Inshort , Every member of MCP is a criminal , And you know what my brother , lf MCP Will continue to ruling Malawi , l'trust you problem will be come worse than this , Every one knows MCP from the back ground , Even Chakwela is already criminal like the late kamuzu banda .
Pafuka usi pali moto zakuphedwa kwa witika mitima yaanthu ikubaya pa kunkuyu ndiponso idzi ndi zoona zake kupha munthu chifukwa cha nkadzi kunkuyu zoona ? Iweyo ukudziona nkhati ndi wa muyaya ?
Pamene papitira mzimu wa munthu mulungu sangakhare chete. Apapa ndi mkwiyo wa mulungu tsopano .......... ndipo zazikulu zichitika Kafunseni moses wa m'buku loyera atapha mu iguputo. Mulungu amakonda aliyense and there is no secret under the dzuwa
Moses kunkuyu ndi chigawenga kupha munthu chifukwa amanyengana ndi bwenzi lake munthu oti makolo ake anabvutika kumuphudzisa mpaka ku collage ndicholinga CHOTI adzakhale pabwino iye kutenga mfuti kumupha mirandu mpaka lero kuli ziii makolo kwasiya manja Ali mkhosi Mulungu mbuye wazolengedwa zonse achite nawe kanthu
Sanali mkazi wa kunkuyu anali bwenzi lake nkazi anapanga chisankho CHOTI ndibwino ndipeze mamuna oti andikwatira and kunkuyu was told that anamuuza kuti iweyo uli ndi nkazi nkukuyu insisted that mpaka kupanga upo ndikumupha is that fare? inuyo mukhozanso kupha?
anthu omenyera ufulu amadzidzula mwanzelu koma mpaka omvera kufika poboweka nanu ndikupaseni chisanzo uyu wa bakili tv amaponya ma odio patali patali anthu amamutsatira kwambili, koma enawo mmmmhu kungokhara ngati sima yamasana yakumudzi aaaa
Ndizoonadi ineso ndakhala ndikukamba kt kunkunyu ndamene anatuma nyamata uja kt akaphe witika muthu ameneyu galu kapena kt fiti yokumwa magazi
Nzoona kumkuyu anapha witika
Ndiyemwe anamupha Witika
Kumkuyu ndi main killer wa Witika motsazembetsa mau
Tikudikila Boma Ili lidzachoke kaye kunkuyu adzayankhe mulandu, Big up
Ayitu koma akupanga zoti akamugwile m,nyamata wa bakili TV amangidwe koma okuphao ayi ndiamenaso akumpangitsa kuti athu azimangidwa osalakwa
Amukhululukilaso aaa
Panali Gospel Kazako 😢😢😢😢😢😢
Mvuto ndi utsogolire tilibe
Good message zoona Mosess kukuyu ndichigewenga
Kma Mulungu ndi Mulungu ndipo magazi amunthu ndiopsa ndipo Mulungu awakathe onse amene anatenga gawo
Wakupha ameneyo amangidwe
Galu ameneyi asamale kwambiri
You have spoken well
Kumkuyu mphavu zachulukila but one day is Coming mphavu zizatha
Ndipo kwambiri tu mmm
Well spoken bro
Keep up brother 👍👍💪
Will do!
Chilungamo bro
Ameneyi ndi savage kwabasi kupha nzake chifukwa cha chibwenzi
Inshort ,
Every member of MCP is a criminal ,
And you know what my brother , lf MCP Will continue to ruling Malawi , l'trust you problem will be come worse than this ,
Every one knows MCP from the back ground ,
Even Chakwela is already criminal like the late kamuzu banda .
Kumkuyu ndi chisiru akuona ngati akuanja kwa witika ndi opusa sakumva kupweteka ndi imfa yambale wawo tikanakondwa kumkuyu akafa nayenso
Aboma muchitepokanthu
Big up Brother
Ndipo live mkumkuyu Nd ch criminal
Kumkuyu mfiti yodya maliro
nsiyeni galuyi kunkuyu ayankha pompano agalu amenewa akachoka chaka chamawachi
Akadakhala kuti ndi munthu osauka opanda dzina bwezi pano ali mndende chilungamo chitayenda
And nkhani iyiyi ndiya Agnes katengedxa yoyamba ndiimeneyi .koma Ya Agnes katengedxa inatha kalekale mutu weni weni unadxiwika chifukwa oganizilidwayo wakunja kwaboma ....... and nkhani iyiyi ikanakhudza munthu.yemwe ali ku opposition kalekale chigamuro chitapedxeka
Kobisika tikaona 2024
Big up bro,mw too much corruption
Ndipo zoona
Ndakumva bwino aisee
Big up
Mawu amphamvu awa
Naye azafa imfa yowawa ndithu Mlungu alipo
Nayeso aphedwe ndi galu
Zoona big nkhani yomweyi kuti alankhule born kalindo aziti watumidwa ndi dpp what is that
Koma asaone kuti ndiiye ochenjera, Sakudziwa chomwe chikumutsata
Umakwana big man tell them straight
Kunkuyu ndiye mwini wa case ija chilungamodi
Kumkuyu Ali involved kumene munthu woyipa uyu.. Mzimai amene uja anamuopseza kumene. Ma Judge agwira njakata ndipo makhothi kulibe kuno. Nkhani ndiyowona akamupeza witika akumudikila....
