Ulaliki wa Father Ntharika muli zinthu umu aboma apuma nawo befu ndithu kuchita kubaya

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 1 дек 2024

Комментарии • 136

  • @JosephNgona-f9v
    @JosephNgona-f9v 5 месяцев назад +3

    AMEN AMEN powerful ndipo zoonadi ndipo umunthu mulibemo apapa ulipo ndi ufiti.akatolika mmmhhh pempherani mpaka titadziwa ZA imfa imeneyo kkķkk akugawana nsalu.chakangazitsa ndi chani .mau mau mau.mcp yatha basi

  • @flourencejamu6455
    @flourencejamu6455 5 месяцев назад +5

    Amen
    Mzimu wa mtumiki wanu Dr.Saulos Klaus Chilima pamodzi ndi mizimu ya wanthu omwe anafa nawo pangoziyi
    Mizimu yawo iwuse mumtendere wosatha

  • @shayrafernandeslatif9556
    @shayrafernandeslatif9556 5 месяцев назад +5

    Mau ogwira moyo muchowona MTSRIP 🌹 ndipoo imfa iyi yatikhudza tonse Malawi,and SKC his words shall always echoi in our hearts,ambuye athangate ma banja anzathu amene abalewa atisiya, ameeen

    • @YunusuMakiyi
      @YunusuMakiyi 5 месяцев назад

      Hi my dear can I talk with you please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want

    • @SoulstinMaulana
      @SoulstinMaulana 18 дней назад

      Amen

  • @OwamThoko
    @OwamThoko 5 месяцев назад +10

    Thanx for your strong message God bless n protect you from chakwela the killer amen

  • @MaxwellMbesa
    @MaxwellMbesa 5 месяцев назад +5

    Amen GOD bless you abundantly keep it up

  • @ElphinaChirwa-qk3cy
    @ElphinaChirwa-qk3cy 5 месяцев назад +1

    Eeeee Komatu powerful msg mmmmm ambuye titonthozeni Ife ana anu osiidwa

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 5 месяцев назад

    Powerful and amen, uthenga wabwno ambuye akudalisen brother elizeyo ntharika😢😢😢😢

  • @GiftHlungwane-q5o
    @GiftHlungwane-q5o 5 месяцев назад

    Thank you so much for your message Amen man of God for prenching and directly to the point

  • @RhodaKalumbi
    @RhodaKalumbi 5 месяцев назад +2

    Amen mau abale inu imfa yomvesa chisoni ngati imeneyi..umunthu wasowadi

  • @paulinekayuni1621
    @paulinekayuni1621 5 месяцев назад

    Zoona ndithu malamulo ngati amenewa siabwino malamulo ena ose amasinthidwa ili osasintha bwanji. 21 days of mourning siikumveka olo pang'ono. We need strong preachers like these.

  • @davieabel5631
    @davieabel5631 5 месяцев назад

    Powerful message ndipo samve kt mwatola simukuchedwa paja

  • @PatrickMaluwaphiri
    @PatrickMaluwaphiri 5 месяцев назад +3

    Amen, Chilungamo chiyende ngati madzi.

  • @MillyKachepa
    @MillyKachepa 5 месяцев назад +2

    Amen fr ... ndpo kuipa mtima chipani cha mcp aaaa malawi tiyeni tidzuke anthuwa aonjeza tikhala chete mpaka liti ... Ambuye tithandizeni😢

    • @GroliaKafumbwa
      @GroliaKafumbwa 5 месяцев назад

      Ulaliki ndi chipani osaphatikiza apa .imvani mau Amulungu ndikuwangwiritsa ntchito moyenera
      Mateyu 26 :35 ndi mpingo anthu musawatape mkamwa

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 5 месяцев назад +3

    Amen koma ife sitiyiwalayi akunama

  • @francisntonya171
    @francisntonya171 5 месяцев назад +2

    Amen, man of God,,,,, but we can't forget it, mmmmmm lord help us

  • @ThandiBinali
    @ThandiBinali 3 месяца назад

    Amen FR mau achilimbikitso

  • @johnchikhanda3551
    @johnchikhanda3551 5 месяцев назад +1

    Very powerfull massage dzivere muntolo...wanzeru wanva apa

  • @PeterThomas-lw3io
    @PeterThomas-lw3io 5 месяцев назад +2

    Paster mwalaluka bwino
    Komano mukumbukiretso kuti
    Malemu Bingu atamwarila maliro alinyumba Madam Joyce Banda ndiamene adalumbiritsidwa u president nde sizachilendo mukumbukile
    Ichi😢😅

