Ndan Yemwe Wapopa Manganya Kuyambisa Chipani?

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 4 фев 2025
  • #politicsnewstoday

Комментарии •

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w 8 дней назад +11

    Manganya ndi chitsilu kwambili yudasi anamupeleka chilima

  • @MikeGomani-tb9np
    @MikeGomani-tb9np 8 дней назад +7

    Kukubweraku aliyense akhala ndi chipani pakhomo pake😂😂😂😂😂

  • @GloryNkhwazi
    @GloryNkhwazi 7 дней назад

    Zankutu bas mabi eni eni 😂😂😂😂😂zaziiii akakhuta mang'ina atinyasepo apa fotsekii

  • @AmosShadreck
    @AmosShadreck 8 дней назад +2

    😂😂 chipani chazimai

  • @ChristinaMshane
    @ChristinaMshane 8 дней назад +1

    😂😂😂😂😂 tchaiii ku malawi anthu aphana ndi ndale😂😂😂😂

  • @BistonMacheso
    @BistonMacheso 8 дней назад +4

    Anthu akumulanje Mitu sikukwera koma ifeyo alomwe sitimapanga zimenezo 😂😂😂😂😂😂😂manganya ndi nakhumwa anthu amenewa khaya anachokera kuti khaya

  • @HenzoniceMW
    @HenzoniceMW 6 дней назад +1

    Uyuyu ndiwa Mcp akungofuna kuchepesa chiwelengelo Cha dpp ndi utm cholinga Mcp izaduse moyela

  • @Chitani100
    @Chitani100 8 дней назад

    Hahaha manganya ndi iwe chitsilu aaaw😅😅

  • @AllanNenan-c3w
    @AllanNenan-c3w 4 дня назад +1

    akufuna kt kummwera kukhale zipqni zambiri cholinga adulirane number ya anthu cholinga dpp izalephere

  • @charitymhone9983
    @charitymhone9983 7 дней назад

    Mmmm angawine Awa, support alibe ngati chinalephera chipan cha chilima ku wina iwe ndiwe ndani kandondocha ka chakwera iwe😮😮😮😮 unapha chilima, ukanapangitsa colour yako ya green not za anzako, kuchikamwa😮😮😮

  • @WysonChilonga
    @WysonChilonga 8 дней назад

    kkkkk awanso ndi a kape kwambiri,kukula mtima ngati ali ndi manyi pakhosi

  • @clairemyegha4315
    @clairemyegha4315 8 дней назад +3

    Ndiye osabwera poyera ndichani kumazembera mumbali. Pawoka sangapange ndale ndizobvuta. Why sanapange green color ya odya zake alibe mulandu.

  • @Hambalisphiri
    @Hambalisphiri 6 дней назад

    Tiyeni nazoni si amakuchememelelani mukamavina dance nde mukuona ngati mwafikapo kkkkkk or dzina la chipanicho kuchita kuwoneka kt saliyekha mulandu ulipo ndithu

  • @JaphetSakala-u5j
    @JaphetSakala-u5j 7 дней назад

    Zangoyamba kuziwika kwa anthu SOPANO ZOMWE bwana a isi amaganiza koma akulu akulu achipani cha UTM anazitulukila kale kuti awa cholinga chawo kunali kusokoneza chipani. Apaso sanati ngati yudasi anazipachika yekha nawoso awa muwawona. Kuti Malawi aziwe kutidi awa anapeleka zawo uja

  • @IssahBwanali-i8w
    @IssahBwanali-i8w 7 дней назад

    Manganya chipanichi sichanyuwani ayi anayambisa kale chilima asanafe manganya poyambilila anapanga ngwilizano chapani chake ndicha chilima

  • @AlfredGanizani-v9f
    @AlfredGanizani-v9f 5 дней назад

    Wachita bwino kutuluka awasiire akaporowo ubwino uss sikaporo

  • @AbeckKalongonda
    @AbeckKalongonda 7 дней назад

    Uyu ndi mpaka kwabasi odya zake colour inali ya green lero yasanduka red kkkkkk mbuzi yamunthu

  • @StellaMichaeal-h8i
    @StellaMichaeal-h8i 7 дней назад

    Musiyeni usi Mesa anamuchotsa Ku UTM

  • @HarlodLemwe
    @HarlodLemwe 7 дней назад

    wachita bwinotu mesa ku UTM anamuchosa nde vuto ndichani

  • @ChisomoMakanda
    @ChisomoMakanda 8 дней назад +2

    Ithink usi is a genius

    • @FrancisNyayi
      @FrancisNyayi 8 дней назад

      Ndipo better apite yenkha awina

  • @EstherChipondo-g7e
    @EstherChipondo-g7e 8 дней назад +1

    Malawi akuonesta kuti chikondi chidatithawa dziko lochepa koma zipani mbweeeeee ine zimenezi zikundinyasa ndithu

  • @stevietungama9775
    @stevietungama9775 6 дней назад

    Koma mulanje central mpaka zipani zitatu constituency ya anthu adyera

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 8 дней назад +1

    HlS exllent professor Peter muthalika
    The president of the republic of MALAWl 🇲🇼🇲🇼🇲🇼 2025 to 2030
    Chuluke wazipani koma zikoli likufunika professor basi .

