This woman is well educated if u don't know. She appreciates where it ought to. Its difficult to fools to understand. God bless this woman and Malawi. Rest in peace soldier.
Muku mu thokoza Chakwera okuphayo wopusa ngati ameneyo,akuphani ndi Poison, Ali NDI poison ameneyo amafuna akamuphe ntanyiwa koma apólice Ku South Africa awagwira munyako kumeneko Ku Malawi ko,akuphani A MCP zigawenga
Munthu yekhayo amene amayankhula zanzeru even opanda script.
She is blessed
Koma Patricia, Mulungu anakupatsa nzeru. Mulungu apitirize kukupatsa wisdom
Zoonadi
Kwabas
That's the kind of speech I wanted to hear from mama Malawi.
God bless you Dr Patricia Kaliati
😊
Brilliant speech, may God stand with you Patricia.
Mother of Malawi good speech from your mouth kumutundu wa amalawi .thank you Patricia kariat
Good speech and deserve to be a minister .God bless
You are such an amazing woman,, full of wisdom this lady❤
Aaaah you're the monther of Africa, always you live great word's to your people
This woman is well educated if u don't know. She appreciates where it ought to. Its difficult to fools to understand. God bless this woman and Malawi. Rest in peace soldier.
Hon Mai Kaliyati alankhula bwino ndithu
ooohh that's great speech madam P. Kaliati... kuyakhula mwanzeru
Powerful and touching speech, mai kaliati, u r more than an activist
She showed the country that she is mature enough to understand and the times we are in as a country
Mai kaliati ndi m'bedu kapena mbambande ndilibe mau great words
Thank you honourable Patricia Kaliati for the great request to the president towards the bereaved family of Lucius Banda may also good Lord bless you
❤❤❤Great speech, taluzadi ndithu, Koma Ambuye ali ndichoringa, Soldier, Rest In Peace
Brilliant speech live and direct mama
speech yha nzeru uyu bas akhale president
Great speech mama kaliat
Haaaaa....Dr. Patricia Kaliati, you are such an amazing lady In Malawi.
Your wisdom, bravo woman
What a great speech, may God stand with you akweni
Courageous lady God bless you
This was beautiful speech 😍
God bless you mami pa speech yanu
May the good Lord bless you always mother Kaliati
Oyesss GOD bless you mami kaliat
A great speech Madam Kaliati
Good speech,,, congraaaa our mother of da nation
Brilliant speech akweni
Great speech by Mai Kaliati
Mai Malawi full of wisdom 🙏
Nice speech madam, RIP soldier
Rest in peace Soldier.amen
Best speech mama🎉🎉
Great speech.
Ili ndiye kholo...the speech alone yandilizatu😢
Mai wa nzero God bless you
Good work mam kaliart
Mzimu Soja Lucius Banda uwuse muntendere. Mayi mwankhula mwa chikondi
Wow great word
Mother of malawi❤
What a speech Mama
Amen
good speech
You deserve the respect
Ndimakukonda kaliat❤
Sorry for the loss.😭😭
great speech
Interellengent woman
Akuti speech yabwino. Ine ndindani oti ndizikati wapala
2 mbiri 7 and Amen mamie
Good speach indeed, back ground song though is annoying, was it necessary?
Rest in peace soldier
Great JB
Mu
UTM Bola atakutsankha uzakhale tsogoleri kuyankhula kwazeru kopanda mantha
Our kweni❤
Eshh akweni
Mwayankhula bho kupotsa mutsogoleri Chakwera
Ndipo straight
Kaliyati , your # 1 ndasimikiza lelo mmmmmm
May his soul rest in peace
Let God be God rest in peace Lucius Banda
Strong words
Mai kaliyati amatha mulakhula ayakhula funfo zoveka kwambili
Zoona.amai ambiri amathawa
Mai woyankhula zomanga uyu
Mai kaliati palibe chanzeru mwayankhulapo , mukuonetsa kuti mukupembedza chakweraemumupepesa chakwera ngati ndani galu ngati iye
😂😂😂😂😂 Osati galu koma garu wachabe chabe
A police akuona ma post onse😂
😂😂😂😂😂
Garu chakwera walakwa chani amalawi kaduka simuzaleka bwanji miseche mukadalinayo Iya.
@@LukaThawe ife tiribe kaduka ngati wakugula chakwerayo ndiye zako ndiwewekha ukuikirakumbuyo NCHEWA nzakowakuphayo ukati walakwachani iwe sukuona mene dxiko walionongera , sukuona nkhanza zomwe akuchita , pamutupako sooayends ndi chakwera wakoyo
Mai kaliati 🔥🔥🔥
Dzikomo Akaliyati mwayankhula bwino.
Kaliati amatha..............landilani ulemu.
akweni😂😂😂
Very illustrative speech especially coming from a vibrant woman indeed.
Zalowa ndale ....akweni ndi ku malilo ka
Udf yomweyo
Amen
Mayi kaliyati mwayankhula bwino kwambili mlungu azikudalitsani "zikomo"
Rest in peace soldier wa amphawi
Kaliyati ndi mamuna🇿🇲
Mais um inscrito no canal estamos juntos inscreve também no meu canal 🙏
Mayi wanzeru uku ndiye kuyankhula
Akweni akuoneka kuti ku utm alibe nthawi ya itali malankhulidwe ofuna kukondedwa ndi chakwerawa akuopsa
Chomathokozera chakwera ndichani nanu😢
Ironic bro.... Opposite words
Ukufuna anyoze kut ziveke bwanj
😅😅😅 amalawi
May kusiya zandale apo koma akweni anga mumatha kuyakhula chaka cha 2025 voti yanga ndi ajubanja kwanga tikuvotelani
🇲🇿 she is mummy
Mhsrip till we meet
Mwanakaz walankhula zabwino n ngat nkotheka tiyeni timveko kulira kwake
Akuti tisunge bata chifukwa choti malemuwa anali osunga bata
Mai Mai
Akweni ndi mzimayi osowa
Zikomo mama
Mau akweni
9yc one speach
Mum mwalakhula bwino .Plas pemphero lamphavu ambuye adalitse ndinu nomwe.komanso tipempha ambuye kut mzimu wa lucius upitilize kuwusa mumtendele
Chakwela anunga magazi
Muku mu thokoza Chakwera okuphayo wopusa ngati ameneyo,akuphani ndi Poison, Ali NDI poison ameneyo amafuna akamuphe ntanyiwa koma apólice Ku South Africa awagwira munyako kumeneko Ku Malawi ko,akuphani A MCP zigawenga
Uyu amayankhula
mwayankhula bwino mayi
Kaliati akudziwa chomwe akuchita
Nonsense
Inu nd mai wafuko kuyakhura mopanda matha ndpo osadodoma
Kaliati amatha
Ndatakasika nanu Aunt Patricia
Zovuta kwabas