  • @EstherAmadu-md3et
    @EstherAmadu-md3et 5 месяцев назад +2

    Powerful teaching words of God amen and amen

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 5 месяцев назад

    Amen uthenga wamveka wakwiya ndiye ochita ntchimolo

  • @EdithKachule
    @EdithKachule 5 месяцев назад +1

    Zoona zokhazokha!
    May their souls rest in eternal peace 🙏🏽

  • @charlesmbewe4001
    @charlesmbewe4001 5 месяцев назад

    Oh! God , father Nthalika my God keep blessing you.

  • @FlorenceSagona
    @FlorenceSagona 5 месяцев назад

    Amen father, very powerful words

  • @GroliaKafumbwa
    @GroliaKafumbwa 5 месяцев назад

    Amen my priest
    Poweful words

  • @ShadreckMatenje
    @ShadreckMatenje 5 месяцев назад +2

    Koma iwe Chakwela unalidi m'busa kumaphwanya malamulo amulungu ndi kumasunga malamulo adziko AAA! Ndichifukwa unalola kusiya moyo osatha ndikuyanja moyo wadziko lapasi imene uli wakutha abusa a Chakwela its not too late lapani tsiku ili lomwe wakumana nalo chilima lisanakupezeni khalani ngati mwana uja akafuna gawo lachuma chamakolo Ake ndikukadya kenako amabwelela kwa makolo Ake ndikukapepesa.mulungu ndiwabwino adzakukhululukilani

  • @horamusicnetcom
    @horamusicnetcom 5 месяцев назад

    Father muntharika mulungu akudariseni kaya mudari ku muthawila parichi munandi phuzisapo pa mthawila God bless you

  • @terezazakeyo2285
    @terezazakeyo2285 5 месяцев назад

    Thank you father for the revelation 😊

  • @KingsleeKandiadoh
    @KingsleeKandiadoh 5 месяцев назад

    Ambuye akutetezeleni father, chifukwa nkutheka kuti uthenga uwu ukubweletselani mavuto. Ambuye samalilani mzimu wa SKC uziusa mu mtendele

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 5 месяцев назад +1

    Amen koma Chakwela watikwana u mast go satana

  • @AdamLano-sj1gv
    @AdamLano-sj1gv 5 месяцев назад

    Amen amen ause mu mtendere Dr skc ndi ena onse

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 5 месяцев назад

    Ambuye akudalitseni Mtumiki mmmm akudziwapo kanthu kufuna kwao kuchitidwe koma Mwazi wa Chilima udzalakhura ndipo udakali okwiya 😭😭😭😭😭😭😭😭

  • @JohnmarkNazombe-hi9xd
    @JohnmarkNazombe-hi9xd 5 месяцев назад +3

    Ameeeen !!!!❤❤❤❤ i hear you man of God....

  • @PhilomenaChikabadwa-dt6vy
    @PhilomenaChikabadwa-dt6vy 4 дня назад

    Zikomo bambo potigawira mau achilimbikitso .Ambuye akutsogolereni nthawi zonse

  • @GraceZumazuma
    @GraceZumazuma 5 месяцев назад

    Amen father, ineso ndinali ozaza ndimafuso kuti zamtundu wanji maliro week sinathe ife misonzi ili mmaso ena akulumbila ndikumavina zoona

    • @isaacchirwa9518
      @isaacchirwa9518 5 месяцев назад

      Mvuto ndimalamulo a dziko lathu, akanaika atleast one month koma analemba kuti within 7 days, nde inu mkubulema ndani? President, vice president kapena malamulo?

    • @isaacchirwa9518
      @isaacchirwa9518 5 месяцев назад

      Mvuto ndimalamulo a dziko lathu, akanaika atleast one month koma analemba kuti within 7 days, nde inu mkubulema ndani? President, vice president kapena malamulo?

  • @FrankMulela-qt1wi
    @FrankMulela-qt1wi 5 месяцев назад

    Katundu uyu aaaa amen amen galu wamkota sakanda Popanda nyama

  • @chrisschikozera7271
    @chrisschikozera7271 5 месяцев назад

    Powerful massage ❤.

