MCP Is Desperate - Bon Kalindo

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 17 ноя 2024

Комментарии • 44

  • @DeenesNurudMeke
    @DeenesNurudMeke 8 месяцев назад +1

    Apm my vote

  • @TiniFrancis
    @TiniFrancis 8 месяцев назад

    APM my vote

  • @FranklinNdovi
    @FranklinNdovi 4 месяца назад

    Kwina ndi ku nsungwi kuseli Kwa katoto shop komanso ku front kwamashopo amended alimulaine katoto shop. Amenewa ndi ena omanga pa Malo a development a Lilongwe city council.

  • @TadalaBirsonkanjanga
    @TadalaBirsonkanjanga 8 месяцев назад

    Mumakwana inuyo ,ngofunika kukhala maso

  • @MemoryKamanga-pu1tj
    @MemoryKamanga-pu1tj 8 месяцев назад

    Zikomo
    Kwambiri potidziwitsa za alomwe kagulu kameneka ndika Mozambique di zoona okonda kutibulana basi,mtundu oipa kwambiri watero Bon kalindo.

  • @DaudBonomali
    @DaudBonomali 8 месяцев назад

    Mfumu yamanyi ya chiyao yoyamba ndi makanjira alipo panoyu ndichitsilu chamafumu ndiasamale (chituchingangane pe role pa bridge kapena pewesa bridge) amakanjira musamale mukunyatsitsa ufumu wathu tuwonegane kanga inganje nowe tukwethe kuposa yenuyo amapwisi

  • @IbrahimWezely-qd4vj
    @IbrahimWezely-qd4vj 8 месяцев назад +1

    Ma activist ongochokera lohmwe belt okhaokha zamasanje

    • @richardbanda9997
      @richardbanda9997 8 месяцев назад

      Ma activists a kwanuko simunawaika chibanzi mkamwa, ayanhula bwanji?

  • @MemoryKamanga-pu1tj
    @MemoryKamanga-pu1tj 8 месяцев назад

    Wakuyikani pantetete lero a Lomwe Bon Kalindo, Kudzikondo mpakana APM yemweyo wakalamba koma osavomeleza ayi Kudzikondo.

  • @AhmadumkomaTambala-lr9gp
    @AhmadumkomaTambala-lr9gp 8 месяцев назад

    APM ❤❤❤🎉🎉

  • @PatrickChirwa-cv5cd
    @PatrickChirwa-cv5cd 8 месяцев назад

    A Kalindo Mtukula pakhomo unayamba kale ndi UDF through DPP mpaka lero. Inayamba ndi MASAF kale kulibe National IDs. Musawapangitse anthu kuti afe ndinjala ndalama ndi za World Bank it has nothing to do with elections.

  • @GiboSunset
    @GiboSunset 8 месяцев назад

    Sakwanisa adyeledwa chabe Koma mlomwe voti ndi APM

  • @KumbukaniChimbalanga
    @KumbukaniChimbalanga 8 месяцев назад

    Iwe bon kalindo ukati opposition sikutsutsa iwe zimene zikuchitika ku parliament sukuziziwa?

  • @phillipstamaley7901
    @phillipstamaley7901 8 месяцев назад +1

    Koma mhlomwe mm satopa amwene kk chakwela high 5 woyeeee

  • @BrightPhiri-z3k
    @BrightPhiri-z3k 8 месяцев назад

    Bon kalindo upite ku mental hospital akakuwone. Munthuwe ngwamisala ndithu.

  • @ChikondiChauma-ib9pg
    @ChikondiChauma-ib9pg 8 месяцев назад

    This one is prophet

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 8 месяцев назад

    UDF mukunenayo inatha ku Eastern region chifukwa cha alliance anapanga ndi DPP ija inaimeza dug aliyense wachiYao wakuMangochi amangoti ife yatu ndi dipipi UDF fwaaaa kutha ngati mukatani. Chifukwatu ukunena zoona alliance siipindulira chipani chaching'ono chachikulucho. Mgwirizano ukatha anthu achipani chaching'onocho amatsalirira kuchipani chachikulucho.UDF yaziona zimenezo.