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 8 дней назад +3

    Anthu akumulanje amitsala OKHA OKHA kunalitso pinganjila apa ali ku MCP nankhumwa MANGANYA otsewa a MCP agalu KWABASI

  • @wysonmpatama4393
    @wysonmpatama4393 7 дней назад

    Chiikangawa Pali winanso

  • @Rasheedissa-f3q
    @Rasheedissa-f3q 8 дней назад

    UTM iphangepo nkandu asumilleni manganya 👊👊👊

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi 8 дней назад

    Malawi can be ashamed manganya akaputa yenkha ndipo antha kuwina uyu

  • @ChrissieNyasulu
    @ChrissieNyasulu 7 дней назад

    Alliance y ujeni iyi , ndani sakudziwa.

  • @Eqrah-hj2nu
    @Eqrah-hj2nu 8 дней назад

    BAMBO A SIKONO
    AZIPITA KU ZIMBABWE AKAJOYINE ZANUPF

  • @WalikoKaponga
    @WalikoKaponga 7 дней назад

    Tirinaye limozi not DPP

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 7 дней назад

    UYU NDI WAMISALA CHAKWERA AKUNGOMUGWIRITSA NTCHITO KOMA PALIBE ANGAMUSATILE ANTHU AKUFUNA KUNGOMUDYERA

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 7 дней назад

    Woyipa Zimbabwe ameneyu

  • @DuncanMbulo
    @DuncanMbulo 8 дней назад +2

    I blame saulos chilima

  • @mabvutomichaelpanagona1949
    @mabvutomichaelpanagona1949 8 дней назад

    Wapopa manganya ndi chikangawa anthu amene adzavotele manganya wa votela MCP

  • @AlfredHaji-h1d
    @AlfredHaji-h1d 5 дней назад

    B13

  • @stevezulu2108
    @stevezulu2108 6 дней назад

    Kusokoneza anthu apa kuli 50- 50.okalamba sadza siyanitsa po vota.

  • @BashilDaud
    @BashilDaud 8 дней назад +1

    Okudya zake alibe mulandu ndiyakalekale ngakhale UTM isanayambe km nkhan ikhale ya colour chfkwa panthawiyo makaka ake anali a green

  • @StoneckJali-s3n
    @StoneckJali-s3n 7 дней назад

    Usi ndi oopsya muvutika naye simu ati

  • @BuggyMw
    @BuggyMw 7 дней назад

    Wazinva koko ma za zalama zaboma

  • @landsurveyor-y8s
    @landsurveyor-y8s 8 дней назад

    Ku mulanje anathawako manganya ndipo last election anali pa 3rd position, pa 2 panali kondwani, pa 2 panali Damson Chilewani, 3 panali iyeyo ndipo pa 4 panali mayi oti anthu amamukondanso, and remember this is the same constituency yomwe Brown Mpinganjira anayimira

  • @BernardKalongah
    @BernardKalongah 8 дней назад

    Mbuyache mayikolo usi watopa kuyamwa magazi amchipani chija choweta ng'ona , wachita bwino wayambisa chake ,,,,,

  • @Gchrinah
    @Gchrinah 6 дней назад

    Kkkkkk ase umaniwaza

  • @AbdulrazaqHussain
    @AbdulrazaqHussain 7 дней назад

    Chipani cha manganya, chinayamba 2012, chinazilala posowa support, this year, wafikanso pa ground to boost or to amplify chakwela movement, my appeal to my fellow malawians, don't be fooled again, he is up to no good, keep your eyes on the ball, rise Malawi rise!!!!!

  • @LeonardNgambi-q2y
    @LeonardNgambi-q2y 8 дней назад

    Chipani cha azimayi chikupita ku alliance ya MCP

  • @HamidavioletYassin
    @HamidavioletYassin 8 дней назад +1

    Jacob juma wakumalawi kkkkkk

  • @Bashir-g1t
    @Bashir-g1t 8 дней назад +1

    Ku Malawi kwachuluka drama serious

  • @EbrahimZahra-f4r
    @EbrahimZahra-f4r 8 дней назад +1

    Mmmmm koma kadziko kamalawi

  • @edwardlucius7316
    @edwardlucius7316 7 дней назад

    Saulos chilima ndiye chitsilu kobasi Lazarous ndi one

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 8 дней назад +3

    Palibe wamupopa koma ndiwamisala

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 8 дней назад

    Manganya alibe molalo ndi mwana wa chikangawa asakupuiseni ndichifukwa alibe plan ndi zake nakhumwa ndichifukwa al kupanga msalu dzofana ndi zipani zina koma akunama achepa nazo

  • @tenexchikumba
    @tenexchikumba 7 дней назад

    Kodi za odya zake alibe mlandu ndi za lero?

