CHILIMA FORETELLS

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 8 сен 2024
  • Edited and Graphics by Chimwemwe Nkhata

Комментарии • 20

  • @CathrineBizza
    @CathrineBizza Месяц назад +1

    Ngati ndilire aaaa Koma

  • @peterchikwakwa8476
    @peterchikwakwa8476 Месяц назад +1

    Munthu uyuyu anachita kukonzeredwa chipongwe chophedwa

  • @daviesedward3229
    @daviesedward3229 29 дней назад +1

    Koma eish mcp zoona osayamika ntchito zonse zimene Chirima anagwira. Kupha Great and Model leader skc . Mcp inaphanso Mr Aaron Sangala- Dick Matenje - Atate Mpakati- Kanyama Chume - Muwalo plus Henry Chipembere - Sidik Mia - Ralph Kasambara and many others. We hope kuti Mulungu ationetsa ukulu wake poononga ndi kulanga mcp ndi Chakwera..... Pa maso pathu ndipo maso athu akuonelera.. monga mmene anamuchitira faraoh ndi asilikali ake.

  • @user-co3wr3rn4h
    @user-co3wr3rn4h 11 дней назад

    Munthu uyu uyu mhuuu mcp zowona pakana kumupha nyamatayu mhuu

  • @lovenesskampira
    @lovenesskampira Месяц назад +1

    Masomphenya anapitaa

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe Месяц назад +1

    Mwatisiya osati mwatosiya

  • @user-td6qe4gr6w
    @user-td6qe4gr6w Месяц назад +1

    Abwino sakhalitsadi, zoona

  • @JevinTeller-en9rh
    @JevinTeller-en9rh 8 дней назад

    Mmmmm😢😢😢😢😢

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe Месяц назад

    Tikimva kuwawa kutisiya kwanu a chilima yee!! Koma inuyo munatipitsa ku phatikana ndi chipani ca kuphachi cha mcp .pano mwatosiya pa mabvuto oopsya .kumeneko mzimu want utichotse mmanja mwa ng'onazi.zakuohazi zi manja a chakwera and mcp party .members

  • @HamzaMangoch
    @HamzaMangoch 2 дня назад

    😢😢😢

  • @gracemkandawire8769
    @gracemkandawire8769 Месяц назад

    Chikhala plugs amadzuka,,tikanati adzuke Kwa chaka chimodzi chabe..Rest in peace SKC

  • @NearBanda
    @NearBanda 28 дней назад

    Ngat boza skc mmmmm😢😢😢😢😢😢

  • @niahyiwombe9140
    @niahyiwombe9140 Месяц назад

    Masomphenya aja anapita

  • @YamikanChirwa
    @YamikanChirwa Месяц назад

    Km ifa ifa ifa bwanj km

  • @JohnstonNyirenda-zw6jd
    @JohnstonNyirenda-zw6jd Месяц назад

    😭😭😭😭💔💔💔💔

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe Месяц назад

    Tikumva not tikimva

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg Месяц назад

    We lost a patriotic citizen