Ndipo kwambiri tu mmm
Kunkuyu ndigalu kwambili
Bro loweranipo athandizeni family ya witika
Pafuka usi pali moto zakuphedwa kwa witika mitima yaanthu ikubaya pa kunkuyu ndiponso idzi ndi zoona zake kupha munthu chifukwa cha nkadzi kunkuyu zoona ? Iweyo ukudziona nkhati ndi wa muyaya ?
No justice in this government
😂😂😂😂😂 ayalutse akuyamba dala
Soona big
❤❤❤
Timadziwa kuti anapha ndiy
It's true my brother simukunama
Pamene papitira mzimu wa munthu mulungu sangakhare chete. Apapa ndi mkwiyo wa mulungu tsopano .......... ndipo zazikulu zichitika
Kafunseni moses wa m'buku loyera atapha mu iguputo. Mulungu amakonda aliyense and there is no secret under the dzuwa
Kukunyu ndigalu kwabasi adzamangidwa
Inenso ndinalandidwa mkazi ndipo amene anachita izi komanso mkaziyo tsiku lina adzaona zoopsa.
Christopher kabanga akanakhala m,bale wako ukanatani
Ndipo Inu
Very true
❤😂😢
Moses kunkuyu ndi chigawenga kupha munthu chifukwa amanyengana ndi bwenzi lake munthu oti makolo ake anabvutika kumuphudzisa mpaka ku collage ndicholinga CHOTI adzakhale pabwino iye kutenga mfuti kumupha mirandu mpaka lero kuli ziii makolo kwasiya manja Ali mkhosi Mulungu mbuye wazolengedwa zonse achite nawe kanthu
Muphunzire kulemekeza akazi amnzanu
Sanali mkazi wa kunkuyu anali bwenzi lake nkazi anapanga chisankho CHOTI ndibwino ndipeze mamuna oti andikwatira and kunkuyu was told that anamuuza kuti iweyo uli ndi nkazi nkukuyu insisted that mpaka kupanga upo ndikumupha is that fare? inuyo mukhozanso kupha?
Pitani court kaperekeni umboni,,
Mboni idagwidwakale ukufuna mboni yanji?
Khaniyi ndiona
Mcp ikagwa mulandu umeneu udzazengendwa panopa sangauzenge adaukhalila si nanga ukukhudza munthu wankulu
Ngat iyeyu salandipo chilango pakupha witika ,iiiiiii afa imfa yachabe chifukwa abale ake sangangokhala chete zophwereka kumuombera mkamwa witika zoona chifukwa chamkaz inu chani ichi ? Mundilore uyu ndimuombezere afere kutulo kumkuyu ngat kumanda kumasangalako kumkuyu amupiteko akasangalalareko
Thawi zinatu pa mudzi timambilana akuti anja ndi mfiti koma kodi zimakhala zoona? Apa pakuonetsa kuti anthu muli ndi umboni pitani ku police
Police Yake it yaku malawi😢
Police kulibe ilipo ndi pioneer.
Police yikupasidwa mabanzi mamawa uliwonse anayiwala ntchito zawo
lnu mukuyankhura kwambili ngati bon kalindo mufuna musonyezeso umbuli ngat kalindo aaaa
Is winiko mbuli? Tambasula tanthaudzo la mbuli
kodi munthu wanzelu kapena oganiza mozama angamaponye ma odio tsikulililose ngakhare kuti akumenyera ufulu koma zina amalankhura zopanda phindu zosatukura malawi
anthu omenyera ufulu amadzidzula mwanzelu koma mpaka omvera kufika poboweka nanu ndikupaseni chisanzo uyu wa bakili tv amaponya ma odio patali patali anthu amamutsatira kwambili, koma enawo mmmmhu kungokhara ngati sima yamasana yakumudzi aaaa
Za boni lalindozo siyani,coz samakutimani kut muzimvera,muli ndi ufulu osamamvera ,ine ndie ndimadwalatu bon kalindo akapanda kutumiza audio data ndi dinyanya
Utha kukhala mbuli iweyo koma sukudziwa.
Ufumu ukazatha azapheka khoswe apa ali bzy kulimbana ndi bakili muluzi TV shame on him wabisala mbataya msana wawonekela uyu
Vuto lama judge akumalawi ndiloti amazenga milandu ndikumanga anthu osalakwa, akuBa ndi akupha ali muboma momwemo, maganga wantchito wakumkuyu yemwe anapha Witika pogwiritsa ntchito mfuti ya mozes kumukuyu nayenso akuyenera aphedwe, musamangolimbana ndikumanga anthu osalakwa, kulibe chilungamo kumalawi