Tinkanena Lero Si Izi - Bon Kalindo

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 17 ноя 2024

Комментарии • 45

  • @MountainBoys-xx6fz
    @MountainBoys-xx6fz 5 месяцев назад

    😭😭😭😭 zoonadi Mr boni Kalindo Koma woyipa watsikilamo mawu anu tawakumbuka ngati Amalawi 🇲🇼🇲🇼🇲🇼 ubwino wake imfa sisankha osawuka olemera wamkulu Mwana zibambo nyamata tsikana nzimayi wawudindo ngakhale anthu osaphunzilafe tili pawulendo olo amene akuti anthu amulunguwo tsiku lawo lili kudza chilichonse azachisiya pansi pompano zoona anthu awawa kupanga gwilizano owazunza Amalawi Chuma chili nthaka lero ndi mphekesela chabe feteleza Kutigulitsa nthawi yakutha kale cholinga timwalire ndinjala chabwino tithawe njala tithawile mayiko akutali nkulesa kupanga zitupa cholinga makolo athu afe ndinjala pomwe ana anu mukudziwa Kuti ali tsogolo lowala Ife tilibe phindu kwayinu zikomo kwambili Koma misonzi yamphawi sigwela pansi wamba nzimu wanu ukawuse mutendele Mr Chilima mwapanga mbali yanu kwanamiza Amalawi cholinga azunzike munali mbali yakonko Koma olo kudzudzula ayi bola anthu akwanu ankakhuta Zikomo kwambili kumeneko muzilongosole pamaso pa angelo Ine ndi Malawi Koma pano ndatshona Ku Zambia kuwopa kubwelera kwathu kamba ka umphawi kuthawa njala olo ndalama yoti ndifike kumeneko kumaliro ndilibe olo takhala nayo singabwele chifukwa yobwelera kunoko itha kundisowaso Koma ndingoti mizimu yonse ya Amalawi amwalirawo ikawuse muntendele Mulungu atonthoze mabanja awo Amen

  • @geraldtuwaga-iz6ll
    @geraldtuwaga-iz6ll 8 месяцев назад +4

    One thing that mr kalindo did to the malawians, is that he apologize to people, for campaigning for this wicked government, as for chilima, I don't have any passionate, to him because he Bettlyed Malawians and he never come to malawians to apologize for the painful governance that people are passing through, he deserve to face this consiquencies.

    • @JonesChingaya-yf4gg
      @JonesChingaya-yf4gg 8 месяцев назад

      I second thus true, Chilima amazimva kwambiri amaona ngat ndi wa nzeru kuposa amalawi onse. Akulandira zomuyenera amalawi tamva kuwawa zedi kaamba ka Chilima lero nayenso akumva kuwawa.

  • @DoricaGoweka
    @DoricaGoweka 8 месяцев назад +1

    Our freedom fighter keep it up

  • @faustinamannual4670
    @faustinamannual4670 8 месяцев назад +1

    Apm My vote

  • @davidkayangemakala7957
    @davidkayangemakala7957 8 месяцев назад +5

    Tikapanga zachamba kuikaso mcp tazamukumbuka bonikalindo

  • @PatrishaHamish
    @PatrishaHamish 5 месяцев назад

    One day the DC said let's play for the late chilima DC is the prophet

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 8 месяцев назад +3

    Agwilitsana chiphwisi athu akuluakulu😊😊😊

  • @austenbushiri-cx1kh
    @austenbushiri-cx1kh 8 месяцев назад

    More fire big 🎉

  • @RodneyMkandala-xn2fr
    @RodneyMkandala-xn2fr 8 месяцев назад

    More fire 🎉🎉🎉🎉

  • @Zaliro87_Frank
    @Zaliro87_Frank 8 месяцев назад

    Big up our President Boooooooooni!!!!! Kalindo

  • @susantembo2076
    @susantembo2076 8 месяцев назад

    Dr Chakwera needs to led his conscious and integrity not by cheap politics. Conscious means being led by the Holy Spirit to gain trust of those that voted him into power.

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 8 месяцев назад +1

    Ulemu wanu akalindo, inu mumaona pataali kwambili, Chilima akulilira muntima panona

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp 5 месяцев назад

    Mundu wAkulu ulemu wanu ❤😂😂

  • @Phill-nh8ru
    @Phill-nh8ru 8 месяцев назад

    Akalindo, mcp ndalama zawapengesa .

  • @DumisaniMhango-e4i
    @DumisaniMhango-e4i 8 месяцев назад +2

    Tithananawo a mcp palibepo choopya apa

  • @WilsLimited
    @WilsLimited 8 месяцев назад +2

    Olengeza zisankho azapange za chamba tizadula khosi masana dzuwa likuswa mtengo

  • @susantembo2076
    @susantembo2076 8 месяцев назад

    Oops! Dr Chakwera needs to allow his conscious to lead him.Hence the Holy Spirit at work to free himself.

