Zoona zeni zeni za kumangidwa kwa Evance Meleka atayamba nyimbo ya chigawenga

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 7 июл 2024

Комментарии • 28

  • @user-hh4wn4vf9e
    @user-hh4wn4vf9e 16 дней назад +1

    Inuyo a social media ndamene mupange zamanyi kwambiri nyimbo lmeneyo ndiyakare

  • @LeooTungama
    @LeooTungama 17 дней назад +2

    Mmmmmh kodi azingomanga anthu aboma wo

  • @fannychibwana1776
    @fannychibwana1776 16 дней назад +1

    Mabodza basi,anthu mumasowa zochita bwanji hiyaaaaa

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 17 дней назад +1

    Sanamangidwe musamafalitse zopanda umboni weniweni

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 17 дней назад +1

    Iwe ndi boma Pali ubale wanji opha achina chilima machende anu iwe ndi boma😢

  • @IssahAluba
    @IssahAluba 16 дней назад

    nyimbo ndikupeka Muthu umanena zomwe zizachite kapena zikuchitik

  • @ThokozaniBondo-em9fr
    @ThokozaniBondo-em9fr 17 дней назад +2

    😂😂😂😂Komatu timangidwa ambiri chaka chino

  • @thapelokasawala5192
    @thapelokasawala5192 15 дней назад

    Koma munachita bwino kusankha kuyimba nyimbo imeneyija😎

  • @cynthiakananji1608
    @cynthiakananji1608 17 дней назад

    Anthu sangakambe zabodza, anthu tu amakukondani koma mukamanama mwachitsa anthu chidwi chokukondan, chigawengadi chouma mmtima chinapha chilima osalakwa

  • @JackMlenga-j2t
    @JackMlenga-j2t 10 дней назад

    Mmmmmn mabodza bas

  • @HarryKandani
    @HarryKandani 17 дней назад

    No smoke without fire....mwina anakutoladi koma akutaya

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q 16 дней назад

    Chitukuko chili dziko Muno ndi kumanga anthu kkkkkk😅😅😅

  • @yowasschitsosa5348
    @yowasschitsosa5348 15 дней назад

    Amen

  • @SamsonSamson-gh6gs
    @SamsonSamson-gh6gs 16 дней назад

    Evasi maleka ndi munthu yemwe amaganiza mwakuya akafuna kuyimba nyimbo ndipo iyeyu ndi doro

  • @user-nb8wg3fh4u
    @user-nb8wg3fh4u 16 дней назад

    Achisilu evasi akupasa ndalama galu ubale wake uti

  • @dumisanimoyo3152
    @dumisanimoyo3152 17 дней назад

    Usatero kuti ubwino wako ndiboma ndiwabwino kwambiri kumbukira chiloma ndiboma unaliso wabwino kwambiri

  • @Mohammed-sk1fy
    @Mohammed-sk1fy 17 дней назад

    Eeeehh Zosayenda ndthu

  • @piousamidu1419
    @piousamidu1419 17 дней назад

    Inutu muli ndi vuto.. wamangidwa liti

  • @SautsoKandama
    @SautsoKandama 16 дней назад

    Boooodzaaa

  • @GladysKapasula-x6w
    @GladysKapasula-x6w 17 дней назад

    Anthutu amafuna kuipitsa mbiri zazawo

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf 17 дней назад +1

    chakwera ndi chigawenga ndi zoona criminal presdant in africa chigawenga cha kwera

    • @philemontitusnkhoma7740
      @philemontitusnkhoma7740 17 дней назад

      Anthu a DPP ndinu oipa kwabasi. Kuteroku kuyetsetsa kuti boma likhale loipa oipa muli inu amene. Mulungu Wathu Sakusiyani choncho. Mumidziwa Mulungu Wathu kuti Ngodana ndi Mabodza.

    • @AlexKaunda-ny2eg
      @AlexKaunda-ny2eg 17 дней назад

      😂😂😂 chakwera nyini yamake Ngati vuwu

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q 5 дней назад

    OK UYUSO NIUBARE.NI BOMA.TIKUPEPHASO BOMA KUTI RIMUPHE NAYESO

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 17 дней назад +2

    Koma wasala pang ono kumangidwa ameneyi

  • @user-rz9rm4cb8x
    @user-rz9rm4cb8x 17 дней назад

    Ndiopusa ubale ndi boma

  • @EsnartGirivin
    @EsnartGirivin 17 дней назад

    Zabodza izi

  • @AnaffSayamika-uh6vg
    @AnaffSayamika-uh6vg 16 дней назад

    Km kumeneko