A Malawi kukonda mabodza, that's cheap politics, tiyeni tipeze zochita zina, much as things are not supposed to want them be, economically, socially, and every aspect of live, but we can not allow people in the name of activism push us to and from. We are grown up persons and come elections will do the needful!
Nice song bring more song zixiwawa achimwendo
Komaso CLIFF CHINYAMA MUSAMAMUYIWALE NDI COMRED WATHU WAPHAMVU
Comrade cc...osamuiwara ...ndinthudi comrade Ntanyiwa...moto kuti buuuuuu🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
mukudziwa. Kale ameneyu muthu wakulu
Ngani yose ndinanenna my Allah protect you mtanyiwa ndi bakili mulusi TV let's gethas her 🤛👎
Komati Mr Tanyiwa inu ndi One 😅
Tanyiwa umatiimilila mulungu azikudalitsa 🙏🙏🙏
Abwanawa ndiopepela akulimbana ndi mwana Tamiya mmmmmm bwanji osolimbana ndi the DC . Zachamba.
😂😂😂nanga titani nkulenga kwa Mulungu
Dziko lamalawi silachakwela , ndi team yake we are Malawian .
Mr Mtanyiwa inuyo ndikatundu more 🔥🔥🔥
Welcome Mr ntanyiwa
A Malawi kukonda mabodza, that's cheap politics, tiyeni tipeze zochita zina, much as things are not supposed to want them be, economically, socially, and every aspect of live, but we can not allow people in the name of activism push us to and from.
We are grown up persons and come elections will do the needful!
😂😂😂🎉🎉🎉 koma Tanyiwa ayi wati bwanji apa ngangnanganganga zaona koma ayi dzikomo iweyo 😅😅😅😅
😂
Mulungu azikutetedzani mwati segura mutu
❤❤
Koma Amalawi ndinu opeperadi 😂😂 Tiyeni tizingonamizana
Comrade more fire
More fire mtanyiwa inuyo ndi one AGALU awawa a MCP atikwana afiti opemphera
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Chakwela akuona ngati amalawi tonse ndife mbuli zoti tizingoti boma ndilomweli , waiwalakuti mbuli ziliku mcp kokha .
Agalu amenewa akufuna abweletse nkhondo Malawi muno serious kumalawi pa 17 September kukesedwa mwadzi munzandikumbuka mau anga
😂😂😂koma ndiye asovakkkkkkkk
Mtanyiwa machine bambo
Welcome back
Mbambande 🔥🔥🤣
All comrades ,God bless you all ,long live
Ulemu wanu basi mr ❤❤❤❤❤
Eish Tamia bola ukanango pakulitsa pang'ono kuti nkhani isapte patali uptatu iwe
Aaaaaaà
Zaziii
Moto kt buuuuu
Comrade Ntanyiwa iweyo umakwana
Tanyiwa umativesa kukoma
Ku statehouse kwasanduka beerhall ndi lesthouse kobelekera ana mwinaso tingot kumatenity hospital kkkkkk chikangawa woyeeeeeeeeeeeeee
Oh God save us from this crocodile party
Ulemu wanu Mr mtanyiwa
Allah azikutetezerani bwana comrade ntanyiwa
Osamayiwala clff
Bg up
😢😢😢😢😢😢😢😢
Nkhangaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaa zaona😂😂😂😂😂!!
😂😂😂😂😂😂😂 inezotu ndasekatu ati ngaaaaaaaaaa 😅😅😅😅 mavuto
Comrade ntanyiwa your a fire 🔥
Long live mtanyiwa
😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😂😂😂😂yomweyo Chikangawa party koma mulimba 😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😂😂😂😂😂🎉🎉🎉😂😂😂
Kkkkk kom abale khan zake 😂😂😂
Koma inudi ndi ntanyiwa zibwerani nazo zambiri kut ife amalawi tipulumukeee
Nanuso tamqtipatsani ma feedback abwana osati kumaonjezela zina zoti sizinachitike mutisokoneza mutu anthuwa ambiri amakupangani follow up so tiwuzeni zoona zinaso ayi
Machine
Kod jb alikuti abale muuzeni fast fast mamvete
A comrade munasowatu inu ife matha kuti chakuchitikilani ndichiyan
Moniwo kwa ben longwe bwa
𝕋𝕒𝕞𝕚𝕪 𝕪𝕠𝕞𝕨𝕖𝕪𝕠
Ine ndimadabwatu kuti chifukwa chomumangilacho mchosakwanira..Personal issues ndi zimene zavuta
🎉
Bro munasowatu.koma Malawi ndichani dzikoli nkhani yake izingokhala yazigololo basi izi ndiye zatikwana.koma kuti azaonekere ng'amba nkazi wina azangomucheka pang'ono wina wogundika ndi azimayi nziko muno.azimayiwa tiziwapatsa ulemu.
Apooooooooo😂😂 ndipamene timaziwa kut wabwera mtanyiwa akat nkhaaaangaaaazaoonaaa😂😂😂😂
Mupole moto a mcp
Tsono ife ayiniyake a fone ndikugula ma data moni sitimamufuna??
Ndi makunyadila ntanyiwa
Inenso ndipatsen moni
Koma
Mm koma chikangawa party ayi ndithu
Kod wapolis anawombera mai said mukandu wake uli litilo?
😂😂😂ok
Kodi ndichifukwa chiyani sankagula atangolowa mmboma akugula akufuna kupanga zisakho?
Go for manual
Mulungu tiyendeleni Satan akuyenda maliseche
Tamiya akanalola kenako ndikunena kuti andigwilila kuti azengedwe milandu ntchito itatha iwe Tamiya ukavumbulukako uku ukulila kuti andigwilila chifukwa ku chipatala amakayeza ndiye akayeza azapeze kuti akumbwindadi akanalipila komaso ndi kumangidwa komwe
Zikomo moni talandila bomali lichokedi ambuye atithandize
Paja amatha kuwaopsyesa ma dotolo kuti asanene chilungamo like za amayi saidi zija zinazimva bwanji kuti anene ngamo kuopa kuzima
@HaroonSaidi-jv3ek kumapita ku za private zikulu zikulu
Anachita bwino kukana akanangomupasapo matenda basi anthuwatu anavunda kale
😂😂😂😂😂
Kufuna kuthila mazi pambwanda yamwana kkkk kuthila mazi pakayera, paimaso, pachimbamba, paimaso ,panyemba penipenipo bac
Pathetic government
🧑💻
PA manual po game ili bho man
Moni
Koma ya ziriko
More fire ntanyiwa
It's to childish
Following from 2nd road Hyde Park Sandton
Kkkkk
❤❤❤❤❤
Inu zomwe mumakamba
Kodi ndichifukwa chiyani sankagula atangolowa mmboma akugula akufuna kupanga zisakho?
❤❤❤❤❤