  • @DesayLuk-ds7jn
    @DesayLuk-ds7jn 8 месяцев назад

    👍👍👍💥💥💥

  • @estherkauyange6548
    @estherkauyange6548 8 месяцев назад

    Komatu anthu amanena za mcp koma kusamva lero ndiiizi anthu akuzunzika dziko lawo lomwe

  • @MilesManes
    @MilesManes 8 месяцев назад

    Bon kalindo usazafe uzangosowa umandivesa kukoma kuposa atrist musician

  • @ThoccoBondo-mx7vt
    @ThoccoBondo-mx7vt 8 месяцев назад

    Timukunyadirani Bon Kalindo

  • @ChikondiChauma-ib9pg
    @ChikondiChauma-ib9pg 8 месяцев назад

    Chilima nthawi alinayo but he's time will appear soon

  • @HendryChiwezo
    @HendryChiwezo 8 месяцев назад

    Kodi chilima si vice President mesa akuchokera ku mngwiliza ko kodi ngwiliza zoona ukhoza kutheka kukhala wa zaka 10 mmmmm kaya koma ndikukayika

  • @mchipengule
    @mchipengule 8 месяцев назад +1

    Kodi bwañji? Mesa a Chilima i ndi a UTM? Nawoso Ali ndi chipani chawo apital ku convetion nawoso. Kenako adzapangaso mgwirizano. Mumathamanga magazi bwanji? A Boni Kalindo ndinu osokoneza inu. Chamba top much.

    • @SamsonMakhwala
      @SamsonMakhwala 8 месяцев назад

      Zophya

    • @godfreykhungwa8316
      @godfreykhungwa8316 8 месяцев назад

      Akalindo is just an attention seeker nde zakukhothi zokhazo apalamula nazo

    • @richardbanda9997
      @richardbanda9997 8 месяцев назад

      Nde a Ng'ona party mukamati aliyense akaimila ku chipani chake kenako adzapanganso alliance, nde allianceyo adzaimire ndi ndani? Mwamutaya Chilima basi vomerezani. Hungry for power, Chakwera wakomedwa, waiwala pangano.

  • @ThoccoBondo-mx7vt
    @ThoccoBondo-mx7vt 8 месяцев назад +1

    😂😂😂😂 Chilima zofuna kusamva apa wapusapo

  • @SophieKamanga
    @SophieKamanga 8 месяцев назад

    zosatheka ku mcp ndipo singaloweso boma

  • @DicksonBanda-gt5db
    @DicksonBanda-gt5db 8 месяцев назад

    🇲🇼💪💪

  • @HaroonMaundala-e4z
    @HaroonMaundala-e4z 8 месяцев назад

    Munkhale kutali ndi moto a kalindo.musawanyengelele athu amenewa.komaso amipingowo muwayaluseso.

  • @SamsonMakhwala
    @SamsonMakhwala 8 месяцев назад +1

    Kkkkkk zophya zamasiku osiliza

  • @yaachinayow-bmw8991
    @yaachinayow-bmw8991 8 месяцев назад

    Mtsogoleri wachipani ndiwagwirizano ndizithu ziwiri zosiyana

  • @AlfredNazombe-j5x
    @AlfredNazombe-j5x 8 месяцев назад +1

    Uyuu wandebvu zoshedayi ndiopoila kkkkkk wapusa bwanji kkkk nsete yache kobs kkkkkk

  • @frezarphiri3480
    @frezarphiri3480 8 месяцев назад

    😂😂😂😂😂 sorry chilima iwe kusava iwe chilima 😂😂😂😂 waziwona mbonawona iwe

  • @chamiyuna.siraji
    @chamiyuna.siraji 8 месяцев назад

    Zoona di

  • @godfreykhungwa8316
    @godfreykhungwa8316 8 месяцев назад

    Nkhan Zina zikufunika anthu amzeru okha ndiomwe aziyankhila nkhani zinazi kodi a Chakwela ndi a MCP and a Chilima ndi a UTM eyetu aliense chipani chake the alliance inu Mmafuna a MCP aikepo chilima? Aaaaaah

  • @andrewmtendere3167
    @andrewmtendere3167 8 месяцев назад

    😂😂😂😂waziwona

  • @Moses51
    @Moses51 8 месяцев назад

    Malawi wawola 🤣❌😂

  • @AlickAlfred
    @AlickAlfred 8 месяцев назад

    Nice bon kalindo

  • @HappyBirchForest-zy8nq
    @HappyBirchForest-zy8nq 8 месяцев назад

    Chilima waona pano iwe ndiwe galu yoti yimadya sete zake waziona munanyoza peter nde achakwera muwauza chani

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 8 месяцев назад

    Zimenezo ndi zakichipani kwawo ku mcp ko koma za gwilizano wawo ndi zinaso Zimenezo azakhambilana Zimenezo zilibe vuto zimatha ndithu

    • @AbelmanuelManuel-q3k
      @AbelmanuelManuel-q3k 8 месяцев назад

      Mmmmmmmmmmm Kodi Anthu inu KUKHALA ngatiso simukuwadxiwa anthuwa BWANJI??? Mukuona ngati chakwelayo angamuikeno chilimayu ??? Haaaaaaaa