May the soul of Soldier Lucius Banda RIP,One word Which We Suppose to Remember is To Keep on Knowing That We Are Here As Vistors, Any Time From Now Something Can Happen On Our lives.
Musazaneni zanzeru zanga,masazanene zakuchuka kwanga...ngati mufuna kunena zinthu mukanene kuti ndinali soldier kwa amphawi...muzimu wasoja uzagona..... Please respect his wish stop praising him in death as he wished
Tisiye nsanje,,nkukhala okondana.
Ndili Joz ine ndikuonela idzi lelo chotsadziwa Autse mutendele 😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢
😢😢 rip sordier mulungu afungatire mzimu wanu mwalimbana nako kulimbana kwabwino
Uthenga sukumveka accordingly as it is being poorly disturbed by the audiobackground..
Indeed the background music very disturbing
May the soul of Soldier Lucius Banda RIP,One word Which We Suppose to Remember is To Keep on Knowing That We Are Here As Vistors, Any Time From Now Something Can Happen On Our lives.
Discupa
Reduce the volume of the background song
Lulu kuyankhula mokhwima munzeru kwambiri , mzimu wa soldier Lucious Banda uuuse mumtendere
Rip sodger we will meet again in the other side
😢😢😢
Lulu wandiyankhulira bwino kwambiri mtima umeneu usausiye.mzimu wa soja uuse mtendere
Mzimu wanu Lucious uuse mumtendere mwatisira nyimbo zanu zophunzitsa munalidi munthu okonda anthu ena
I have been touched from his first album till today ,he has been and he will be my only BEST in Malawi when it comes to music...
MHSRIEP
@@CliveWhitman-rr9ew and he was an icon indeed
Popeza kunalembedwa kut cha moyo chilichonse chizalawa imfa ndipo aliyense adzafa ndithu ine ndingoti zimu wawo a soldier uwuse muntendele kufikila tsiku lachiweluzo lomwe tizaonane nawo abale onse amene atisiya munthawi imeneyi tiyeni tilire koma mwachiyembekezo
Bad eeeeeish
Mulungu awadalise kumwambako soldier
M😂ay he rest in peace
It means he was controlling lots of people
Rest in peace soldier
REST IN PEACE MY DAD SOLDIER 😭😭😭😭😭😭
The song in the background title please 🙏🏾
Black Jack title ndapita
Rest in peace
Ambuye atichitile chifundo😭
Musazaneni zanzeru zanga,masazanene zakuchuka kwanga...ngati mufuna kunena zinthu mukanene kuti ndinali soldier kwa amphawi...muzimu wasoja uzagona..... Please respect his wish stop praising him in death as he wished
Nyimbo zamatathauzo tizisowa
RlP
Anali ozichepesa kwambiri watimenyera ufulu.
Ambiri tamvutika mzimu wake uwutse mumtendele
So sad
R I P😂
Komawamwarirayo ndikatundu
Koma ma jacket okupsya waa