Aphanatu anthu awa ku konveshoni ya MCP moti alengeza motele lero

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 28 июн 2024

Комментарии • 80

  • @PhiriChitani
    @PhiriChitani 2 дня назад +8

    Zaziiiiiiiii zopanda nazo school akuti next month is August 😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅. Mpc ndi Mcp basi

  • @user-xe1so5xj2w
    @user-xe1so5xj2w 2 дня назад +9

    Musapange convesion chifukwa ndinu okupha ndi akuba ziko lamalawi tsilikukufunani

  • @Lee-lee-w1r
    @Lee-lee-w1r День назад +1

    😂😂😂akuti akamanena kuti fees akumanveka ngati akuti fisi chifukwa cha kukalamba 🤣🤣🤣. Anthu mwakwiya

  • @josephchitsulo5882
    @josephchitsulo5882 2 дня назад +3

    Zilombo, nkhalamo zokha zokha tazionana, zokupha paliinupo mukungoganiza kupha anthu

  • @IgnatiousFote
    @IgnatiousFote 2 дня назад +4

    mbwelera zenizeni 5 million cholinga anthu ena asakwanise

  • @user-fd1tu6ku1r
    @user-fd1tu6ku1r День назад

    May the innocent Souls of Late Right Honorable Dr Saulos Klaus Chilima and other 8 Malawians continue resting in eternal Peace

  • @Musa1828-l5d
    @Musa1828-l5d 2 дня назад +5

    Anthu akupha inu simungawineso

  • @carllewis2744
    @carllewis2744 2 дня назад +2

    MCP has failed us. Good for nothing

  • @joyahmedjoma4615
    @joyahmedjoma4615 2 дня назад +4

    Akupasani ndani ndalama uchisilu et

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q 2 дня назад +1

    Zausataniki zokha zokha ukunenaapa inu mukufuna kutipha tose amalawi kuribe magazi kusi kwa nyanja mwagwa nayo

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 2 дня назад +1

    MUSAVUTIKE NDI KUONONGA MISONKHO YA A MALAWI SITIDZAKUVOTERANI AGALU AKUPHA INU MOTI MULIBE MANYAZI , PALIBENSO ANFAKOMDE CHIPANI CHANU CHAKUPHACHO ,MBUZI ZA ANTHU PRESIDENT WAKUPHA ,WAKUBA NDI NDUNAZAKE TIKUKHAULITSANI

  • @faizanvahora2728
    @faizanvahora2728 2 дня назад +4

    Musazivute inu simudzawinaso ai aaaaa zaunyapapi

  • @felixjoseph8161
    @felixjoseph8161 2 дня назад +3

    Pitani kapangeni Ife tilibe Nanu ntchito anthu okupha inu

  • @IssahAluba
    @IssahAluba 2 дня назад +1

    MCP yatha bas iyaaa

  • @JeanBanda-zy6wu
    @JeanBanda-zy6wu 2 дня назад +2

    Convention ya 2029 nso muzatchaje ndalama ngati zimenezi kwa ozafuna maudindo bcoz muzakhala muli out of government muzawone hehedeeee😂😂😂😂

  • @ChifundohMitulo-bg2lv
    @ChifundohMitulo-bg2lv 2 дня назад +4

    Anthu ndi okalamba awa akuchita kulephera kunena ku fees akut fisi

  • @SolomonShaibuh
    @SolomonShaibuh 2 дня назад +1

    Zaziiii kwanu kwatha agalu inu

  • @BENSONRANGWANI
    @BENSONRANGWANI 2 дня назад +1

    Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zach

  • @HenryLaidon-pl9ly
    @HenryLaidon-pl9ly 2 дня назад +2

    Thambani Thambani amwene

  • @PhiriChitani
    @PhiriChitani 2 дня назад +2

    This is june next month is July kaye kuda

  • @tingo3155
    @tingo3155 14 часов назад

    Ana anjoka, paja afiti amagwiritsa ntchito gule usiku pofuna kulodza munthu

  • @user-gx3xc9lk8x
    @user-gx3xc9lk8x 2 дня назад +1

    Zaziiii anthu akupha inu angakuvoteleni ndi ndani hiyaa

  • @goatsasha2653
    @goatsasha2653 День назад

    Osavutika ndi convention ingoikani Yomweyo aone nyekhwe 2025 ino😂😢

  • @augustMag
    @augustMag 2 дня назад +1

    Eeeeee koma ndiye kusowa chokambatu oti kumpando wa president kulibe okapikisina bwanji 5 million yachani

