  • @user-nl5nk2wx1q
    @user-nl5nk2wx1q Месяц назад

    KOMA MALAWI WAVUTA

  • @kondwanimunthali7401
    @kondwanimunthali7401 Месяц назад

    Think of poor Malawians before going for a sit in

    • @liki-likiladies---lilongwe6963
      @liki-likiladies---lilongwe6963  Месяц назад

      Them too are poor Malawians!
      They have a family to bring up.
      They should listen to them.

    • @hastingskaira324
      @hastingskaira324 Месяц назад

      Even health workers are poor Malawians, let the government think of all poor Malawians

    • @hastingskaira324
      @hastingskaira324 Месяц назад

      Even health workers are poor Malawians, let the government think of all poor Malawians