  • @AishaJuma-z4f
    @AishaJuma-z4f 8 месяцев назад

    Ndipo ndagwilidzana nazo

  • @kennedybanda
    @kennedybanda 8 месяцев назад

    Anya nayo amenewo thanks for the tips

  • @davieborniface6699
    @davieborniface6699 8 месяцев назад

    inuyo zomwe mukulankhulazo zikuveka ndithu koma siinu omenyera ufulu ayi ndinu achipani cha dpp

  • @MartinMajola
    @MartinMajola 8 месяцев назад

    Dc chakwela mbava chilima bomaa

  • @YonaGoliat
    @YonaGoliat 8 месяцев назад

    Pitilizani madala mumakwanila

  • @Moses51
    @Moses51 8 месяцев назад

    DC wayankhula mobveka bwino

  • @mikeasmachine4581
    @mikeasmachine4581 8 месяцев назад

    Zoonad

  • @AhmadumkomaTambala-lr9gp
    @AhmadumkomaTambala-lr9gp 8 месяцев назад

    Akuopa kut akhesedwa mwazi alindizida zoopsa

  • @DicksonBanda-gt5db
    @DicksonBanda-gt5db 8 месяцев назад

    💪🇲🇼💪🇲🇼💪🇲🇼💪

  • @MasiyeLowani
    @MasiyeLowani 8 месяцев назад

    Ndakutopela matako ako ufulu wakowo osati waife munthu omenyela ufulu koma daily kunyoza mcp koma namachende uyuu

  • @robsontyg3928
    @robsontyg3928 8 месяцев назад

    Dzimachende ngati dza nkhumba ahlomwe pathako panu nonse

    • @juniortsegula3847
      @juniortsegula3847 8 месяцев назад

      Iwenso nyini ya mako

    • @robsontyg3928
      @robsontyg3928 8 месяцев назад

      @@juniortsegula3847 alhomwe pamtumbo pambuyanu, dzipitan kwanu ku Mozambique dzitsilu, dzimachende dzanu ndi Peter munthalika wanuyo

    • @Yahiya-wm8nd
      @Yahiya-wm8nd 8 месяцев назад

      iweyo ndiye mbuli yothelatu kunkhalila kutukwana every day aaaaaa chepesani MN mungopeza naso Zina ix

    • @robsontyg3928
      @robsontyg3928 8 месяцев назад

      @@Yahiya-wm8nd mbuli ndiwe mankhwala amako wava

  • @DaudBonomali
    @DaudBonomali 8 месяцев назад

    Ndipo chaka chamawa tikufuna tizavote chimodzimodzi 2019/2020 aliyense akavote sitikufuna kungwilitsa ntchito n ID tifuna aliliyense avote no nations ID

  • @DaudBonomali
    @DaudBonomali 8 месяцев назад

    Komatu boni kalindo ndiye akumanenatu

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o 8 месяцев назад +1

    Akalindo vuto lanu ndichiyani kodi womenyela ufulu wadpp .kod alomwe mlibed nzelu eti daily kuyankhula zamcp kapena kunyoza chakwela iwe kulephela kupanga zakubanja kwanu chifukwa cha mcp ndinu agalu achiwewe zisilu chimtundu choipa

    • @mussafrank-ev6zx
      @mussafrank-ev6zx 8 месяцев назад +2

      Inuyo mudana ndichilungamo

    • @JonesChingaya-yf4gg
      @JonesChingaya-yf4gg 8 месяцев назад +1

      MCP ndi imene ikulamulira thus why akuyenera kumadzudzulidwa. Mwina ndifunse kut kod nthawi ya DPP Timothy Mtambo ankazuzula MCP??

    • @TiniFrancis
      @TiniFrancis 8 месяцев назад

      Chisiru chachikulu ndi iweo Kodi ukuona ngati MCP ndi Malawi
      Usaiwale kuti Malawi ndiwawina aliyense pamtumbo Pako wamva

    • @JonesChingaya-yf4gg
      @JonesChingaya-yf4gg 8 месяцев назад

      @@TiniFrancis Kutukwana sikungakuthandizeni, ine ndapereka maganizo anga inunso ingoperekani anu. Mukanachita bwino mukanayankha funso langalo osati kunditukwana.

    • @beinhardkausiwa7107
      @beinhardkausiwa7107 8 месяцев назад

      ​@@JonesChingaya-yf4ggndiiweyo wayamba kutukwana.....APM my vote