  • @CharlesNtasa
    @CharlesNtasa 7 дней назад

    Azimayi atipwetekesa chifukwa chotengeka

  • @Princevenasiyo-b4b
    @Princevenasiyo-b4b 8 дней назад

    Colour doesn't matter, what matters are the words, there's no UTM there, so what's long with you DPP and UTM people? Mukumuwopa Dr. Usi eti, vuto a DPP munayimisa nkhalamba and this time ayitchetcha mosavuta anyamatawa.

  • @MussahCassim-o6u
    @MussahCassim-o6u 8 дней назад

    Kkkkk km eeeee 😂😂😂😂

  • @AbdallahYunusu-c8m
    @AbdallahYunusu-c8m 8 дней назад +1

    Don't you know that he started Odya zake before joining UTM?

  • @bellsnampanda
    @bellsnampanda 7 дней назад

    NDALE ZA UKAKA

  • @ChristinaStambuli-q3e
    @ChristinaStambuli-q3e 7 дней назад

    Satana kwake ndi kupha,kuba nkuononga kusongonyeza ...alomwe mwatani kodi?

  • @WisperSaid
    @WisperSaid 6 дней назад

    Ndigaru kwambili

  • @FredsonNelson-p6k
    @FredsonNelson-p6k 8 дней назад +1

    Ndale Zaki Malawi 🇲🇼

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo 8 дней назад

    Nkhumba iyi yandikwana bwanji

  • @AlickBenford
    @AlickBenford 8 дней назад

    Sawina ameneyo akungotaya nthawi

  • @DAGAMAaaaa
    @DAGAMAaaaa 8 дней назад +1

    Ndalama zukoma kudya

  • @TonyMhone
    @TonyMhone 8 дней назад

    Takhala tikunena Kuti uyu ndi Traitor. Chikangawa kuyetsetsa Kuti UTM tithe basi. Wadya Bibi yake yomwe

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn 8 дней назад

    Plan yake ndiyoti kachipani kakeko akalowe Nako mu mgwirizano ndi MCP cholinga Chakwera akamutenge ngati running mate

  • @aaronbanda4494
    @aaronbanda4494 8 дней назад

    Watumidwa!

  • @PriscaBanda-u1w
    @PriscaBanda-u1w 6 дней назад

    Mabvuto alipo

  • @Chisimo-k6j
    @Chisimo-k6j 8 дней назад +1

    m c p yamupopa usi koma akunamakwambili

  • @MartinNgoma-tp2jk
    @MartinNgoma-tp2jk 8 дней назад

    Zazii maiko usi alibe sogolo

  • @Molsonabdul
    @Molsonabdul 8 дней назад

    Ndale it's dirty game sungazivese

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 8 дней назад

    wakhoza,atenge,masapota,a,utm

  • @AlickBenford
    @AlickBenford 8 дней назад

    Waba zambiri ameneyo

  • @CharlesNtasa
    @CharlesNtasa 7 дней назад

    Koma moyo uno

  • @anthonysawa2039
    @anthonysawa2039 8 дней назад

    Kutha kwa dziko

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o 8 дней назад +1

    Chakuvutani ndi chiyani aliyese ali ndi ufulu

  • @BwanaGD
    @BwanaGD 8 дней назад

    Tiana ta chikagawa iti

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 8 дней назад

    kunja kuno kulidi anthu oipa ndaoners apapa

  • @GuifitibiriatiFumbi
    @GuifitibiriatiFumbi 8 дней назад

    Kkkk

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn 8 дней назад

    Akanakhala dolo akadayika makaka ake a green osati kutengera za Utm izi zikusonyeza kuti alibe Chikoka pandale

    • @BeatriceNjunga-dj1uh
      @BeatriceNjunga-dj1uh 7 дней назад

      Anthu mmm! Akadapanga makaka a green bwezi mwati ndi MCP
      Musiyeni Micheal naye ndi munthu

  • @EsnartGirivin
    @EsnartGirivin 8 дней назад

    Omwe akuyenda ndi manganya ndi wa mcp afune asafune

  • @SeventeenSosten
    @SeventeenSosten 8 дней назад

    Kamanganya ndikadolo

  • @SymonBlack-h4g
    @SymonBlack-h4g 8 дней назад

    X
    P
    B

  • @AlfredHaji-h1d
    @AlfredHaji-h1d 5 дней назад

    B13