Asiyeni awo, akuputa kwiyo chabe, kwa Yehova wathu ndi chakwera wa woyo azibambo Ambuye a zikuza malile anu, mumayakhura chilungamo inu, kuti chiyende ngati madzi aziwona amenewo Mulungu wathu. awakatha ndithu, ndipo mu Dzina la Yesu 2025 mu September mo sawina awa a mcp
Time's Radio Station that's the only & Powerful Media Sector that are still remain on justice
Very powerfull message,, azibusa opusa kwambiri and achititsa manyazi dzina la YEHOVA
Kma abusa ometa mbalimo angalangize bwanji mpingo😂😂😂😂😂
@@LennieNyirenda-w6p za masiku omaliza
😂😂😂😂😂 madolo inuyo mumatha
Ikwiye zenizeni ngati mmene mwakwiyila mbuli inu zaziiiiiiiiiiiiloooooooo zakumidima basi 🤣🤣🤣🤣
😂😂😂😂😂😂😂😂 awuzeni zowona zeni zeni adziwe kuti salufunika ulamulila malawi mbava zimenezo 😂😂
Azibusa akumidima 😅😅😅😅😅😂😂😂Chikangawa midima party 😅😅😅😅😂😂😂
Koma zomati ndinu azipembedzo musali achipembedzo, mutha kuipaaa kwabasi, Mulungu satsibweni anu😢
Rest in peace sk
Kmtu guyz iyiyii imakwanira heavy 😂😂😂😂😂
Mbava zazibusa msusa is true man
Musatchula dzina lamulungu pachabe...musapereke umboni wonama ...chakwera ndithu ako mizimu ya athu 9 yakwiya eroding saulosi Kraus chilima ...may soul in peace😢😢
Anapanga meeting before this
Mbava ndi ma hule awa osalimbana nazo
Rest peace skc ambuye azaweluza
Kkkkkk iweyo ayi umatha kkkkk
Mbava izi😪
Achini abushiri awo
Anawatuma ndi namachende chimwendo munthu oipa ntima uja ambuye mukutisungila mfiti imeneyi mdziko mwathu pls abeg zachitengeni chatitopese ife
Chakwera sadzayupezai
Usatchure Mulungu wakonpachabe munawerengako koma maguys inu
Azibusa wojiyawa 😂😂😂😂
Zidakwa izi , amafuna ya Kachaso
Asiyeni awo, akuputa kwiyo chabe, kwa Yehova wathu ndi chakwera wa woyo azibambo Ambuye a zikuza malile anu, mumayakhura chilungamo inu, kuti chiyende ngati madzi aziwona amenewo Mulungu wathu. awakatha ndithu, ndipo mu Dzina la Yesu 2025 mu September mo sawina awa a mcp
Video ili kuti?inde a Malawi akudziwa Kuti Chilima adachita kuphedwa koma content isamasiyane ndi zomwe tikumvera kapena kuonela zokhazo zichepe
Go deeper guyz
chilungamo chiyende basi osatengera zipembezonso pano
Title kumasankha bwino anthu azakukhulupililani mzolemba zanu
Zitsilu za atsogoreli amipingo nyasi zawanthu devil's zitsilu kwambiri
Isn't still kuyankhula izi guys,,, tiyeni tisiziye mmanja mwa mulungu
Ma vidio yo alikuti
Mlungu atiyankha nthawi yakwana yokha
Anapatsidwa ndalama anthu awa you can see there faces
Amakhala osasambanso sasowa ayi mbuzizaanthu
Atola nkhani amasiku ano amatenga mbali
Kkkkkk
Eee km anyamata inuyo eti eee anakonza
Chinatumacho mchopepela , Chimwendo
😂😂😂😅
Inuyo nokha musakavote Msusanso alapenso mabodza ngatinso inunso ngozi ya ndege imachitika ndithu koma chonde chonde musamayense kuti maliro ndichinthu choseweretsa kapena chomati aDPP azikutumani nkumawachitira kampeni poti sindinu atolankhani koma ,macadet
Kkkkk
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Chipani cha mcp chatha mzeru thats why akupanga zoterezi chakwera is finished no matter what ngakhale azigwilitsa ntchito kuti aziyeretse koma sigwira madzi achita katondo basi.
😂😂😂😂😂😂
😂😂
😂😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
😂
Ofunika akalapedi kwambili izi nzopusa apangazi
Kufuna kupeza ma subscribers with fake headings?? Poor channel
Where is the video? Don't lie to attract attention, nkhani iyiyi siyosewelesa bwana.
zomalemba mutu wa video wina content ya video ili ina ndi utchisiru, kufuna attention??
Kkkkk