  • @annembepula
    @annembepula 5 месяцев назад

    Amen zowona zake dzinvele Ntolo

  • @PatriciaSaiti
    @PatriciaSaiti 5 месяцев назад

    Father mukunena zoona. Mulungu apitilize kuikiza zinthu pa inu.

  • @NearBanda
    @NearBanda 5 месяцев назад

    Amen imfa yimeney yinapweka aliyense

  • @christophergibson72
    @christophergibson72 5 месяцев назад

    I'm a catholic member koma mchifukwa chake amtinena kuti mpingo wathu umalowelela zandale

  • @LawrenceMalinda
    @LawrenceMalinda 5 месяцев назад

    Amen 🙏🙏 God bless you.

  • @YusefMakawamonjeza
    @YusefMakawamonjeza 5 месяцев назад

    Powerfull...

  • @MaxwellMbesa
    @MaxwellMbesa 5 месяцев назад

    Yes Mulungu wayenda mulaliki uwu

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 5 месяцев назад +1

    Malamulo ndichikhalidwe ndizosiyana paja inu ndalomwe ndiye sitikudabwa ai

  • @Maxielyies
    @Maxielyies 5 месяцев назад

    Powerful message

  • @LudavikoTimothy
    @LudavikoTimothy 5 месяцев назад

    Uthenga wambuye amen

  • @deborahngwira724
    @deborahngwira724 5 месяцев назад

    Kodi za novena simunakambilanebe? Inetu zundiwawa nsanameyi. I want to see something. 😢

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 5 месяцев назад

    Amen powerful words

  • @joicemumba3608
    @joicemumba3608 5 месяцев назад

    Amen koma imfa iyi 😢😢😢😢

  • @ReginaNyilenda-ug1lf
    @ReginaNyilenda-ug1lf 5 месяцев назад

    That is true...ameeen

  • @robertnkuliza5718
    @robertnkuliza5718 5 месяцев назад +2

    Zoonadi Akuziwa ndi Yehova

  • @TapiwaMwanjah
    @TapiwaMwanjah 5 месяцев назад

    Amen very powerful

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 5 месяцев назад

    Uthenga olamitsa olasa mtima amen father

  • @AvrelChirwa-ho9wf
    @AvrelChirwa-ho9wf 5 месяцев назад

    Very powerful message

  • @AwaliBlack
    @AwaliBlack 5 месяцев назад +1

    Ulaliki wabwino kwambili emen abusa

  • @RabeccaGama-f7m
    @RabeccaGama-f7m 5 месяцев назад

    Powerful words

  • @LangfordMabaso-z7u
    @LangfordMabaso-z7u 5 месяцев назад

    Powerful msg

  • @KnowledgecGodwin-xo4pw
    @KnowledgecGodwin-xo4pw 5 месяцев назад

    Amen munthu wamulengi

  • @KabiluAnthoni
    @KabiluAnthoni 5 месяцев назад

    Mau aphavu. RIP SKC

  • @JonathanMtambo-w6e
    @JonathanMtambo-w6e 5 месяцев назад

    When you shed innocent blood this is what happens

  • @RhodneyBwa3
    @RhodneyBwa3 5 месяцев назад

    Amen and amen pastor.