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 7 часов назад

    Mbiri yanu yinada basi palibe wokufunani inu a MCP akupha inu

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 2 дня назад +1

    Ayabulos anthu okupha inu tinasiya kukukhulupilirani

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm День назад

    Dzilombo inu dzigawenga dzianthu dzakupha sitikukufunan ife a Malawi pitan muzikavina gule ife moyo wathu sitikufuna inu

  • @ChimwemweBottomani-hc5ju
    @ChimwemweBottomani-hc5ju 2 дня назад

    Palibe anakuthandizeni ...Malawi ndiokwiya nanu kwambili ...

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 2 дня назад +1

    Chipani cha magazi cha kupha agalu

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 4 часа назад

    Mbuzi za wathu zopanda Mano kunsi afisi olutsa Inu akupha mwamudya chili mimba za ambuyanu

  • @user-xe5lb4uf3n
    @user-xe5lb4uf3n 2 дня назад +1

    Mwakonzeka zomwe mumafuna zatheka anthu akupha inu

  • @user-is5dl7np9g
    @user-is5dl7np9g 2 дня назад +3

    Agalu afisi okupha inu stupid 😮

  • @JohnAsendi
    @JohnAsendi 2 дня назад

    😂😂😂😂😂😂 Kuyamba kuphupa tiyeni nkhani ndi chaka chamawa palibe chosatha amatsiku akunkanasintha sakubwerela m'mbuyo kwende nayo kweleko ku chipani chakulaga nganinpata voti jangu 😅😅😅😅😅😅😅😅

  • @NearBanda
    @NearBanda 2 дня назад

    2025 no MCP

  • @user-fd1tu6ku1r
    @user-fd1tu6ku1r День назад

    Nenani bwino bwino kuti Gulu la zawuchifwamba la Emusipi osati Chipani Cha MCP Ayi

  • @PetroJack
    @PetroJack 2 дня назад

    Awa aphanako😂😂😂😂

  • @EllenPhiri-xt8pt
    @EllenPhiri-xt8pt 2 дня назад

    Kodi akuyankhula zichani Kodi pamenepa anthu akuphawa Kodi akuzivutiliyanji akuziwa kale kuti sazawina aaaaaah

  • @IsaacMusa-py2jm
    @IsaacMusa-py2jm 2 дня назад

    Zopusa zimenezo,n uzipatse ulemu madala iwe mbuzi

  • @jangiya03
    @jangiya03 День назад

    Uuuuuuuuu anthu mungotukwana kkkk

  • @LukeWenje
    @LukeWenje День назад

    Mafuno abwino Ku MCP

  • @TecksonKaima-dr6er
    @TecksonKaima-dr6er 2 дня назад

    Ukatape kumtumbo kwachakwera ndalamazo. agalu inu kwabasi.

  • @user-dn8pt4uz3q
    @user-dn8pt4uz3q 2 дня назад

    😂😂😂😂zakhutu

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 2 дня назад

    Koma osayiwala kuti president wa 2025 ndimanganya mugwirizano wa tose alliance utero according ndipamene ananene malemo chilima between mcp ndi utm wina 5years wina 5years

  • @ElliottBelon
    @ElliottBelon 2 дня назад

    Agaru inu angakumvere ndan mboro zanu mwamva

  • @AdgoKaxsy
    @AdgoKaxsy 6 часов назад

    Mbore zanu aMcp 😂😂😂

  • @MadalitsoTamayenda-ez5pj
    @MadalitsoTamayenda-ez5pj 2 дня назад

    Khalambaa zokhazokha zonukha sete zeni zeniii chomcho osawasiyira anyamata bwanji nde tikuvoterenii inuyoooo ng,oooo!!!!! Mwaremba madzi😂😂😂😂😂😂😂

  • @AngolanChinga
    @AngolanChinga 2 дня назад

    Zimachende zanu nonse

  • @MandisaDelubom
    @MandisaDelubom 2 дня назад +1

    akulu akulu wina aliyense tisalole zopusa chaka chamawa. please wina aliyense angazavotele mcp akalowa kumoto💥💥💥💥💥💥💥💥💥💥💥💥💥💥💥💥

    • @inessmsiyambiri8517
      @inessmsiyambiri8517 2 дня назад +1

      Vutotu nloti iwowa apanga maplan oopsa kumadera komwe kuli zipani zotsutsa nrb makina ake sakugwira ntchito

    • @inessmsiyambiri8517
      @inessmsiyambiri8517 2 дня назад +1

      Ndeno amalawi tikalora kuti kudzabvota ndi ma id Tanya agaluwa aberanso awina

  • @ShafieIdrissah
    @ShafieIdrissah 2 дня назад

    Uyuso mapwala anu pamoz ndichakwerayo agaluinu

  • @thomasjesale
    @thomasjesale День назад

    Aphana chifukwa chiyani?

  • @JydonKolalah
    @JydonKolalah 2 дня назад +1

    kuimila udindo ndalama ooooo

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp 2 дня назад

    Chokaso apa sachamba

  • @QasimMuhammad-c4l
    @QasimMuhammad-c4l 2 дня назад

    11

  • @user-lk8kj9zv6x
    @user-lk8kj9zv6x 2 дня назад

    Gule kwao nyawu nthawi yake yatha😊

  • @YamikanChirwa
    @YamikanChirwa 2 дня назад

    Aaaaaa za ziiii

  • @ConfusedAstronaut-qv6wq
    @ConfusedAstronaut-qv6wq День назад

    Agalu inu,afisi,ngona inu

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn 2 дня назад

    Or ndalama itandiyamwa sindingachite bola kumupasa wamisala

  • @YohanneSakuwa
    @YohanneSakuwa 2 дня назад

    Guys what's this buying the portfolio what a joke. Is this a part or a sellout look at it pipo.

  • @user-uy8uk7so9d
    @user-uy8uk7so9d 2 дня назад

    Zaziiiiii meeeee

  • @jamesgama5489
    @jamesgama5489 2 дня назад +1

    Za nyawu nzasataniki

    • @user-rf4br1fv2z
      @user-rf4br1fv2z 2 дня назад

      Koma mau awa anyau wa eeeee amandikwana moti titakumana pa maso tikhoza kuthana moti popeza pa masamba amchezo pitizani koma eeerrr amwene tsiku lina tsiku lina tidzaona mulungu

    • @jamesgama5489
      @jamesgama5489 День назад

      Yes God will judge us according to our believes

  • @PeterLemani-jk3mw
    @PeterLemani-jk3mw 2 дня назад

    Zilombo

  • @joyahmedjoma4615
    @joyahmedjoma4615 2 дня назад +4

    Za zii 😂😂😂zoti sitikukufunani a mcp mukukaika

  • @user-qq4ks5mf2s
    @user-qq4ks5mf2s 2 дня назад

    Why it's like u a crying?

  • @Mohammed-sk1fy
    @Mohammed-sk1fy 2 дня назад

    2025 tikumana koko afit inu

  • @user-hh4wn4vf9e
    @user-hh4wn4vf9e 2 дня назад +2

    Nkhalamba zokha zokha basi kuyankhura kuchita kukanika

  • @user-si7po9sd5i
    @user-si7po9sd5i 2 дня назад

    The witches have met

  • @PastorjTongole
    @PastorjTongole 2 дня назад

    Map kkkkkkkk