  • @RosemaryMagwira
    @RosemaryMagwira 5 месяцев назад +1

    Let Love Lead Amen

  • @JohnFrank-cg1yh
    @JohnFrank-cg1yh 5 месяцев назад

    That's true, amen

  • @GloryShera
    @GloryShera 5 месяцев назад +1

    Mwayowoya asembe wali namakutu wapulike

  • @OssmanAbubaker-xu7ql
    @OssmanAbubaker-xu7ql 5 месяцев назад

    These is true something it's wrong in the city of Malawi

  • @lillynhlema9656
    @lillynhlema9656 4 месяца назад

    Powerful

  • @davidkayangemakala7957
    @davidkayangemakala7957 5 месяцев назад

    God is speaking with Malawi

  • @LucyThambo
    @LucyThambo 15 дней назад

    Mau oona and ogwira mtima

  • @NellieMsamala
    @NellieMsamala 5 месяцев назад

    Amen and amen

  • @HappyAutumnTrees-cd9ye
    @HappyAutumnTrees-cd9ye 5 месяцев назад

    Amen brother,

  • @DamianoNombo
    @DamianoNombo 5 месяцев назад

    God is in control

  • @JoshuaJumbo-mp3ze
    @JoshuaJumbo-mp3ze 5 месяцев назад

    Ndi zoona amen abusa

  • @eunicesaiti
    @eunicesaiti 5 месяцев назад +1

    Amen 👏

  • @joaquegerman2250
    @joaquegerman2250 5 месяцев назад +1

    Ameeeeen abusa

  • @GraciousGIbbu
    @GraciousGIbbu 5 месяцев назад

    Ati ndi malamulo angati dzuwa liri nde amene mwakanika kuwasunga

  • @coollife-is7ir
    @coollife-is7ir 5 месяцев назад +1

    Akutitu masiku 40 ohoooo

    • @JosephNgona-f9v
      @JosephNgona-f9v 5 месяцев назад +1

      Mau awawa eshhhh week yomweyo ayambapo kugawana zinthu mmmmhhhhh AMEN muli uthenga tu umu ineyo ndinaona kut mzimu wa chilima suusa mpaka zoonadi zitadziwika soon

  • @EmilyEmuzy
    @EmilyEmuzy 5 месяцев назад

    Amen Father E.

  • @MemoryChiwanga
    @MemoryChiwanga 5 месяцев назад

    Amen 🙏 my father

  • @GiftHlungwane-q5o
    @GiftHlungwane-q5o 5 месяцев назад

    Something is loten in Chakwela's and his stupite part

  • @macmsiska2937
    @macmsiska2937 5 месяцев назад +1

    Amen

  • @FlorenceDouglas-x5c
    @FlorenceDouglas-x5c 5 месяцев назад

    Amen and amen 🙏

  • @HarrisonKalonga-k7p
    @HarrisonKalonga-k7p 5 месяцев назад

    Pajatu mcp akumamanga anthuwa akalankhula mumangesotu uyu ndi uchisiru wanuwo

  • @EdwardMguwela
    @EdwardMguwela 5 месяцев назад

    Mau achilimbikiso ndithu olo patatalika bwanji Koma chilungamo chidzafukuka mizimu ya anthu 9 simasewela Wina asavuka basi

  • @AustinManes-m3w
    @AustinManes-m3w 5 месяцев назад +1

    Amen 🙏 🙏 😢😢😢

  • @WarriorKB-u3k
    @WarriorKB-u3k Месяц назад

    Chikangawa ndi mcp amvele uthengawu

  • @chipiesato-ut7hx
    @chipiesato-ut7hx 5 месяцев назад

    Amen ❤❤❤

  • @PaulMwachande
    @PaulMwachande 5 месяцев назад

    Mwalalika zonveka wakunva wanva bolaso asakumangeni anthuwa ndioipa bambo

  • @SemuKachoma-i7o
    @SemuKachoma-i7o 5 месяцев назад

    My father.

  • @PephoMungomo
    @PephoMungomo 5 месяцев назад

    Anagawanadi zovala zake ndipo Malaya ake anawachita mayele

  • @NedsonMatia-f8i
    @NedsonMatia-f8i 5 месяцев назад

    Amen ntumik wamulungu

  • @HlupekileMazunda
    @HlupekileMazunda 5 месяцев назад

    Ine simmene ntima unandiwawila dzulo mpaka ndinazimitsa tv nkupita ku church ntima ukundiwawa ndinapephela pephelo lowawidwa ntima

  • @SteveChirwa-ne9nt
    @SteveChirwa-ne9nt 5 месяцев назад

    Amen !!!!!

  • @DorothyMikundi
    @DorothyMikundi 5 месяцев назад

    Amen.

  • @staffordchibambo6439
    @staffordchibambo6439 5 месяцев назад

    😭😭💯 amen and amen

  • @MaryMakungwa
    @MaryMakungwa 5 месяцев назад

    Ulaliki mbambande

  • @SmileMalanda
    @SmileMalanda 5 месяцев назад

    Amen🙏

  • @BENSONRANGWANI
    @BENSONRANGWANI 5 месяцев назад

    Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zache

  • @yamikanilukah
    @yamikanilukah 5 месяцев назад

    ulaliki wazifukwa

  • @nessiemfunie
    @nessiemfunie 5 месяцев назад +1

    🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏

  • @NafeAlie
    @NafeAlie 5 месяцев назад

    Zkm brather